Malawian musicians Paul Subili and Rodrick Valamanja have come out of silence saying they are set to release a new album titled Pastoral.
The duo’s Subili said this at Andiamo Music School in Balaka where he was practicing with Alleluya band in preparation for a live show which will see Alleluya and Real Sounds of Skeffa Chimoto sharing the stage.
Subili told Malawi24 that they have not stopped singing but they had some personal issues.
He added that their break has taught them a lot of things which have made them to come up with music that carries serious and sensitive messages going to different groups looking at what has been happening in the country since they released their last album in 2010.
Asked why they named their album Pastoral Letter, the musician said the word is not new to Malawians because the album is carrying songs that criticise all people in the country.
“As I said we have been listening to the present music and watching what has been happening in the country so the album is criticizing government, nongovernmental organisations, youth and men of God who seem to be speaking for the people but after being bribed by government they betray the nation,” said Subili.
He also expressed concern on the issue of OG ISSA who stopped buying music from the artists as one of the challenges that has made them to be silent in the music fraternity. Subili said the coming of memory cards and flash disk has made a lot of artists not to make profits.
He however expressed joy because their old music is still being played in different local radio stations which symbolises originality and genuine music which gives them courage in the music industry
Adding on the project of their album, he said they are planning to record it with Lulu, Petros Ching’oma and Joseph Tembo
Paul Subili and Rodrick Valamanja who are popularly known as Njobvu ziwiri za ku Balaka released albums like Maidyaidya, Tigwire Mtengo Wanji, Yobu 13:13 and Musanditaye.
Keep on producing nice music njovu ziwili za ku Balaka
Bring it on guyz we mis u
thats good idea keep it up .osat maibidwe amasiku anowa
We patiently waiting for sweet cakes from you Njobvu 2 zaku Balaka.
Iam Zambian and love the music of these two.Of late,I got a consolation by listening to the music of M’LAKA MALILO,but I have come to love his music even more.Ndiye ndingoti awili wa tikuwalandila ndimanja awili.
I love their songs, welcomed back guys
Adali Kale Amenewo Pano Kumangofira Amakonowa
Welcome back. Proud of u people
Welcome back men after missing for a long time
Wellcome boys, lets see wat u have now
Tinakusowani , welcome back.
Music tests changed they should really work hard on it
I like Rod Mvalamanja,nyimbo zake ndi more,zafundo zohitika
To be honest these guys knows better there position than this stupid music zamasiku anozi…zoti kungoimba nyimbo imodzi ikangotchuka ayamba matukutuku mmataonimu kutisowesa mtendere kubwela pa stage kuti ayimbe kumakanika nyimbo yao yomwe.come to this guy poul subili,you will be suprised with his performances with alleluya band…he performs better than these so called oyimba anyuwaniwa, more like listening to their real cd’s…
iiiiiiiii
Bwanji
kkķķkkkk palibe
welcome back njovu zakubalaka,nyimbo za mfundo zinatha pamalawi pano.perekani chitsanzo chanyimbo.
Imbani tibenesebasi
Za ziii. Nkhani ndiyaa Chaponda
welcum back koma msithe type mziyimbako zamakono
OYAAAAAAA!!!!! TATOPA NDI KUVELA NYIMBO ANTHU ASATANIC AMASIKU ANOOOOO!!! Munthu kubadwila ku malawi kukulila ku malawi sukulu yake yonse malawi zakudya zake zonse mmalawi. Koma akuti zao zonyasa zakunja zabwino bwanji kodi mmalawi? OR UTANI NDIWEBE MMALAWI BASIIII
Proud of u guyz onyoza NDE Malawi yo ameneyo. Ajapanda kunyiza zadziwika kuti ndi Malawi. Ndizomwe tatchuka Nazo pa Malawi. Chinaso sanje and ufiti.
Baby suit in my mind
Ukatha watha basi upeze china chochita lol,
Rip Evison Matafale
Vuto Amalawi kutengera za eni,simudziwa momwe akukhalira azanu maiko mwao,yendan muone,chikhalidwe sachiwala,nchifukwa Malawi Ali osauka kamba ka nsanje,tiyen tione dancing yake ati ya kunja koma kutalitali!!!!!!dressing yake parallel,koma ati RNB,siyani za eni tiyen tikonde za mdziko mwathu,ur welcome guyz mwina nkukumbusa chikale
Amene Asafuna Kumvera Nyimbozo, Atseke Makutu. Ife Tigula. Welcome Back Guys….Forward Ever,…,Backward Never.
Penapake ukananyonza mzako uziona kuti ndiwe yani ndipo uli ndi tsogolo lotani galu iwe! Poul &subiri inu bwelani ine ndilipo.
Khwisa boys ( njobvu ziwiri za Ku BK) tiyenazoni zikakoma tili nanu zikanyung’unya mmmmmm tili mu Zambia chabe mmwemu na Nigeria
Humm anthuni zakale pa nthawiyo zinali bwino enafe timanvetserabe ndipo timakumbukira m’mene moyo unaliri pa nthawi imeneyo. Zonse ndi zabwino ndipo zonse ndi zachabe.Muziganiza kaye musanayankhule.
Welcome guys
Welcome.
Most welcome
These guys rocks kkkk waiting patiently.
Nsanje basi a Malawi sitizatukuka tiyeni tipange zathu kuti ena aziyamikile.Kodi inu anakupasani luso lanji?
vuto la a Malawi kunyozana ndikumene kwakula ,mukuti zinthu zinasintha sitingamvele nyimbo zawo ndiye kuti chiani? Malawi wasintha pati? umphawi omweutu .Maiko aanzathutu nyimbo zachikhalidwe zikuimbidwa mpaka lelo.Guys welcom back plz.
Sure amalawi to much msanje welcome guys ife tigula cd yanuyo basi tili kumbuyo kwanu
Kkkkkk
Fikan njobvu tinachisowa chamba chanu balaka woyeee!
Wellcome guyz
Njobvu ziwiri wellcome kuti muzatiyiwalise mabvuto osataya mtima pali anthu sipalephera openga enawa ndi jelasi.Dont be khumu.
Tikulandirani
Njovu ziwiri zaku balaka
Azitorera nde kuti
SIKUTI ABWERE NDI ZAMBWERERATU
Welcome back guys
That’s y aMALAWI tili osauka kwmbiri stimachitana support koma kunyozana bax,wel come back guys mutiveseso kukoma,,,more fire njovu za ku Balaka
Anthuwa ndimayetsa adatsiyana ?? Oyimba ambiri amayamba bwino mngwiridzano wao kumapeto akayamba kupata azipondananso ndalama chomwe chinapangitsa kusemphana pa mngwiridzano wawocho chatha sichizachitikanso????
Hahaha
i welkom u bak in the Malawian muzik industry afta a long tym wthout u,show-case what u hav brought 4 us
Mumatiimila anyamata a kumufz
Most well come
Welcome
WELCUM BACK GUYZ.
Oimba amasiku ano akumaimba nyimbo zapanda m’tanthauze zachamba zeni zeni
Wina ndi #billy_kaunda ngakhale akukakamila kuimba koma style yawo ndiyachimakedzana osangosiya bwanji..
Iwe ndiye usiye kugula nyimbo zakezo, ukagule zomwe ukuzidziwazo komanso ubwino wake samakagogoda pakhomo lamunthu kuti pitani mukagule nyimbo zanga. Ufulu ulinawo okagula, nyimbo za oyimba amene umawakonda enanso ndi amenewa akuti abwererawa. Komanso iwe, ndikadakondwa utayamba kuyimba kuti tiwone anthu atamakunena chonchi ungamve bwanji?
Kodi chifukwa chiyani anthu amayimba ?@ jafali
Koma anthu ena kupusa or kuzimbabweko ali chamba chawo amati sungura kulichinanso amati zora ndiye ifenso amalawi tiyeni tipereke full sapoti
Kwa anyamata athu ozamvera awo amene amakala busy copright zamba zaenu ake ine ndimava chisoni kwambiri
Don’t forget that majority of Malawians are aged between 18 to 50 years, therefore gone are days when Malawians used to listen nyimbo zodandaula.Tell those men to find something to do than singing , coz music industry has completely changed.
N dnt forget that abt or around 95% of malawians live below poverty lines…so music iz a feeling….pipo wld rather listen to such kind of songs.#who knows it feelz it
zoonad bro J Kay nyimbo sikudandaula koma kusangala anthu ndikuwaiwalitsa mavuto kkk this is 21th Century…..wake up man!
Ndileke kumvera Madala Maffo ndizikavera za adole kkkk abwere ndi chamba chinatu
Welcome anyamata akwathu
Pano tinayamba kumvera Hiphop
Welcome njobvu za ku Balaka
Welcome back guys, where were you guys all these years , and you have to bring your friends Henri rash and Mac Miye
Takulandila #njonvu ziwiir za BK
nkhani za masewelo a m’pila
Icant wait my artist
Tatopa ndi 2 ghata 2 ghata wlcum back madolo
Achititseni manyanzi amene sakukondani. well come back anyamata
Wellcome back guyz
Samatha kuyimba ndmakape apite ku zimbabwe ndnyimbo zambwelera zawozo ife oyimba tilinawo ndpo akutikwanila Jungle Jex
Takulandilan njovu zakubalaka
Mmalawi weni weni amene nndimamudziwa ine ndi ameneu, wa CHISANJE wina akati apange chinthu chazelu matukutuku mbwe ngati alimkanthu haha. Ngati ikhale style yakale ija zikhala bwino ati kumbutseko kale sizalelozi.
Welcome back magents, i hop u wil release sensible music as u did b4, now the lyks of mafo,matse,dan lu,nep man,gwamba, etc to be honest they failed our music industry,
Anthu akuda kodi tinakhala bwanji kuthamangila kunyoza ,tiyeni tidekhe muzanyoze muzakamvela sound.
Vuto ndi kusasamba anyamatawo
Mwakula tsopano akanganya inu
Bring back our cultural music Brothers. we missed u alot. Hip Hop, RnB > Over seas.
Ur most welcome mumandivetsa kukoma amalawi tiyeni tizikondana tisamangoziwa kumakonda nyimbo zakunja pomwe azathu akunjawo sazikonda nyimbo zathuzo amakonda nyimbo zao zokhazokha nsanje sipindula takonde amalawi azathu zakunjazo pambuyo
Bwerani akuluakulu Mai anga amasowa nyimbo zoti nkumvera, nanga Mai anga Azimvera Phwaaa! Landira Chimbama,
Welcom
Welcome njovu ziwili.
I missed this duo
Kkkkkk…. When you listen to their songs, it sounds good. But try watching their video songs mmmmm,too boring and scaring.
Welcome back
good news
njala yavuta ayenera kubwera nanga boma siili likubaso chimanga
Bring it on…..This so called hiphop…RnB…they always copy…Bring real Malawi music…local is lekker.
welcome back aname…
Anali kale awa nthawi imeneyo kul ma tape,,,ukafuna kubwereza nyimbo kumachita kupukusa ndi cholembera pano dziko likuyendera technology kunabwera akut ma disc,,ma frash & ma memory card ukafuna nyimbo ina kuli next kapna prev,,,,ndye mangerengere awowo kwawo komko
Mr Sosola it seems like u didn’t get anything from this,,,munayenera kunena kut Welcome back,,,osati kunyoza,,,munabadwira kuMudzi eti?Lmo
Akulu pano zinthu znacntha,,mufuniranjinso umboni wina
kkkkkkkkk koma na ngati zili zachizimwale zomwezija………
njovu ziwiri za ku balaka
A wirinu mumabwera booh tanjoyanso Balaka.Woooye! New technology imakubwezeretsanidi mmbuyo koma osadandaula. Musaaowalenso matate Paulo Banda. Tanjoyanso ndinyimbo za chi Malawi zezeni. Wiihi. Kukhala Moto kuti buuu fumbi kobooo! Kathu kamnyeka.
Pano kulibetu ma type, musazinamize
kuzatani?
This time they must be serous because listeners always have different choises.
Thats good idea
tikulandiran anyamata musavere za anthu osungidwawa amakonda nyimbo za kunja koma akuwatukwanira agogo awo sanje lekan amalawi zanuzo sitivera mulibe langizo tikavereife kumangot champhweteka nchimanga
Kkkkkkkkkkkk aimba chamba chanji pano?? Zinthu zinasinthatu
MALAWI WINA WAKE UTI NANUSO, NYIMBO ZIKUIMBIGWA 2DAYS ZATHELATUZI?? SINDE BOLASO KUMAMVELA NYIMBO ZA KALE ZA LATE LOBART FUMULAN PAUL BANDA NDI ZINA ZAKALE ZINALI ZOTHYAKUKA. NYIMBO ZALELE ZOTI ZIKANGOLILA 2DAYS PA REDIO ZATHAZI. MUSAOPYEZE ANZATHUWA AMAIMBAKO NYIMBO ZA TANTHAUZO TIWAMVELE.
mumangofuna kt mu nyimbo muzingomvamo “ZYA-ZYA” basi, pali anthu ena omwe anawasowa anyamatawa nde musamanene zonukha zanuzo.NJOBVU WOYEE!!
Njovu ziwiri za kubalaka kkkkkkkkkk
Mwatopa ndi kulima??
Akubwera ndi r n b anyamatawa ,paja naye soja lucius anasinthansotu ,
welcome back my brothers ,nyimbo zoti munthu kumavela nkumapezapo nfundo,osati zamasikuanozi .akuti ghetto yuthi adye money kkk koma makosana munthu angadye money ?
Abwere tawalandira amenewo tinawasowa ife.
Maybe they will going to change their style because people nowdays they like #hiphop, dancehall and Rnb
Dont Generalise Pliz.Some Of Dont Like Ur Type Of Muzik.
Hahahahaha but most
People nowadays? we don’t listen to your useless songs its only these savage boys of today they listen to such kind of music, and moreover full of copying what others did already no creativity at all. I don’t have to waste my time your name tells it all.
If u knw that u
That’s why we are welcoming back those two guys coz they are original not fake like your so called Rnb, hiphop playboys.
Kkķkk different likes
aaaaaaa akuyesa ngati Malawi wake ndameneuja tinkavera chiterera chawo chija kkkkkkkk koma xinazi afuse Charles nsaku pano Malawi ndiwina akadamangolima soya kumudzi osati zoimba
Man jealous bwanji inu panokha si dziko la Malawi, inu ngati simungamvere pali ena amene adzatsangalatsidwe ndi nyimbozo nsanje ndi chinthu chimodzi chimene chikubwezera chitukuko dziko pansi.
we r moving forward man,,,, chiterela ai
A malawiii hahahaha. Ife nde timazikondabetu zachikale timakumbukila nthawi imeneyo! yo yoyo mela, osati zalelozi. Kuzolowela wayi chukucha basi. Kkkkkkkk
n that waz real music…not the trash n nonsence that these ladz are singing pano
Ife timakonda chitelera chomwecho man.
Koma ngakhale ayambileso sadzapindulanazo coz zamacompact or ma CD zikupita ziitha akanandifusa ine ndikanamuuza..
Mmmm!! Koma amalawi aeshei msanje to much taimbani zanu tionetu nanga
Tinyimbo tanu tamasiku ano tokoperato ine AYI! Nyimbo koma zakale, za ORIGINAL. Keep it up Njobvu Ziwiri Zaku Balaka!
oimba ake amasiku ano aulesi….nyimbo imodzi koma anthu 15 eni akewo ati collabo..kunena chilungamo oimba alerowandochepa amene akuimba nyimbo ya 3 minutes osabweleza verse..
kkkkk ngakhale mmamidzi anthu tikumveraso zamasikwano..chiterera mmm tinasiya
Mukati azingolima soya zoimba ai anakuuza kuti iyeyo basi ma plan ake ndi olima?? Chipongwe ndi mwano kunyoza kudelera ufiti majelous umbuli unkhutukumve ndi wachabe
Zina kumangoona kusiyana ndi kuchita ma comment ombwambwanawo
Moving forward wake uti apa jealous basi nyimbo zake ziti zimene mukuti malawi wasintha kkkkkkkkk!! Taonani maiko amzathu for example zimvabwe kuli anthu oti naonso adapitita kuschool koma amayimba chamba chawo basi nanga ife amalawi ndi ziti
Ntchito kunyonza oyimba athu basi mmmmmmm!! Koma yaaaa!! Mukalira yomweyo!!!
Moving forward wake uti apa jealous basi nyimbo zake ziti zimene mukuti malawi wasintha kkkkkkkkk!! Taonani maiko amzathu for example zimvabwe kuli anthu oti naonso adapitita kuschool koma amayimba chamba chawo basi nanga ife amalawi ndi ziti
Ntchito kunyonza oyimba athu basi mmmmmmm!! Koma yaaaa!! Mukalira yomweyo!!!
Kodi adali kuti eshiiiiii kutha mkuyambaso bola muzingilima thonje uko
hahahahah their tym iz gone we listened to the back in 2002 3 4 wen we had nothing to listen when they were heavyweights but now there ara superboys who coup their crowns
mwasekatu, ineso ndikusekeni HAHAHAHAHAHAHAHAHAHAHHAHAHAHAHA KEKEKEKEKEKEKE muwawona mmene avutitsile.
avutisa kwa azimwale
Kkkkkkkkk!! Azi mwale ndiye kuti chani taimbani zanu timve welcome back guys balaka woyeeeee kwao kwa oyimba