Zipatala zinayi zomwe zikumangidwa ku Neno zichepetsa mavuto a zaumoyo
Boma mothandizidwa ndi Bungwe la Global Fund likumanga zipatala zinayi Zing’ono zing’ono Boma la Neno. Zipatalazi zikumangidwa kumadera ovuta kufikirako omwe alikutali kwambiri ndi zipatala za Boma. Zipatala zomwe zikumangidwazi ndi Gonthi, Godeni, Feremu ndi… ...