RBM yati ithana ndi amalonda amene amakana ndalama zina ponena kuti zidatha mphamvu
Reserve Bank of Malawi (RBM), yomwe ndi banki yayikulu m'dziko muno, yachenjeza kuti ithana ndi aliyense amene apezeke akukana ndalama ponena kuti inatha mphamvu ndipo potsindika za nkhaniyi a RBM ati ngakhale ma 1 tambala… ...