
Timu ya Red Arrows ya m'dziko la Zambia yati ndiyokonzeka kugonjetsa timu ya FCB Nyasa Big Bullets pa masewero a mu CAF Champions League omwe achitike mawa (18 August 2024) pa bwalo la za masewero… ...