Mabokosi awiri maliro amodzi: Gwengwe waloza chala Malondera
…akuti “a Malondera analemba zigawenga” Ya pa chiweniweni: phungu wa chipani cha MCP ku Dedza, a Willard Gwengwe omwe bokosi la maliro lomwe anagula lakanidwa mochititsa manyazi, aloza chala phungu nzawo wa chipanichi a Steven… ...