The sports fraternity in Malawi will still have to wait a little longer until the magnificent Bingu National stadium is opened as money amounting to K500 Million is needed to wind up core works before the facility comes to full use.
This was revealed by Sports Minister, Grace Chiumia after she led the Vice President Saulos Chilima in a visit to the facility in Lilongwe.
According to Chiumia, the money is meant to be used for the maintenance of the sewer system, planting of network and electricity cables among others.
She said that this has come about due to emergency situations like floods which saw government coughing out a lot of funds.
She says the Ministry of Finance and Economic Planning has been informed on the required money and that there is hope it will give out the money so that the stadium is opened for use.
”We require up to K500 Million and we hope it will be given to us soon. We assure Malawians the stadium will be opened this year” said the Minister.
On his part, Chilima asked Malawians to take full care of the facility when it comes to use so that it lasts long.
While arguing that the issue of planting flood lights at the facility could not give government a headache now, he said in the meantime all the games could be played during day time until the lights are made available.
The initial plan was to open the stadium by June this year but this revelations mean the stadium will not be opened by that time.
The K26.6 billion Chinese government-funded stadium will attract the soccer fraternity since it has 60,000 capacity, a far higher capacity than that of the old soccer cathedral, Kamuzu Stadium.
I wish all of the best to our intentional stadium.

Basi chisiyeni Malawi needs that more in other areas than sports which is just entertainment.
Mukuti dziko lathu liribe k500 million? Ndakaika.
Last days indeed
Last days indeed
If that is the case government must write proposal and submit to ian chidzulo investment then I ll borrow the government such amount
Kkkk kkkkkk koma
kkkkkkkkkkkkkk mukuseka man kkkmm ndalama zili kwa Ana masiku ano

Kodi mmesa akuti contractor anapereka chithu chi kuboma kusonyeza kuti anamaliza ciliconse??? Nanga mukamati ndalama zikufunika 500 million to complete mukutathauzanji??? Mukundiuza kuti boma LA China linapereka stadium yi kuboma ulibe matoilet komanso zithu zina zili zosamaliza??? Ndikukaika mwina winanso akufuna adye ndalama zina Poona kuti stadium yi yatha kapena???

Borne in poverty Die in poverty thats Malawians, no peace, fredom, unity, food, money, every thing. Just like empty backet. Mmmm koma tili pamoto
Big up Malawi!! Mwatichotsa manyazi !
Joyce Banda anakatenga ndalama ku China nkumanga stadium nde mwati inu mwalephela kutsegulila chifukwa chani? Hahahahaha! put politics aside.
Ndi akadzi opusa okha, amene amalola amuna awo kukagula zovala, pamene m’nyumba mutagwa njala
The chinise government did an incredible job,but it our government which is a flop.You the whole government cant release K 500.000000?This is joke.Then privatise it some people should take over.
Just pray to God,nothing z impossible
Yamangidwa ndindalama zaife amalawi
Kkkkkkkkk kuba kwa kilini komapisa wekha nthumba nkupeleka
Poyamba munatiuza ife?? Mwaona zakukanikani mufuna mukusuzumira mmatumba awanthu osauka tiyeni ukooo!!!

500 millz z nofing pliz petr and ur govt do somfing on dis zinyawu stadium even walter and ur stupid fam u can raise dis money if u werent greeeedy
How can I explain this testimony to the public about a great man who help me out in serious illness I have HIV AID for good 3year and I was almost going to the end of my life due to the way my skin look like all I have in my mind is let me just give up because life is not interesting to me any longer but I just pray for God every day to accept my soul when ever I’m gone lucky to me my kids brother run to me that he found a doctor in the internet who can cure HIV online he help me out on everything, the doctor ask for my details, so he can prepare the herbal medicine for me from his temple after all he ask is done one week later I started getting more stronger my blood start flow normally for 4 to 5 days I start getting Wight before 6 days my body start developing my skin start coming up after 8 days which he told me that i will be completely healed, I went for HIV test and I was tested negative I’m so happy that I can say I’m not a HIV patient if you have HIV/AID or any sickness he can still help you in getting your ex-back to you please contact him via his email: [email protected], or whatsapp him on +2348143143878.
ask bushiri to help
Uku nde kuyesana
mukagule madeya a5milion kuzambia tidye than zazii ngat zmenezo amalawi kusalila ngat tinadya thak..lagalu
zachabe chabe.sitimasekerela zopusa.
Kudya kulipo.A country where production of audited accounts if not necessary.
kuzolowera kuba basi. masende
Zikuchita kubhebhatu
Koma anthu osaona pataliwa kkkk bizy bizy kusaka njira yosololera dollar
How many capacity or siter for that
Ha ha ha this is buying time! This government want to use this stadium as a tool to 2019 general elections basi paja a Malawi we are weak minded always!
ikanakhala ku Blantyre bwezi itatha.
Vutorakwathu rimenero
Panyapawo mbava zimenezi shupiti
Panyapawo mbava zimenezi shupiti
ndiye mwati million osati billion kkkkk koma maiko enawa abale inu
a 5 miter pali chani apa agomenyesa mzuzu dabe,komanso bt dabe pabwalo limenero basi ndalama zapezeka koma osasololora

Yatha basi chikopa chiyambidwe Apa. Akungofuna kugawana dollar Zomaliza agalu amenewa.

Moti muzikakambilana za stadium pamene ogwila ntchito ku EDUCATION ndi ku HOME AND INTERNAL SECURITY ANTHU Mawachotsa ntchito mumanama kuti headcounting sipeleka mavuto lero anthu sakulandila tinene kuti mumauza zoona amalawi?

Ma program a boma ngati personal programs, ndi zosatheka ma program a boma kumayenda ngati amapanga ndi modzi

boma likapephe thandizo kwa masten paja mwala wamaziko anaika wokha samaphweketsa masten.

Ngati mungakondetu ndikubwerekeni k500m yakatapira mumalizire ntchito yatsalayo.

Zautsilu eti mupange spend ndalama zonse chonsecho pipo are dieng ndinjala kupanda zeru. Eti atsongoleri onse opanda zeru ndithu mulungu azakulangani mukuzuza mizimu yake

Mboli usiku
I hate Unitary government more than toilet shit cos poor never benefit

Yaaaa dzilipilipo
Ineyo sindimazimvetsa za chuma.Ndinamva kuti boma linakongola ndalama zomangira stadium mothandizidwa ndi china ndipo izabwezedwa pa zaka khumi.Pano ndikumva kuti akalowa parliament 500 mil ifunika kuti amalizile.Komanso sakanatha kumamaliza stadium pamene anthu akuvutika ndi njala.Kodi pamenepa zimayenda bwanji???????? Yamangidwa ndi ndalama za ngongole kapena za budget ya malawi?????
Za ngongolezo anagulira chimanga chifukwa chanjala ,komanso zotsalanzo ndi zimene amangilazo,kukongola Ndalama chifukwa cha stadium ,mesa anaona kuti sangakwanitse kuyamba ndi kumaliza ,

Kkkkkkklkk oyessss kkkk Kuchitekete
Kkkkkkklkk oyessss kkkk Kuchitekete
Kkkkkkklkk oyessss kkkk Kuchitekete
Kkkkkkklkk oyessss kkkk Kuchitekete
Nde yasalandiyo
Nde yasalandiyo
Nde yasalandiyo
Nde yasalandiyo
Iyayi ine ndikufuna ndimvetsetse chifukwa ndikuona ngati maplan owonjolera aja amakhala ngati amenewa man

Nyasaland sungayimvetsetse mubale.
Nyasaland sungayimvetsetse mubale.
Patient wamenya wodwala!
Patient wamenya wodwala!
This begs the question why the Chinese handed over the facility well before completion of what is being described here as ‘core’ works
Amalawife timakhala tikuba zipangizo pamenepaja..u didn’t hear?..the stories were everywhere.The chinese had no option but to be re-purchasing the items stolen,thereby exhausting the proposed budget money.

Who was responsible for security issues during the construction up to the final handover. I don’t want to believe that if burgalary is the issue, items stolen constituted main or core works as indicated here. Yes, some unpatriotic citizens vandalised the facility, that much I know and this happens in most of the donor aided projects but surely its not justified that they should leave us at the cross roads. As a matter of interest if the Malawi Govt. decided to borrow or use another financial window to complete the remaining works and wish to acknowledge the financiers, I see a divided appraisal despite the major works having been done by the chinese

Basi zinazo zalowa mmatumba ,mukufuna zina?
Inakakhala ku Blantyre bwezi itatha
Agogole kwa Bushiri minister of sports…… Apange agreement…..
miracIe money needed,mutha kuwatumira amzake a Bushiri a ku Mzuzu aja ngati mukupanga manyazi
Bodza ili poyamba stadium ndalama anazitenga kuti, Amene anayambitsa za stadium anadziwa kuti ndalama zikwana ndiye zina zapita kuti? Muwauzenso omwewo kuti ndalama zapelewera awonjezera zina. Program ili yonse poyiyamba imayamba ndi fulfillment yoti tiyamba ndalama zilipo. Auzeni Ma china omwewo amaliza akakana ndiye kuti ndalama zinali zokwana koma mwathyolera mthumba. Vuto Amalawi mumafuna kukolora msanalime.
Who said it is Bingu stadium
u want it to be called by ur mother’s name?
Stupid. Are the names finished. Is it only the names of useless people that we can name the stadium?
Bingu Stadium Its Enough It Waz A Gift 4 Hm 4rm China Gvt
kodi ndalama imeneyi singapezeke via gate collections tikalowamo?mxieew
yonseyo iphwasuleni basi
Shit goverment dis iz f**ckn shit
tiphe njovu 100 then tigulitse nyanga zakezo. it’s easy ndalamazi zipezeka
kodi ma salary aakwera liti?
kodi ma salary aakwera liti?
Musayerekedze kulandira ndalama kuchoka kwa Bushiri, mudzaphensa anthu pa bwalo limeneri

Kkkkkkkkkkkk usowatu
Kkkkkkkkkkkk usowatu
Kkkkkkkkkkkk usowatu
Kkkkkkkkkkkk usowatu
Misonkho Yalero Ipite Kuground Mwamva Kaya??…

How much money would the ivory pending for ablaze could fetch us if we opt of selling them? Shake head’s may be we have that much

The ivory got burnt already!.sorry.
The ivory got burnt already!.sorry.
Ooh! When?
Ooh! When?
Go to major 1 musachite manyazi
Akungofuna kuti zilowe mmatumba awo zimenezi.

koma ntchitoyo izatha koma chiyambiren bingu alimoyo panopa mpakana anaola ikadakali ntchito bas mkufunaso pitala aoleso isanathebe et?? iiiiiya

Basi ingokhala chonchi yatha iyi iyaa ndalama zachani …

Bushiri mwamupempha koma?? palibe nkhani apa tangomuuzani akuthandizeni

Malawian it wil b nothing for ever
Malawian it wil b nothing for ever
Boma kupusa ili.chimunthu chopanda mano ichi kukonda ndalama 2much apo chkufuna chthyolele mthumba basi.araaah!!bolanso raaa amai akulamuliraaaa coz anamenya nkhondo stadium imangdwe ku L-city
Zopusa Basi
Amayi ake ati nanu anapanga chani chanzelu? Moopa mulungu ngati anapanga chanzelu ndikusiya lock otsegula anthu mkumakatenga ndalama.

Ndiye awawa apanga chiyani tatiuzeni
Zopusa achewa inu mbuli zeni-zeni tatiyeni tigawane mpoto payekha mzionere nokha nyau inu
Dats gud mwayesesa koma ikanakhala ku BT bola mukanapindura koma alimi angakaonere mpira ndakaika kkkkkkk

Zichepesen Pemphani kwa major 1
akupasani
lol
Zichepesen Pemphani kwa major 1
akupasani
lol
Ask Bushiri for the donation don’t hesitate akupasan miracle money

Eeeh! Mukufuna Tizizangoluza? Ndalama Zaminyama Aytpamenepo.
Nanga tiziti boma lingasowe ndalama ngati imeneyi
bushire wa manyi?
Mmmmmm
Koma ku malawi nde kayatu
Komanso dzina lake likhala limenelo?ikani,ndidzalichoka tikatenga boma.

koma nde kutionjezatu
koma nde kutionjezatu
Koma abale! Njala mkati !koma zinazi ndiye kukampempha patient ali pa bed ku chipatala! Isiyeni basi

thats gud kuti akuba azibabe
thats gud kuti akuba azibabe