Admarc to start buying maize

Advertisement
Malawian-Maize

The Agricultural Development and Marketing Corporation (Admarc) has said it will start buying maize from farmers next week.

According to the parastatal, farmers will be able to sell their maize at its 337 markets countrywide starting next week.

Malawian-Maize
Govt will start buying maize from farmers next week.

Admarc officials told the local media that government has given the company K7.5 billion to buy maize from smallholder farmers.

This comes weeks after smallholder farmers complained that they failed to sell their maize to National Food Reserve Agency (NFRA) because politicians with links to the ruling party were prioritised.

The agency was buying the maize at K130 per Kilogramme despite government setting a minimum price of K170 per Kilogramme.

According to the Ministry of Agriculture, Malawi this year produced a 30 percent maize surplus.

Earlier this year, government banned maize exports. After farmers harvested their maize, there were concerns concerns from farmers that the ban was affecting them since they could not benefit from their sweat because local traders were buying maize at prices below the government set minimum price.

President Peter Mutharika lifted the maize export ban last month to allow farmers sell their maize wherever they wanted though some quarters said the ban was removed at a time farmers had already been exploited by traders.

Advertisement

108 Comments

  1. Anthu Musamatipusise Mukufuna Mutipase Njala? Chimanga Timagulisa December? Ndiwe Mmalawi Koma? Osangoti Yakwama Thawi Yoti Tibe Dollar, Ah! Ndinasala Ndikachinkhulupiliro Pang’ono Ku Boma Ili Koma Na Apa Suzaionaoso Yaine 0%

  2. Iziz mukuchta tsiku lina a Mw tizakutoperan la 40 lizakwana tizakuwawulan machende nd Moto. Muzgula pano chimanga.Mukutinamiza ngat ana in fact muzgula nokha coz munachta dala kulesa kugulisa chmanga kunja inuyo osawagula a2 instead mukuwagula a)alim ovutka kale molira through mavenda( akukuguliran inuyo) then mukutsegula nsika mochedwa dala mkumadzigula nokha mokwera. pal zeru???? getting fat on expess on ur own ppo???? Mulungu wanga ine Chikathen chithu ich tatopanacho plz.

  3. Ndye akamat u r a prince of thieves mkumadandaula mbux iwe??? nanu ma general asilikal kamatengeran chitsazo chabwino cha azanu kuzimbabwe uko mul dyo bakha akutiluma nd chilomo chake.

  4. Pankholo panu mwava!!!! Kd ndnu otan ndpo mumamufuna anthu zalire bwanj kt muzave??? Stupid ,Useless leaders. leaders who pulls everything which good to there side you regard mw as ur gogo’s estate. Muzt tikusoweka ulemu?? mudabera kale a2 anyan othena inu mudalimapo mzere pa munda.

  5. Anthufe Tisadabwe Chifukwa Mtsogoleliyi Pa Nthawi Ya Kamuzu Akusonyeza Kuti Sanali Mdziko Muno Ayi. Chifukwa Adminstration Sakuidziwa Had It Beem Kuti Akuidziwa Tikadati Iyeyo Amangidwe Zingwe Ulendo Wa Ku Bwaila Kapena Ku Zomba Mantle Hospital Chifukwa He Is Mentally Disturbed

  6. dpp goverment mukutichitsatu manyazi apapa or kuku bakilani kwake apapa mkumatino bwanji? Its 2much is it true kuyamba kugula chimanga pano? What about june july?? Losing majority bcoz of dozng like a gurd

  7. Chimenecho ndiye chamba .Panopa anthu chimanga achitenga kuti? Anthu akolora May panopa chiimanga mukufuna kugulachi mugura kwa ndani?Iweyo unawonopa chimanga akugura November?

  8. point of order Admarc will start buying maize from vendors not from farmers.This government need civic education,during Dr Kamuzu Banda,Admarc used to start buying maize from farmers around July /August such that farmers were able to buy inputs for the next crop season.

  9. ukundiye kupenga misala kuzelezeka uchitsiru kupusa kumbwambwana chimanga alimi amangulitsa lero kufuna kutipusitsa eti amalawitu pano tidapenya kangulitseni ku zambiako

  10. mulungu akuoneni afuna kugula kwa alimi a irrigation ndiwo apindule tsoka ulimi wa mvula dis yr osalima chochuluka tidzalime othilira admarc idzatigule mwina cha mvula chiribe quality ku msika wa kunja

  11. this government know that if malawi will be developed it will not make money so no development will take place.

  12. Izi zikusonyeza kusakudziwa ku malawi kumene anthu amadalila ulimi kuti uziwapasa zosowa zawo, bomalo likuganiza kuti chimangacho chinakalipo oti timayamba february kutenga ndalama za eni kumati ndikupasani chimanga ndikakolola tikatelo chilichonse cha umoyo maso pomwepo, munthu woti sanakhalepo kumudzi ndizoveka kumanena kuti akufuna kuti agule chimanga lero chifukwa sadziwa ngakhale nthawi yomwe timakolola kutereku akuona ngati tikuyamba kukolora kumene pamene pano mpamene tikuvutika ndi njala zololora zinatha kalekale.

  13. Ngat Pali Company Yopepera Ndi Admarc, Katangale Basi.! Msatipase Mabizy Ife Pano Tayamba Kulima Paja Mvula Yagwa Mwamva?

  14. I feel to understand this. Which farmers amend amakolola nthawi zinu. Aliyese akupanga zinthu mene angafunire. Chonde take the Admarc head to mental hospital as was Wandale

  15. Inu anene zowonakuti mbuzi za anthu ndalama alibe panyopanu ndambuyanowo omwewo chimanga chogula usiku ndalama kulanditu kumbali patuuzu

  16. kugura kulibe nthawi mwayamba panthawi yake pomwe anthu akukonzekera kumunda ndalamazo agulira fert ndi mbeu,gurani kwa munthu amene alinacho

  17. Kagulireni magetsi ku Mozambique ndalama zimenezo, musaiwalenso kukamulanda Chaponda ndalama zomwe akupanga pillow kunyumba kwake zija kuti magetsiwo akakhale ochulukilapo tapotananu mabwana inu mxiiiii!!!!

  18. Ife zomwe tikupempha Mbozi zija zija zimadya chimanga zija zisaiwale kubwera season imeneyi chonde! tiwone kuti kodi next coming year ADMARC And the Vendors mugula kuti ma K70 anuwo! agalu!!

  19. Chimanga chakeso chiti??? Kodi admarc ikusogoleredwa ndi alendo.Mlimi angakhale akasungabe chimanga mpaka pano kudikira admarc?????? tsiyani tizigulisana tokhatokha thumba 6 pin inu simukufuna january emweyu mutigulise 12,500

  20. uku ndiye kupusatu mukagula kwa ndani chimangacho poti anthu akudzala? stupid admarc thinking they r doing ryt decision mutagwirizana kale ndi mavendor zogulitsana chimanga nanga munthu wamba akanalinachobe chimangacho ino ndi nthawi yolima mmesa ma coupon mwapeleka kale? ndinu ombwambwana et

  21. This government is sick they already know that farmers haven’t have maize why they just say from vendors?

  22. Seems politicians and their associates are keeping a lot of maize which they bought at low prices….now its time for windfall profits from public resources via Admarc. For starters Admarc doesnt have the cash for this purchase but Treasury will rush to provide the money to purchase a commodity which Admarc doesnt really need.

  23. Akamanena kuti mbwampini akuchukutsa kugona vitsilu vina vimakana uchokera kalekale sadayambepo kugura mbewu November.

  24. next week farmers will be busy planting mbeu not including maize poti its not marketable….admarc yo ikanangothetsedwa ndithu

  25. Mukagula kuti, popeza munalekerera ma venda anagula kale kwa alimi anuwo? Inu munali kuti, nthawi yonseyi Chapondanso ndi uja anatibera uja.

    1. Ndiye iwe kwanuko ngati kulibe nyumba yabwino, umaganiza kuti umanga m’boma lake limeneli pamene iwe sukugwira ntchito? Ugwire ntchito, ukhetse nthukuta ndiye uzamanga yako yabwino kapena walephera nawenso kuba m’bomamo anakumbandiramo? Ndiye ukuchita jealous, usadandaule bwanawe boma ukulifunalo likadzawina nawenso uzakhala makhumutcha mawa.

    2. iwe jafali Tambala tazinvetsetsako zinthu zina osamangothamangira kulankhula usakudziwa chimene ukulankhulacho imagn anthu chimanga anakolola mu april ndikuyamba kugulitsa mu may kwama vendor mtengo wake 40-50/kg nthawi yonseyo admarc kuli zii ndiye alimi chimanga chija chatha mkugulitsa kuma vendor mcholinga chokagula mchere lero mvula yabwera alimi akudzala ndiye mkumadzati admarc ukuyamba kugula chimanga sikuba kumeneko? and zoti kale anthu amamanga nyumba mzoona osati izo ukunenazo si zoona mwina popeza ndiwe cardet mukubera limodzi koma udziwanvera chisoni anthu akumudzi kwanu wanva

Comments are closed.