Unduna wa za maphunziro mogwirizana ndi bungwe la Malawi Communication Regulatory Authority (MACRA) wakhazikitsa gawo lachiwiri la maphunziro kwa anthu amene amaphunzitsa chiyankhulo cha manja kwa anthu amene ali ndi ulumali . Maphunzirowa amene akuchitikira… ...
Articles By Peter Mavuto
Apolisi m'boma la thyolo akusaka bambo Nyozani Phiri a zaka makumi atatu zakubadwa powaganizira kuti ndi amene apha mkazi wawo wachinayi, Lucy San wa zaka makumi atatu zakubadwa. Wachiwiri kwa mneneri wa apolisi m'boma la… ...
Dziko la Israel lati likufuna a Malawi okwana 100,000 kuti akagwire ntchito zosiyanasiyana ku Israel. Izi zayankhulidwa lero pamene nduna ya zachuma mu dziko la Israel, Nir Barakt, anali ndi mkumano ndi mlembi wamkulu mu… ...
Wapampando wa bhodi ya Mulhako wa Alhomwe watsutsa mphekesera yoti bhodiyi yachotsa mtsogoleri wakale wa dziko lino a Peter Mutharika ngati woyang'anira bungweli. Mukuyankhula kwawo pa msonkhano wa atolankhani mu mzinda wa Blantyre lachiwiri, Muchanakwaye… ...
Nthambi yoona za nyengo yati madera ambiri m'dziko muno maka mu chigawo cha kum'mwera ndi pakati, ng'amba ikhala ikupitilira kwa sabata imodzi kamba koti mphepo ya mvula ikuombera dziko la Tanzania. Ngakhale izi chili chomwechi, mkulu… ...
Due to the continued spread of cholera, authorities in Zambia say schools in the country will remain closed until February 12, 2024 to protect the lives of people. Education minister Douglas Syakalima said at a… ...
Mkulu wa Mwanza Social Welfare, a Mary Msidwa, ati boma la Mwanza lakwanitsa kuthetsa maukwati a ana achichepere okwana 118 mu chaka cha 2023. A Msindwa anena izizi lero pamene anali ndi zokambilana ndi khosolo… ...