Ine ndi MCP mpaka kumanda – Mussa
A Uladi Mussa omwe amatchukanso ndi dzina loti a Chenji golo, anenetsa kuti iwo sadzatuluka mu chipani cha Malawi Congress kamba koti afika tsopano. A Mussa anena izi pa pulogalamu ya Cruise 5 ya pakanema… ...