Bata tsopano labwelera pomwe apolisi ku dela la Makanjira m'boma la Mangochi awombela pa mimba ndi kupheratu Peter Davis wa zaka 25 lero kutsatira mkangano omwe unabuka pakati pawo m'bandakucha wa lero pa malo ena… ...
Articles By Mphatso Khutcha Richard
Angry Community members at the Chiponde border in the district of Mangochi have killed the Police Officer in charge of the police as he and other officers tried to calm rioting villagers in the area.… ...
Mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera ati lipoti la zotsatira za kafukufuku wa ngozi ya ndege lipelekedwe kwa maanja okhudzidwa pofika lero Lachisanu. A Chakwera atinso kuyambira lolemba lipotili alitanthauzire mu zilankhulo zina za… ...
Aphungu a Nyumba ya Malamulo lero adutsitsa bill yoti boma livomeleze ngongole ya ndalama kuchokera ku OPEC for International Development yokwana 20 million dollars yothandizira ntchito za gawo lachiwiri la Shire Valley Transformation Program (SVTP),… ...
Mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera ati akudziwa kuti feteleza anthu akugura pa mtengo wa K105 thousand pa thumba la 50kg, ndipo ati ngakhale zili choncho alimi akukwanitsabe kugura thumbali akangogulitsa matumba awiri okha… ...
M'modzi mwa omenyera ufulu wa anthu mdziko muno a Bon Kalindo ati zomwe anayankhula akuluakulu ena a chipani cha Democratic Progressive (DPP) ku msonkhano wa ndale ku Ndirande mu mzinda wa Blantyre ndi zokolezera udani… ...
Zina ukamva kukamwa yasa, anthu okhala m'mudzi mwa Phanisa m'boma la Mulanje usiku wathawu agenda ndi kuvulaza alendo okawona phiri powaganizira kuti amakayika zipangizo zomwe zibweretse namondwe wa Chido m'phiri la Mulanje. M'neneli wa apolisi… ...