Malawians who were travelling to Blantyre Malawi on Intercape bus are desperately stranded in Mozambique after their bus was stopped from leaving the country.
The bus was stopped because it hit and killed a pedestrian in Mozambique. The vehicle left South Africa on Tuesday and hit the pedestrian before Zambezi River in Mozambique around 9am Wednesday.
A passenger who was in the bus told Malawi24 that the pedestrian was knocked down when he was trying to cross the road.
According to her, the driver did not stop at the scene of the accident fearing that onlookers might torch the bus.
But Mozambican police were alerted and they later stopped the bus. By 9am on Thursday, the passengers were still stranded in Mozambique where they are under police protection. So far, no passenger has been attacked by locals.
The development comes at a time that there have been reports of violence targeted against Malawian vehicles transiting through Mozambique.
Last month, trucks carrying Malawian fuel were set ablaze in the neighbouring country in the civil war currently ongoing in Mozambique.
Bwanji nafe anthu obwera mudziamvetsa kuwawa anzanthu a chitetezo.Koma kuno kwanthu timavutika kwa eninso timavutika.Kodi tidzasangalara kuti?Ifetu timavutika Maiko enawa kwambiri.
NDIZOWON AMW ANZANGA KOMA MONGA IFE OKONDA NTENDELE KOMANSO OPEMBEZA KWAMBILI. Ndizowona zomwe mukulankhulazo koma chimene tingaziwe ndi chakuti mz ndi ziko lomwe lidakhalapo ndi nkhondo anthu ake ndi amwazi tisachimwe nawo kuipa samaphunzila
Anthu aku mozambique ndi oipa kwambiri km akabwera kuno timawasekelera
Koma guys tifera chikhristu amalawife bwanji! Anthuwa amatizunza kwathu kuno ndia fulu heavy!
God bless Malawi no place else! !
Mmalawi #KUPUSA KWAMBIRI l blame Kamuzu Banda anaopsyeza our Great Fathers no wonder we siblings do stupid things always
Vayani asilikali mukuchedwapati muzingomanyada mukavala ka mo4leg nkupindapinda m’mikonomu kumati menya ife ndimeneyotu ayiyamba ngati mukuwopa munene
Mbava za amocambique
Amalawi kupusa kwathuku ndikotipweteketsa naonso mapolice ma roadblock mbwee mmisewumu koma kumangolimbana ndi Chamba chikhalireni wina akudutsa pompo opanda passport zoona zimenezo? Ena akuti amagwiritsa mtchito gatepass, kodi gatepass malire si 20km .nanga kuchoka ku Mwanza kupita Bt ndi 20km nso? Apolice koma kulimbana ndi ma Minbus, Makala, ndi Chamba ndi zomwe amazidziwa basi amatero?
Malawi ulemu utipwetekesa
Poor malawi
Chinthu chofuka kwambili aliyese wochokela ku mozambique amphedwe
Guys..please read the article carefully and understand it before typing your useless comments here…and if you have no understanding of the story whatsoever then it is wise of you to just shut up…and read other people’s comments. #concerned….
athama ngisidwe anthu akumoshiko basi ndianthu oipa
basi malamulo agwire ntchito hit and runner
we malawians y do we luv our enemies? chonsechotu ma refugges frm the same mozambque akusungidwa by amalaw tomwefe! bt kwenkwen tkuwasungiranj??here in mwanza!
Don’t change the subject admin: Prophet Bushiri is selling the blood of Jesus.
SA detain 16 people at mesina police station almost a week without water after a driver abandoned fled the soldiers roadblock and abandon his bus with passangers on it
Ndatha kuvetsetsano vuto sinu a Malawi24 koma awa akuwerengawa paja pali kuva ndi kuvetsetsa nde awa angova sadavetsetse muwakhululukire
Kodi ife timawanyengela bwanji?Iwowa magalimoto awo amadutsa muno koma sanachitidwepo chipongwe nde tawotchela ma Galimoto awowo
Chisoni chinachuluka amalawi 3rys ago kusanje apolice amoshicowa musaiwale adatiphera wathu kudambo boma or kudzudzula. Dziko malire wake sakhala njira amakhala river moti ifeo malire wake ndi kuzambezi bridge akutizuzanso amene akutsutsa andipeze ku inbox
MMMMMMM ZABODZAZO
boma lathuli ndiye mmmh ndilopanda pake ndithu aMZM adayamba kale kale ziwembu koma saopsezedwa aMZM kodi kumakhala kuopa? ndichifukwa chiyani chomalembera asilikari chaka ndi chaka? Ntchito yao ndi kulanda makala ndikupita ku DRC RUANDA ndi SUDAN? iyaa
Free data! free data! Ukuononga ntundu wa anthu ndiithu! Ma comments nd nkhan parallel! Kkkk try somtymz kmakhalako nd ka 50 ba kotsekulirako tmalink kut mudztha kwerengako full story! B4 commenting! Eeiish! Enanu mukungoonetsera2 umbuli bwanj! Sorry! Vuto siinu koma free data!!
Alomwe Ndi Omvuta
Life.
Kapeu angofuna ma coment bax
Nkhondo ku #moçambique sizatha inakali mkati pano,ndiye eeeee xorry opita ku south africa.
tisanayambe kunyoza or kutukwana tiziyamba tawelenga nkhani kuti ikutinji not kungona ka headline basi mwanyoza kale muzanyoza nkhani zabwino nazo shame shame on u guys
Iyabitsen kumeneko tikubwera
Intercape ndi bus ya south Africa si yamalawi nonsense ndege ikapangidwa hijack amakaitenga ndi eni ndege osatinso eni ma passenger ..do u assume kuti onse anali mu bus yi ndi amalawi okhaokha?? Mxm ! Poor reporting!!
hey these are poor minds people coz most of them are uneducated
Koma inu a 24 uzatipangisa kuti tinene boza kuanthu zomwe mkuchitazi, bwanji simkupereka full story
sangayibwenze popandachifkwa??????????
Renamo !!!!!
Bad
How I wish this page was blocked!! Ur full ov shit u Malawi 24.
What exactly happen for the people and a bus to be detained?
Pemphani boma likawatenge.
Braz tikutumidzen mupita? Kkkkkkk
Ife nkhondoyo ayi!
Kuzolowela nkhondo agalu amenewa
Eeeee komatu hehehe kugothamangira ku comenta musanawelenge nkhani yose kkkkk pali link apo kuti muwelenge koma free data ndiyo yavuta…..bus inaguda munthu and sinaime pamalo angozipo nkana awagwira
sukunamad uh akatero azifalisa zaboza
Kkkkkk ngati unama .mmmmm a Malawi sazatheka basi.
Chonguuuuu!
Dis z de true story but it waz not an intercape bus yomwe inagunda mwanayo.
A Malawi ndife anthu opusa pa chilichonse nanga lero si izi.
dont force mater becz mater gonnar force to move
Bad mind never take a live
Eeeee tiwopa kubwerela kumudzi
Dats fuckin shit
https://m.facebook.com/story.php?story_fbid=10154298769243834&id=72003263833
Let’s fight against them. Akutionjeza ……….sure
too bad
Mmmmh my Malawi kumvetsa chisoni.Nkhani simunawerenge koma kuthamangira to comment.Pali link yomwe a Malawi24 ayika kuti mupange open kuti mumve nkhani yonse koma mukuwauza kuti angokupatsani headline yokha??? shame shame shame
Ma units alibe, paja kuli Fb ya ulele
It pains me a lot ndikamaona anthu akuyankhula ngati ozindikira koma akuonetsa umbuli.Ndiye kulibwino kungokhala than kupanga comment pa nkhani yoti sunapange gather much needed information
Sad
Akufunanika Kuthilana Nawo Bout Kungoti Malawi Ndiyaulesi Bad
malawi24 mudzitiwuza mkhani mwa chi ndunji.Izi zimachitika nthawi zambili not only in Mozambique.
koma posachedwa pompa ndimaonera mkhani pa mbc kuti chiwelengero cha anthu akumozambique mmakampumu chakwera koma iwo akupangabe nkhaza athamangitsenimo ndalamazo muthandizire anthu aku malawi kumkuno nduoyekedwa bwanji amenewa
Malawi 24 try to give us full story not only headlines {thanks}
thanks ngati zenizeni! can’t you see a link pompo? timasindikiza mawu a buluwuwo mkatimo mumakhala nkhani yonse…I hope suzabwelezaso
Thanx andrea for collecting me, but i try idd’nt see full
I know Malawi imadalila mulungu mudzina last yesu mlungu ali ndi inu
Mmm mwanyanya ku kongora akukwatirani kimeneko salora kuti ndi amuna anzizathu ameneo
Intercape yake iti poti pa mwanza pano yafika kale kuchokera ku juberg
Bus yo akuti inaomba munthu ndie driver sanaime ndi chifukwa chake ikusungidwa Ku police.
I’m not happy with it
what actually happened,flee de innoncent mw’s failing which iwil stab any mozambican 2 death hu wil seek medical treatment 2 mw.they hv crossed beit bridge n who r u 2 detain them
This is bullshit#Malawi24
maybe these Malawi 24 dont travel thru Roads! its not the first time! its their Right to detain the bus if they have the reasons to do so! Who knows they might be protecting the bus and the people from some major accidents! Malawi 24 be specific and find enough evidence b4 writing you wrong info the audience! Which at the end of the day you are contributing to the ENERMITY among nations thru us(people).
i dont see anything wrong with malawi24.they have jxt reported as it is& didn’t say mozambique is wrong to detain the bus.they further said no malawian has been harmed as they are under the protection of the police.what’s wrong there?
have red the full story or ukungoti bola walavula mawu akowo? anthu enanu kma
have you read the full story or ukungoti bola walavula mawu akowo? anthu enanu kma
Guyz ngati chilichonse mukusutsa nde chanzelu chikhala chiti? dnt forget this z nt politics
Inu a #Malawi24 takutulukirani kuti ndinu abodza chithunzi chomwechichi last tym usaid amalawi ali stranded ku Benon south africa kamba koti anabuka bus yamunthu osamudziwa lero mukutinso amalawi ali stranded ku Mozambique zoona zake ndiziti? do u think we dnt hav eyes kuti sitingaone chithunzichi kkkkkkk
nonsense!! iwe sibola wava nkhaniyo? iwe can’t u see kuti basiyo ndi intercape?,,,kkkk
The tumbuka expert,dont forget they are well educated.. ???
Iwe chinthunzichi is just for illustration purposes can’t u just use common sense sometimes?
Nkhani ya basi yaku Benoni ndiyowona akulu muzipanga follow zinthu bwino bwino mwene
Iwe khaya ukuziti chavula kaya chavala,do you think pple can comment b4 they read? Iwe ndi mbatata eti. Umaona ngati coz u r a tumbuka so u r wise. Ukutukwanitsatu atumbuka oganiza bwino not mamina ukuyankhula apawa. Wapurika siBWEni?
Amene mukusutsa nkhaniyi ndinu dzitsilu I dnt knw kuti munayamba mwawerengapo nkhaniyi? anena kuti malawians ar stranded in SA kamba koti bus imene anapanga book yaonongeka ku Benoni nde dziko lamalawi latumiza bus kuti ikawatenge chithunzi chake chomwechichi
Iwe #Conel ys we ar well educated so wat? uli nafe milandu? idiot i
Okay ndamvaa
Please use alternative routes, guys isn’t there any route beside mozambique?
Aphwitikizi amenewa ativuta bwanji
Wats rily happeng in Mozambique ??
Plse, Malawi 24 try to give full details on what account the bus has detained not only give the headline and stoped. Thats no sense.
free data ikupusisani.what details do u want?the bus hit a pedestrian and the driver did not stop.it was later detained to allow investigations be undertaken.meanwhile,no passenger has been harmed as they are being protected by the police.ndakuthandiza m’bale wamvako i think
Lol
iwe mbuzi eti? can’t you see the link down there? free data imeneyo? lol!!!
Open the link kuti unve zenizeni
This Mozambicans must go to school real they have lot of shit nxa_aaaaaaaaa
Anthu woyipa aku Mozambique awa, chikhalirecho akumabwera mmaliremu kumafika mzipatala kumalandira mankhwala a ulere, mtawunimu akumabwera kumagula katundu wosafunsidwa chirichonse komano tikapita kwawoko zochitika mbwee, tinafatsa kwambiri a Malawi.
mocambicans r wild dogs, heartless animals.
Did u research y de bus ws detained?Think b4 u speak.
Pofatsa panadutsa koma kupepera anthu amenewa amandikwana zedi
No need to research anthu akumozambique ndi ankhaza kwambiri
mwati kufatsa eti,kulemekeza kapena mawuwo..ndife an2 opumbunara m’bale wanga continent yonseyi
I hate this people aaaaaa
Anthu woyipa kwambiri amenewa, timawona zomwe zikumachitika, no need to research atate.
Hahahaha! Koma Bwanali,mpakana anthu opumbunala. Ifedi ndife aboboyito
Sorry
SI BOO KUTI AZITIPANGIRA NKHANZA IFE ANTHU OSALAKWA KOMA AZIWE KUTI NJOKA YOFASA IMALUMA KOOPYA
koma mukudziwa zoti company ya intercape si ya ku malawi?if it was malawi police,would they let the bus go?
Jms jnr mulewa wagundikatu kuwalongosolela hahahah
Mozambique Now, Is Not A Good Root To Use, Coz It’s Now A Battle Field, Then Fuck Policia Moc,ambicano.o
Correction ROUTE NOT ROOT
I Use Shortcut Words When Typing Here…#Tabeni Gondwe
Kodi tiyenda mwamantha chifukwa cha Mozambique
It’s A dead Country Man!
That’s too much im preparing to go home now l must think what will happen in Mozambique border.thy full of shit
Try To Use An Aeroplane Man!…lol.
Yeah i think is plan B i will do that lol.
The Problem Is These People, Are Not Well Educated And They Don’t Even Know God, They’ve Been Inthe Jungle fighting For So Long Thats Why They Now Act Like Wild Animals.Then Killing Is Not Aproblem For Them.
Kkkkk
But they mustn’t take chances on us. bcoz we don’t like fighting
Yes! U Better Use Airway Root When Homecoming, To Avoid Dieying Hard…lol.
#Hydron lakhulani bho as human being.
Kwa amene amayendapo zomwe zimachitika akuzidziwa,,, Malawi24??
Thanx malawi24 for informing us bt ur English should be well constructed .
koma a malawi kufatsa udyo
Mmmmmmmm talembani za nzeru kungomva musanafufuze
Agaruwo athamagiskeni kumarawiko basi kwawo akuvuta bwaji!?
nnmmmm dziko lokanika iri
amalawi mwatani kodi,atiwotchele mathamkala amafuta,atiphele anzathu kumangosekelera ndiye azithawila kuno asowe let them go back home.
I hate Mozambicans
zabodza bax the bus arrivd in blantyre ystdy
its true da bus its still their. i gat a friend who is on bord
That’s 2bad
i dnt c n thing wrong here, tel us smthng.nkhani zakutherani eti? its the same f t happens here n malawi,th veco z t b detained pending investigations.
U dont know these people when you are involved in an accidents
kod iweso ukukamba chan,iwe nde mbewa yeniyeni ndizosangalasa zimezo,,atipangilapo ziwembo zingat aku Mozambique
Tamuwuzeni sakuwadziwa athu akumozambique
chitsiru cha munthu kumalankhula zopusa anzathu akuvutidwa galu mako
Is informing people on this issue having no story to tell? mkuru ndinu osekesatu kwambiri!
You don’t see anything wrong? i don’t think you’ve ever travelled through Mozambique, coz if you could ever travelled then you would have seen something wrong, mozambican police are bastards!
sioseketsa kma omvetsa chisoni. zima bastard di zapolice za mozambique adandizunzako ine ndili ndi mwana kumbuyo.
mulibe m,bale wako ndichifukwa chake ukukamba za ndowezo iwe uli ngati boma laMw kuopa pochita zinthu eti?
Nayenso Ndi Wakomweko Thats Y Akunena Zopusazo.
Iwas arrested coz didn’t shown them money when i was travelling to SA,these pple are idiots and wena u busy commenting shit u ain’t clever buh abig fool uyanya
Menyanani. Ati ailuze atola malaya athawe yekha.
Yalakwanso chani bus????
ooo ma gosh!, they are at it again!
Its there own mistakes because every one knows that Mozambiki now its hard there is no peace.if people are killing each other and we already loose our cars even the fuel steel need to connect its your mistake not from god.
I think ua drunk,,therez no any country pipo dnt travel,mozambique is not an island neither.
MDF bwanji mungomenya ka friendly paja mungokhalatu, mpata wapezeka tiwone mphavu zanu…….God bless Malawi
Achimwene simukudziwa zomwe mukunena ,Mukadzaziona mdziko mwathumo simudzayiwara pamoyo wanu wonse, Tango uyesani kuyenda m’mayiko momwe mulikhondo mudzaone, Kuno ku DRC anthu akuvetsa chisoni amai ndi ana, alibe mpata owonera tv or pogona alibe , Mulipabwino musasilile azanu ali pamabvuto
Zoona madala ife chathu ndichikondi basi
What kind of pple r mozambicans?tgere hearts r full ov war..tzmawathamangtsanso kwathu kuno ationjeza iyaaah!
Jesus,,, eish was better de drive to stop the same time Mozambique mmmmmm people are tough especially police haaaa
Wts th main reason to detain th Bus?
bad news koma dziko limeneli likufunika mapemphero
Mafana amenewa amaopa mphezi,,kod GENERAL YOHANE anamusiila ndani?
Tatyen Tngowapha Awa Akumozambq Akumathawa Nkhondo Ndkumabwera Kunowa, Kuno Ndy Kothawira?? Kwawoko Kungodusa Kokha Azitpanga Nkhaza?
ndipo inu
God will protect them, nothing will happen to them IJN.Much love from Nigeria
tiwathibule amane ali kuMalawi kuno
Wao,,,,,,das 2 bad.
Mmmmmm please god help them
Dziko lokanika ngat galu,anthu alakwitsa chani nanga?eish,we must teach them a lesson which they cant 4get it..iyaa,nkhaza bwaa….
no where in this world where a driver would hit a pedestrian,mkuthawa a police mkusachitapo kanthu.even kwathu kuno zikuyenera kutero baxi
thats 2bad
thats 2bad
Shaaaa
Anthu oipa awa akuiwala kuti akumathawila kumalawi komweko
Not gud
Kodi amalawi tidatanit zina zilizonse kuopa anthuwa akutijaila zedi kofunika kumathana nawo zitsiru zaanthu kwabasi
WHY?
apeza polekera
Chifukwa chani? @ #malawi-24
tithana nawotu asa jaire
Let them go their families are waiting for them What’s wrong with u Mozambicans
Kuzolowera Nkhondo Amenewa
Saziwa nkhondo agaluwa ask soldiers who go for U.N. peace keeping, they ‘re the list when it comes to training…