Mavuto akuona maule sikuti ndi pa galaundi pokha iyayi, ngakhale ku chipinda kumene amayenela kupeza mtendere kuli mavuto osaneneka.
Atayambilanso zosaona pagolo pa masewero awo a sabata latha, timu ya Bullets yaganiza zoimitsa mphunzitsi wa timuyi a Nswazurumo Ramadan.
Malinga ndi malipoti, timu ya Bullets yauza a Ramadan kuti apume kaye ndi kulingalila bwinobwino za maphunzitsidwe awo a mpira ku Bullets.
“Sitinawachotse, tingofuna aunikile bwinobwino za tsogolo lawo ndi zomwe akuchita nalo,” atelo a Bullets.
Pa nthawi imene a Ramadan akhale akupemphela kuti Ambuye awakondele kuti asawachotse, timu ya Bullets ikhala ikudalila a Eliya Kananji kuti aitsogolele ku madzi odikha.
Ndipita ku Khoti basi
Ndipo amene anakhalapo wamkulu wa timuyi, Bambo Kondi Msungama aopseza kuti apita ku Khoti kukatenga chiletso.
Iwo ati akukatenga chiletso choti kampani ya Nyasa isapitilize ndi dongosolo lake lofuna kuthandiza Bullets kuziyimila paokha.
“Ndi zofunika kuti Bullets iyime pa yokha, koma dongosolo lake sindikuliona bwino iyayi,” anatelo a Msungama.
Iwo anaonjezelapo kuti auza loya wawo kuti aunike bwino nkhani yofuna kuti Bullets iyambe kuyima payokha ndipo akaona kuti sizikulongosoka apite ku bwalo la Milandu kukamang’ala.
Nkhani yoti Bullets iziyimile payokha yakhala ikumanga nthenje zitadziwika kuti timuyi idatafuna ngati tomato thandizo limene adapatsidwa ndi kampani ya Nyasa manufacturers.
A Nyasa adawapatsa a Bullets theka la biliyoni Kwacha kuti azithandizile kwa zaka zisanu koma patangotha chaka chimodzi, kunapezeka kuti ndalama ija aichecheta ndipo kwangotsala ka chenji kokha.
Team isagulitsidwe iyi, vuto langokhala mbuzi (executive) kulephera kukonza/kugula ma players during off season ndikukonza momwe munali munali mavutomo, kufuna kumangodya dolazo amvekere tisadandaule team ili bwino koopsa lero ndi izi. Very shameful and a disgrace to the pEoPlEz team. Think deeply……!!
Manyaka
Muziona chakachino mumangova
Once a bullet, always one!!!. if u argue wth Noma fools, they will bring u down to there level, n beat u wth experience, atayeni ndi ma rubbish awowo, ana opusa akura akulima fodya yemweyo, osatiso kwawo koma ngati ma tenant, tazingokodzerani ma goal, mbatata inu. super league ndiya azibambo.
GUYZ CITIMUCI NDI CATHU BASI, IKANANKHALA KUTI NDI GALIMOTO OLO ITAMACITA MAMBAMPU KOMA SITINGAYITSIKE AI.IKUNGOFUNIKA KUYISALIRA CAKUDYA NDIYIPEPHELELA MOKWANIRA BASI
Koma the pipos team ahaaaaaaaa
nonse ndinu agalu pamodzi ndi bengo nzelu mulibe
Palibe timu sifuna kuwina
coach sasewela pagraundi komama players akale anachita nkhwidzi ndi ana atsopano katangale wamapleya akuononga mpila pamalawi.
sungamayo machende ake team yo siyake ndim.mene zinthu zilili ku bullets panopa akuenela anyasa aitenge bas ineyo ndiweni weni sapota wabullets
Kkkkkkk
Kkkk ndiye wina uzilimbamba ndife manoma tikungowerenga nawotu ife kkkkk
Viva maule for life
Atayimbilanso zosaona pagolo kkkkk quote of the day
kondi msungama asayiwale kuti ankatenga katapila kuti ayendetsere team mpaka team kumakhala ndi ngongole zambiri kodi a kondi angapereke more than k100 million kuti neba bullets angwiritsire ntchito pa season? neba bwera ku Lali luban udzawone momwe timayendetsera team with sponsorship or not.
Nanu Admin muzilemba bwino nkanizi iyaaaaaaaaaaa
Koma kumenekooooooo muziona simunati atsara ma player tigawananso ena atitsata ku nyerereku
KKKKKKKKKKKKKK KUSOTA KUMAONONGA MOYO ANTHU OFODYA MITU SINGAGWILE
Bbbb more fire koma dzikandigundika ndikupita Ku team inayake yayikuru Malawi momuno,
Noma kuti buuuuu zanu izo amimbulu fc
zitsilu inu mwasowa zokamba eti. Muvulalanazo zimenezi
kkkk kamlete fc ena oyikonda amangoti bomba fc uzigwila sunati uku mkuyamba chabe
Nsanje
BB NDichitimu Chochitisa manyazi angopanga ngati ana pamene ndichi timU chama nkhalamba,kkkk
Timu iyi ya Bullets ndi imodzi mwa matimu akulu mmalawi koma ikakhala ndi sponsorship timuyi siyenda bwino kuchuluka anthu adyera,sapota,masapota nawo mmalo moti angopita ku stadium kukachemelela timu akufuna nso malipilo kuchokela ku timu, ngati sapatsidwa mumva komiti iyi sili bho
Ndikufuna amene ankakocha kale mtimui ikuchedwa bats bulesi
Amenewa ankapume Kaye kuli bwino mtimu ya BB inkhale yopanda oyiyang’anila zili bwino kwabansi.poti mwana amalila ndi nkodzo wake.
Neba ine sindikubisila kanthu tikuchokela muzinda umodzi!iwe ulindi radio/TV mnyumba mwako zikumakuuza kusuta kuwononga moyo !ndipamene iwe ukupeleka MWANA kuchingambwe zelu ulibe neba
chiphwetherere chatimu,manyaka,manyowa,bibi,nyasi,tunvi,mamima,abwampini,,pitilizani kwnanako,komaso simunati apapa mukulemba practical nde ngat ikukunyerani chonchi nde theory mulimba,,,,mumanyazitsa mpira wakumalawi agalu shupit,, noma kill dem 4 me
panyero pako wamva!!!
ntchito kutukwana basi,,,mpaka kuchita kubalalika ngt akukukakamizani kusuta chamba? mesa mumasuta 2010 inu? oh paja ndiwa expire nchifukwa chake mukupenga shupit
Kkkkkkkk koma Neba sulira Khedee
matimu akuluakulu samenya kaye mpira until national team ibwere,matimuwa ndi noma ndisilver basi,,km manyaka onse akhalabe akugwiritsana magobo, ndipo team imene ikuyembekezera relagation (little bullets) ndiye mtsoleri wazogwiritsanagwiritsana magobowa
aleo apita ndi nsamilo kkkkk
Kaya zawo izo ife mkaka tatopa nawo zathu zikuyenda
Guyz tasinthani zinthu kukangana sikungathetse mavuto,,bullets ndi team yayikulu abale ndipo tmakunyadiran kwambiri!!!! Zoluza si nkhan ya chilendo olo real Madrid imaluza kambiranani mwa ntendere guyz!!!!!!!
Kkkikkkkkkkkkkkkkkkkkkk
kkkkkkkkkkkkkk! kampopi,chingambwe,barry,2010,batchala,jaman fc kwinako pitilizan guys,sizatheka ayi,kaya ndi umphawi kaya ndi umbuli,kkkkkkkkkkk! mbola guyz,chi team chomvetsa manyazi kwambiri,kkkkkkkkkkkkkkk!!! dhilu ndi ma blues basi,mkaka wokhaokha
Kodi ma blues ndiye ati? mesa ndinu a orange inu? PP yanyamuka kkk iweso ndiye ndiwe mbuli gwape weniweni, kapolo shit!
Kkkkkkkkkkk! Big Mbulizi fc,team ya fungo,ya ana maskin opemphetsa,munali ndani inu popanda nyerere? Muziyamika kuti Wanderers sitopa ndikukuthandizani amphawi inu,kkkkkkkk! Kandalama komwe amapeleka anthu opanga chingambwe aja kosakwanira,osamayamika bwa? Ana opusa zedi.
anyani,abakha,ma tissue chamba chili bobobo
Kondi apite ku khotiko ifeso timakudziwa tikachosa chiletsocho wakuba kondi
you can’t solt out technical fault mid of the first round
take note every season you so called journelists talks bad about bullets is the season we image championship no wonder this season we are going to be champions i bet
kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk hahahahahahaha,7 games 11 points,,noma 4 games 12 points
are you mad does noma compete for superleague championship ? If you could talk of silver icould agree
Team imeneyi inatha kalekale chifukwa ndi yakale maseweledwe achikale,ma suporters zopanga zawo zamake zana,kuyambisa ndeu zachikale,satilani nyelele nthawi yafika tsopano yosintha ndi kuiwala za kale
tathokoza may malawi 24
Ineyo ndi wa silver,Kondi is right chifukwa company ikatenga umwini ku bullets ndikudzaona kt sakupanga ma profit monga ankayembekezeka,adzathesa team nkuisiya pa dzuwa..kumbukirani Escom united,komanso kunali Sucoma(Illovo) mmene anathera ma club awa!!
Bullets inakhalapo opanda sponsorship for years I can’ t even remember koma sinathe, achuluka ndi adyera amatenga ngati munda wawo…
tikukonza timu.
Akondi mkufuna mzidyerabe team iyi ma player azipitilira kuvutika? Mpira ndiwovutatu
Zavuta basi neba kungovomereza
Zoona msungamayo ofunika tithane naye ndiwakuba ameneyo.
Neba ndikufunira kukonza bwino team yako.Palibe munthu wamuyaya pantchito.
VIVA MAURE I LOVE IT
sungamayo ofunika amenyedwe coz akufuna kusokoneza asakhale ngati team yake
Ine ndiye ndalowa kunoma basi iya khalani muzikangana iiya
Mumakwana Man Ur Most Welcome Fill Free
Ndikumakhala okhumudwa kwambiri m’mtima mwanga ndikamamva nkhani ngati izi. Chikuvuta ndi chiyani kumvetsetsana Ku team ya fuko BB.Ndikumachita manyazi ine oyikonda bullets (Chris.m. Chiweza. Or Vunja man).
Madala pliz khalani odekha coz mutha kukweza nazo Bp yanu kenako timva kut mwatisya ngati Mfumu ija yaku Thyolo. Zitayeni izi ndi za mpira.
kkk zawo izo Noma woyeee
Yoeeeee!!!!!Kkkkkkkkkk
Woyeeeee!!!!!Kkkkkkkkkk
Ukakonde bullets lero zakalekale
KKKKK NO COMENT
neba kusamva plus makan apapa ndie mmmmmmmm yayang,ana ku ngolo mumva kuti atemanako
And sungamayo ndi wakuba mundisimikiza sakuifunira team. Zabwino aiiii
Guy koma madziwa kuti kananji ndioosokonexa ali ku wanders technical panel yawwo kunaliso gwedegwede iye uja ama user. Nyanga not talent ine idont see vuto pa ramadhan guy
Bullets ndi team yokhazikika, mutopa nokha ndikulemba,
kkkkk….team yaminyama iyi!
koma yea zambila izi iiiiiiiiiiiii
Sono asamalembe.
kkkkkk muona chakachakendi chino inu m’mati nthawi zonse muzichita bwino ai chakachino siyilani ena kkk
ife nyelele basi # noma pambeli
Kķkk
Ramadan ndiwosanva iye kuyiwala kuti ndi masapota a team yomweyi adamutulusila zikwanje pa ground ndikumuwuza kuti asowe lelo nkumabwelela komweko,kenako anzamva nkhwangwa ili m’mutu
ok maule osatekeseka ngnganga NGAKHALE YESU ANANYOZEDWA NDI ANTHU WHAT ABOUT THIS LIFE? NDIMENE ZIMAKHALI
Eeeeee zovuta kuzivesa kwabasi ,, kod pakana season ino ithe tikungokangana????kom ndchan kwenkwen???zina sizinathe zikubwelaso zina ishiiiii my team zandikwanano saname..
BB imandimvetsa kukoma
When you move in a smooth road you donot develop strength I hope after this intermingled bottle they will b light at the end of tunnel
Bullets-ndi-nyatwa-how-turf-situations-we-can-meet-we-will-overcome-n-be-successful
zoonadi bullets cant fedup bro
Bullets ndi nyatwa sitikukhumudwa ziyenda boh
kkkkkkkkkkk tifa ndi kuseka apapa
dyera la ndalama a bullets muona muyaluka chaka chake ndi chino
And ikatheras pa 10 ndmwai
Ma Adim achamba enawa!
Kampopi f.c
neba fodya wamupweteka,,,, paja akut 7X3=11 ??? hahaha Algebra neba! !!!
Simunati BB akuyimangira Stadium komaso Basi waganyu manyazi bwaaa
wot is wrong kondi is right and removing Ramadan is not a loose
LIPIPA FC ,Kampopi fc, aziona mesa paja amatumbwa kuti wapeza coach oziwabwino ntchito?
Ee Akuluakulu Mavuto Anyanya Ku Bulets Kod Vuto Ndi Chan Tandithandizan
Mwayambazopusatsopano,kod Mukufuna Akumudzfetmatce?Zkutwawatu,mudzwe R.
Malo mowauza anthu mbola kapena kuti manyi omwe wasankha coach wanu wa flames zimene zukagawa ma poits ku RSA muli buzy kulemba za bulets kkkkkk makape ati cholinga apeze macoment
kd paja kubullets ateng angat axe
Uwaziwa sunday lino flamez italuza ndi Tanzania
makape inu mpikisano umenewu tsititenga ma prof coz timafuna ku onanso talent ina
Bola ngati mukuziwa kuti ma profe ndiomwe mwawasiyao kkkkk pa sunday mtibu wazigoli
Kikikikikiki
kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk nakomokaaaaaaa
Ndikutitu popanda kulemba za bulets news simugulisa bulets moto kuti buuuuuuuuuu
kodi kani Malwi24 yayamba kugulitsidwa?
Where ar u man ?
Out Of What? Tiziwa Bwanji Ife Zakampopi
Ndichifukwa chake muzigula ma news then muziziwa man the peoples team ndi team yokhayo yosangalasa mdera lanulo
Makape a Malawi 24 mwasowa cholemba eti kodi team kuimitsa coach ayamba ndi a Bullets? Team iliyonse ili ndi malamulo omwe imatsata polemba coach ndipo gwirizano wa coach ndi team amakhala ma results ndiye ngati team siyikuchita bwino palichifukwa chotsungila coach?
kkkkkkkk a Edward tambasulani bwino kuti anthu amvetse kodi kuluza si ma results? kapena ma results ndikuwina kokha kokha?
kkkkkkkk zakuwawa? zako izo uziona ndikuzigwira komwe iya
Uuuuuusovenge kkkkkk
Hey!! Kkkkkkk Kweleko Amjomba
mukdzaymba kuwna cholemba chdzasow, tangogniz kokha, bwaj sanalembe za silver kpn noma
Bale wanga malawi24 siikulakwitsa,ikutiuzammene zilili ku timu ya bb,kwaine ndikamaonera game ya bb vuto sicoach timu ija imasewera bwino,kmano mtima omati anthu amadziwa kale kt ndimachinya akafika kutsogolo amakhala ngati achinya kale kma mpira usanafike paagolo,kusonyeza kt coach ntchito yake waigwira bho bho chikufunika mkungoika mtima akalowa ground ndikudziwa chimene alowera ground,ngati munaonera mpira wamalawi ndi comoros gaba zimene amachita akapeza mpira kutsogolo sizoyenera strikers zimene zija fukwa striker weniweni sangafike goal area mkuseweretsa mpira kt adyetse mpaka goal keeper ayi ndoxhifukwa mpira ukutivuta kumalawi kuno.
N’zomwe Tmayembekera! Go 2 Hail Bb, So Wht Next? Yathapo-baasi,
Ndiye kampopi fc kkkkkk Ine ndikumwa wamkaka
Mtundu watha
mmmmmmm
Kodi live show ya Mlaka Maliro ku Zomba ndi free of charge olo ya dollar,,,,,,,, tinatopa zomamva za NeBa iyaah
So what??? Pokonza zinthu mumayang’ana nkhope???
The Wrath Of Bullets’s Vengeance