…govt accused of imposing the revised budget
There were clashes in parliament today between the opposition and members of the ruling party after one of the opposition legislators called Malawi President Peter Mutharika a ‘dictator’ after a heightened row.
This was when the Members of Parliament (MPs) deferred a revised MK 4.4 Billion allocation sliced from the MK 8.3 Billion. In an argument that the legislators made, the increase of MK 100 million allocation for the August House does not tally with the works that the house is involved in.
This forced the Speakers to suspend the house for two hours after which the MPs got surprised to see a document which had indicated that the MPs had approved the revised budget instead as seen in the amendments bill were passed on.
This then led to an unceasing war of words between the MPs with some of them going to the the extent of dressing down Mutharika.
Malawi Congress Party (MCP) Lazarous Chakwera was quick to question Minister of Finance of Finance Goodall Gondwe on the amendments papers passed in the house yet the house had not agreed on miscellaneous votes in the revised budget.
Gondwe had later apologized after the house nearly became a boxing ring with legislators form the government side backing the move
It was at this point that opposition legislators ganged up and railed the Mutharika led government.
Vocal Peoples Party acting Veep, Kamlepo Kalua turned his ire on Mutharika branding him as a dictator and calling him names that saw deputy speaker of parliament, Esther Mcheka Chilenje to adjourn the house Friday, 11th March 2016.
This comes at a time when the opposition has been asking Mutharika to step down claiming he (Mutharika) is clueless on how to run the country and therefore needs to call it quits, something which the Malawi leader branded as ‘hatred’.
In the revised budget, government adjusted the budget downwards due to a decrease in local revenue collection.
Presenting the midterm budget statement in Parliament on last week, Gondwe proposed that Members of Parliament should approve an adjusted budget since government did not meet its revenue collection targets.
In June last year, Parliament approved a K927.9 billion budget which was to be locally financed but Gondwe on Friday proposed that it should be reduced by K23.7 billion so that it should now be K906 billion due to under-collection of revenue.
Ndiye zofunika
Tizinyadira b’coz akumenyerana ifeyo, aphungu opanda nzeru inu,tizakumenyani ndiifeyo tizakwiya aalah m’malo momvana mukutosan m’maso taaoneni MBUZI mchsuuu!
sanamenyane amaongola manja,anachita zanzi parliament ndikukhalisa.
kamulepo is after ministerial post
Nonsense MPs
til ku egypt,tlimbike kupemphla mulungu atpulumuse

Oky
Oky
Uchisiru wanu tatopa nawo ife.ngati mwakhuta mukagone,dictator ndaa?zoputsa basi
Most politian in malawi they dont why they involved them self in politics.
Kod :iwe kamle po mbuz ya mano kunsi mmene zinthu zilimu mungasinthep o chan ndi gulu lakolo l;op usalo y cnt js unite 2 embact dis p roblm we av iwe ndi anzako ndinu owong’ono ndakwiyana pofuna ku panga zithu amadekha then u cn com wth a gwd postv idea
Mungasankhe bwanji munthu opanda mano mkamwa angakugulireni nyama nzeru zose zinapita ndimano pano ndimakani okhaokha opandaso phindu nanjiso ndi gey ameneyo nzoyamwira

Dzikoli lero lino liribe Rimoti control lomwe ungapangire next kapena forwad ,chomwechi zonsedzi a Malawi adzanga tikutha kudziona,koma ikadzafikanso term ina ya election tidzabweredzanso mistake yomweyi chifukwa chakuti tapatsidwa k1000 yathawi yakanpeni.koma ziwani kuti maiko adzizathu sidzitero ,iwo amayendela malingana ndimmene boma limenelo lapangira chitukuko dzikomo onsati ndalama yolandila payekhapayekha yamitsonkhano yokopa anthuyo kapena kulandila nsalu zachipani ayi tsimchocho.Tiyeni tinkonze a Malawi dziko lathu,tinkonze tsogolo la wana wanthu.Onani lero Nigeria komanso Ethiopia economic growth yawo ndiyotsogola koma zonsezi zachitika pa few years yokha ife tiri mpopanja pa Welesiki kapena thangata system.Be clever guys it’s not time to sleep,It’s atime to see the difference.

za chamba
[READ MY STORY. ON HOW I GOT MY HIV CURED].
Truthfully, i was tested HIV + positive for the past 8 years. I keep on managing the drugs i usually purchase from the health care agency to keep me healthy and strengthen, i tried all i can to make this disease leave me alone, but unfortunately, it keep on eating up my life. So last Two Months i came in contact with a lively article on the internet on how this Powerful Herb Healer get her well and healed. So as a patient i knew this will took my life one day, and i need to live with other friends and relatives too. So i copied out the Dr Collins the herbal healer’s contact and I contacted him immediately, in a little while he mail me back that i was welcome to his Herbal Home whereby all what i seek for are granted. I was please at that time. And i continue with him, he took some few details from me and told me that he shall get back to me as soon as he is through with my work. I was very happy as heard that from him, as i was just coming from my friends house, Dr Collins called me to go for checkup in the hospital and see his marvelous work that it is now HIV negative, i was very glad to hear that from him, so quickly rush down to the nearest hospital to found out, only to hear from my hospital doctor called Browning Lewis that i am now HIV NEGATIVE. I jump up at him with the a test note, he ask me how does it happen and i reside to him all i went through with Dr Collins. I am now glad, so i am a gentle type of person that need to share this testimonies to everyone who seek for healing, because once you get calm and quiet, so the disease get to finish your life off. So i will advice you contact him today for your healing at the above details: Email ID: [email protected] or you can also add him up on whataspp +2349036950737. CONTACT HIM NOW TO SAVE YOUR LIFE AND DOCTOR ALSO CURE ALL KIND OF DISEASE AND SICKNESS: [email protected] AS HE IS SO POWERFUL AND HELPFUL TO ALL THAT HAVE THIS SICKNESS..
Ife tinakusakhani kuti mudzikakambilana dzamabvuto, komadzomwe mukupanga sikugwilizana ndi zomwe tinakusakhilani mungopangadzoziwanokha, mutifuna nthawi ikubwela tizasovesana.
Ndiye amamunamizira? Simukuona mmene zinthu zikuyendera?
He mst b!
LIverpool is better than Manchester United, hit likes if u agre
Find a solution to our economy crisis basi that’s all we want not blows
hahahahaaha ati chifukwa chani analimata amenewa??
Menyanani bola musagwilane. Timuone wamkulu ndani. Lilidi manja mwa agalu dzikoli
Dziko ngati lakukulirani ndibwino kunena mwina tiyitane anthu adziko lina adzangotenga basi tatopa mkuva zinthu zopusa iyaaaaaa
zautsiru mukana tibulana zenizeni iwe amene waleletsa ndeu imeneyi mapazi ako ndithu
asiyeni azimenyana anthuwa zawo ndi zimodzi, iwe ndi ine tigwile ntchito
sindidziwaa kuti ndi chani, koma ndinaona ochita malonda akulira! nkulu oyendesa chisankho analira! sing along with Nkasa
Ndi chulere uja
Ndi chulere uja
The house of Idiots. Izi zamapwevupwevu ndizamakani koopsa, swanani muphane, tazolowera kale tikhoza kukhala wopanda Boma. Zikusiyana pati ku ndende ndi kunja kuno.

I’ve noted a problem with parliament.Government side doesnt want to listen to the opposition whether the opposition is talking sense.There was a heated debate vote(250)Education.The opposition was saying the budget for education must not be cut and were giving very good reasons yet government couldnt take.There was contradition between what the minister of finance and education were saying.Another example is the issue about MSB.Parliament agreed NOT to sell the bank soon after parliament government went ahead to sell the bank.So being in opposition doesnt mean these pple are incompetent
Mbava zazikulu zaku Malawi ndi zimene zili mu Parliament.
tsiku lina lake likufunika kuzakutira tear gas ma mp mwamva.
the poblem is this people they dont know the reason which brought them there
He is just tht NO SUBTRACTION.May b addition of th MOST FAILED leada Malawi has ever seen.
I lyke what South Africans do, they criticise where needed to be criticise even if it’s the president. Our Mps on the ruling side always clap hands whether it’s good or bad.

Ngakhale zdakwa pachikhuthe zkakhuta zmamenyana momwenso inu mukukangana pakuti ndalama its not a problema’ maallowance daily komanso zakuti kulinjala ndinjelengo kwainu

Zifafanthanani ndi thukuta lathulo.Kuima pa chi mzere chofoledwa 3 o’clock m’bandakucha, kuchokapo 2 o’clock masana. Kuvutikila iwe usalinso m’bale wanga.
Udzandipeza zaka zitatu zikudzazi. Zigogodanani chomwecho.

When Our Mps Shall Behave As Matured People?And How Do They Rule Their Families?
Akanango swana awatikite osamvawo mwawaziwa kale aweta galu wakuda amenewo.misonkho yathu yikungo vulala,akanati asamawapase ma allowance anthu amenewo,ango manga hostel ku parliament azigona mu hostel azimenyana mmenemo ine sindingawatchuleso olemekezaka coz tinawalemba ntchito ndife tinati azikayambana? Tsiku lina tizawapitila konko.

Adziwa litilo avumbwe amenewa kuti ndi dictator

Akudziwana
Akudziwana
Amenewo Atha Kumenyana,ali Ndi Mphanvu, Alinayo Gaga Akudwa Akukhuta.SOKA KWA OVOTAFE.
Let them fight
Let them fight
lwe pitala mutharika mbava zinzako za dpp boko haram’zo mwayaluka ndi kuba , mpaka azungu kwa America kuchita protest. ndalama za budget zisadulidwe, osanamizira kuti simunatolere misonkho yokwanira ,pomwe mungopindira mmatumba. kodi bill imasainiridwa aphungu asanachite approve mnyumba ya malamulo, zinachitika kuti?? umenewo ndiye uchigawenga tiukanawo. kuyambira mawa 2 weeks suspension nonse a dpp boko haram.
Eeeh kaya,kma nzipatala zathu mankhwala omwe alimo ndi aspirin,nde any desease treatment mkumakhala imeneyi.limbikirani kuchotsana mano treatment yanu ku Garden city aliko.

Parliament iy ndie ay coz ikalowa imangocitako ma DRAMA or COMEDY malo momanga mfund zotkula mMalawi apa.

Aonjeza koma asamapange choncho plz
Aonjeza koma asamapange choncho plz
Osamakambilana za kusowa kwa mankhwala mzipatala, kusowa kwa chimanga, kubvomeleza kwa mathanyula, kukwela kwa mafuta (petulo dizilo) kukwela mtengo kwa katundu!

guys malawi akupita kut uyu komaso amalawi ndifi opusa tinamulora osatha kuyakhulayu kut atilamulire lelo siizi aaa mkulu wake analephera kod unali ufumu omalowa pa chibale

Hahaha wrestling in parliament.
Hahaha wrestling in parliament.
Zizankhala better
Zizankhala better
Wonse alikunyumba yamalamulo kuyambila speaker ndi agalu anyaninso mukumafuna kumenyana anthu akufa ndinjala kumidzi

tingo gumula nyumba yamalamuloyo timangepo malo omenyerapo boxing bas.

Wonse alikunyumba yamalamulo chaka chino ndiagalu okhaokha opanda nzeru

Ma mp lakula ndi dyera pamenepo iwowo apanga ma million’s kungomenyanako osaganizira anthu omwe anawasankha. Ma mp adyera onse 2o19 azasovaa

#Thomas zona akavulazana apita kuGardern city clinic or Millpark clinic iwe kwako ndi quenzi kapena ku Kamuzu centrle

Tazikutumulanani maonamo phindu
Tazikutumulanani maonamo phindu
May b iz political without principles
May b iz political without principles
Yaa koma kumeneko ziribwino zimenyanani kumene muphulitsane mimbazo m’malo mokambilana zanzeru zitsiru inu eti

Very Shameful & Saddness
Very Shameful & Saddness
Ofunika amenyane kumene chifukwa kuba kuchepa aziwopa kwambiri anthu akuba amenewa dziko LA ling’ono ngat ilo kulephera kulipangira budget ,,,,,leadership sali bwino kwambiri

tiyeni kumudzi mukawone mavuto athu akuvutika tizinganiza tikakhala

Kuti THANYU!! #Pitala kuthanyulira muthako la mamuna munzake nyasi kuti mbwerekeke!! Wathanyulira pitala

Commenting…………
Commenting…………
Akwanamizira ngati ” he is a dictator of course”

Speak hands for me munyumba ya anthu olemekezeka? Tadzamenyanani tsiku lina kuti amalawi tidzaone olimba ndani?

Malawi Watsopano Kkkk, Osamawopana Kutumulanani Mulandira Ma Allowance Ambiri Ndalama Zathu Zamisonkho Zikugwira Ntchito Ayayayaya.

hello big men sup this is malam mohammed call me on this 0269056991 / 0549365291

Kodi kupaliamentiko munapeza maloosewelelako ???????? Nthawizonse mukakumana kumangokangana mumakanganilana ufiti? Mukutisokosa nazo ndale zanu zolondanazo.

Aphungu Ngakhale ali ku parliament koma zikuoneka kuti chomwe amapitirako sakuchidziwa mpaka pano.Zoona mavuto omwe ali m’malawi muno ,angamamenyane ngati kuti akusowa chokambirana ku parliament?

Kamlepo yure great man umakwana ndiwe wekha

YOUR CRAZY INSTEAD OF EXCHANGING BLOWS WITH FIXING ECONOMY YOUR BUSY WANT TO EXCHANGE BLOWS OF USELESS THINGS KIKI! COME ON MALAWI !
Vuto ndiloti WAMISALA akaphatikana ndi amoyo onse amasanduka amisala.Nthawi zonse Kalua amalankhula zoduka mutu.Moti kumunena kuti Olemekezeka Kamulepo Kalua ndiye kuti iwenso ndiopenga.l cry to see my favourite party joining hands with this fool ooooh!! Very funny as well.

Mmmmmm Ndikukanapo Kuika Mulomo Wanga Pamenepa Paja Akumakusaka Kufuna Akumange Nde Ine Otsauka Opanda Ndi Phinifolo Yemwe K50,000 Yabelo Ndikaitenga Kuti.? Menyanani Akuletsetsani Apolice Alikomweko Komaso Misokho Yanga Tikutumizani Ku Zipatala Za Kunja Ine Ndikusowa Ndi Aspirin Yemwe.

koma Kamlepo kudela kwanu chitukuko chikuendako? osamangotokota zaukape kwanunso muzikumbukilako

dzitsiru inu kukonda kubera dziko menyanani

Ziphanani..mukamaliza zizithera konko
Ziphanani..mukamaliza zizithera konko
Kalua is semi mad, quarter normal and other quarter wild animal
Hahaha ok nkhani yabwino kma nde kumalawi kwavuta

Zitsilu izi shut up parliament
Zitsilu izi shut up parliament
No remarks.
No remarks.
DPP goverment does not want to be cricited.I have never seen this type of leadership since 1994. They are real dictators as we have heard that wanted to exchange blow in the house.

Dpp gurus tell wamathanyula peter that we are still waiting for pregnancy in ur swthat’s womb, Getrude wamathanyula
Za ziiii

stonard. ndi agogo ako tu amenewo ukufuna akafere komko kkkkkkkk

bwampini anapanga dryup sangabeleketsenso thats why akupanga encourage mathanyula kt asaziwike.

Tionge ndiye agogo saberekasa
Tionge ndiye agogo saberekasa
Mawa nose chibalo,aliyese apititse kudela lake matumba 20 thousand achimanga. Ma MP opusa mwapanga bwanji

Mtundu wa atsogoleri watha, nzeru zoyendetsera boma zikupelewera chatsala ndi mantha kwa a Malawi.
Mtalika’s Administratin must balance options inside his Party and opposition which can drive Malawi forward.
DPP is still making the same mistake which UDF did in 1994, to hunt MCP Gurus as a result he failed to grow Malawi economy.
Dalaivala ali ndi sisitasi, zikamuvuta amapempha chithandizo,sikuti ndikulephera ayi koma koma kuonetsana mutu.
Pomwe zafikapo, ndikukaikira kuti a Boma nokha muzitha, zikuvutani.

Go On And Fight Tomorow Z Another Gud Day 4 U,,,kma Amene Adzandiuzenxo Zovotayo,,,,,c below

Only parliamentarians pass a bill in parliament.if anythng else,then indeed that’s Dictatorship

Fighting or arguments, these have no solution to the problems we are facing right now in Malawi. As honourable pple speak honourable language that will unite and help alleviate poverty.

dey r all idiotic pple
dey r all idiotic pple
bola pamenepo yamanjayi sopano
bola pamenepo yamanjayi sopano
Mbuzi za ma MPS inu mmalo mokambilana zoti mutipangila chani ife tinakuvoterani mwayamba zamanyi kumeneko. Anthu akuvutika kusowa ntchito , mmalo mopezera anthu ntchito inu mukumenyana . Tachitani zoti zithandize amalawi onse, osati inu nokha ayi.

Amathanyula ndi amathanyures akumana tsopano. Zitibulanani ubwino wake ma Hawker’mu panado alimo muzikagula muzichepetsa ululu paja zipatala zathu mankhwala mulibe

Nanga atumbuka zikuwakhuza buaj apa?
Nanga atumbuka zikuwakhuza buaj apa?
Iwe kape eti lingakhale funso limeneli?mtundu wako ndi ndani iwe?mbuli zotha ntchito,waiwala kuti enanu mwatengela atumbuka kumphunzira? shame on yu!!!

Mumangokhalira kukangana instead of discuss thing of changing peoples lives.

Dont waste our precious time. Your ernegies must be spent on constructive developmental debates.

Timbanani mukomane kutchayana waka yai
Timbanani mukomane kutchayana waka yai
what are the evidences that he’s adictator?

Its nt Mcp member who oposd the deal guyz, its Pp anyway they are sayng the truth.

No wonder somebody labeled them agalu inu.its time be construve. whom do u think will make nyasaland a beta place to dwel in.be serious this is childish.munakakha mkalasi u would dig toilets

mmalo momakambilana zanzeru mkumafuna kumenyana ana osavinidwa inu

Misonkho yathu ingopita pamenepo mmalo momakambilana zanzeru

Aaaaa! Yalephelekanso ndeuyo? Basi mawa iyambikenso. Olemekezeza oduka muti Awa ndithu.

eti masiku ano anthu akugwilisabe phone ya charger chamutu waungono?

he was right he’s a dictator,
he was right he’s a dictator,
menyanani! iye iwe iwe! iwe! ntikite,mpondelere!,ntintinti,palanawe palanawe palanawe!,tiwuzeni zambiri mphunzisi!
Kkkkkkkk koma yaa

Kkkkkk, still not matured, democracy simunaiziwebe zaka zonsezi kkkk shame on you

yaaa that’s better!let them fight themselves,they mustnt bring their differences into our heads its just too much

zimenyanani,, achuma okhaokha kumenyana sizoti ife tizida nkhawa ayi,, mukavulazana zipatala zanu zili kunja pomwe ife ndi community hospital kopandaso mankhwala aaasah,,, mbuzi inu m’mene wafika malawi pa anthu osawamvera chisoni ndie muzitukwana zosathandiza….

Kusowa zochita basi kmenyana ndiyamba kugawa ma tear gas azi poperana mmaso

Nn of ma bsnss
Nn of ma bsnss
Tazimenyanani Mukamaliza Sitizakuvoteraniso Agalu Inu.
Zili bwino muzikunthana nokhanokha

asiyeni aphulisane mimba zao zazikuluzo mxii,

Bolani pamenepo
Bolani pamenepo
Koma mcp yanyanya kutsusa chilichose tatopa nawo ife

Yah not unexpected these MPs are not wealth to be called olemekezeka

Anyapapi awa palibe chomwe akuchitako koma kuziwa kupanga criticize the government iwo asakupanga kanthu koma kukhutitsa mmatumba awo! Tsiku Lina zomwe zizachitike kaya sindiziwa coz anthu inu tayamba kukutoperani!

ife nd ochemerera !ali boh ,,azyambana pafupipafup coz amakambrana zosatkhudzaa!

Sanati aphana posachedwapa munvela tingoti pheee

Kakudzumulanani nde ntchto ya makwacha olandla dairlywo

kkkkkkkk!!!!! yeah! it’s better like that. adzimenyana iwowo osati ife ayi