
Apolisi m'boma la Dowa amanga bambo Andrew Makanjira a zaka 45 powaganizira kuti apha bambo wina yemwe a Makanjirawo anamupeza akuchita za dama ndi mkazi wawo. Bambo wophedwayo ndi a Yekomia Weston James. Malingana ndi… ...