Apolisi ku Mangochi agwila Bambo wina wa zaka 40 kamba kogwilila ndi kupeleka mimba kwa mwana wake.
Malinga ndi onenela a Polisi mu boma la Mangochi, a Amina Daudi, Bambo amene watsekeledwayu kwawo ndi ku Mulanje.
Iwo ananena kuti Bambo ameneyo ndi mkazi wake banja linatha.
Iye ananyamuka kupita ku Mangochi kumene anakwatila mkazi wina. Ali kumeneko anaitanitsa mwana wake wamkazi kuti azikhala naye.
Apolisi akuti mu mwezi wa July chaka chatha cha 2016, mkazi wa tsopano wa bamboyu anachoka. Kumusiya mkuluyo ndi mwana wake. Mmbuyomu mkuluyo anakakamiza mwana wake kuchita naye zadama.
Mwana uja ati anathawila kwa Mayi ake omubeleka ku Mulanje kumene miyezi itapita anadziwika kuti ali ndi pakati. Atamufunsa anakanika kuulula kuti wanyamula katundu wa Bambo ake. Iwo anamuthamangitsa, kumuuza abwelele ku Mangochi.
Ku Mangochi, Bambo ake anamusungitsa kwa chibwenzi chawo kuti mkazi anakwatila uja asadziwe.
Koma anthu a mmudzi podabwa anamupana mtsikanayo amene anaulula kuti atate ake ndiwo anamuchimwitsa. Nkhani inakafika ku Polisi ndipo Bambo wadyelayu anagwidwa.
Mkuluyo akuyembekezeka kukayankha mlandu ogona ndi m’bale wake.
Poti mwati lake osati langa kapena lanu so nkhani palibe apa
Kkkkkkk koma adha zinazi…..odi nzingodya chamba changachi
Tidikile ambuye yesu basi..kkkkk
Akweeni? Ndichocho
kunkwima basi akazi osewa munthu ukagone ndi mwana wako zamanyazi
Wagwilila mwana wake not wanu.palibe chifukwa chakumanga ameneyo. Mwana ndiwake.
nyere yake yamtundu chani abale?
Nanga akanapanga bwanji ngati akazi wawo kuchipinda sakupeta mokwanira kkkk
Mpaka mwana obeleka yekha,muthu akuopsa kuposa mkangodi eti,ngati kuli ku khwima mukukhwi kuipa guys
Vuto Nd Mayi Ake Amwanayo, Chfukwa Amakaniza Mdyombayo Kt Anyofwetsd Ngini. Ndye Yaponda Yamwa Basi!!!!!
Very common amongst pipo from those districts! Y we don’t know but suspect zokhwima khwimazi basi
What a disgrace
Zimenezo sizachilendo,ku Nsanje kuno,bambo wina ali ndi ana ake anayi atsikana+nse anagonana nawo,wachinayi atagonana naye anapititsa nkhani ku Police,anamangidwa,khani inapita kubwalo la milandu(khoti)chikhalilecho mkazi wake ali naye koma mkaziyo amachita mantha kuti banja lingathe,Zomvetsa chisoni kuti bamboyo ali positive,just imagine,This is a true story,I know him and his daugthters too,its nor kukhwimila 4 him but he is stupid.
Aaaaaaa angomupha mchitsilu
Ycfyçh GHz
l
Mmalala amanei!
Zomamanga munthu woti wagonana ndi mwana wake wobeleka yekha lamulo limeneli ndilopusa aaaaaa kodi lamuloli ndi la boma,dziko,Africa kapena la world? Za ziii
Chitsiru cha munthu
Apa achewa saonapo mavuto ndichikhalidwe chawo
amanga osalakwa koma coz umakolola chomwe unadzala
Ndimadabwa eee mdyomba ingapange zonyasazo kikiikiii usayi chiii
Alibe ulesi ameneyu et dzaka 40..olo kusowa zochitako
shame
Ine sinkuonapo mwana apa onsewa ndi akulu ndipo pofika kupatsana mimba sanayambe lero zangovuta kuti mwanayo ndiwake
ameneyo simwana ndi nzimayi
Yea Ndi choncho, yomwa mazira amayibudula milomo
Zopusa kumuphwanyira tsogolo lamwana awo apatsen life prison
A Lomwe a lomwe !! Mophiya!!
Kkkkkk
Mbuzi kapena kuti nkhuku chitsiru munthu opanda tsongolo galu ngati George chaponda
Vesani uyu simudyombaa mchakumulanjeku akweni
Kkkkkk mulomwe kkkkkk
Vuto la midyimba ndilimeneli,
amangidweameneyo
21yrs ndizimayi wankuru,amadziwa chimene amachita.
Zonse izi nkhani yake ndikukhwimila Basi , zauli basi yakhala pamkhate baba.
shameee
Bmbo zaka 40 mwana 21 ~~~~~ sanamugwilire panali chibwezi apa yamvuta ndi mimbayi pachikhalidwe cha achawa NYASIIIII»»»»»»»
Kumawelenga bwino comment before posting munthuyo akuti ndi wa ku Mulanje umbuli basi
Mulanje achawa ziwakhudza bwanji kumawelenga kaye musanatsekule pakwamwa
Ndiye ku Mulanje kulibe achawa? Kumafufudza inu ozindikila pang’ono.
Next george chaponda
Anayambana kale athuwo, akudziwana mpaka mimba
Nkhani yabwino
Vuto siiyeyo mufufuze chimene amapangilacho mudule ndiye kut sadzachitaso
baaaaaaaaad
Mwana Palibepo Apa,zautsiru Basi!
Kkkkkk zilibhooo
Mulomwe mmmmm Nzeru alibe next is Chaponda
Masiku otsiliza
Nyele chani? Osakanyenga mahule bwanji? Kufunakukwima chani? Mbuzi yamuthu kodi akaziake alibe nyelo bwanji? Ngti alinayo osakanyenga mkazi wake bwanji? Unyakundende ukanyenga khomauziwona ble mwina umangova.
Nyele chani? Osakanyenga mahule bwanji? Kufunakukwima chani? Mbuzi yamuthu kodi akaziake alibe nyelo bwanji? Ngti alinayo osakanyenga mkazi wake bwanji? Unyakundende ukanyenga khomauziwona ble mwina umangova.
Koma Ndzoona Zimenezo
Musana postite nkhani muziyamba mwalemba ndikuiwelengaso nokha then ndikuposta osati nyasi mumaposta zagramalayi,chochobe poti munapeza mwayi ogwila ntchito kumeneko bola mukumalandila palibe vuto