Dan - Lu

Kumenya kugwetsa!

Oimba odziwika bwino m'dziko muno, Dan Lu, yemwenso pakatipa wakhala akuyimba nyimbo zotamanda mtsogoleri wa chipani cha Malawi Congress (MCP), Lazarus Chakwera, wakwidzingidwa ndi apolisi masana a lero ku Lilongwe. Wachiwiri kwa ofalitsa nkhani ku… ...