Malawi Queens beat England to win bronze medal at Fast5 tourney

Advertisement
Malawi Queens Fast5 Netball England

After beating South Africa 36-21 and losing to New Zealand 52-27, the Malawi Queens produced a stunning performance to beat England by 35-32 to win a bronze medal at the just ended Fast5 netball series in Australia.
https://twitter.com/Fast5Netball/status/792639320163098625

New Melbourne Vixens signing Mwai Kumwenda, who top scored for the tournament with 151 points, led Malawi national netball team, The Queens, to famous win which will likely be remember for the side’s spirited post-match dance celebration.


https://twitter.com/Fast5Netball/status/792641429277249536

https://twitter.com/Fast5Netball/status/792639081452711936

The Queens will arrive through the Kamuzu International Airport on Tuesday.

And in the final, New Zealand dominated their Australian counterparts 41-16 to once again be crowned the Fast5 Netball world champions.

Advertisement

223 Comments

  1. Bravo maQueens anga . Nyamilandu mpila akuyendesa ngati chipani mpaka kubela mavoti. Trust me akazangochokapo mpira uzayambaso kuyenda bwino

  2. It’s very unfortunate they don’t get the much needed support they deserve…koma. Koma kakaka ndi mpira wamiyendo omwe sumapindula nkomwe

  3. Queenz nd moooooo guyz osat manyakaaa enawaa,,,,,et amat ndma flamez kayaa,,,,ama ndma flamez kchimbuz kapena kt? I rlly doh knw kkkkkk aaaa FAM nd Sulom shem on uuu…….. Ma Queenz nd dhilu ma Queenz nd zma3lu,,,,,, kip it up!!! Nxt ma Queenz muzakhala pa top bax……. Oxadanda God bless uuuuu,,,,,,,,ndmak3raa olwez osat znazo hahahahaaha

  4. Up up queens amene mukutiika pa map osati #FAM cha kumangodya ndalama zaulere basi aaaaaa jersey chidulirecho ngati mukuchitapo zanzeru iyaaaa mutsitse mtengowo #malawiQueens more fire

  5. I wish if the government can switch its interest from football to netball.
    In simple swap the sponsorship
    Ya azibambo ipatsidwe kwa azimai
    Ya azimai ipite kwa azibambo

  6. Kod tidalakwa chani kut team imenei idzitipatsa manyaz chonchi
    aaaaaaaa frames ofunika kungotaya mnyanjaaaaaa basiiii
    PROUD OF UUU OUR QUEENZ

  7. TIMAKUNYADILAN MAQUEEZ MUMATICHOTSA MANYAZ ZAFIKAPA NDIKANAKHALA PREZI NDIKANATSEKA MPHALA LAFULEMUZI CHIFUKWA AMANGOTHA NDARAMA KOMA PARIBE CHOMWE AMACHITA MUMAKWANA MAQUEEZ PITILIZAN KUTICHOTSA MANYAZ GOD BLSS MAQUEEZ

  8. MULUNGU DALITSANI MALAWI-DALITSANI AZIMAYI AWA KUTI ASAKHALE NDI MANTHA PA LUSO LAWO POPEZA AMATIPUPUTA MISOZI TIKALIRA NDI MASEWERO A AZIBAMBO.

  9. Kufunika kukwatilapo m’modzi apa. Ma queens athu abwino kwambili. Mwaaaaa!

  10. Number 3 in the world, then number 1 Africa, wow thats good news and we are proud of those girls, dont give up next time we wanna be #1 in de world

  11. When it comes to netball, Malawi Queens is the best team that hold our flag, you remove us into shame when flames put us into shame, thumb up netball playerz, u deserve the best!

  12. Ndi Mfiti Yokha Yomwe Siyimayamika Chifukwa M’mimba Mwake Imasunga Miphika, Fam And Sulom Kodi Mukuchita Chani? God Bless Malawi Queens. Congrats

  13. thumbs up 4 the queens,wat an outstanding perfomance.we r proud of our Malawian sisters kkkkkk osati zinazija kaya amati flames kaya .mphale zokhazokha kkkkkkk stadium anamanga ija akadangolimapo chimanga mwina bwezi zitapindula

    1. Zikukugwirizana. Mufumukaziwo amanya ma game angati? Apambana angati, nanga agonja angati? Last year adakunthidwako uko. Stop comparing netball with mpira wa mapazi.

    2. hahaha with the mediocrity that flames put up comparison ikuyenera kuchitika, coZ wen it comes to football in mw there is nothing to show of hahaha mwina ma record oti flames inabandulidwa .sizampila koma masanje okhaokkha#flames siidzamva

  14. Malawi akatero NDE kuti akukoma osati zinazi zopasa an2 mthenda za Mtima ndi B
    P ngat sakupasidwa ndalama inde ndizochepa komabe patriotism is needed

  15. Ndekuti kwasala kumenya ndi Australia ndi Philipines. Kungochinya matimu awiriwa maqueens akhoza kukhala panamba 1.

  16. awa nde amatilimbisako mtima ku Malawi kuno,,,,pliz build gud infrastructures for these ladies ,,camp asamakhale 2 wks yokha ayi koma mwezi or kuposera

  17. Koma azimayi awa ngofunika kukwatirako mu modzi sure akhonza kumalimbikira chimodzimodzi mu banja awa. Zoona kutiposa ife aamuna mu masewero anrhu a football timangokodwa poyerayera ha ha ha koma flames yinalidi yachina Kinnah Phiri sure

  18. Tiwatayire Kamtengo amtsikana athuwa ndi coaching panel yonse,kulingalira ndi ndalama zomwe amalandila amtsikanawa tisaname amalifera dziko,boma ndi ma company achitepo kanthu,takunyadirani ma Quees.

  19. Amatilimbitsa mtima kutichotsa manyazi maQueenz awa Government ichitepo kathu Queenz hve no cort Gvm ikufunika kumanga malo abwino oti ma Queenz adzisewelerapo

  20. To say the truth,nah ngat pali chinthu chimene chikuyenda bwino Mmalawi muno nde Team iyi ya Queens,Timakunyaaaadiran

  21. big up NAM ndi maqeens koma simanyaka a Fam ndi sulom ntchito kubera maclub ndi tima ban tanu topanda mchere tija mungothetsa timabungwe tanuto NAM ilowe mmalo i

  22. MALAWI

    Jane, Chimaliro, Thandie Galleta, Joanna Kachilika, Bridget Kumwenda, Mwai Kumwenda, Takondwa Lwazi, Joyce Mvula, Grace Mwafulirwa and Towera Vinkhumbo.

    Chi team

  23. i edge the government through sports Obama chiumia do something to the Queens considering the way they perfomed need wel stanfard colt believ u me tizakhala number 1 nthawi ina yake proud the Queens bravo malawi

  24. Wow the Queens are just amazing this is probably the best results ever, I only hope that next time we are crowned champion thumbs up

  25. Tipemphe boma anawa akhozeleni mphatso yoposa mpira wa miyendo akumbire anyamata akhumbire mmene zimakomela ndalama mkachita bwino.

  26. May God keep on blessing Malawi. Indeed our football team, the Flames,trails behind on universe but the queens are best and deserve much support. Keep up ladies! U r the soul killer of our nation.

  27. Osati wolezerawa. FAM should put the price of a malawian football jersey at 400(four hundred kwacha)
    How many uppstandard netball courts do we have? The chinese could have built us a 5000 netball sitter stadia than a 30000sitter hall of shame of soccer.

    Up Queens
    Down flames

    Netball jersey 15pin
    Football jersey 4hands

  28. Kkkkkkkkkkkkkkkk kumva kukoma makwini athu apha mdani wamkulu. Pano Malawi ili pa no 3 padziko lonse lapansi. GOOD NEWS FOR MALAWIANS, A football achite manyazi

  29. Great team, great administrators. siza FAM & SULOM with all financial support but failing the nation. Bravo NAM, bravo The Queenz..shame to u FAM, pliz borrow a leaf

  30. Great team, great administrators. siza FAM & SULOM with all financial support but failing the nation. Bravo NAM, bravo The Queenz..shame to u FAM, pliz borrow a leaf

  31. wawiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiii adzikadya macaronne uko azungu wo kakakaka imadoda da da flamequeenz c zochexaaaaaaa 1 n Afriq hahahahahaha wakwiya ndi mfiti,Dr Malinga akuti Go on wth life, Papa o teng kwiyaaaa kwiyaaaa

  32. Great team, great administrators. siza FAM & SULOM with all financial support but failing the nation. Bravo NAM, bravo The Queenz

Comments are closed.