President Peter Mutharika has appointed Paramount Chief Lundu as the new chairperson of Malawi Blood Transfusion Services (MBTS) Board of Trustees.
According to a statement that has been issued by Office of President and Cabinet (OPC) and signed by Chief Secretary to Government Lloyd Muhara, the appointments of the Paramount Chief Lundu and other members of the Board of Trustees is with immediate effect .
The statement names Paramount Chief Lundu as the Chairperson of the Board of Trustees while members are Mr Robert Mdeza, Mrs Agness Sentala and Mr Lewis Msasa.
Secretary for Health and Population and Secretary General for Malawi Red Cross are Ex-Officios.
Paramount Chief Lundu is one of the traditional leaders in the country who usually defend the Democratic Progressive Party government.
lundu chairperson wa anamapopa
magazi ake a ndani uzitenga iwewo
ok
Lundu- a Chief suffering from mouth diarrhoea!
Ha ha ha kkkkk kkkkk
Mfumu yachiphamaso #lundu
Awapatsa award because of chaka chatha anawombera kwambiri mumanja mpakana zikang’a kutuluka.
Zazii
So?
Mbewa zikatha amanona ndi aswiswiri ziizi tinkanena,ulamuliro wanji womasakha anthu owola mkamwa,anthu omayakhula zokoma zainu basi dziwani lero mungonza kukhala ngati mukukonza zinthu koma pa mmawa mudzapusa,chabwino mukanasakha mfumu gomani ka mwana kamzeruka anthu akanakuyamikirani koma Lundu apo ndiye mwanama.koma alangizi anuwo amakulangizani chani?pena bwenzi mukumawatsutsa kuti ayi zimenezi onani lero
mamvuto ku malawi kumvotera chilekwa zowona kumapatsa udindo anthu adyerawa
ACHAKWERA kwerani mwachangu OPITARAWA apitakale mwamva
peter sakudziwa chimene akupanga trust me .this man called peter is more mad than mr WANDALE
hahahaha…..Mpaka kusankha chief
Zabwino zonse amfumu Ku company yopopa magaziyo……….
He he he wansanje apsya mtima
It’s not about Nsanje we need people who can change lives and nation. People who can make the difference especially to the poor
ANAMAPOPA! kukalowa mnyumba ya magazi tsopano
azigweru amasankhana azigweru okhaokha tiye nazoni tiona….
2019 ife tikuika chakwera pampando kaya lynduyo zimuthera bwanji kayaa!aa
Lundu akudyerathu,apitila limodzi 2019
blood what?like really????????i wonder what next
Anayesetsa mnyamata uyu kuwombera mmanja mopanda pake moti mphoto yake ndiimeneyi, dyerantuni mukaluza next year muona kuti muchita bwanji.
Controversial Chief he will later be appointed Minister of Health
Ha ha ha not possible
This politics anything can happen to hand clappers
True Falesi Zambezi bwampini eneyu atha kupanga zimenezi kkkkkk
These hand clappers were there before you Mr.President, so plz open your eyes and see.
Kuyamba kugula mafumu eeeeeeeh
Adyeretu nthawi ndiyomweyi
what?????? Mad people
Purely political appeasement move not for the betterment of those in dire need of blood, bingu died early for lack of relevant medical experts since he hired a bunch of incompetence bootlickers, soon Peter will be in need of blood and suffer lack of blood for trusting ignorant and incompetent people to lead MBTS! even if there are technocrats in the board they will have all their suggestions shot down as long as the suggestions are technically sounds and politically unsound. Blood collections have been low MBTS need a strategic and knowledgeable individual to lead it! this political appeasement is killing US!
People without knowledge wisdom and understanding. Thieves
ndikukwiya kwake kuja(nanga amamwetulira awa)kopopako kukumukhala!!
Madyera mphotho alundu ndi munthu wa ndale osafunika kukhala mfumu moti ngati anthu akwawo ali ndi mzeru akhale pansi mkusankha mfumu yina uyuyu adzipitiliza za ndalezo
Mphoto yolongolola, watsala Ngolongoliwa
Yes iyi ndiye nkhani yabwino mipando yononayi tisamaiwale achinyamata!!! Zabwino zonse chief Lundu may God help you
Achinyamatawo ndiye ati? Mukudziwa chimene mukukamba kapena simukudziwa chilichonse?
Wachikulile osati wachinyamata point of correction
Point of correction not collection. Kkkkkk sakumudziwa wachinyamata uyu
Ndipo lundu ufumu adangowubvara chifukwa kwao anthu adatha kukanakhara kuti kuli ena amzeru akamubvulitsa ufumuwo mkumuwuza pita ukapitilize ndale zakozo ndi Mr ibbu
Guys mwawerenga mwaphuma dekhani muitolera chifukwa ndaphatikiza mfundo ziwiri pamodzi
sunalakwise olo mr president ndi mnyamata mpaka pamene atazayammmbe kunyela chitosi nde azavomeleza ukulu wawo kkkk
mad people mad decisions
Awanso nde nchani
zabwino zonse a Chief, gwirani ntchito mwachilungamo, mwasankhidwa munthawi yake.
Ndimadabwatu ine lundu ku jijirika kuja oowoooo…!
Kuganiza kwa a purofesa, #madness
UMANGOZIWIRATU. NamApopa
Amafuna timafumu totokota pa MBC ndi mabodza awowo nkumatipatsa timipando tonona
Akuganiza DPP ipeza ma voti mng’oooo!
Am sure ndimlomwe ameneyu…..tiye nazo Mr President
Mutharika wabalalika!
appeasement appointment, what good can come from this dull chief…….corrupt, empty president…..anamapopa okhaokha….