
Elon Musk wavulidwa
Mpondamatiki Elon Musk, yemweso ndi mwini wa tsamba la mchezo la X lija linkachulidwa kuti Twitter, akusambwadzidwa ndi mai wina yemwe anamubelekera mwana koma sakumuthandiza. Mayiyu yemwe dzina lake ndi Claire Boucher koma amadziwika bwino… ...