Oyimba wa kale wa chamba cha hip hop Jolly Bro (JB) akupitirizabe kuthira makala a Malawi a ku South Bend ku Amereka. Pano waonjezera mkwiyo kwa mkulu wa dambwe Tay Grin. Ati kumene akukayimba kumeneko… ...
Articles By Lindiwe Sambalikagwa
…52 miliyoni yanga ya bet yapita Zija ankapanga azimalume kalekale zomakunyengelera chimanga chophika kuti akonze nsewu zamuonekera James Chaola amene anawina bet ya 52 miliyoni. Kusiyana kwake ndi koti iye sanamubwenzere ndi komwe chenje, amuuza… ...
…akushopa pa kaunjika wa kumeneko Kumudzi kuno Lulu ndi namandwa oyimba. Zithunzi zake za makabudula pamene ali ku Amereka zikuoneka za mtengo wa patali. Koma oyimba Jolly Bro kapena kuti JB ati tisatengeke nazo. Ku… ...
Tanzanian combat engineers have left Malawi about two weeks after they were deployed to restore and rehabilitate infrastructure destroyed by Cyclone Freddy. The 59 were sent to the southern region of the country towards the… ...
…Wadzudzula mchitidwe ozithandiza wekha Kudya beti ndi kosangalatsa inde. Kwa ena kupambana mayeso kumene kutha kukhala chinthu cha mtengo wa pamwamba. Koma zonsezi sizingafike pa kugonana. Kugonana ndicho chinthu chokongola kwambiri pa dziko pano, watero… ...
…boma likupanga malamulo atsopano okhaulitsa ma dalaiva a chakumwa Phungu wa dera la pakati mu boma la Mwanza a Nicolas Dausi anachemetsa ku nyumba ya malamulo pamene anadzudzula nduna ya boma kuti imanyogodola anthu omwa… ...
…misonkho ikuthera ma lendi mu Lilongwe…nduna ndi ya nsanje yotenga mkazi ngati kapolo…ana 5, amayi 5 Nkhani ya nduna yoona za masiketi, imene pena imapanganso za chuma, ikupitilira. Mayi amene anabwera kugulu ndi kulengeza kuti… ...