Apolisi a mu dziko muno achenjeza a Bambo onse a danzi kuti aziyenda mosamala zitadziwika kuti Bambo wina wa danzi achiwembu amupha ndi kumudula mutu mu boma la Mulanje.
Apolisi ati Bambo wina wa zaka 86 amene anali ndi danzi anapezeka ataphedwa ndi kudulidwa mutu ku Mulanje. Iwo ati anthu achiwembuwo anakamutaya mu chimbuzi atamupha.
Apolisi ati agwila mnyamata wina wa zaka 23 pokhudzana ndi nkhani imeneyi.
“Padakali pano, a Thyolani Khoriwa a zaka 23 atsekeledwa mokhudzana ndi nkhani imeneyi ndipo anzawo ena awiri akufunidwa ndi Apolisi,” mneneri wa Apolisi a James Kadadzera atelo.
Nkhani zopha anthu a danzi zayamba kudziwika kuyambila pamene boma la Mozambique linachenjeza kuti mu dzikomo anthu achiwembu akusaka mitu ya danzi ati ndi chikhulupiriro choti muli golide.
Sabata ziwiri zapitazo, Apolisi ku Mozambique adanena kuti anthu a ku Malawi ndi ku Tanzania ndiwo akutsogolera khalidwe lonunkhali.
Very Sad
guys to have baldness it does not mean that some one has possessing gold iam really touched and iam not sure that its indeed happen in mulanje but its like that lets play hard for them .they are also people like us ,we have to respect their rights .my God please help us to fight for rights of our friend who are in serious temptation i know for themselve its really difficult handle this situation off but ur miraclious present willbe of great signicficant ,effeciency ,effective and answerable to them and to the entire country amen.heiveesent r uslike e that
Mugule chipewa.
Thank U 4 Notice This Kuliona Mmene Dziko Likuendera Kungatisinthe Muzambiri Somehow Unyamata Ndi okomedwetsa Ndi Zadziko
GYZ MUTHUU MWATI ADULA MUTU MWAZIWA BWANJI KUTI ANALI NDI DAZI KKKKK
This is all coming of our Lord Jesus Christ, satan knows his time is near, he now demanding his egents to do all these kind of nastay and evil things, tidziwe ichi onse akupha anthuwa akutochita kutumidwa ndi athu achuma chawo, ndipo ziwaro zawathu komanso magazi omwe akukhetsedwa m’mudziko rathu zina zikutumizidwa m’maiko akunja, remember akwawo ndi mizu ya kachere anakomana pansi, akuruakuru akuzidziwa zonsezi, koma mudziwa akakhara pa nkhate khoswe sapheka, akuteteza ana awo ndikumatuma anthu kuti adzipha adera Mighty God sees it all, mudzayankha mlandu wanu patsiku la chiweluzo
Koma Malawi yeka Ndiye kaya sopano kumangopha basi anthu osalakwa zoona eeee iziii Boma lamalawi limaziwa koma samapanga kenakalikonse ndithu Eishii kungowona anthu opha anthu adasi mmm osapita nawo Ku police kumangowapha bas zikuchitika apapa ndi zautsiru sopano
uli galu mulanje does not belong to tumbukas so there z no reason talking about tumbukas while lomwes are the ones found in mulanje where they have killed a person umbuli ndi wanu amakuletsani ndani kupita ku school
Apindulanji munthu kukhaka ndi chirichonse cha m’dziko iri ndi kutaya chirungamo cha Mulungu ndiso moyo wake omwe?
The world has gone mad
Pakufikanso massive awareness campaign apa before its out of hand again!
I think Government should do something real quick and community leaders and religious leaders should be part of the campaign
Iiii golide???pa dazi???zoopysa kwabasi
Kwasala muyamba kuwapha olumala
shaaa koma guyzz!!!
Mapeto anthawi
Munthu ndi opatulika pazolengedwa zonse anamulenga mmchifaniziro cha Yehova palitsoka lalikulu kuganiza kuti kulibe Mulungu koma chilungamo chake Mulungu alipo ndithu ndipo ndi Mulungu oopsa pa Ulemelero wake palibe ngakhare mmodzi pansi pa thambo ili angakwanitse kuima pamaso pake koma kugwa kumapazi ake Lekani kupha abaleanga ganizilani Yehova!
kkkkkk speachless
ndizoona ndipo ine ndawaona anabwera kumotchery
Aaaaaagh munaziwa bwanji kuti mutuwo ngwadazi? ngati amafunapo dazilo bwanji mutuwo munaupeza pompo?
Ntaba z next
Just pure crazy!!!
What’s wrong with Malawi. Pathetic issues over and over again. Does the government exist to tell all sane Malawians that killing fellow people due to beliefs is evil, and never make someone rich/or better in this cyber age. Come on…Where is the Malawi government on these issues? Terrible of the the still dark ages Malawi, if such is true!!!!!!!!!
munthuyo anaphedwadi ndipo anamponya mu nsinje wa ruo koma sanamudule mutu,
Ba Besa Mwila mukwai kwenda mulelolesha kaaa
Reality or fictious?
Azungu akamatiseka ndi nkhani ngati zimenezi ndikumadandaula, eishhhh
kkkkkkkkkk. Koma eeeee
is
not about umphawi
or that they seek for rich all what i know is ufiti basi ndiomwe wafika povuta
but remember kuti Mlaliki akuti
zonse nzachabe
Coz Mulungu azayimba mlandu za izi pa tsiku lomakiza do not think that we are the clevers
kuno anthu akupha akadzidzi kutsata goldy
mmm zovuta2 izi mwamaliza alubino aja mwayambanso adanzi chipongwe
Nde wina kumasauka golide ali pamutu pako pomwe…
Geni ya zipewa guys….. adazi samalani…..
Kondwani Magombo I have to hide u ,,Uona bwa
Ndigura Galimoto apatu.
Lol
bald is money???? kkkk busive
Eeeeeeeee mamvoto tilinawo
Bola kumangovala ma sindiketi basi chifikwa tchingila ingawuluke ndiye udzavaya nthawi isanakwane lol
Kkkkkklll
My question is, Kodi dazi limene mwajambula pamwambapa mwalitenga kuti? Chifukwa likuoneka kuti si la mdala amene waphedwayo.
For those who are seriously need to do away with Danzi contact me on this number 0888568921
President opuma Dr Bakili Muluzi asamale
Dazilaga lindiphesa ine ogooooo ine ndinalakwanji kukhala ndi dazi? That’s my question kkkk
Kkkk kulakwa,kauniuni chuma chobisika danger
Mungofuna kumphimba anthu mmaso koma target yanu yalepheleka
Very pathetic
Inu mukut wadaz kma amudula mutu mwaziwa bwanji
Simon Tembo, MK John Yobu-EliGills, Mphepo Zalozga Kampangachi Griffin panji ni Dyson kkkk
Kuneni Dyson Kumuzi phone zikana naye walikutola mutu wa diamon wula???????
kkkkkkk voicemail forever
Rip kadazi
machende anu nose
kkkkkk wali
Kkkkkk⚡⚡⚡⚡⚡
mwetuuuu
Iyi ndi nthawi yakumapeto aliyense akhale cheru angadzatsale.
So sad! Ambuye atithandize ndthu!
Mulungu Akuwona Zonse
not good guyz
Mzowona zake azivala zipewa, cz wina aliyense moyo ndiofunika pa u moyo wake…..
Zayambika eti tithana
munthu wadulidwa mutu mwadziwabwanji kuti ndi wadanzi????
Nanga mutuo ngwa ndani
kenako muzanva kt atumbukaso ndimakwacha FOKOFU
Afufuzidwe amangidwe
anthu apeza mutu palibe ndiyeno dazi lo waliwona ndani bwinotu akufufuzani
Bias In Media.
too bud.
Vuto Ndi Asing’anga Ayamba Kunamiza Anthu,boma Lingo Liyambe Ku Panga Stop Asing’anga Ntchito Zawo.
Adanzi tonse mogwirizana ndi ma alubino timatche basi atipatse ziphaso zokhala ndi mfuti zamthumba polimbikitsa chitetezo chathu.
oooh sad news malawi tikupita kuti kuchita kuphana ngati khuku zomvetsa chisoni.
Ubwino wake mtaba. Amayenda ndima bodigadi. Palibe chakudandaula
Amayoooooo dziko langa ndalila mokweza inee
ma rubish
Eiish sad news Malawi y y y
kenako timva azimayi a ndevu. umbuli, umphawi ndi njala ya ulemelero wachangu zakumana
Nothing to say even my cheeks hot tears stop burning me,why?we listen to evil news always.Pple still believe in idols,wealth and famous.Do u think God is sleeping?Do u think God does not see all these things?Do u think u r clever?No u r making a mistake but because we are not belong to this world,I surrender my life for the sake of God.
No where to Go no where to run lets pray hard basi ndi kwa namalenga ekha komwe tingathawire basi
Tsono ngati apeza atadulidwa mutu, adziwa bwanji kuti anali wa danzi?
This might be fake.Which part of mulanje?in mocambique it has been reported yes
dziko likutha ili ambuye bwelan nsanga
mmmm pepani
Tiribe kothawira basi…. ndauyambapo wokakhala refugee ku Sweden
Kkkkkk,amdziwa bwanji kut ali ndi danzi pamene mutu wake wadulidwa kkkkkk mwina ndawerenga udyo ndine guys
Business ya pamalawi yandiopsa
Yes plse Lord have mercy
God save us from these wicked people
RIP
Onse adazi akuitanidwa ku mwambo olandila zipewa zaulele kti muzibisa ma sollar anuwo angakubeleni
Watch your mouth broh next time will be your father or child remember danzi limabwera olo utakula kale so u better zip ur mouth than talk like this
nchifukwa chiani tsamba lino limakonda kusindikiza nkhani zabodza ife tili ku mulanje komko tatiuza mbali yomwe kwa phedwa munthuyo kt tikaone amalaw nthaw zonse timafuna kunamiza azathu ena omwe ali kutali cholinga chongofuna kuipitsa mbili ya dera
Amalengezaso mma radio nkhani yi
Iwe Balala,this Only Issue Is True,tsambali Amalemba Zowona Vuto Ndinu Anthu.Makulini vge, Mj Boarder Pali Msewu Wa Chiringa Mutenge Umenewo,mukapeza Mtsinje Wa Mloza Mukadutsa Gawani Ss,b4 Likanani Cdss,mukafutse.Thanks
Koma Danzi mwaikali munthu wake ndikumudziwa kkkk
Yah awa ndemasaini akubweraa kwamwana wamunthu mmawa tinva azimai andevu
Too bad
Hahahaha its funy… When u think of a human head consisting GOLD… But also pathetic when u think of these tragedies…. Killings and stuff…
Gold, Yangokhala Language Yawo,mutuwo Akumapangira Njira Zopezera Ndalama.Osati Pamutu Pali Golide.
So sad
Its true zachitika m’mudzi wa makuluni m’malire a mulanje nd phalombe pafupi nd muloza bridge
Koma ndiye zosakhala bwino
akagwidwa aphedweso
Ngati anadulidwa mutu munadziwa bwanji kuti anali wadanzi mwina many munalipompo!!!!!!!!!
ooh Peter Muthalika
Kutha izi kubwera izi kma tilimba mmmmmmmm
Mwadziwa…..bwanji…..kut….anali,,,,,ndi…….#DAZI
pot amudura mutu inu mwadziwa bwanji kut ndiwadadzi??????. . bodza basi
Dumisani Nganya Makwakwa Rendson Toothblush Mhango
ndiye pakwathu tangotipo mbweeee!!!!! eish
yanapweri ija yadzidzira
Tatopa nazo zausilu zanuzo
Very bad.Last days indeed
Olakwa Ndi Boma Cifukwa Anthu Opha Ma Albino Amawapatsa Chilango Chochepa Aikeso Lamulo Loti Opha Nzake Aphedwenso
Zoona izi koma?
Nanga mwadziwa bwanji kuti anali Wa dazi? Mesa mwati amudurapo mutu??
Zabodza izi
Akanakhala wandevu zikanakhalaso zina. Koma dzikoli. Kaya
Eee Wat A Kind Of Malawi Are We?
Once a peaceful & God fearing nation but has turned into a killing field now,, lord have Mercy…
Aziyenda mosamala what do u mean?that’s not a solution damn do something
Cry my beloved home Mulanje.
zotsatira za maluzi mukuchinjikanao anthuwa ndizimenezi
Kwa amene musakukhulupilila khulupililani nkhaniyi ndi yoona ndithu. Ndipo ophedwawo anali amalume anga a mmudzi mwa Makuluni TA Njema mboma la Mulanje. Timawati bambo Khonanga Makwete ndipo anali a dadzi koma okalamba ndithu. Malemuwa amasungidwa ndi ana awo ndipo amagona okha mu kanyumba komwe amagonako. Kucha kwa Monday mnyumba mwawo munapezeka magazi koma iwo munalibemo. Anthu anawafufuza dzuwa lonse koma sanapezeke. Thupi lawo linapezeka Tuesday mu chimbudzi chokumba cha nyuwani pakhomo pa banja lina koma lopanda mutu. A police anatenga amayi a pakhomopo pomwe anawo omwe amatchuka ndi khalidwe lakuba athawa. Mayiwo ndi omwe akuwulula zoti ana awo ndi omwe achita chipongwecho akuti anapeza nsika wa mutu wa dadzi. Tikunena pano mayiawo ali mmanja mwa police ndipo anthu okwiya awotcha nyumba ziwiri za pakhomopo. Chabw a Malawi14 angoyifotokoza mwachidule koma nkhaniyi ndiyoona
Pepa mchimwene wanga poluza malume. Dziko lapansi likupita kuti?
May his soul rest in peace!
Wat ashame amalawi?
Ooh! Sorry brother Lameck.
Ndithudi kwa Mulungu tinachokera ndipo kwa iye tidzabwerera
Iwetu umafunika ukhale ntolankhani wa Malawi 24. Ungakatamuke
Kumaona pamalo poika ma joje nanu achiphwisi
KKKK ZASITHASO AMALAWI 14 ANGOIFOTOKOZA MWACHIDULE
Tipatseni picture yeniyeni coz ili apayi ndiyosadulidwa mutu
Jah
Zikukhulupir zafikapo penipeni .disis de end of de world let us see what God wanted to do in period
fanz yakwiya,searchin’ for gold,akumanamizana choncho,coz zaymbila ku mozambiq.
Mulu mwala wagolide?
eee musandiphereko bambo anga ku mulanje chonde
kkkkkkkkk Ali ndi dazi
eee lalikulu
Kkkkkkk koma Achee
awona bwanj dazi mutu palibe kkkkk
These evil act and believe should be stop who practice and do should be investigated.and be arrested
the imaginatios of man are always evil
Nothing to say poti nanenso vuto langa ndilomwelo…rip
Dziko la pasi chop money ndichomcho komaso kumakumbuka tsiku lakutha moyo wako. umadula mzako mutu lelo usanalandile zammanja umazidikila Mulungu kumakuitana smart.
Mutu atenga or angousiya? Ngati atenga mwadziwa bwanji kuti adali ndi danzi or waphedwa chifukwa chakuti adali ndi danzi? Be professional pliz. Dont only be writing things to be famous rather than popular.write something u r sure of. The truth will b known only when the murderer is cought. Osakolezera kupha adanzi pliz.
Simunawelengetu baba nkhaniyi chifukwa mafunso onse mukufunsawo mayankho ake ali munkhaniyi
Zoonadi sanawelenge chifukwa nkhani ikuveka bwino kwambili
Sorry mapeto adziko
If stephen aman richly blssd by GOD and full ov power performed great miracles and wonders among the ppl was stoned publicaly by members of the council ,why is it the grvment ,police seeking for aprove by bring murderers b4 court ,they shld stoned publicaly 2
Write a comment…zachamba
Ziko ili
Kkkkkkkkkkkkkkkkkkkk koma
Koma abele zikoli posachedwa mlungu aliwonongaso chifukwa machimo achuluka
Nde mwati padanzi pamakhala golide?Koma ngati nzoona nde tili ndi chuma koma choti chakwililidwa muzipewa zamulaza.
Kkkkkkk
Kkkkkkkk u hv to be serious wamva
kkkkkkkkkkk ndakomoka nkuseka
After adazi muzati asitsi la white hair akufunidwa eash kukhala pa Malawi ndikulimba tsopano
Eee its end of the tym, kenako tinva kut ama hip
kkkkk
Kakakakakka
Kkkkkkk kenako amatewe ndi kissmabondo kkkkk
Kkkk
zosakhala bwno sheeee
GAEZ PENAPAKE KUMAKHA SERIOUS PAZTHU. OSAMANGO WANAMIZA ANTHU PAKHAN ZMENEZ…
Ndizowona guyz adadi wadazi ndiwamudzi wamakuluni T/A Njema Mulanje Limbuli
Komangati ndizowona Eee agalu amenewa ndiye afikapo kenakotinva kut anthu aafupi akupezeka ndi mitimaya ifupiifupi yomwe ikuyendamalonda ku ulaya komabe tingowalimbikisa anzathuopanga zipewa zamulazakuti nthawiyolemela nawoyafika apanawo agulemagalimoto chifukwakusoka chipewa chamulazanso ndintchito
#Sindukhulupilira
Uzakhulupilira ataukhapa wakowo
Ngati wapezeka atadulidwa mutu, wadziwika bwanji kuti anali wadanzi?
Read whole story madala.mesa akuti munthuyo waphedwayo anthu akumudziwa awanso awa
Kenako muyamba kupha onenepa,kenako oonda, kenako oyera, kenako akuda!
This is bullshit, umphawi unatipweteka. We are only thinking of shortcut ways to get money. Sad
mwati anadulidwa,how then did u conclude kuti ndiwadanzi? All the same,thats very pathetic
This is shall to the world not in my country I may better hear this happening to other countries
A police mukumalimbana ndi ma min bus driver ndi ovala camouflage za masana izi malo mothana ndi mchitidwe umenewu ntchito yanu ndikuteteza anthu adziko lanu…umuzigwira ntchito usiku oasmangokhala pa office
Mwaziwa bwanj kut anali wa danz popoeza mwanena kuti anamdula m2
Mukutipha Ife Nde Mulamulirano Ndani?
Dziko Lili Mmanja Mwa Agalu Tsapano, Nanga Kungomva Kuti Ndi Chifanizo Cha Mulungu Nde Akuti Tibwelere Komwe Tinachokera?? (aboma Taganizani)
kkkkkkkkk
Atsala amagwelu
Very bad
Dziko ili nkona lili losauka.
The police should have said, a danzi onse azivala zipewa kuti asaphedwe
Boss…in most cases imakhala link ya anthu woti akukuziwa…..sikuti upandu umachitika ukangowonedwa ndi dazi NO!…ts a game plan…..anyways partially ur point can work
Sure…
Zipewa sizingagwiree” xhifukwa anthuwa timakhala nawo amatidziwaa
Ine ndili nalo #Dazi
that’s really a pathetic behaviour. but that’s not the way to prosper in life. no no no…. Malawians calm down. our colonial masters have something to do with this. I will explain. u guess their main agenda is to blindfold us. they want us to stop believing in biblical things. I do bliv that they want to lie to us. they want some pure lunatic educated people to convert us. especially these tumbuka who takes almost 45 yrs doing primary n tertiary education. we all know how stupid they are. but wait. they will use those bones n skulls to provide some cheap n shallow proofs . I don’t care what some dick heads will try to look like they r saints. the truth have been said . all my statements are normative. don’t talk trush
but they r the ones who brought the bible…, why wldnt they also want us to blv in it?
Never heard so much bullshit in my life!!! What an idiotic thing to say
What’s supposed to do with tumbukas?????
When I started reading your statement I thought your smart, but no your idiot
tumbuka’s are de causative agents, may God turn ur mind into foolish
High Grade At Its Best, U Just Hav A Hatred Towards The Tumbukas I Guess Mxiewww, To Hell With U!
This started in Mozambique so how does it have to do with Timbukazi ????
How would be this news if it happened in Rumphi/Mzimba? Thanks för the input.
Wolemba bullshit comments ?????? alandirenso ????????.
I pray that this dude must go straight to hell when he dies. He is full of bull freeping shit
Kkkkkkk, nkhani ija mpaka atumbuka yawakhuza mwapadela? kkkk, koma nde wandisekesa
lf you have run out of comments just go hang yourself, empty vessel
Tumbukas?where’s the link?umdziwe Yesu……mphenzi yako ikudumpha dumpha Ku dubai
Nafwaaaaaaa
David Guest or whatever u call urself. U shud know that u are a SEASONED IDIOT from today. Stop using ur balls as ur brain.
Nonsense
Idiot
mtumbuka ndi nkhaniyi zikugwirizana pati xaaaa
Tribalism is not good at all,eeeee so much hatred this guy,I don’t see how tumbuka’s are related to this story,you are a human being with full of bitterness,you are a waste of resources in the universe,with the stunt you pulled here,pple will start arguing to each other
Almost 120 words of poorly written nonsense.
And he doesn’t even know that we start a sentence with a capital letter.
Tapocation Kondowe anathawila pa window.
Don’t b stupid! Wy u’r against tumbuka. Mwakhapana nokha anthu opanda nzeru. Matongo yako!
Tawauzani makape apolicewo ndithana nawo akapanda kupeza wapanga zimenezi .. Koma kuba basi.. Infa yamunthu iwowo amafuna ndlama zilowe nthumba bas
Nanuso mazoba mwaposta nkhaniy ndnu otani? Simunaonepo wadazi ataphedwa?
thank God ndilibe dazi
Its not funy if u don’t have
ZILIKO KUMENEKO
koma ku malawi ai
Zonse tingosiya mmanja mwa mulungu kuti amene atsalawo awateteze
Eeeeeesh umphawi Ku Malawi unanyanya,zochotsana maliseche ,kupha albino zatha tsopano ?zayamba zamadazi ..bwanji Ku Botswana ,Zambia ,Namibia Kenya ndimaiko ambiri mu Africa sizinachitikepo izi…
amudula mutu!? nde aziwa bwanji kut anali wa dazi? anaupeza mutuwo?… guys uchifwamba uli paliponse nde akaphaso muthu wanfupi munenaso kut amupha chifukwa chakufupika?
What the he’ll men?
Shit!!!
Zamasiku otsiliza
Permanent Hair Disaster(PhD) likhalenso vuto lot tizvutika nalo..? plz plz muzimvako chisoni…mwapha albino…sakukukwanani pano mwatembenukila kwa anthu adazi?? mmm almighty God will intervene & bring judgment to all people who indulge themselves in that stupid business.
The next will be short pple the only way to eliminate this notorious conduct in Malawi is mob justice once caught the should face stones in full view
I dnt believe this..
Yooooh
Hahahahahahaha madula mutu mwaziwa bwanji kuti anali ndi dazi?
Kkkk akuchenjedzedwa anthu otsalakwa malo mochenjedzwedwa okuphawo? Mmm Malawi
Mmmm
Eish
Ok so bad,if that is true Oh! Lord Have Mercy
Eshiiii the situation in Malawi iz getting out of hand. Too much nyakanyaka everywhere
Koma guys sibho
Zachoka my Albion zafika kwa anthu adadzi?why Malawi ? Why mutharika ? Tikamange nyumba dzathu kuti komwe kili chitetedzo? Ku Area 30 akuba aba macurtain church
umm people have criminal minds
New business miracle mone dazi.com
ngati mutu panalibe aziwa bwanji kuti anali wadazi
mwaziwa bwanji kuti anali wadaz?,nanga ndimbali it I ya MULANJE,?,guys musaopseze ziko
.
ndzoona T/A Njema
ooh, ndne wakimulanje ndfufuxa man good day
inenso kaya and nd dera lakwa2
Timawati bambo Khonanga Makwete amalume anga a mmudzi mwa Makuluni TA Njema ku Mulanje. Ndi zoona izi man, mkutheka nthawi zina Malawi24 imalemba za bodza koma izi ndi zoona.
sorry #lameck,ause mumtendele
pepani
Malawi ukupita kuti eeeshi?
iwowo adziwa Bwanj kut ndiwadazi???? zabodza basi
NO COMMENT
Mmmmmmm zayambikanso ku malaw
Kenako tivanso kt a mashalubu onse ali ndi copper! eish ili dziko latha bax!
Hahahaha Hahahahahaha koma ndiye wandifikapo
Kkkkkkkkkk iwee
Kakakakakka koma adha
Mboraa! kkkkiest
Kenako andevu onse ali ndi dyamond
Ndie kusakadzatu,chigumura cha Nowa!
Kkkkk mpaka diamond eish mashalubu ndithu atiphetsapo apa.
kkkkkkkk…guys dziko lavuta ili deal ndi chipewa bax kumangomenya tchingila
Si deal amakupha ndi wokudziwa a Malawi mwataninso , chitetezo ndiye deal!!
Kkkkkkk kenako timva amatewe Ali ndi luban kkkkkk
Hahahaha! palibe kuthawaa!
Hahahah koma eee
Kkkkk koma NDE zizavutatu
Koma kumeneko! ziko lathapo ili
Ndichiani Kod Amalwi?
kkkkk koma malawi sazatheka basi
Mmm umphawi wafikapo pamalawii
Wats a f**ck!!
Koma
New world order
Mmmm ndiye dazi litiphetsapo pamenepa
Dazi kayamba kuposa alubino sopano?? Koma !!!!!
Uchusilu wa amalawi umenewu kumangotengela zlizose
Malawi Government is really useless,zoona instead of warning the killers koma akucheza anthu amene sali olakwa,that’s madness.
Mmmm last days
Chitetezo kumalawi chili slack
Wow another trouble why my country
RIP.INE NDIMADABWA KUTI DZIKO AZITILAMULA ABWAFUBWAFU;LINGALONGOSOKE?
Vuto si president zifwamba zinalipo even during MCP
akulu during mcp kunari chitetezo not zimene tikuonaz
PEOPLE Have BEEN KILLED EVER SINCE. Abwafubwafu ndiye kuti chani? Shame on you
Mutuwo awusiyaso? Kapena angotengapo dazi lokha?
Why Malawian?
KENAKO TIVA MA SHORT AYAMBA KUPEZEKA NDI IVORY KKK
iiiiiii abale inu
nde mwaziwa bwanj kt ndwa danzi pot amudula mutu?
Eti?Kungoona Thupi Basi Adziwa Kuti Ndiwadazi?Aaaaaaa
Anthu omudziwao amufotokoza
Koma pafundo I-square tichedwepo munthu timamuzindikila kamba ka khope ndi chifukwa akuba ambiri amava mask kumaso kuti asazindikilidwe, ndiye mutu wadulidwa aziwa bwaa mmmmmmmmmmmm
mwina mkazache anapita kukaona zovala Komanso zina ndi zina, nanga anthu oduka mitu pa ngozi amadziwika bwanji
AMalawi muli pano kumamvetsetsa wanena m’bale wawo kut analid ndidanzi malemuwo, ndipo anali abale aked, ndeno kubweleza bweleza Why?
R i p bambo Danzi
Zayambika??? Umbuli komanso umphawi wavuta pamalawi. Adazinu chonde samalani. Ambuye akupaseni chitetezo.
The works of devil