The ongoing heavy rains in parts of Malawi have caused a major traffic snarl the M1 road around Phwezi and Mchenga coal mine in Rumphi district.
Trending social media images hows how pathetic the situation is.
Some motorists blame the road’s poor drainage system and have since called upon the county government to address the problem.
HERE ARE SOME OF THE IMAGES.
Recently, the Department of of Disaster Management Affairs (Dodma) said up to 3159 families have been affected by heavy rains and storm that have struck Malawi this rainy season
Abusa alowelelepo basi
Waima panseuyotu aziyamika Mulungu akanatha basi
Ikanamutenga
Mesa akuti yakokolola chitukuko chonse
Kkkkkkkk
Mmene ndikuonela ilinkhonde mwa Peter Munthalika kkkkkkkkkkkkkk
Ndiye yalowela kuti a malawi 24
Roads must be prepared before rains
Vuto ndi misewu yakeyo
M1? Kkkk. Kwao kwa J Zuma ndi # R 562.
Kkkkkkkkkkkkkkk mmmmo
Izibwela mmene inga bwelele palibe vuto
Wina akatamukapo apeze ma contractor a fake
ngati palibe amene wafa nkhani yabwino,tikufuna vula.mseu akoza aboma koma moo wamunthu sangakoze
ngati palibe amene wafa nkhani yabwino,tikufuna vula.mseu akoza aboma koma moo wamunthu sangakoze
titati tifufuze timva contractor wake anali omwewa amu chirimbawa. ma road constructioniwa muzingopatsa group 5 kapena mota engil basi.
And you call that a road? Hopeless Malawi.
Poor Road costraction taonani nokha palichizenje madzi palibepo
Pamenepo wina angoti male, roadgate iyooo! yabwera yokha.
So Bad
That’s very bad ,komapokozapo kulintchito.