M’bindikiro ulipo pa Chingeni sabata ya mawa – Kalindo
Amene akutsogolera zionetsero zotsutsana ndikusayenda bwino kwa zinthu m'dziko muno a Bon Kalindo, ati ngati boma siliyankha pempho lawo pa nkhani ya katoleledwe ka ndalama pa malo otolera ndalama ku magalimoto a Chingeni komanso Kalinyeke,… ...