Bungwe loyendetsa zisankho mdziko muno, la Malawi Electoral Commission (MEC) lati anthu omwe ali ku Israel komanso mayiko ena akunja sadzakhala nawo mwayi oponya mavoti pa zisankho za patatu zomwe zidzachitike m'mwezi wa September chaka… ...
Articles By Ben Bongololo
Apolisi ku Kasungu akusunga mchitokosi njonda ina ya zaka 35 zakubadwa kamba kopezeka ndi katundu monga wayilesi za kanema zinayi za mtundu wa plasma ndipo njondayi ikuganiziridwa kuti idachita mokuba katunduyi. Wachiwiri kwa mneneli wa… ...
Tsopano nthambi yoona zanyengo ndi kusintha kwa nyengo yati kuyambira mawa pa 1 February mvula ikhala ikugwa m'dziko muno patapita pafupifupi sabata ndi masiku kopanda mvula maka m'madera am'chigawo chapakati komanso kum'mwera kwa dziko lino.… ...
Sukulu ya ukachenjede ya Luanar yapereka zilango kwa ophunzira okwana 19 kamba kopezeka olakwa pa mlandu owonera mayeso ndipo atatu mwa ophunzirawa awachotsa sukulu. Ophunzira pamene khumi ndi anayi ayimitsidwa sukulu kwa zaka ziwili, ena… ...
Dziko la Japan lapereka ndalama zoposa 1.99 biliyoni kwacha kudziko la Malawi kudzera ku bungwe la UNICEF kuti zithandizire kuthana ndi ena mwamavuto omwe alipo m'madera ena omwe anakhudzidwa ndi Namondwe wa Freddy. Malinga ndi… ...
M'modzi mwa akatswiri omwe amayankhulapo pa nkhani za mdziko muno, a Lyford Chadza, ayamikira boma kaamba kothetsa mlandu wa anthu atatu omwe adanjatidwa kamba kosokoneza galimoto zapa m'dipiti ponena kuti izi zidakaononga ubale wabwino pakati… ...
Boma kudzera mwa nduna yoona zamagetsi mdziko muno a Ibrahim matola, lalonjeza kuti lithandiza nyamata uja wakonza magetsi oyendera madzi ndi mpweya ku Dowa kufikira masomphenya ake oyika magetsi pa sukulu ya Kongwe 2 komanso… ...