Dan Lu ayanika mimba ya mkazi wake pa m’mbalambanda

Oyimba otchuka mdziko muno ndi nyimbo za chamba cha Afro, wazizwitsa mtundu wa a Malawi pamene wakhala mMalawi mmodzi yemwe waika zithunzi za mimba ya mkazi wake pa Intaneti.

Anthu ambiri ati zomwe wachita oyimbayu ndi kunyazitsa chikhalidwe cha amalawi komanso kulaura.

Oyimbayu yemwe watchukanso kwambiri ndi nyimbo yake ya “Sweet Banana”, adalimba mtima kuyiwala chikhalidwe cha ulemu cha chimalawi pamene lachisanu adaika dzithunzi dza mkazi wake Emmie Kamkweche koma dzovula mimba yonse ili padagu pa tsamba la macheza lija la facebook.

Dan Lu wautsa mkangano pa Intaneti.

Malingana ndi mwiniwake Dan Lu, yemwe dzina lake lonse ndi Dan Lufani, poti iye adachilimika kuyimitsa Emmie iye wati ali tcheru kudikira kuti akhale bambo a mwana yemwe akumuyembekezerayo, pamene awiriwa akuoneka okondwa zedi ndi kuyimaku.

Koma malingana ndi anthu ena amene akhala akuikapo maganizo awo pa tsambali, akuonetsa osakondwa ndi mchitidwe umene oyimbayu wachita poti wayalutsa mkazi wake komanso wanyazitsa chikhalidwe cha ulemu cha chi Malawi.

Malingana ndi macheza a pa gulupu ya whatsap yomwe Malawi24 yawona, yomwenso Emmie ndi mmodzi mwa ma membala, zaonetsa kukwiya kwa anthu pamene anafunsa mafunso mzimayiyu chifukwa chimene achitira izi poti pali anthu ambiri otchuka ndi a ndalama zochuluka mdziko muno koma safika mlingo uwu, koma mkazi wa Dan amangoona ma uthenga ndi mafunso koma samayankhapo kanthu.

Gulupuyi yomwe ndi ya azimayi okhaokha, afunsa Emmie ngati mimbayi ili yoyamba ndipo kuti ndi ndani uyo adapereka malango kwa awiriwa pa tsiku la ukwati wawo womwe udachitika mchaka cha 2016.

“Koma kudziwika kuli apo koma abale ulemu ndi ofunika, ndi ndani adakulangizani koma?”

Advertisement

1,002 Comments

 1. chitsilu ndi mkaziyo. iye angamalolere zopusazo. akuziyalusilanji.

 2. nothing bad @ all its just celebuleting as wel to everybody did whn he pregnate his loved one n if w can see vry wel to tht picture vry z nothing wrong i see on it even my kids i can show them

 3. palibe vuto pamenepo akunyadila mimba ya nkazi wake kapena kuti akunyadila mwana wake azabadweyo mukanena za chikhalidwe munama ndi chiwalo chiti chobisika wachisiya pa ntunda? mimba sichiwalo chobisika and this z not old days evrythng now z changing evryday mukafuna Zachikhalidwe muzikapanga ndi oyimba akumuzi not Dan lu ndi oyimba wapa town ameneyi simungafanane zochitika.

 4. ayi zawonjeza ife kumalawi kwanthukono zimenezi kulibe ndipo ine ndili ndi dzaka 29,,,,ndikuyamba kuona malodza ngati awa..nde amati anthu akawona nde atani…iiiiiiiii ayi ndithu mamawo zina bwezi akukanako olo kufuna kutchukako….

 5. a dan amanu adakati aziyika pantunda mimba yako adakawatengela otani?uwu ndiuchitsilu tisakambe mokunyengelelani mwana wobadwayo adzakhala otani?adzahadzakha

 6. MCHAWA UYU MIMBAYI SIYAKE TIZITI MONSE MUJA SAMACHINDA KUTI IKAKHALE MIMBA YOYAMBA? APA MPAMENE NDAKHULUPILIRA KUTI ACHAWANU AKAKUZINGANI MBOLO KUBELEKA KUMAKUVUTANI.

 7. MCHAWA UYU MIMBAYI SIYAKE TIZITI MONSE MUJA SAMACHINDA KUTI IKAKHALE MIMBA YOYAMBA? APA MPAMENE NDAKHULUPILIRA KUTI ACHAWANU AKAKUZINGANI MBOLO KUBELEKA KUMAKUVUTANI.

 8. Kuyaluka kumeneko mn ine ndimakufilani mm km izi zokha ndiye ndizausilu pa ntundu wa amalawi ngati kuno Ku cape town south Africa ndiye sizachilendo km kumalawi mwawonjeza mn km ndimakufilan zandinyasa ndizomwez

 9. Kkkkkk kuteloko amayi akewo sakukhulupilira kuti atenga miracle mimba pakana kumangowawonesa ndi ana omwe heheheeeeee kma kuti Hoooooooooooooooh

 10. This is bustard, Malawi ndi Malawi,u can’t charge like America, if u want go to America u murder fucker ,u showing kinds bad example

 11. Palibe chifukwa apa yose bho man D……
  Ogwirira azimayi ndi a tsikana osamawayika pamtanda sanya bwanji??????kusowa zodzudzula eti

 12. Enanu mukutanthauza kt Dan ndiopambana kwambiri km iyeyo alibe umunthu ndipo anthu podzudzula samaopa maonekedwe kapena chuma ngakhale kutchuka km zonyasa zakezo asamaike pa gulu bwanji atenge nkukaonetsa mako ake ndil ankaziyo

 13. Ngati amafuna kuti tisayankhule pa zolaula zaozi sanakaika pa public platform, akanakaika kuchipinda. Sikuti pakudzudzula nkhalidwe woyalukawu ndi jealousy koma kumukonza kuti asazapangenso. I for one have got nothing to be jealous about Dan Lu, he has lived a shameful life. I appreciate his talent koma mwaganiza mopelewera. Ena mukuti culture yathu ikusintha nde tizingoona zomwe zizichitika, asa! Ine nde ndikhala mmodzi mwa amene titamenye nkhondo yoteteza chikhalidwe chathu. Aliyense amene wasangalala ndi photo imeneyi ndiwachimasomaso. A well behaved lady can’t expose her pregnancy like that. Under the control of someone but not God Almighty. Go ahead and prostitute your bodies like that but know that Mkwiyo wa Mulungu udzaweluza onse opanga zochimwa ndi amene amasangalala nzauchimo ndikuzilimbikitsa zauchimozo. Think about the Glory of God before you act, write and say anything. Dan Lu is so immature.

 14. Inu mungoti nyonyo apa chikhalidwe chake chiti inu mimbayo mwampasa ndinu? Simesa ndiyankazi wake chimizi chani, ngati simmamfila dan lu khalani ife timamfila he is our seleb and to a seleb thats wat ayenela kumapanga wachimizi khala ndichimizi chakocho we love u dan lu big up

 15. Malawians mind ur own business. This z life of celebs.maybe it was just a photo shoot featuring a certain magazine.mudziyamkhula m’mene mungatukurire dziko lanu instead of minding other pipos business.

 16. Akuziyetsa dolo coz wapereka mimba????mmidzimu mphwanga muli ma memba anzako ali ndi ana 11 koma samatumbwa choncho,,,,watch out

 17. tazilimbanani ndi george chaponda wakubelani ndalama za chimanga uja,musiye dan lu ndi sweety banana wake ndi sweety banana junior!muneneni momwe mungathele koma muzigonabe ndi njala

 18. Inu musamuykire ku mbuyo ndiwausiru uyu amadzimva, we r Malawianz not Americans, mwina ndikuyamba kupanga mimba, akunyaudira ndani? Chachilendo nchani apa? Ifeso timatha

 19. It’s time of division and union in specific divisions.Of the same feathers flock together.24:15 Joshua,life is full of choices depending on both spiritual and physical realms we are present.

 20. Ngakhale ndapeza nkhaniyi anthu muta commenter kale ineyo mbari yanga ndineneko Bambo Dan ngati chili chamba pepani mwayalutsana nazo komanso Mmene wapangila apapa mmmm ndukaika ngati umaganiza mwaumunthu, ndipo mwana angakupose , Iweyo chachilendo ukuona kuti ndichani chomwe wapangila zopusazi? ngati umaona ngati upitiliza kutchuka apa nde wapusa, Taona anthu ife osati nyasi zanuzo, kapena unadya chamba chambiri sumadziwa kuti u kupanga chani? Koma simudzachiza nokha akazanuwo uchitsiru wake umene mwaonetsa apau, bola mawa musawauze kuti ayende mbulandatu akaziwo, Muyaluka nazotu zakupezani mochedwa Eti ndinu Achitsili mwamva Abambo inu Dan

 21. Ziwanda bansi., uchisiru.,chamba,mowa,ma drugs,pansi pa nyanja/usatanic bansi…..thats stupid a dan ndi kachibwenzi kanuko nde mukuwawonetsa ndan…. alipo samaiwona mimba ….nde mukufuna ife tikaiwona mutitani mutilowetse? Munya mukawauze amene akutumaniwo..zamanyi.,…!

 22. inu aulemunu osangokhala bwanji mwangotengela matchasi bwanji mwinaso ndi olowola munasonkha nao pangani zanu mwanandiosowatu kena tizatokota za inu zachikale basi

 23. amalawi kusowa zochita ….chukukhudzani nanga chani ….mukhala ngati mimbayo wayitengela ku lodge bwanji ,mesa ndiyanyumba mwake……

 24. To be honest i see no problem with that plus they are not the first malawians to take pictures of the baby bum . Its art abale plus memories to their new born . Get a life

 25. Idk why most of yall fuzzing about those pictures anyway…..to some of us they are normal and we dgaf.. Koma enanu kuzitengela pa mwamba!!!! Malawians thou.. Am done with yal!

 26. kodi anakwatira hule? eeeee ndikuvera pompa koma anachita bwino orongosoka ndi mahure omwewa or diamond anapangaso zotezo mkazi wakeso wa ku Uganda kumuonetsaso mimba pambalambanda

 27. A Malawi mmene Dan Lu mu nyimbo yake ya sweet banana kuti ”Umakwanitsakwanitsa”inali clear evidence that he practise what he sings!!Majority ya anthu omwe akulimbikira za culture dont dare to practice even abit.Its high time we embrace to precipitate what we preach.Malawians were just very good at formulating intelligent policies but we always fellow to summit them on ground.I remember one time when Bingu was ruling kunabwera ma officials ochoka mmaiko ena a SADC like Unganda,Kenya,Tanzania etc kudzaphunzira how FISP is run,mukaunika mmaiko amenewa njala ndi mbiri yakale chuma chawo ndikumakwera pa mene mphunzitsi malawi angoloshoka mu umphawi mkumati kodi mphepo ya elnino yo amangokatha ife tokha nanga Zambia inakolola bwanji oti wealther pattern is almost similar.Conclusion,lets practice what we preach,tisathamangire kudzudzula eni pomwe iweo chi log cha baobab tree chili maso mwako kuti neng’a!!!!

 28. Whether u say kut its uptown, ndi Celeb, ndi wandalama, wats our business, ndife achimidzi, we shud get a life bra bra bra,, shootin a photo with his beloved wife is not our problem, my concern z y showing us the baby bump like that? We all know wat it looks like. If he wants to create memories then thats simple, take a photo of his wife and save it in his handset. Why showing it to the whole world? Tikaona titani nazo?

 29. Zonyasa,zonunkha ice kwathu kulibe zimenezi a Dan mukuzitenga kuti nawenso mkazi iwe ukungoselera zilizonse nonsense zanuzo ukooooooo

 30. ambuye yesu bwlan .athu.avutaa pamalawi . ambuyee athu akukuiwalan chifukwaa chan.moyo mumapelekaaaa ndinuuu. ambuyee chikond chanu chapamwambaa kwabax eeeeeeeee. thawi.yakusaziwaa mulunguu analekerelaaa

 31. Akuti “amalawi nsanje ikukuvutani” munthu ungapange nsanje ndi ziwandazo?
  Kuli Anjiru Fumulani,Mlaka Maliro,chizondi onsewa sima celebrity?
  Sanawapatsepo mimba azikazawo?

 32. Amalawi mumayamikila mzanu akamalakwa ndiye mumakondwa.apa dan wankoza?uyu muuzen kut walakwa ndipo linakakhala mayiko achiluya anthu awa anakalandila chilango chowawa ndi kupusa kwaoku.amalawi uwu timat uchitsilu obadwa nawo.

 33. Ma PLAIN
  ma plain
  ma Plain
  ma plain
  ma plain
  ma plain
  ma plain
  ZIKUCHITA KUONETSERATU KUTI APA PANAFA MA PLAIN.

 34. Is nothing to talk about ,,,,mimba yamkaziwake kodichimidzi chimakupwetekani eti guys ??????? Talowaniko maiko anzanu izi sizachilendo kwa anthu akunja guys be serious about this things ur posting big up Dan lu

 35. Amene akuti Dan lu wapanga zazelu apapa ndi chitsilu chamano kusi ngati mbuzi,anthu ngati amenewa amayenela azionesa chitsazo kwa anthu osati nyasi zopusazi.2 mkaziyo nayo nzelu alibe akavale choncho osazilemekeza mimba kungoyisiya pamtunda ngati fodya kukanengo poyitanila Malonda,respect ur self first then people will retain respect to u.

 36. Dan yu sikuti walakwisa ayi,izi ndi zomwe ma cerreb amachita ndipo ngati ndi ntchimo atha kukhululukilidwa, palibe nkhani apa,ntchimo koma ili wapanga Chaponda, nde ntchimo lalikulu loti nkovuta kukhululuka pokhaulisa ntundu wa a malawi ndi njala.EMMA & DAN keep it up,kwasala ka blue move mutioneseso,nanga tizingona mimba yokha?

 37. Azimayi enanu amene mukukamba nawo nkhaniyi mumavala motani mmiseumu? Mabere akumakhala pa mtunda yet you are condeming this? Be not the first to cast the stone!

 38. what Dan Lu has done is of course out of this country,, Koma guys lets be honest Malawi culture ikutha pang’onopang’ono,,anzanga amene mukukhala mu town mundivomereza ,,zimene akuvala atsikana ndi azimayi athu mtownimu is that Malawian culture? He is wrong yes but pliz dont over judge him coz nanunso mabvuto muli nawo munyumba mwanumo,,luk @ the way ur relatives or urself dressdoes that show someone coming from God fearing nation?amalawi tinatayika basi tivo,,

 39. nanunso a Dan timakuonani ngat ozindikila koma shaaaa!!!!!Chabwino komatu mwayaluka potengela chikhalidwe chakuno,ndinu munthu oyamba kupanga izi mu history.Koma sitsatila khalidwe mwayambali coz ndizacbwana hevy.

 40. End times. i wonder kuti abusa awo olo aku church atawona zimenezi anati bwanji. u celeb uli apo koma i dont thin anthuwa anapita kuschool. coz munthu oti anaphunzirapo sociology zimenezi sangachite. chitawonicho chili apo i think they need to go back to school to some concepts on how we shud live in a society. Ngatiso abusa awo ali ndi uzimu he shud counsel both of you.

 41. Za usavage bax umbuli si dhilu watokhala oyamba ndiye kubeleka amene mukut chimidzinu mimba xanu muzidzayenda nazo pantunda osangovomeleza kut we are malawians bwanj umphaw uli thooo muno kumafuna kukhala ngat anthu akunja andalama

 42. Pachikhalidwe cha mmalawi muno,mkazi olo atakhala ndi pakati zovala zinali kachikopa kongobisa maliseche,kodi ndekuti mimba imabisidwa pamenepo? Bwelelani mmbuyo a Malawi nde muzilankhula zopusa zanuzo,tsweeeeeee!!

 43. Let the man be it’s his wife not your wife so why are you making a big deal out of it Tjooo my fellow Malawians please learn to mind your business…Just go get your boring wives pregnant so you can post it as for you Bitches who are talking shit it’s just because your jealous maybe Dan fucked you and dumped you some time back a Malawi muzafa yopolama maliro anu azativuta kuongola

 44. kungoti mkuluyu wakula moyo wovutika kwambiri.panopa angowona ngati ndi nthawi yake yoti athamangisane ndi dziko.ngat anafika pozola yelesa.

 45. Muzapanga comment zinthu zoti zijuchokera kwasatana amalawi ndichani???? Nawo adan lu panyapawo mwamva osamaika mimba zotoporazo pa air nudxabereka naxo slippers cox anthu anakhwima kunja kuno akhoza kukuchesurani uchitsiru mwapangawo

 46. Mmmh kkkk kma guyz amalawi tinapitadi mukati ayi poti anthu akumavura bola kuvurako cos sakuvura mimb yoti mulimwana ndichibwana chaxhikulu chimenecho sinsanjenso ayi kma kumumvera chisoni cox chinthu chomwe wanyamulacho sigaluyi kma munthu en akhoza kupeza nazo tsoka kti mmalo mobereka nkupititsa padera cox sikuti mulungu akusangalatsidwa Nazi zomwe wapangaxo enanu mukuti ndichimidxi amalawi mukuzinamiza nokha inunso bwanji mimba zomwe munali nazozo simunaike Pa air kuti anthu azione bwanji??? Takharaniko ndinzeru inu osamangiti poti mwasirira nkupanga comm

 47. Koma ngati uli u Celebrity ndiye kuyalusa nako makolotu. Basi makolo a Dan Lu ku mtima mbeee mimba ya mpongozi wawo ili pamtunda. Malaulo.

 48. Sanachite bwino zawonekelatu kuti osewo ndi mbudzi komaso mimbayo ndi ya ena ikanakhala kuti ndiyake akanamupasa ulemu dona wakeyo.Komaso samamukonda mkadzi wakeyo,kaya adziwona wakula watha.

 49. Paja a Malawi kudziwa kulankhula koma kuti mupange mukulephela, kudziwa kuzuzula koma kuti mukhoze mukulephela, this shld not be story kuti muchuluke nzeru, everything is for Dan just leave, takambani za cashgate, kuphedwa kwa ma albino, maizegate etc, inunso a Malawi 24 mutanthauza kuti inu nde achikhalidwe? Azikazi anu sakhala ndi mimba? Anthu sadziwa kuti mwawapatsa mimba akazi anu? Vuto anthufe timakhala busy kuona anzathu kuti akupanga chani kusiya zanu, what Dan has done can be much better than enanu mukuti fwi! fwi! Uyu wabwera poyela apa koma inuyo you can’t do it.Aaaaa a Malawi tasambani mmaso mukukhala ngati mwamugwira ufiti hiiiyaa! Ndapita ine

 50. forget about it this is no news you guys are doing far much worse thing when night falls, now write somethings that will help this miserable nation where all necessities of life are scarce ,you know sometimes i dont think chilembwe deserves credit for fighting against colonialisnm he was one hell of a stubborn fool who chased the british even before they had developed this country,we should have chased them now imagine how malawi would have been?

 51. Dan lu sanalakwise. muli buzy kumanena kuti akuyuza ma drugs komanso wataya chikhalidwe chachimalawi mmalo momaona zovuta zenizeni zoipa? mukukwatilana amuna okhaokha komaso akazi okhaokha, mukupha alubino komaso kumataya mimba nkumamunena munthu amene akunyadira mimba ya mkazi wake kuti wataya chikhalidwe? bravo dan

 52. Makolo ndi akumpingo akuti chani?
  Tisamangoti celeb celeb apa zisanalongosoke…inuyo mwabalabalapo,mwakhalapo kapena akazanu kukhala napo pakati ndani anaonesa?kodi 21century ndiye tizitero?
  Mukati tikusiya mavuto athu ndiye kuti chani?.mavuto samatha tinawapeza tizawasiya..komaa izizi izi zikonzedwe zomaonesa chinjazi…anthu amabala at old age samapanga choncho.zalakwika…kukhala ngati zachilendo zamimbazo? Asaaa!
  Afunika mlango….

 53. Kd enanu mukut DAN ndiwandalama mukuganiza kt ndalamazo zimamuuza kt azivulana? Kmaso mahule ntchito yao ndi uhule ngat nkaziyo akufuna kumavula ngat mahule azivula choncho kmaso enanu nkaziyo mukumudziwa kt anakatengedwa my bar ndizosadabwitsa. Iwe ukt ndiwandalama kapena ndiozindikila uwelenge bibble uve zanowa mwina utseka MAU ako opusao

 54. Mimba imeneyo ndchta kulowa #FISI nde lero akamabwera poyera ndmimba yopeleka ine ndingodabwa,,,mudkre mwana wobadwayo Angozo enieni!

 55. Which malawian culture are u talking about coz zitenje ndi zinazo ndiye zochokela kwa azungu,if u thnk he z wrong u mst put a pic of our foregrandmothers wearing a chitenje during pregnancy or in anytym,

 56. What’s the matter with you people, while you just indulge in other people’s happiness. I don’t see it wrong, The couple is just jovial for their gift of the baby and then is this what you’ll condemn them. Your just pathetic. Useless writers.

 57. Culture is important please don’t take outside things especially in Malawi you like cope wat ever you see in south Africa you bring it in Malawi you don’t have your won culture Malawi change

 58. Iiiiiiiiiii koma anthu kumalawi muli ndi vuto moti mudzipanga zanu muli busy kukamba zazanu, ine ndesimkuona vuto linalililonse masiku ano ndimene waimvelera komaso ngati zikukuwawani musamaone mudzitsizina basi. Asiyeni apange zakufuna zamoyo wawo ma pics amenewa ndawakonda kwabasi ndipo ndasilira next time ndiine ndi hubby wanga nafenso tidzaika hiyaaaaaa. Inu mudandaula bwanji poti ndalama zomwe alipila photographer ndi mzawo data yomwe amagwiritsa ntchito ndiyawo komaso mimba ndiyake sanaike yanu zomwe mukuyankhulazo ndiza ziiiiiiiiiiiiiii

 59. Kkkkkkk wanzeru amangokhala chete nkungopsyinyira diso tikanena kuti ndizabwino ndi uchitsiru bwanji osamagwirana mimbazo mzipinda mwanu kkkkkk koma yaaa dziko lithe basi akatiweruze

 60. Bvuto lanu ndichani agalu inu tiziwalo tazipsyera ndikuda tikuyanikidwa mmatauniti bwanji mulibe nthawi yoyankhura zimenezo mkumalimbana ndi Dan Lufani bwanji

 61. Mmmm kayandife aphawi, kma ku mwamba kulibe kuti uyu ndi ochita bwino kapena osawuka,tonse tikakhala chimodzi-modzi ngati tichitabwino panopa madziko la pasi

 62. Imeneyi ndi imene munaona kuti ndi nkhani yoti mulembere mtundu was a Malawi? Mukanalemba z kubedwa kwa ndalama ,ogula chimanga zija the better. But wasting ur tym and resources writing this? U r all useless…

 63. Enanu mukulimbana ndi #Dan Lu kamba kawu mphawi munaka khala mulikathu sibwezi mukulemba phusi zanuzo, Chinaso kusayenda muthu ungo khala ku mudzi uko uziwa bwanj #Life muziyenda muziwona muthu wawonesa mimba mukuchita kutha mawu chochi nanga atawonesa zinaz mupitila kwawokoko eti?

 64. Pachikhaledwe cha amalawi
  ndi uchitsilu kapena kuti dan
  ndi ozelezeka mu zelu zache
  zotendelazi kumaziwona
  kenako ayenda mbolo pantunda mwiniwakeyo sinanga aliyese
  alindi mbolo kumango cop chili
  chose mupusa nadzo adan lu

 65. Kamuzu Banda ananena kuphuzila si school yokha mudziyenda muziona zimene anthu ena amapaga it not about cerebrity izi amapaga aliyetse ndipo amapita ma mall azimayi mimba ili patunda palibe chachiledo amalawi

 66. Amalawife chikhalidwe chutionetsa umbuli pena pake dats y tili otsalira zina zilizonse sindikudziwa mukadzapita kunyanja kukaona mmene anthu amavalira akamasamba mudzalemba zotani . kungowonetsa mimba zowona ikhale nkhani ? shame

 67. Ano ndimasiku otsiliza zikuynla zichitike yesu watsala pang’ono kubwela azaweluze ziko lapansi.ndipo izi muzionazi zikuchepa muona zina zoposa zimenezo.

 68. Eeeeish Opita Kujando Ameneyu ! Hmmmmmm Ukufunik Kument Iwe Ndi Mkaziemweyo ! & Akakuvinilenis Litiwo Mwawnjeza Asease Mukuzimvacha !? , Hmmmm Usayalutse Achawa Mwanaiwe !!! Mapaziako Ndithu Kumeneulik !

 69. a Malawi mmalo mot tidzikambirana mmene tingathetsere umphawi basi busy kumakamba za munthu oti zake zinayera , kod mukut chikhalidwe nd miyambo ingat yomwe inasithidwa kamba kwa kusitha kwa dziko, be civilised guys and get life munakagonabe eet, komaso inu mmat a Malawi 24 mwasowa chochita? ngat nd choncho ubwere udzakame agalu kuno, as a matter of fact malawians learn to mind your business and some things beneficial #TeamDanLu

 70. Ine sindikuona vuto pa nkhani iyi, moyo unasintha and tiyenera kudziwa kuti zofuna zanthu sizofuna za anthu ena, kwa amene ayenda ndikudziwa moyo andivomeleza: moyo wa kumudzi ndi mtown ndiosiyana kwambiri and Dan lu, ndi celebrity, komaso ndimunthu yemwe zonjoya amazidziwa

 71. Chonde wina aliyese kuno kwathu akakwatiwa kapena kukwatila amapasidwa ulemu kusonyeza kt alindimwini ndipo ziwalo zina amakazionetsa kwa iwo okha awiri buc ,Vuto ndilot ena mwainu simumava malangizo ngakhale chikhalidwe chakuno kwathu kumalawi .Mabanja ongotengana opanda akuchimuna ndiso akuchikazi thats wy amat muzipita kumudzi kukaphuzila chikhalidwe kmaso vuto ndikobadwila kd nkaz waumunthu angavomele kumupanga zopusa ngat izi pagulu inu ovomeleza zopusa ngat izi ngat ndikukapempha kwa chitsilu chanuchi pitan chabe kokapemphako osat kuvomeleza zauchitsilu ngat izii

 72. zachita kuwonekerathu kuti inu a dan lu mukamuyanikaso mkaziwanu kokachira mwanayo kodi amalawi akazakuwonetsani mkaziwake akuchira mwana mwanayo wangotulutsa mutu make akumva ululv woopsa muzachilandira bwanji? tingothokoza malamulo amakhala kumeneko ndithudi akanazachita ichi. masiku omaliza kaya tsoka kwa okwanilitsayo.

 73. DAN LU CHAMBA CHA KWAMERECA,NIGERIA, MOZAMBIC NDI KUMALAWI CHAKUPANGITSANI KUYANIKA MIMBA YA KAMKOTA KANU KAYA GANJA WAKE NDI WADZIKO LANJI MWAVULA NAYE CHOTELE KAMKOTA KANUKA.

 74. abale banja mpaka pamenepo? mwati liri ndi ankhoswe limeneri? ndi ife tomwe aku word apart tawonanawo a Dan Lufani Kuvula malawi kumeneko nyasi zimenezi mwakazitenga kuti? koma dzina lamulumgu limatchulidwa mubanjamo?wina nkumati ena amayenda ndi panti yekha mtauni mu mahule anuwo mumawaona nokha kutaliko tikukamba apa ndi banjatu koma wavula amayi ako iwe!! mwati mkaziyo sanakamutenge ku bala koma uwu ndimuchitidwe wamahule osati inu amabanja kutukuka tinene uku malawi mukufikatu pa sodom ndi gomora ndife amodzi amalawi kuno si ku america kapena ku india kuno ndikumalawi mulumgu watifulatira and mzimu wanu ulikuti nonse mukusapota zoyipazi aliyese woti mzimu wamuchokera azatenga chinthu chonyasa kukhala chabwino CHENJERA IWE PULUMUKA NDIMOYO WAKO usachimwe poganiza.

 75. Kkkk mmm alawa! !!! Palakwika chani apa kodi mesa nkaziyo ndi wake? Kodi ngati mukutelo pa izi kuli bwanji mukanamva zoti Dan Lu ali wakhapidwa mutu kuchigololo ali muchipatala mukanakamba ziti??

 76. abale banja mpaka pamenepo? mwati liri ndi ankhoswe limeneri? ndi ife tomwe aku word apart tawonanawo a Dan Lufani Kuvula malawi kumeneko nyasi zimenezi mwakazitenga kuti? koma dzina lamulumgu limatchulidwa mubanjamo?wina nkumati ena amayenda ndi panti yekha mtauni mu mahule anuwo mumawaona nokha kutaliko tikukamba apa ndi banjatu koma wavula amayi ako iwe!! mwati mkaziyo sanakamutenge ku bala koma uwu ndimuchitidwe wamahule osati inu amabanja kutukuka tinene uku malawi mukufikatu pa sodom ndi gomora ndife amodzi amalawi kuno si ku america kapena ku india kuno ndikumalawi mulumgu watifulatira and mzimu wanu ulikuti nonse mukusapota zoyipazi aliyese woti mzimu wamuchokera azatenga chinthu chonyasa kukhala chabwino CHENJERA IWE PULUMUKA NDIMOYO WAKO usachimwe poganiza.

 77. ineso ndilondoleze ndikodzele peni penipo ibwele mimba ine nde azangovala bra ekha mimba pambalambanda ntaikumbatila nkulemba kuti ndaika nthanga zanga

 78. Tumizani aboma akamange waphwanya lamulo chikhalidwe mpaka liti?? Mudakauzabe Ana anu kuti mwana amagula eti?? Inuyo Pangani zanu naye apanga zake basi

 79. Zoti mimba ndiyobisika anakunamizani ndani?ndipo pali zifukwa zimene eniwake apangira zimenezi,woimba muchenjere naye azakuimbani nyimbo,zasanje ayi malawi nde zimene amapanga akunja ife tingalephere chifukwa,ngati mukusalira ndinu ife tikupita

 80. bola poti mimbayo ndiyake pankazake,achikhala ili ya wina ndichibwenzie mudakalankhula motani?zathupilake,zakezomwe izi!!

 81. Mmmmmmm é fool doth thnk h z Wise bt é wise man knws hmslf to b a fool!!!!! they r stpd indeed ine nde cndngasekerere nyasizo Entseeee!!!!!!!!!!!

 82. Palibe Cholakwisa Apa Bora Akanakhara Mkaz Wanu Zikanaveka Ndiye Pot Ndikaz Wake Zakuvutani Mlibe Manyaz Agalu Inu Achabechabe Osangolemba Za Chimanga Bwaa Chija Amat Agura Kuzambia Lili Bodza Chosecho Agura Momuno Ndiye Dan Lu Ndiufulu Wako Iwoso Ngat Akufuna Athakukapanga Bola Akhale Akaz Awo Muisova Khobwe Sinyemba Agalu Inu

 83. Malawi’s civilization,where is it?instead of finding lasting solutions eg to the cash gate and maize gate like other countries did to solve their problems eg Egypt they inverted shaduf machine that helped them doing irrigation, what can Malawi benefit from this immoral behavior u call it civilization????

 84. Pali chani APA anthu akuyaluka kuyenda maliseche ndiye muziti wanyozesa Malawi hahaha mwasowa zolemba eti yendani mizindamu muwone kuyalusa Malawi…kkkkkkk wamwa utobwa iwe eti

 85. The issue is ‘kulimbana ndi a x wife’ sipaja iwowo anakamba zambiri banja litatha, mpaka anati dan sabeleka,so this is to prove her wrong plus kumuwalira

 86. I think dis pple from Malawi z very schupit//am syng I think oky!!kod mwamuonera nkaziyo pano kulemera kuli ndi njira zambiri so dre z no one can judge afrnd hre undy de earth its only god//so some of u u r judging “Dan luu” y ?

 87. Wachita bwino akunyadila pakati pamkazi wake. Ndizonyadilitsa anthu akukwera achina sapitwa koma osatheka ena kumaliza mitengo kumwa gondolosi, mthubulo,zimswa ndizina zotelozo komabe osatheka

 88. To those ladies who are saying there is no problem with that have u ever done that before during your previous pregnancies? Or u are just saying coz dan lu is acereb?tisalankhuleso mopsapsalika apa zomwe apanga anthu awili awa ndikupepera kapena titi kuzerezeka kwenikweni. Alawula ndiwo kukhala ndimimba?zathu akamapita kuphompho ndi bwino kumubweza .ngati awili awa sakuwona vuto pa izi ndekuti mkutheka mitu sikugwira bwino ntchito . M

 89. Mmmm e’ fool doth thñk h z wise bt Wise man knws hmslf 2 b a fool!!!!! they r stpd indeed ine nde cndngasekerere nyasizo

 90. Amene zikumunyasa atseke maso asawone zachimizi basi ngati ena akuenda ndi pant malawi momuno kukakwela ndege mimbaso ndichani plz plz learn tu mind your on business

 91. What brother Dan Lu has done to his wife is morally bad ,and can not be encouraged in Malawian cultural platform, Any society has its own culture and social morals. There is every need for celebrities like Dan lu to help in selling Malawian culture to the world at large. Women in Malawi is
  the national asset every body should be proud of .

 92. dzikoy yinali yogona no wanda kt zili chonch nde anjatchuwa akapita nkumaona anjao openya nawoxo afuna kutionesa kuno.watinyasa bwanji!! Arthur Wachibwibwi Muongola Felix Nyirenda Foster Chibayeni Morris Jossia Ownery Tabia Juvinali Aubrey Ansomba Wamoyo Evance Njanji Winnie Mafunga

 93. Vuto lokwatira maHure .. Makolo akamatirangizatu penapake zimaoneka ngati akutikhomerera..lero ndizimenezi mukupepera kuyalusa makolo..

 94. Fuck you Malawi 24 im not even going to open it surely this is nonsense and so uncivilised very stupid u should rot in hell u and whoever else wrote such stupid articles let the man live tf?

 95. What’s wrong with that?Amalawi kuyalusa kuli pati?things are now changing. for example, kale kunalibe zoti amuna azipelekeza ku sikelonndi ma spouses awo.panopa timapita nkumakaimba ndi ma pregnant mothers .Ndiye munthu alekelenji kuwonetsa chikondi kwa wokondedwa wake.More over pamenepa he has demonstrated to others how to show love to our spouses. Mumafuna azibisa zoti Ali naye wake? MAHULE NDI AMENE ZIKUWAWAWA.MNZANU WAKWATIWA NDI mamuna WA CHIKONDI.ine kusilira.

 96. Ndatsatira macomment koma ndapeza kuti ambiri mukukondwa ndi khalidwe la mchawa mnzanuyu ndi mbuzinso zosadziwa kathu nkomwe, inu a Dan lu olo mutakhara nawo pafupi mungawatenge ngat mutu wawo umagwira boh? Tiaana tokulira mwa m’baluku mbuzi zeni zeni ngatinso mimbayo athira ndi iwo pomwe timabatile tidauma kalekale ndi chamba. anthu apeleka mimba mmidzimu osat kwa achawanso ayi! mwana wa Abusa?

  1. inu ndi dan lu mungafanane ?? zinazi osamangoyakhura ndi cholinga choti anthu akuveleni end khani imene ili apa ndi yamimba achawa yawakhudza bwanji ?? kodi iweyo kaya ndi nchewa kaya ntumbuka kaya mati alomwe what ever kodi amako anachita kusakha mtundu obadwira kapena anangozindikira kuti abadwira kumtundu wakowo. ndi kakhala ine sinasakhe nabadwila kuchiyawo ena amati mjomba ndipi ndilibe nazo vuto koma tichexere bwino ife zamitunduzi sitikonda kunyozana zili ngati chilema. uchiphwisi wakowo uwone kokapangila wava ndipo usayelekezeso kutchula zina lachichawa pano mboli yamako chupit mwana wahule sorrytu ndangotsuka nkamwa guys

 97. Malawi24 get a life.
  Zimimba zomwe timawona minsewumu bwanji simukamba kathu?
  Dan Lu ndi mkazi wake ndi anthunso ngati simukudziwa ziwani lero.

 98. Iyeyo iz it his 1st mariage? i think w nid reason bfore doing something, zitachitika kut mkaziyo wapita padera azanenaso? wwhat childish iz

 99. Kkkkkkk eeee malawi the warm heart of africa ???uzatitumizilenso live pic akubeleka nkaziyo man lu wayamba bwino ichi timati chitawuni anyamata ahipap??

 100. komatu ine or chitaunicho mkazi wanga sindingalore kuchita zopusazo .thupi la mkazi liyenera kupatsidwa ulemu.ndiye popeza akazi owatola ku pub nkhawa anapachika nde mapeto ake ndi izi

 101. Dan keep it up akutelewo sanayende ur true a hero palibe anawonesako luso losilika ngati ili ur the first kufa mwana ndi thawi osati coz of display the pregnass za ziii tizingosalila awonese che lufan asakufuna akakolope nyanja Ku salima

 102. Kkkkkkkkkkkkkkk Malawian are funny people what’s wrong but you give delivery woman mwachonsetu anyamata akubereketsa azimayi mzipatalawo

 103. Do u know why people(malawians) dont post pregnancy pics? Its because mwanayo sanabadwe ; Nanga atabadwa wakufa or kupitilira or kupanga miscarry muziti chani anthu mwawulutsa ku Dziko lonse lapansi? Malangizo kwa mayi a chiyembekezo ndi awa, pitani mukafunse malangizo okhuza masamalire a mimba kwa azakhali anu ; bambo Dan Lufani awongolereni akazi anu moyenerera mimba ndi chinthu choopsa mwina bwezi mukumati pano mukutsara kudya ndi kupembezera moyo wa mwana ndi mkazi wanu kuti achire bwino ; Langizo lomaliza muchite break kweee muyende mosamala musamusemphe mwana meaning khazikikani mwakula

 104. Akunama Dan palibe cholakwika APA iwe ukunyadila chomwe wanyamula mkazi wako Iwo akazi awo akakhala oyembekezela amawabisa go DAN GO ndakunyadila

 105. Ma celeb akumalawi ofoyra . Just bcoz diamond expose his wife pregnant on internet nawonso ati ayesele . Manyaka amunthu thats wy malawi sakutukuka copying everything just bcoz kuti usawoneke ngati osalira . Osangovomeleza bwanji level yomwe muli ? Diamond znt ur size . Wina ndi uyu just bcoz trump said that he will make america great again nayenso ati basi he will also make malawi great again kkkk malawi uzafa ndi mtima .

 106. Kodi mesa mimbayo ndi yake? Tsopano ife chikutikhudza chiani? Ifenso tili ndi akazi anthu, nawonso akazakhala ndi mimba kaya tizatani zizaoneka patsikulo

 107. Looking foward to the malawi in 2030 wen maybe news will be news and malawians will have better things to critisize and have contempt for rather than other ppos endevouirs.

  1. Blacks are not backward people they do things according to the black values the only problem is that you are comparing black people with Europeans which is not good let black people be directed by black values not European values we are black lets accept that we not Europe lets be unique and be happy with our culture lets avoid copying what Europeans do coz its according to their culture aswel lets accept the fact that we are black and we are Africans #pan-african.

  2. Stain Chigumula now thats a lie????? blacks especially from Malawi we always talk about Culture….. Things that agogo awo a agogo awo used to do in ignorance…. Be civilized, even every App or Cars keep updating, i remember kale even munthu wankazi akavala trouser kumayenda mu Town anthu amachita kumukuwa mostly ma Vendor ati hule……. Even a mini skirt mkazi ati asavale……. People please

 108. Bvuto lokwatila mmalo omwela mowa ndilimeneli kumuza ichi amangovomela mutu unabaiizika kalekale I tink mkazi wanzeru zake sakanalola kuvundukula mimba nkuisiya panja. Akanaibisa betele.

 109. mwaika ma comment omubakila nonse ndi zisilu inu olo mai anu anayamba atachita izi koma muli ndi uzimu inu? Kapena nanu ndi chiwanda ngat Dan lu osamaombela mmanja zilizonse agalu inu bwanji inu azikazanu simawaika pa air ? Tizit simunakwatile inuyo zonsezi ndi zosala ulemu ndi chikhalidwe ndie zofunika komaso munthu wa moyo aziganiza za umulungu nanga apa za umulungu zili pati?

 110. Aliyese alindichisakho chake chimene iyeyo akachita amati zilibwino ndeye athu tiyeni tichepetse kupanga zawina tizipanga zathu zimene zingatithandize Dan lu ndichisakho chake mlekeni

 111. mmh malawians know how to exaggerate… i see the comments are filled with hatred, Dan Lu has done something bad yes bt this is not how you can correct this, zalowapo nsanje apa tisaname though dan lu sandisangalasa…. ambilinu mukuyankhula zausilu apanu mumavulilatu maliseche bolaso apa, kwangosala siku loti muzayaluke lachi 40.

 112. Iwe mavutoakondi chani kulemba nkhani yolusa ngati imeneyi.. Mind your own business. Lembani nkhani zenizeni apa osati zopusa ngatiizi… He is a Celebrity what did you expect… hahahahahahahaha Pambalambanda pambalambanda chani..?

 113. Opañda nzeru inu mukubakila nyasi izi…….maiko akunja alindi chikhalaidwe chao kunoso chthu bwanji ngati munkoña kuti ndzofunika osawauza makolo anu aziika nyasizi APA…………usatanikiwo ntchito zasatana izi ife tikaona tiatan saziwa ñdani kuti anthu akakwatirana amanyengana mkupasana mimba kma mpaka ife tiziona apa…….mulungu simunthutu akuziwa wanyamula mkaziwakeyo Danyo???? Kenako azationesa akunyengana kuti tione mmene amapangila ziwanda zaozo…….Malawi wasochera

  1. AMEWO NDIYE MAWU, AMENE AKUKONDWERA AVULE AKHALE MALSECHE NGAT SAVULA ALI PA SOKA LOCHOKELA KUMWAMBA SINZELU ZIMENE WACHTA NZANUY AMENE MMUCHA INU DAN LU KOMA INE NDMUCHA WAKUMIDIMA SAONA.

 114. mmm koma amalawi uchimizi kulaula, walaula ndan apa dan luu tikunena tsiku ndi tsiku kut muziyenda maziko azanu muziona zomwe azanu amapanga mukutipasa manyaz bwa mukuona ngati mumawelenga nokha nkhan izi ziwan anthu akunja nawo amawelenga ndipo amakutengan umbuli chabe apa mimbayo ndi ya mukaz wake akanakhala wachibwez mukananena kut walakwisa mimbayo ndiyosonkhelana iiii apa pokha changamukan dziko likuchangamuka ili siyan kugona abale. mumalo molimbina ndi maizegate mukulimba ndi munthu osalakwa Dan luu pitilizan aman anthu ogona tulo awa akadalipo pa malawi inu imani ngangali ndikuziwa ikafika nthawi azazuka mutulo tomwe ali nato panopa

 115. Hahaha koma a Malawi vuto mchani inu apa musiyeni munthu ndi celebrity yake ndipo ali ndi ufulu opanga zomwe wafuna please tasiyani kumalonda amzanu mapazi mkumapanga zanu (I respect you brother man thts what we call romantic)

 116. Kkkkkkkk koma yaaaa pamalawipo!! Iwe Dan lu koma zikuyenda ndi alungusetse wakoyo kapena akuuzani choncho kusataniki wanuwo? Ndiyetu muyaluka umaleka bwanji kuonesa maliseche ako pa nthawi yomwe mumatulusa zomwe watupa nazo m’mimba khwevemulezo? Zauchisilu

 117. We are Malawians don’t adopt Europeans culture! Azungu ndi azungu ifenso amalawi ndi amalawi basi, please don’t lost our culture becoz of Europeans.

  1. iweyo wandisangalasa kwambiri. walemba in a western language on a western platform criticising western culture yet your name is in western language…. my friend you are so ignorant

 118. Zoona.ndi zomvetsa manyazi komaso chisoni kwambiri uko ndiye kutaya chikhalidwe chathu. My question which human right he had violented?why the human right are so quite about this sin?

 119. Inu amene mukuyamikira izi ndinu opanda nzeru,akhwakhwa ,agulugunyinda ,analikukuti ,akhaniwa nchifukwa chake Malawi ili panambala wani pazasataniki mkhalidwe wake umenewu kutengeka,,munthu wanzeru sunganene kuti Dan Lu sanalakwise ,,,imeneyo ndiye misalayo ,,mimba ndi chinthu cholemekezeka pachikhalidwe chachimalawi,,,tisanene kuti dziko linasintha,,,linasinthira ndani,,,zoterezi abale anga mwa ambuye tichenjere nazo izi titha kupereka mphamvu kuziwanda, because last minute always danger,,,,nawenso mkazi mkumalola chithunzi chako kuchiika pambalambanda,,iwenso Dan mkumaikadi ukumwetulila ,,,sitinganene kuti sakudziwa kuti mimba imalemekezedwa onsewa anabadwira kuti,,zotere amalawi tisamazisekelere,,,tizuzule molimba ,,,,osati jealasinso taonatu mimba I’ve osati zochezazi ayi ndipo anthu abereka koma sanachitepo izi,,,,pofunika banjali liyambepo kupemphera anziwe mulungu weniweni,,,,,,,, ,,,,,,,,,,,

 120. aa, nde kuti dan lu ndi mkazi wakeyo apanga zimenezo ndimtima wonse, nde mumutani? mum’mangisa? makapeso inu eti, umphawi wathuwu unatipundula bac, zilizose? chikhalidwe chake chiti?

  1. Ulemu wake utiwo anthu mukuyenda maliseche town umu…. Mimba ikakhala yako zimafunika kuinyadilira tatopa nkumangona ana pa fb mimba zake osaziona… Komanso zinthu zikusintha pano

 121. DAN si CELEBS koma ndi osaganizabwino iku mkusambula #MALAWI.akumuonetsa ndani mimba yamkaziwakeyo? Nde tikaona titani?? Sangajambulitse chithunzi cha mkazi chimimba chiliphwee mkuchiika pambalambanda potere mkumbwambwana.Inu azimai mukuti sanalakwitsenu mumaganiza bwinobwino?? Inuyo mumatani kumayenda ntawunimi muli chimimba kapena kuti muli ndi makati ngati uli u CELEBS?? munthu wochokera kukhomo kwa anthu sangapange zopusazi kutengera zinthu musakuziwa tanthauzo lake mapeto ake nzimenezi; anakuuzani kut munthu akakhala otchuka sasamala zachikhalidwe ndani?? NAYE MKAZI KHOSI GENEKELEEE CHIMIMBA CHILIPHWII NGATI NG’OMA YOFUNA KUKACHEZERA KUYIMBIDWA KU MLAKHO WALOMWE #ZIWANDA ETI??

 122. mwangosowa zolemba eti, azimayi ndi atsikana akuyenda matako pamtunda town osawalemba bwanji kuti akuyalutsa chikhalidwe, ndie mimba ndi matako choyalutsa ndi chani apa, ndaniyo sadziwa zoti mimba imabwera bwanji, za ziiii,

 123. Palibe chalakwika apa chifukwa. Sanawonesepo chiwalo cha chobisika ngati mukumuyenda maphazi ndiye.Mwayalukapo. Fuso nkumati nankha. Bwanji simuku blamer amene akumavina nyimbo zanu atavula malayamalaya ????????? komaso komaso atavala timasiketi tatifupi todhinda zobisikazo nakha ovinawo mukutiuza. .kuti si amalaw?????? Asass amalawi sibwino kumakhala busy kukamba
  Za mbaja la ena ayi

 124. Komaso palibe chikuwoneka kut ncholakwikai vuto la athu akuda ndichoncho mexa iyeyu akunyadira mkaz wake komaso iyeyu waima pachulu kukumanyitsani inu bwanji osaimaso ndi wanu kut athu amanye sanje bwanji athu inu Kkkkkkkkkkkkkk nde mukhaula aikaso china

 125. Koma iwe umalembawe koma kuchipatala munapitako ndi ndi mkazi wanu ku sikelo? Nanga munamvako zoti pano amuna azikaonelela kubadwitsa ana ku maternity ward? ukadzaona izi udzakomoka shuwa !!!! Akadakhala wachibwezi ukadatani. Upite ku joberg ukaone zolaula pali chani apa!!!

 126. Ndikupusa kuonesa mimba ya mkazi wako pa gulula anthu, lthink mwina mimbayo samaonesaife, mwina akuonesa anzakeakuja omwe anajoinanawo ujeniija.

 127. The man is so stupid as well as mad.He cant do that.What seed is he planting on youth?Thats so stupid.He needs deliverance before he completely went mad.These are the people TB Joshua needs.

 128. Abale satanayu akatigwila bongo sititha kuziletsa ndipo timaona ngati ndimmene zinthu ziyenela kukhalira uwu nduchitsiru ndithu ….mukamati masiku ano ndiena mukutanthauza zichani???: zinazi mzochokera kumidima chenjerani muzamva khwangwa ili mmutu zikanakhala zimenezo bwenzi dzuwa likusintha kolowera kapena kotulukila anthu amsiku ano tikufera chitauni kapena kuti kufuna kuchita zomwe anzathu anachitapo dziwani satana wakonzeka kusintha anthu oduduluka ndizanziko…omwe asakha kukhala adziko lapansi amadudulukila zanziko lapansi ndi zatsopano…. ziwani zinazi nzapansi panyanja