Outspoken lawmaker for Salima North West constituency Jessie Kabwila has said late President Bingu wa Mutharika would resurrect if she joined the ruling Democratic Progressive Party (DPP).
The remarks follow reports that Kabwila is on the move to join DPP due to internal wrangles in the Malawi Congress Party (MCP).
Further reports revealed that Kabwila got money from the ruling party to spearhead calls for MCP to hold an early convention.
But Kabwila has downplayed the reports arguing the academic freedom saga created a cat and rat relation between her and DPP.
“Inetu ngati ndingadzuke lero ndikunena kuti ndifuna kulowa DPP, ndithu kumanda kusekuka, Bingu achita kubweleranso kuti nde masewera amenewo (If I can just wake up today and announce that I want to join DPP, am telling you Bingu can resurrect to stop me from joining),” said Kabwila.
She further added that DPP cannot buy her arguing she gets whatever she wants by working and getting paid as a Member of Parliament.
Kabwila is well known for her strong stance in defence of section 33 that provide freedom of academic after former Inspector General (IG) of Police Peter Mukhito had summoned Chancellor College based lecturer Blessings Chinsinga over an example he gave in class.
She together with other academicians demanded Mukhito to apologize for violating section 33 of the constitution but the late president Bingu came in defence of the then IG arguing “A Mukhito sapepesa” (Mukhito will not apologize).
Is this humane?
She knows that dpp can’t accept her she just wish
Asabwele ayi
Oasapanga ndale chifukwa cho mtsogoleri akuchokera kwanu, chilungamo enanu mukuchiziwa kut mtsogoleri wabwino ndi chakwera komaso osasankha mtsogoleri chifkw cha ndalama zake, dziko salamulira ndi ndalama zake koma misonkho ija! Nde tidzikonda atsogoleri anzeru pa misonkhoyo not mbava. DPP ngati idawina mwachilungamo ndichifukwa choti anthu amkayesa ngati aona nzeru za bingu koma pali mbola coz nthawi inayake abingu zinthu za ma shopo zinayendapo bwino komaso alimi ananjaya ndithu komaso zomangamanga zinalipo koma osati zalero zongomanga basi kaya nde stionda coz kudula katundu too much
Za ziiiiiiiii Kabwila ndindaninso pano?
That’s JK well learned , bad mannered personality!!!
Kodi Jessie Wabwila chani? Mayankhulidwe amenewa ndiye ati? Mukulephela kumvana ndi amoyo anzanu ku MCP ndiye lero mwati muphwekele Okufa? Machitidwe anu akuonetsa kuti mukudziwa ndithu kuti MCP siyabwino munangolowela chipyela mtima..! May the good Lord forgive Jessie Kabwila..! R .i. P Prof. Bingu Chitsime Chakuya Wa Mutharika
kkkkkkk Koma yea
Black woman with black cock what du yu expect from her than blank black minded speech…
kkkkkk m’bale wanga zomvesa chisoni bt she claimed to be Educated. Anthu ophunziranu mmmmm?
xol works better with umunthu if we dont have umunthu in every ting baba its zero pa ten
where ever she can go I have no problem with her Coz as much as iknow her she is not a game changer but atrouble maker,she is like Sulumba (the Nyasa Big Bullets player) wongotchuka koma wosathandiza team
Choice z Ur’s, bt u mst no dat u wll loose our vote next year. Dnt think zat we are a doom pipo, let meet on campaign
Tiyeni tikamakamba nkhani tisamanene za munthu amene anamwalira chifukwa mudzalandira matembelero.Mai Kabwila ziwani ichi Bingu anamwalira koma inuyo mudzamwalira liti?Osamatsewera ndi imfa inuyo sindinu munthu opambana pa dziko lapansi pangani ubale ndi Mulungu kuti mumphunzire kunena zachilungamo.
Kulankhula kwa makape,sitinyoza munthu wokufa.tonse tizafa.Anthu onyoza ngati inu mulungu sangakupaseni mwai.
Great
Kodi mbale wakoyu amayakhula bwa Kondwani Magombo,,,infact we cannot accept her aaaaa
Ha haha koma ndie kunyoza kwakukulutu uku. She remains the best for us.lol
If he is to resurrect NDE kuti anzangompasa mbama mkumabwereraso
No need for her to join DPP…..even Chakwela doesn’t need her….she is a prostitute. …and Chakwela doesn’t entertain prostitutes likewise DPP.
She can why not?
He would rely resurrect to get her out of the party and get back to sleep
Dont trust politicians as politics is like football a game of possibility
wat is it bra?
NGATI MCP INGADZAWINE 2019 KAMUZU AZUKE KUMANDA
Kabwira ndi wa pakamwa kachasu amampweteka 2 much muleke Bingu ku mpumulo wa bata wamva iwe mxu!
Muziona inu a Dpp mwayamba kale kunjenjera izoooo kkkkk
Tangoyamba kkkkiki
za ziiiii umbombo alindi ufulu wake
wasowa chonena
to hell wt all politians,,
its bcoz of such pple that Mw is unable to develop since 1963 to date. tiyambitse gulu la zigawenga kut Mw adzuke & selfish greedy leaders shud fear de power in pple nt us fearing pple in powr.
Ur welcome to blue party,,, MCP will die in opposition,,we need women of ur character in government side
chenjezo langa kwa kabwila nali: ukakhara usamathe mau chifukwa umdzachita manyazi mawa lino . adalipo anzako m dziko muno omwe adanyoza dpp koma lero tidawalandira ku dpp .komanso kumakamba za bingu munthu oti adamwalira kale sibwino ,
With these speeches , i think women are worse to be given top positions in gvt .
2019 it seems kuti kuzakhala ntchitoo.
How does that have anything to do with the dead.shame on you
Malawi24 Always Timawelenga Political News Bt There Is Many Areas Nid To Be Talked About Like Social And Economic. Plz Try To Improve On That.
DPP won election in 2009 and 2014 without Kabwila. I don’t think that she has anything important. DPP is stronger than ever.
Ndipodi,Jessie is mcp material hahaa
Nkhope yonyasayo kabwila
Iwe wokongola???
Just a mistake.she would have said, ‘…..chakwera will resurrect’,because chakwera is dead in mind.He will realise how strong DPP is after loosing alot of supporters.Its when he will start to play a true polical movie.
Amufumbatisa kale k12,000 very soon mumva kuti walowa mu DPP.
Mbuzii,,,,Bingu chamukhudza ndichani osangokana bwaaa mmm u suck big time
Very certain coz he knew MCP to be a killer Party & one automatically becomes another just by that thought of being a member of the MCP.
Chamba eti
Let her do wat on her mind she is not a kid she knows wat she is doing by the way am not believe that she can join this thief party
Indeed mumatiimilila you can not join MCP 2019 Bomaaaaaa
Zazii
Kukumbukira tati bingu uku hahahaha. Tiwanyenyenyanyenya
Kkkkkkk sakuziwa
Or itasiya kupanga campaign ma vote tathana nawo kaleso
Anthu azakhala akutchulabe bingu as Tate wadziko lino. DPP still goes on nanji mavote atheka kale or itapanda kusachita campaign
Zipani zonse zili ndi zofooka zake monga. Robert chasowa njaunju komaso pa 20 July osaiwala
Haha mkhito sapepesa
Good decision sister
Do your work lady, mw politics dangerous
nde Kabwira ameneyo
Koma mayi wokudayu samayankhula bwino
Ameneyutu kungolowa Dpp ndiye kuti tsogolo lake lokapezeka ku nyumba ya malamuro lathela pompo coz Salima maka maka dela lomwe amaimila iyeyu chiyambileni cha zipani zambili phungu wa chipani china sadawineko amangopambana ndi wa Mcp basi chimodzi modziso Salima north ndiye akudziwaso iyeyo pomwe alipo
No casing of any body here, if you have nothing to comment just shut up your mouth.
We love U. You are stronger woman than jb
go and kill the killer .Dpp!!!!!!Dpp!!!! 19 Bomaaaaaaa kkkkkkk
aaa anangosowa zochita ameneyo , enaso amati akalowa mcp kamuzu akhozaso kuzuka. nde zikusiyana patiiiiiiiiiii
This is politics just wait and see what gonna happen in nxt 2 years in another interview
Dear God dnt let any man marry this maize mill
Mama speak to inspire young girls who want to be like u
IWE KUNGOJOINA DPP bola kungomwalira
Ken Nsonda, Gwira nawonso ankatero.
Zowonadi mai zimenezo
Ngati ndiwe wa mcp kabwila,bwanji ukupanga decampan. Mcp/chakwera.zimatinyasa kumanyozetsa mbiri ya mcp chiyembekezo cha a Malawi
Kodi iwe Kabwila ulipa banja? Ngati uli single changu ku inbox
Woman just do politics do mention people who have gone to rest in peace.
Jessie is jessie and is very special i like her
Abale
Panya pako hule Bingu siosewelesa wamva?
Chepetsani ukali Phiri,kkkkkkk
Osamatha mau
Pepan mama msatelo ndthu kuchoka nchpan skuthetsa mavuto. tmasangalala tkamakhalananu ku MCP kwathu kuno.
Mwayamba kare, mwayamba kare =kunjenjemera!!!! Atangova Mia walowa mcp kunjenjemera….2019 mcp basi tizizagulako zinthu zamitengo yabwino pamodzi ndi zomangamanga osati zanu mzokhalira kumanga basi mukuona ngati tizikhuta zimenenezo? Inu mutadya zabwinozabwino koma anzanu chinsima tsku lonse kaamba kwakudula kwa zakudya zoonjezera koma chosecho materials ake ndi aku malawi.
Kodi zilonda zija zapola?
Inu a jessie,kodi muyankhula za ma drug chani?
Neither Kabwila will live 4ever . .R I P Bingu
Politician those are fu……
sure DPP is a terrorist party
kkkkk zanu zimenezo akakhala ine naleka kuvoter. phindu sinuliwona tele
aaa this woman it seems its a ghost akulimbana ndi munthu emwe anamwalira,why???
Osamatha mau mai kabwila dziko limazungulira
ZOPUSA
No com
I thought she is educated and mannered enough!
You cant utter about the departed like that.
She is educated in fact but she has to say how she feels about DPP regardless of her educational back ground
Fuck you Martha misguided fool
Anthu andale sasiyana zochita ndi hule, bola kumapanga zako basi.
This woman is now becoming a nuisance. I used to respect her but she is a re ability to MCP.
She better join DPP even if Bingu resurrects we do not care.
have respect for the dead.Bingu died we can now remember for those good things he did while he was alive…like many others Bingu had errored but that is wrong for a role model to say.
In fact Dpp can not accept her, I she can join Dpp I may leave this country
Sindimadziwa kuti akabwira ndi mbuzi yoganizani ngati nkhuku
Ndi ndale izi mawa timva wa joiner kkkkkkk kambwiraaaaaaaaaaaaaaah
akumutuma uyu !!!!
pati bii pali minga
Kabwira is another party herself.
Get to know who Kabwira is.
Evil is in her
Not her in evil.
Same to these other politician.
While some are in evil
Some, evil is in them
Who knows?????
Kkkkkkkk tell Them.Jessie ndipo azaukira mu state house momwemo kupangisa fans yonse ng’ondooooo kklk koma mathawidwewo angaseketsetu imagine Peter akulimbirana pakhomo ndi mabody guard hahaha koma movie ingKome iyi..plz Jessie try it aaa i wanna see
let the dead be , you are worse than the devil himself
Nobody is worse than the devil my freind unless if u r the devil himself..then u knw ur altitude..
Do u hv arelative who died? Idont think, lucky uu,,, ndasirira
Some people r just men by name hahaha even the bible says akufa sadziwa kanthu bii nduchimo ukupangitsani kulephera kutchula akufa..ndipo ineso ndiyankhula ngati Jersy ine kuvotera dpp bambo anga azauka kumanda….sometimes be men who understand what other things mean jersy was trying to say she cant do that equally as the dead cant resurrect ….think beyond ur nose men hiyaaa
Tell them kkkkk Viwuzemo!
thats stupid
Hahaha corrupt mind.
Anamupempha ndindani kuti a joine?akufuna yekha ife akweni aliko komanso jeff
No word
kabwila akungotaya nthawi
We never miss u where u are! ok?
Na ine chipani ichi chotchedwa MCP sindingajoine.
Who in Malawi ever thought Msonda will be in DPP ,MIA to MCP ,ATUPELE to DPP the party which sent him to Maula .My friends this is how politicians play their cards .
Tikanakhala tonse timaona chimodzimodzi ngati choncho sibwenzi ma so called politicians akupembedzedwa
Nsonda ndi hule spanner,he can move to any party at any time
Yes my sister caro ,Malawian politicians are all the same .First they have to enrich themselves ,They all dream of sending their children to UK/US for studies .Trust me these are the biggest crooks in the world .Every politician will say what Hon Kabwira has said
Tchaka ,anthuwa amangofunamo ndalama mu ndalemu .Osamanamizidwa kuti akufuna athandize osauka .Zitheka bwanj MP wa ku Rumphi kumakhala ku Blantyre ,nde mavuto a anthu a mu constituence mwake awaona bwanj
That is a point
Jessi jessi….yoooo this woman nawawooooo
bodza ili, ndiye ndalezo.
I admire this lady’s politics. Big up Jessi
U are an asset in opposition. Without u the opposition comes alot more weak
Fuck politicts…we r finally awake n’ we wont be fckin blinded by ur useless poli tricks…tidziwa chochita tokha come elections
Shaaaa kodi et
Let her just go to her DPP, MCP will be far better off without her.
The statement by honourable J. Kabwira if it is true then I find it absurd. It is not even different from that of Jeffry wa Jeffry. Politics is a game of certainties. You cannot rule out possibilities. After all, Kabwira has friends in DPP. They meet in women caucasses and forums. Bingu is gone. And gone for ever. And Kabwira cannot afford to harbour hate of that degree. We shall surely laugh at her when the opposite turns true.
Kkkk
Tiyeni nazo daily nkhani yikhale ndale ma media nawoso asochela Malawi will never develop with such kind of media
wht kind ov development will they wrote if there iz none all this ruling wht they know is to steal money
That’s kind of baby thinking do u think there is nothing that the government is doing Kkkk Malawi at its best politics is a dirty game indeed
Reporting of such kind is not wrong. Citizens should know what these politians are saying wherever they are holding their rallies. Now media are our eyes and ears who let us know what they have seen and heard. Then we digest the matter at hand and make a conclusion what to do next.
How can we develop? We have diverted focus from our daily trade to political journalism . Can’t we discuss something important? All I hear is mutharika this mutharika that , Mia this Chakwera that . We will be poor for decades to come . Just join politics if u want
Be quite guys all you have to know is that politics make news as well as promince people and proximity you are Malawians so these are kind of stoties we have to hear for us to make proper ideas when voting……
Be quite guys all you have to know is that politics make news as well as promince people and proximity you are Malawians so these are kind of stoties we have to hear for us to make proper ideas when voting……
Bingu resurrecting? kkkkkkkkkkkkk
In politics many join to lie, but they end up like torn apart curtains.
kkkkkk tili nawo akweni athu kuno kabwira sitikumufuna,
Kkkkkkkkkk mayi uyu sazathekaso
Kkkkkkkkkkkkk
Manong’onong’o mu mchipani.
What is in her mind this prostitute guys ?
????
Prostitute wa makobili
Thats not the essue kambani nkhani ya ndale not like that nonsence
she prostitute indeed after all who cares about her
Hahahaha , upabgisa ndi mutu wache wautalio huleyo kkkkkkkkkkkkkkkk bladfulu zache hahahaha.
Mutuo ndiumene umupangisa kutalikako kkkkkkkkkk
Prostitutes? Zachamba eti you haven’t even seen her back. Foolish
Iwe Sitho , foolis ndi mwachende akowo chokozera chosadulacho galu iwe
Tiye uko ndi hule lakolo Idiot !!!
Kkkkkk,koma guys,y u fight each other for vis nosense thing??
Kumangoyankhira nkhani zosaziziwa do u kno wat a politic is? inu koma kudziwa kutukwana kukulira koweta ng'ombe eti shem on u idiots
Prostitute like your mother Evance WA Amazango Phirih???
ngati wayamba kutchula za dpp nde kuti ali pafupi kulowa ameneyo, tiona mmene zithere
Kkkkkkkk
Kwacha!!!
kkkkkkkkkk Thus Jessy i know very crazy kkkkkkkk anyway Mcp got my vote
Nkhani dzandale zomwedzi people can say crazy things just to gain popularity
One thing you should understand is that these guys enter politics for money not popularity
with popularity comes votes then money
Kaawila was already a house hold name before she joined politics
kabwila can’t join dpp coz dpp is ful of thieves,satanic as wel as kiling
Agadama adaphedwa ndi dpp paja ?
Then you don’t understand politicians my brother .They will say this today ,and that tomorrow .
Mr Magongwa,i think you Don’t understand politics.When we say politics we mean all dirty things happened in our society every day.Look at Kamuzu times,Bakili Muluzi,Bingu,Joice Banda.people were killed without mercy so what do you want to say here my friend?Pandale palibe oyera ngati mwabadwa dzulo you can say That.Mind you bro don’t ever trust apolitician.
Jessie Kabwila is now God?
I Dnt Care bt to say fact dpp is full of devils even the boss is satanic
Mukuziwana asatanic nokhanokha
Being adevil or satanic its achoice of averybody,but whose clean after all,dont speak lik achild.
Luis my brother ,those are serious accusations .You suppose to have proof other wise you are attacking wrong people
But its a bad choice because there is hell fire I don’t know if the devil tells his followers about that.
iwe ndi mbuzi ndale suziziwa
mbuz ndwey kape nyan wav
TULUSILANANI ZIKWANJE HAHAHAHA
Cadet ituluke APA kkkkkk Ife phee
kkkk kma faz
Iyi ndiye mbuzi yeniyeni kuganiza ngati nkhuku
kkkk ndimbuzidi iyi or uone pic yakeyo akumizi enieni
hahahahahahahahaha basi gyz, mwangomusiyasiya chonchi. tiyenayeni madolo
Shaa koma Speewy nde wanyozatu
Zochezatu izi ,tisalodzanepo apa hahaha
satanic killing???? umboni wako ulikuti?? kubako ndavomeleza cos chipani chilichose chikamalamulila chimabako ndithu
Bwana Pheston kutchowezera kumeneko
Luis kkkkkk upsa mtima adha sunati
Kaya Mcp Ine Ndwa Mcp 4ever
Kabwila akudziwa pomwe alipo kuti kungolowa Dpp ndiye kuti wasiyana nayo nyumba ya malamuro coz komwe amaimila iye uja ku salima momwe zidayambila zipani zambiri mdziko muno sadapambanepo phungu wa chipani china akudziwaso iyeyo chimodzi modziso ku Salima north wachipani china sadapambanepo ndiye mwachidule ndinganene kuti zili ndi iyeyo bola salima akuidziwa kuti imadana ndi chipani cha anthu akuba
mr kalibu i can agree with u mbuz zinaz zmangokamba za mkutu akuona ngat kabwila angalowe chpan cha kubacho ng’oo mwauponda
kkk kma ntchto ilipo ku malawi
Watopa dimphepo ya utsiku#NGWANNYA
ndi dilu
I wonder why sometimes ppo crazy like this why Insulting eachother fo nonsese things anuwake ali pheee kudya zonona inu mukuvutika makomo mwanumo mkumawaikira kumbuyo anthu opanda pabwino ngat amenewa fuckoff
timangokonda ndale kma sitidya
Chisankha chili ndi mwini wake amene akuyendetsa Boma si anthu aku Salima okha komanso Chipani cha MCP sichili ku salima kokha ayi dziwani zimenezo
So Tembo is now in DPP…cause I know him as a killer not DPP
nanga njauju chasowa bwaj?
Akanafa galu amenei amatikwana ife nkhope ngati pazi la mtumbuka
who is kabwira? which kabwira? malawians very fun inded….. if call others satanists is kabwira holly? stop rwreckless remarks
Shut the fuck up
udzapenga ndi chamba
Please Kabwila don’t do that , we love you at MCP because of your heart of patriotic heart you have to MCP
Kkkkk kma m’mayi ameneyu kkk
Who gives a fuck about this bitch?
Mrs DPP mukuti bwanji kodi???
Mrs DPP ndani?
iwe kabwira iwenso galu eti? osamasewera ndi anthu akufa nyani iwe. bwanji osatchula ambwiyako anafa kalekale aja? leave our Bingu alone.