Urban artist Stich Fray has bombed all musicians that are mocking him following his failure to claim an Urban Music People (UMP) award despite his dominance in nominations.
Some musicians have been making fun of the Blantyre based artist on social media, since the awards night. They maintain that his five nominations were as good as nothing.
In retaliation, the Zoti Ndimakukonda hitmaker said his critics have to produce hit songs and perform at many shows, then they will be in a better position to mock him.
“Muli busy kulemba ma status omunyoza Stich Fray pamene olo ndi hit song yomwe mulibe or even a nomination. Kuma shows simutengedwaso nkomwe. So before seeking Facebook likes in a way of makin fun of me coz of the awards, yambani Kaye mwapanga hit song and get more shows..” exploded Stich Fray on Facebook yesterday.
He also cited some top artists who are basking in the glory of their hit songs but came out as losers in the UMP awards.
“Inee, Martse, Theo Thomson ndi Tay grin taluza ma awards koma tili ndi ma hit songs ndipo tikuyimbabe sitinamalize. Ndaona kuti wina wake watasa pa mudzi pano.”
The musician cum producer was tipped to win big at this year’s awards by virtue of being the most nominated. He earned nominations in the following slots; Best Producer, Artist of Year, Best Song of The Year, Best Afro-Pop Artist and Best Music Video.
Real name Steven Chibwanzi, he is trending with his two afro pop songs, Zoti Ndimakukonda and Wamupeza.
Paize bro
Ztaye ase #stich_fray
Ther iz always nxt tym
Osadanda fray nyimbo yako “zoti ndimakukonda” ndi lullaby yanga ndikugona nayo bhobho
no need 2 worry man stich wabwno ndwabwno
Afana Agobo Kalawe
Kkkkkkk I kno a few that are insulting him but most are sympathizing….z tht ur observation also Robin Intercessor Pemba
kkkk exactly . . . sizinayende mwa fair amwene
Zoti ndimakukondaaa! ayeeee eee, nzachite kunena bwanj zoti iwe ndiwanga iwe,,
Michael Michael-Es Sazuze
Stich tu uyu abwere,fredo tu uyu my foot!!!! Kkkkk
stitch frey never iluv ur song _wampeza
Next tym zzaenda neva gv up! the sky is the limit
Pa low bra, just imagn Theo ndi bg koma taona nde kt sinthawi basi.
Apse Ntima Zenizeni ulira utopa aise
Kkkkkk zavuta zinthi or mpira osewela bwino amakhala ambir kma wina kungobwiza kamodzi chakumapetopeto ndiku golesa chigoli amati iyeyo ndi man of the much zimadabwitsa kwaifeonela usalileusalile
fray iweo ndiwabho we lov u zathapo izoo dats lyf look forward de journal stil goes on focus …
Stich fray umatha iweyo pa low next time uzatenga zonse inhopitirizani kutipatsa mingoli ya bho osafooka ghetto yut
This oz urban man wait ayambisaso entertainers of the year where u pipo belong surely u gat them all but this awards were for men real men men!! Don’t u get t bra!!
iii ndimavotitu izi Afray.kk
Don’t give up, Stich Fray. Your time is surely coming. Don’t take this as a yard stick to see who more popular and talented. This should even encourage you to do more. Keep it up
zake zimenezo
Osadanda stich ndi ma award opusa ngat awa
Unakakhala mpira bwenzi tikuti ma prayer omenya mpira mwa kayang’ana phadzi ndikomweko””” amenewa oyimba akuti???
so painful
not gd at all
Ndangomva kut status yanga yapanga appear pa nyasa times
hahaha stich asadandaule coz mene anayamba kuyimba nsakaziwa kut kuli ma award eyeyo he shud just focus kutipasa nyimbo zabwn bax
Honestly the wards were not fair, ma guys a dollar ndi amene a wina
kumo nkumalawi fulll with katangale stich surpose to won
Iwe anzako anali ndi ma whatapps group amatumiza ma units iwe oro uwina bwanji
He deserve an award,but look how it goes??,some guys didn’t deserve even a single medal but they’ve won,to me fraud has happened
Asadande apanga ma awards ina l best losers awina ameneyo
Stich Fray umatha, mumatiimilira madala.
Stich Fray umatha, mumatiimilira madala.
Dellilah ndi nyimbo yomwe yaulula kuti ma awards awa nga China…
ine zangondidabwisa…. fredokiss awina bwanji popeza mu top 5 nyimbo zake munalibe…… akhala bwanji best raper nyimbo yake mu top 5 mulibemo……..there is no way anywhere in the world an artist kukhala artist of the year nyimbo zake osapezeka mu top 5………
Inenso kudabwa kuti wafika apapa bwanji coz l can say si urban yokha, pafupifupi aliyense atha kumudziwa Stich frey maka ndi his hit of the moment, ndiye kumvetsetsa za izi, mmmmhhh…. Komabe mfanayu asadande amathah
Top 5 yake yiti.
Which chart r u talking
you didn’t see kuti panali nyimbo 5 zoti zivoteredwe…… ndikunena that list……ukhala bwanji best rapper nyimbo zako palibepo
Ndekut waxy wagulanso… ndalama zake wazitenga kwaaani
follow every step of the music then you will realise why ntchana deserves it
anywhere in the world this happens only in Malawi……
One step at a time achinafredo anayamba kaletu koma akaluza they were picking themselves up
Tikanena zomwe zachitika Chaka chino pama awards-wa everything was miracle miracle miracle !! ….. and apart from #Stich_Fray kudandaula koma the truth is …. Paenda miraces…… Zakaisara zipite kwa kaisara
Stich Fray ndi dolo osadanda man nxt time muiphula basi!!
Kkkkkkkkkkkkkkkk #oscar stich fray umamuzwa?
Don’t Worry Stich Fray Asiye Azipusitsana Iwe Sound Umatha
Samatha uyu amangokuwa nyimbo zake
stitch fray Ali ndi luso kwambir he is a producer koma a good singer usafooke!!! tizachite kuzicheka kut uziwe zoti timakukonda stitch fray. don’t give up your small boy ngakhale anzako akukunyoza kkkk we Love u fray
Be patient boy…. Dont rush, wait for ur turn mmmmmmm…… This was not ur turn, do u copy..?
Don’t waste time with this. .
if he wants angojoina satànic bas dhilu will be over
Prince Mhango Repro K. Reproof
Ndebola atamadandaula nyamata wa Delilah Saint””
Ndikuzwa Kuti Pampiksano Aliyese Amakhala Nditima Yoti Atenga 1, Koma Ukalephela Kuvomeleza Ndibwino, Taonani Nyimbo Zina Zotchuka Kwambiri Koma Ayi Kulibe Coz Akufuna Imodzi Basi Ndiye Inu A Fray Mtima Pasi Mawa Ndinu
Asova
stich frey nde uti????
amene amazitsata stich deserves an award coz zoti ndimakukonda it’s a hit song like seriously but UMP amangopatsanapo pakudziwana kwawo
but not better than apse mtima
mmmmmh iwe apse mtima it’s only for youths where as zoti ndmakukonda ngakhale makolo amamvera coz uthenga wake ndwaaliyense
Ray cee ukunena zoona nyimbo izikhala ya tanthauzo komanso shud hit all corners of the Society children, Adults elderly ngangale omwe samakhala ndi chidwi chomvera nyimbo
sure Harriet u r right
Ma awardz angopita kwa anthu amene amaimba useless music bax…..
Ena alibe luso lopeka nyimbo kumangoimba zopanda pake nyimbo kumangoti tchweee mwana tchwee Kkkkkkk kaya amatero kaya pomwe wina nkhani yoziwika bwino ya delira ndi Samson anaipanga Twist kukhala nyimbo mkumamveka nyatwa!!! Who deserves an Award
Harriet dziko ndilokondera ili akuti Hello Mr Yesu iyi nkukhala nyimbo yoti nkuwina award ???
kkkkkkkk akut fredo best hiphop artist guys….. bola pa live act paja zikumveka
ali ndi njira zawo
Apapa UMP yatinyenga heavy
Fredo nd ntchana he deserves all in all
Nyimbo anachita kuba siyake,,,mizimu yakwiya. Ng’oooooo
do not worry broh next year uzatenga onse iweo
Kkkkkkk stich fray nyimbo yake it inu???? ?akakhala ma videos osalongosoka
mmmm hmmmm
Nsanje
Iwe ako olongosoka ali kuti, uzafa osauka
ai afana wa amaenela kutenga kma seriois guyz
Mmm,koma kunena Ngamo mwanayu amatha kupisanso zina zomwe zapasidwa ma awardz-zo.sakunama ai ayenera kukwiya nazo
why mocking him we know he is good but not everyone can win at a single time
kkkkkkl
Iwe stitch fray nyimbo yake it ikukufilisa maso? Umaimba za akaz unkat maunitsi ovotera uwapasa? Ovota ndife nde usova
Kkkkkkkkkkk mganda wake uja
Ndi mzake wa delilayu
Kkkkkkkkk
Mmmmh dzipongwetu guyz.
Kkkkkkkk guys lekan jelasi mwanayu ndi dhilu
Hahahahaha yambani kuimba inuyo timve nyimbo zanu
stich fray ndi sir patricks ndima choir master
Anayamba ayimbapo ku church kwanu
Ma hater samasowa
Ankamuthawa Revolver ankaona ngt paokha angathe! Aziona sanati
Iweyo yamba kuimba timve
Kkkkkkkkkkk kuno ndi Ku Malawi
amene ali ndi nyimbo ya Bossaro Music andigaileko
ndilinayo ya new
+256992 270 122 share