
Wolankhulira Polisi ya Balaka, Gladson M'pumpha watsimikizira nyumba zowulutsa mawu m’dziko muno kuti anthu enanso awiri amangidwa m'mamawa wa Lamulungu kutsatira nkhani yokhudzana ndi mayi Matako omwe anawanjata dzulo chifukwa chozunza mwana wawo wamkazi atampeza… ...