Breaking: Ex deputy ambassador to Ethiopia arrested

Breaking News

Reports reaching Malawi24 indicate that Malawi’s former Deputy Ambassador to Ethiopia Doreen Kapanga has been arrested.

Kapanga who was Deputy Police Inspector General before being sent to the Malawi embassy in Ethiopia has been arrested in Lilongwe, sources privy to development have confirmed.

Last month Malawi24 reported that Kapanga and secretary Fletcher Chowe in Ethiopia were suspended on suspicions that they were involved in a series of corrupt activities that saw the Malawi government being defrauded money amounting to MK293 Million.

Initially, the amount a preliminary audit came up with was MK20 Million before it skyrocketed to MK293 Million after a subsequent audit.

Advertisement

50 Comments

 1. Zisakomele mbuzi kugunda galu azimangwidwa amenewo osati nthawi zonse tizimva mwapasa bail zichepe. Oba nkhuku imodzi pompopompo koma awa nde eeeeish, zimatipweteka.

 2. Kodi mwamugwira kt chilungamo chiyende kapena mwasemphana ku ndale mwina tiziti mukufuna kt akugayireni ndalamazo? Osati vutitsa ndizakumva ife.

 3. Palibe chifukwa chomauzila mtundu wa Malawi zandlama zobedwa zambilimbili pamene iwo akukonza makomo awo ndi 50 kwacha zachamba kwambili zimenezo. Mukamaliza chumacho chomwa amalawi amavutikilacho likubwela tsiku lachiweluzo mudzawafuna. Mulungu adalitse ma fell Malawians anzanga.

 4. Wawezye zyose pala walinazo BOMA likagulire munkhwala muvipatala.
  Zani Muwone.

 5. Office abuse at its best thinking the long hand of the law is short to hold on the culprit.THe nation is suffering right now for acts perpetrated by such people.Who can we treust if Administrators who have the fiduciary obligation to look after Public Resources are the same defrauding the Government dubiously without conciousness with the outcomes.?She might not be even the only one,some are doing it or have been doing it and she copied from them who knows?
  Wonani Tsono.

 6. Ndalama zonsezo mmene pavutira pa malawipa? Pano funding ya April siinabwere ma department a bomawa,mu zipatalamu mukusowa ndi zikolopa zomwe,wina kungombwandira chuma chonsecho.

 7. Nkhani ngati izizi zinafika pokuti a Malawi fe musamatiuze chifukwa nzopanda phindu. Izeki uwuse mu mtendere wa Ambuye

 8. Yet DPP has the audacity to tell us that CASHGATE was a baby of PP!!!! What DPP begun under Bingu is continuing.

 9. Kkkkkkkkkkk,Malawi for sale,my mother Malawi kuyenda yekhaa….so sad my beloved country.

 10. mukutitenga ngati ana eti inu zibani no worries ife sitimadya ndalama zaboma ayi ine zanuzi zachisakhozi zimandinyasa heavy mwava agalu inu mboro zamanu pantumbo pano noonse anyani mwatha ntchito muziyenda mmidzimo muziona mmene amzanu akuvutikila muziba ndithu.

 11. ndamvanawo poti makutu alibe mpata bt ihv nothing todo with that,mbava zikuluzikulu ngat izi kumalawi kuno boma silimanga kma amphawi nde ishhhh!

 12. Really Malawi is not a poor country Nanga ndalama zonsezi zapita mthumba lamunthu kodi sizikadalipira ku company ya soap kapena fertiliser kuti amphawi athe kugula okha pamtengo wothandidzidwako ndi boma .Nanga zomwe zabedwa mosadziwika nzingati?.kungoganidza chabe.Ambuye bwerani muzaweluze dziko la Malawi

 13. Gulu la cashgate limenelo. Osamanyengerera. The money which is easy to steal is that in the Government . Refute that as well . Kkkkk

 14. Tikamati inu ogwira mu boma mukusakaza misonkho yathu wena mumatstutsa .lfenso apathebafe pafunika pamwanza tisamalipire customers .chiyambire sitikuwona komwe kumapita phindu lathu .ma office apa boader osalongosoka timakontena tosapentedwa. Ma million omwe akupangidwa pa hour amapitakuti?

 15. Suspicious or she has take indeed?…. If so amangidwedi cos zimangothera momwemo

 16. Kumugwira nde mwamugwiradi, koma kuti mlandu uweruzidwe eeeh it wil tke deiz, wks, months & yrz,oky fyn zonsezi Mulungu akuona one dei He wil spk 4 us.

 17. Iiiiiiiiiii ndiosadandaula awo poti ku malawi kulibe ndende yawo koma ndikadakhala mphawine kuti ndaba mk10,000 bwezi pano atandigamula kale 8years imprisonment with hardlabour

Comments are closed.