Dan Lu ayanika mimba ya mkazi wake pa m’mbalambanda
Oyimba otchuka mdziko muno ndi nyimbo za chamba cha Afro, wazizwitsa mtundu wa a Malawi pamene wakhala mMalawi mmodzi yemwe waika zithunzi za mimba ya mkazi wake pa Intaneti. Anthu ambiri ati zomwe wachita oyimbayu… ...