Nkhatabay Police Station is keeping in custody 29-year-old Gift Mbale for raping a 6-year-old girl.
According to Public Relations Officer for Nkhatabay police Cecilia Mfune, the suspect and the girl’s parents stay at Nkondezi within the district.
On Saturday the rapist found the girl alone at home and he raped her.
“When the victim’s parents noticed the girl was having difficulties in walking, she revealed the whole incident to them.
“The matter was reported to police and suspect was arrested on Sunday,” said Mfune.
The victim was referred to the hospital where results showed she was raped.
Mbale hails from Mwaluweyu Village, T/A Mwelang’ombe in Karonga District.
He will appear before court to answer the charge of defilement.
Amafuna kukhwima ameneyo coz munthu wanzeru sangapange zopusazo
He must stay to prison all this life thr is more prostitute in different bar y dont he go dat side his up shirt
kumavuta kufunsira mkadzi wamsikhu wake kapena?pepani eni mwanayo ndipo lamulo ligwire ntchito kwaochitayo.Pepan kwambiri
He Is Worse Than A Dog
Ndw ntchito zatumbuka zimenezo sizachilendo kuchitumbuka koma ndizachilendo kw achewa
Ayi madala zonyoza mtundu.
Ooooo paja ndinayiwala brother sorry
“Man arrested for defilement” . This sounds better than “Man arrested for rape”.
A 6 year child has been defiled not raped.
Mwachitika uli na amudala pakana kukolere ka mwana nadi?
Mumvapo chani pa mwana amangwetu
Koma zimandivuta kumvesa pankhani yogwilira anayi kodi akazi atichulukirawa ndie kuti simukuwaona??????? Akazi kunjakuno amisinkhu yawo akusowa amuna ndie inu mukusiya amenewo nkumalimbana ndi wanache chichi??????
Must have serious discipline stuff upon him.
He Is A Butcher Because Raping Is The Same As Killing.This Man Deserves Capital Punishment
I hope thy lock him n throw awy th keys,
Koma zoona munthu nkulukulu mphamvu zake zonse kukathesela pa khanda LA zaka 6 eishhhhh #Ndamulila mwana ameneyo
Kod chimakhla chli chan?
Men are dogs ended
ufiti ndithu
Komatu mahule akutchupatu .ngati zafika pakhosi osangopita kwahule bwanji? Nanunso mukulakwa koma.
Mahule momwe antchipilamo
Amafuna ku khwima ameneyo…
Kodi kumakhala kuti mumapititsa ngati mkazi kapena pali zina zomwe mumatenga ine sindivetsa please guys tandiuzeni kodi mukuti mwana wa zaka 6 pamachitika chani ,kukhala mwana wanga ngati a police mungadzampeze munthu ameneyo alimoyo ndukaika nditakwirira nthumbirayo kudzalapo nthochi
Aise fra mulungu amapulumusa anthu mwana uja akulira ife timaona ngati wangodwala tinamuuza sister kuti apite naye kuchipatala zonsezo zimachitika ada omwe adamugwililira ali pompo ine ndi mzanga yemwe ndi bambo wa mwanayo tinatalikila titabwelera sister ija inatibitsa inangoti ati mwanayo tipite nayo tonkha mzanga uja atangofika ndi mwanayo achipatala adangoti mwanayi tanena kale kuti amgwililira atangova choncho adamfusa mwanayo ndipomwe amanena kuti gift wamlowesa chinthu kumaliseche kwake atamupasa 50kwacha pompo adatenga mpeni kuyamba kumusakasaka mwamwayi apolice adamgwila tikadali kumyang’anabe ndipomwe adapulumukila
PEOPLE ARE HEARTLESS. It’s demonic influence.
@niko koma zooona ?
Chomwe ndikunena ndichoti munthuyo ochita zimenezozo amati akugona ndimkazi kapena amakhala akutenga zizimba ,tiyeni tinene zoona mwanayo osatha msinkhu koma kukakamiza kuti alowe
No bail for that monkey please. He’s not a man he’s animal. Please men let’s stop this shit and be real men
kodi mahula kulibe kumeneko kusowa umunthu kumeneko
Amwale vani izi kuchoka pomwe zachitikila izi ndi pa bala yoti ili ndi mahule ambirimbiri pali mtunda wa20metres khulupiliani man komanso ada ogwililirao amakonda kucheza ndi mahuleo
ndimbali iti bro niko?
koma ndichiyani chibaba chake chotani osandoipepha bwanji akazi onsewa mpaka mwana pakhambi
Ashad ndi ku mkondezi
Komanso guyz sindine wa chipatala koma kungomuona munthuyo guyz zake zinada kale kale ndikhulupileni timagona nyumba imodzi nthawi zina pamodzi ndi dala yake ya kafanako
Anthu Ena ndi zitsiru ngati chimenechi
34 minus 6 equals 28 akhale 28 zaka ali nkati
Mbuzi.
Umboni wamwana ndi poison wobvuta kuukana kkkkkk
Km zooona ife tikusowa zomwezo inu basi kwa mwana kukazithela komweko mh mh ndakudandaulilani .
mmmmmm koma shabim
Sukunama aixe kkkkkkk
Kuvula ndikuvu kuvulila mwana mwaonjeza
i from Mkondezi in nkhatabay where this happened and i hv seen the child eish guys ndizomvesa chisoni
wadyabe konona olo akumange
AMENEYO NDIYE TIMATI WAGWILILIRA NDIPO I JUDGE HIM PERSONAL HE IS SUPPOSED TO BE IN JAIL FOR 34YEAR’S. NEXT TIME A MALAWI24 MUZALEMBESO ZOLINGANA NDI MISIKHU YA MUNTHU NDISAZAVE KUTI MUKUTI A MAN WAGWILILIRA MWANA WA ZAKA 17 NDIPO AMUPASA MIMBA MWAMUNAYO ALI NDI ZAKA 21 ZOMATIMANGA CHIFUKWA CHOSAVESESANA ZICHEPE
Kupusa mahule onsewa.akazi onsewa kukanika kuti mai ndakukondani.20years ameneyo
Guyz nkhani imeneyi ndiyoona mwana anagwililidwayo ndiwamzanga chawanagwa phiri ndipo titapita ku police ndi mwanayo gift anavomeladi komanso adao zaka abisa he is 34 or above. Mutha kundifunsa ndikuyankhani
Nzakoyo analikuti mpaka mwana kuonongedwa choncho eishhhh
nkhata-bay delanili?
Mkondezi
Alipo
That’s murderer case
6 year…
All these ladies why
usawi chichi death sentence is applicable here
Gadaf anavuta mu trouser kkk
Kkkkkkkkk koma
Kukanika kumucontroler kkkkkkkk
Kkkkkkkk inu!!
He is a demonic
Koma zimakhala zowonadi zimenezi?