Reports reaching Malawi24 indicate that Malawi’s former Deputy Ambassador to Ethiopia Doreen Kapanga has been arrested.
Kapanga who was Deputy Police Inspector General before being sent to the Malawi embassy in Ethiopia has been arrested in Lilongwe, sources privy to development have confirmed.
Last month Malawi24 reported that Kapanga and secretary Fletcher Chowe in Ethiopia were suspended on suspicions that they were involved in a series of corrupt activities that saw the Malawi government being defrauded money amounting to MK293 Million.
Initially, the amount a preliminary audit came up with was MK20 Million before it skyrocketed to MK293 Million after a subsequent audit.
Zisakomele mbuzi kugunda galu azimangwidwa amenewo osati nthawi zonse tizimva mwapasa bail zichepe. Oba nkhuku imodzi pompopompo koma awa nde eeeeish, zimatipweteka.
Kodi mwamugwira kt chilungamo chiyende kapena mwasemphana ku ndale mwina tiziti mukufuna kt akugayireni ndalamazo? Osati vutitsa ndizakumva ife.
Palibe chifukwa chomauzila mtundu wa Malawi zandlama zobedwa zambilimbili pamene iwo akukonza makomo awo ndi 50 kwacha zachamba kwambili zimenezo. Mukamaliza chumacho chomwa amalawi amavutikilacho likubwela tsiku lachiweluzo mudzawafuna. Mulungu adalitse ma fell Malawians anzanga.
Wawezye zyose pala walinazo BOMA likagulire munkhwala muvipatala.
Zani Muwone.
Office abuse at its best thinking the long hand of the law is short to hold on the culprit.THe nation is suffering right now for acts perpetrated by such people.Who can we treust if Administrators who have the fiduciary obligation to look after Public Resources are the same defrauding the Government dubiously without conciousness with the outcomes.?She might not be even the only one,some are doing it or have been doing it and she copied from them who knows?
Wonani Tsono.
Ndalama zonsezo mmene pavutira pa malawipa? Pano funding ya April siinabwere ma department a bomawa,mu zipatalamu mukusowa ndi zikolopa zomwe,wina kungombwandira chuma chonsecho.
Nkhani ngati izizi zinafika pokuti a Malawi fe musamatiuze chifukwa nzopanda phindu. Izeki uwuse mu mtendere wa Ambuye
Yet DPP has the audacity to tell us that CASHGATE was a baby of PP!!!! What DPP begun under Bingu is continuing.
Amen malila mtonga
Yooh
Kkkkkkkkkkk,Malawi for sale,my mother Malawi kuyenda yekhaa….so sad my beloved country.
mukutitenga ngati ana eti inu zibani no worries ife sitimadya ndalama zaboma ayi ine zanuzi zachisakhozi zimandinyasa heavy mwava agalu inu mboro zamanu pantumbo pano noonse anyani mwatha ntchito muziyenda mmidzimo muziona mmene amzanu akuvutikila muziba ndithu.
ndamvanawo poti makutu alibe mpata bt ihv nothing todo with that,mbava zikuluzikulu ngat izi kumalawi kuno boma silimanga kma amphawi nde ishhhh!
Eeeeee sopano mukam’manga abweza zonsezo
Atakhala oba mkhuku akaseweza .poti ndalama muyiponda
wakuba nkhuku ten years wakuba ndalama zaboma zambiri three kumeneko ndiye ku malawi.
Mbuzi imadya pamene aimangilira.
…..
Really Malawi is not a poor country Nanga ndalama zonsezi zapita mthumba lamunthu kodi sizikadalipira ku company ya soap kapena fertiliser kuti amphawi athe kugula okha pamtengo wothandidzidwako ndi boma .Nanga zomwe zabedwa mosadziwika nzingati?.kungoganidza chabe.Ambuye bwerani muzaweluze dziko la Malawi
You can say that again Henry ,eisjhhh
Life is difficult for the poor trust me monica
Mmmmmm amutulutsa si mulandu umenewo, koma anakakhala kuti waba nkhuku pano atamutcheja kale zaka
mumapindula chani abomanu simuwina milandu mukutinyasa bwanji chabwino mukawagwira ndalamazo azigulira chimanga
Takumana mbava zokhazokha.
anyapala amenewa tizithira moto aaa mxiee
Ameneyo Nde Malawi Ine Siningadabwe
Inde anthu ena adyelapo ma allawance woposela pa k293,000.00 yobedwayo.
Dziko lathu ndi lolemera gyz koma timaoneka osauka chifukwa boma limene limalamulira mukumakhala mbava zambiri
Akangoyamba njomba ameneyu sathekanso. Mumva kt bp yanga yakwera.kkkkkkk azimayi ndi mbava zedi kumalawi kuno.
Gulu la cashgate limenelo. Osamanyengerera. The money which is easy to steal is that in the Government . Refute that as well . Kkkkk
lets kill o thieves in malawi not okba nthochiwa ayi.Akayamba kudwala ameney sukambidwanso
olemela amalakwa koma chuma chao chimawabisa komabe aziwe kuti sazadumpha dzenje lamanda
Tikamati inu ogwira mu boma mukusakaza misonkho yathu wena mumatstutsa .lfenso apathebafe pafunika pamwanza tisamalipire customers .chiyambire sitikuwona komwe kumapita phindu lathu .ma office apa boader osalongosoka timakontena tosapentedwa. Ma million omwe akupangidwa pa hour amapitakuti?
Suspicious or she has take indeed?…. If so amangidwedi cos zimangothera momwemo
ZAZI KUSOWA NTXHITO EETI KUNGO NKHALILI KUSECHANA BASI TSIKU OSAPITA KUKHALILA KUMANGANA MMMMMM MPAKE MALAWI SAZATUKUKA
Kumugwira nde mwamugwiradi, koma kuti mlandu uweruzidwe eeeh it wil tke deiz, wks, months & yrz,oky fyn zonsezi Mulungu akuona one dei He wil spk 4 us.
Amufinye zenizeni ameneyo sanali yekha awulula.
Ndamene-akutsaukiza-malawi–Ndalama-zimenezi-bwenzi-dziko-muno-atapangila-njila-zachitukuko—-this-country-Eishiiiiuiiuuuuu
Iiiiiiiiiii ndiosadandaula awo poti ku malawi kulibe ndende yawo koma ndikadakhala mphawine kuti ndaba mk10,000 bwezi pano atandigamula kale 8years imprisonment with hardlabour
Mwatelo man kkkkkkk
Inde ndatero moyo ukomera alinazo
Nanga inu mul mbal it?kkkkkk
Mmmm jo disadvantaged side
Wakulu inu.kunenera amzanufe kkkkk
Rule number 1; steal but don’t get caught
tinaoni basi osanyengelelaso
Arresting All Thieves Is Good,
Eee koma azimayiso ndie mukutsogolatu.
Our country is full of thieves
Long case
Ooooh! Shame, very good