Sindidabweretse njala m’dziko muno – Chakwera
Mtsogoleri wa dziko lino Lazarus Chakwera wati njala yomwe ili m'dziko muno sadabweretse ndi iye koma zifukwa zomwe zachititsa kuti zokolora zichepe mlimi aliyense akuzidziwa. A Chakwera anayankhula izi pamene amatsegulira ndondomeko ya zipangizo zotsika… ...