Chibuku Malawi
Ngakhale mpingo wa CCAP umaletsa kumwa mowa, kafukufuku wasonyeza kuti akhilisitu ampingo wa CCAP mumzinda wa Lilongwe ndi omwe amamwa mowa kwambiri ngati kulibe mawa. Kafukufuku wasonyeza kuti zidakwa zochuluka mumzinda wa Lilongwe ndi akhilisitu… ...