MDF soldier severely beaten in Mulanje after shooting incident

Advertisement
MDF

Irate communities in Mulanje district have roughed up a Malawi Defence Force (MDF) soldier, one of the militants believed to have a shot a man found cultivating close to Mulanje Mountain.

According to reports that Malawi24 is following, the soldier in company others had brutally beaten a man who they found ‘encroaching ‘ in the mountain before reportedly shooting him.

It was after this that the communities ganged up against the soldiers and they managed to get hold of one of them whom they nearly beat to death before police officers from Muloza station came to his rescue.

MDF
MDF soldiers not wanted in Mulanje .(File)

The identities of the soldier are yet to be known.

It is said that the others had fled from their camps having noted the people came to ‘revenge.’

While it is sketchy whether the shot man in alive or not, the locals there have stuck to their guns and said they do not want the ‘cruel’ soldiers around the district anymore.

Mulanje district hospital publicist, Innocent Chazimba is quoted by local media as having said that the injured soldier had deep cuts on his body and open fractures.

Malawi24 understands that the soldier has been referred to the Queen Elizabeth Central Hospital in Blantyre where he is receiving treatment.

In May this year, the MDF deployed soldiers to the Mulanje Mountain which has suffered massive deforestation over the years.

The country’s defence force had been granted permission to look after the mountain by the city councils of districts that surround the mountain which include Phalombe and Mulanje itself.

This followed increased cases of charcoal burning and logging which are making the mountain look bare.

Advertisement

224 Comments

  1. Bwana #joe musatero bwanji asoz athu amamenyedwa kuchitiridwa chipongwe ndi asilikali aku Tanzania wa,chosecho athu Ali pompo,athuwa ndizisiru taonan taluza munthu nkhan yake imeneyi ,mwanayo adamupeza .muz not Ku forest zandinyasa heavy amathatha ma chance pama sivilians, chochose paakamuna azawo amaopa ndakwiya nazo heavy

  2. KKKKKKKK MWACHITA BWINO AMAZITENGA NGAT MADOR OFUNIK KUMAWAPHETEMURA KUMANE KMSO KUMALAWIKUN MMMMMH SILIKAL MUKUMUPASA CHITO YOLIMBANA NDIWAMAKARA NDYE NDZIMENEZ AZIMENYEBWA KUMENE NDYE NGAT TKUMUPHEKESA SILIKALI TZAWOPA NDANI?

  3. Awwww! Zoxasangalasa kumva bt amene akunena zot msilikali samamenyedwa ndiopusa coz i hav neva heard dat ku training ya u soldier amaphunzisa Tai-chi.so,u need 2 tnk 2yc b4 post ur unnecessary comments.ndakwiya nanu a Lhomwe.

  4. Atumbuka akuwaopa amenewa Ku chikangawa. Koma pa alomwe mpolimba. Agalu inu mukalimbane ndi Tanzania uko ngati multi ndi mphamvu.

  5. Nanuso Masoja Asamakuphweketseni Chikuvuta Ndichani Kukatibula Mbewawa Zimenezi? Mufuna Mudzipezeleledwa Ngati Apolice? Mupange Zoti Pasanafike Pa 1 January Mukhale Mutathidzimula Kamudzi Kose Ka Akanyimbi Amenewa Kapena Tata Yanu Ilibe Mafuta? Muyesetse Ndithu Kukabandula Mbuzi Zimenezi Mukazibandula Mbuzizo Muuzeni Bwana Wanu Kuti Mdf Siimagadila Mitengo.

  6. Nanuso Masoja Asamakuphweketseni Chikuvuta Ndichani Kukatibula Mbewawa Zimenezi? Mufuna Mudzipezeleledwa Ngati Apolice? Mupange Zoti Pasanafike Pa 1 January Mukhale Mutathidzimula Kamudzi Kose Ka Akanyimbi Amenewa Kapena Tata Yanu Ilibe Mafuta? Muyesetse Ndithu Kukabandula Mbuzi Zimenezi Mukazibandula Mbuzizo Muuzeni Bwana Wanu Kuti Mdf Siimagadila Mitengo.

  7. It is nt true dat the young boy fired withn a forest bt de incident happened outside forest it was sad to me because it happened in my village kuteteza nkhalango sanakafka mmudz kupha munthu osalakwa beta znakachtka mu forest.

  8. ziko limatetezekandi asilikaliwa nde mukawakhumudwisa amalawi zitiyendela???muziganiza pochitazinthu etti asaa zitsilu nose musazayambileso agaru,komaso inu mukusapota zisiluzi nose mulibe zelu simungakhale atsogoleli adziko nose ndinu mbuzi zopanda mano seeeeeee

  9. onse amene zawakhuza amenyedwe msilikali samagonja ngati simutelo nde mwalowadi china mupite ndi tata mukawalange ana amwanowo bcz ndinu bomaka aaaaaaaa ndikanakhala ine wankulu wa asilikali tikanapita nthawi yomweyo ndikukakwapula afinye onse opanda khalidwe

  10. Kukuteteza zachilengedwe. ndikofunika kungoti zochoselana moyozo ndiye ayi. Asilikali athu a std 7 zovuta zedi

  11. Apite akathane ndimagulu awa ngati ndi asilikali Al shabab, ISIS, BOKO HARAM kapena RENAMO pasidyapa pa Mozambique osamangotha migayiwa ya boma. Kumangotha ma uniform kuyendera mmakachaso. Atibulidwe amenewo

  12. These communities must be punished u can’t attack an MDF member in that way ,i wish soldiers must organise & go back to that community for a revenge bcoz that community don’t respect the law

  13. kkkkkk.panel beating a soldier,kkkk.what is the mdf job description?,mps job description?,and malawi forestry security job description?,Iam sure mdf is acting outside its mandate,they have to review this mission on forest guarding.pliz go to congo,syria,nigeria,they are looking for strong soldiers like you and you will get paid good dollars.kkkkk.shame on mdf management.kkkk

  14. lomwe pple are good fighters for beating offecers.goerge chaponda de minister of agriculture was beaten near to death at likubula in de district.to day we talk abt awell trained soldier.lomwe tribe z nt tribe to play with.u could hv killed him no fear to anyone

  15. The soldier is innocent!!! Why in the first place the gvt resorted to be using the army while police is around? They needed an intensive security. This is the security they needed

  16. Tanzanians have occupied our lake, bt sodiers are doing nothing against them, nw shooting their fellow country men jst bcoz he was cultivating on protected land. Wat astupid deal is this?

    1. Nkhani ya nyanja its apolitical issue,oyenera kukambirana za nyanja ndi ma politicians not soldiers,ngati ma politicians akumakambirana nkumamvana then what do you think mdf can do..remember nkhondo imakhala ndi malamulo & nkhondo ikamachitika m’dziko amene amavutika kwambiri ndi ma civilian not soldiers.

  17. Using soldiers on the protection of our forest and other naturals,its realy a gud idea,thnx to every 1 who had decided an came up wth this idea…..Pena a Malawi ndifee okanika,siizii mvula yasuta chamba yapengeratu,izii madzi angosefukilaa kusowa misisi yoti ingaphimbe kuthamanga kwake,mmbali mwamtsinje mwangokhala donthi misisi yosee mulibemo

    1. Bruno ukunena zoona koma nkhani yonseyi ndiumphawi pa Malawi pano chikhala tinali ndi ma alternatives bwenzi nkhalango sizikupangidwa tamper, chitsanzo chimodzi: amalawi ambiri timadalira nkhuni…makala koma boma likuti tisamadule mitengo kapena kuotcha makala…Good! Koma nanga anthu aziphikila chani kkkk boma lilibe mayankho …no alternative…yoti awauze anthu. Do you think magetsi ku malawi kuno anafikila aliyense? Yankho ndiloti ayi, ndeno anthu apanga survive bwanji?

    2. kale tikadula mtengo timadzalapo ina ingapo pano zinatha tukomedwa ndi zithu zambiri tikuononga chilengedwe pano ndi izi every year floods

  18. Mmanja Mwanu Anthu Aku Mulanje, Kd Futi Amangowombapo? Nanga Munthu Amuphao Ana Ake Aziwayang’anila Ndan? Acita Bwino Kumutinya Akanaphelatu, Ngati Asilikal Mukufuna Nkhondo Pitan Ku Naija Muzikalimbana Ndi Bokuhalamu Ife Kuno Takana Nkhondo, Mulanje Pipo Osa4ka Akabwelaso Atemeni Adziwe.

  19. Mmanja Mwanu Anthu Aku Mulanje, Kd Futi Amangowombapo? Nanga Munthu Amuphao Ana Ake Aziwayang’anila Ndan? Acita Bwino Kumutinya Akanaphelatu, Ngati Asilikal Mukufuna Nkhondo Pitan Ku Naija Muzikalimbana Ndi Bokuhalamu Ife Kuno Takana Nkhondo, Mulanje Pipo Osa4ka Akabwelaso Atemeni Adziwe.

  20. MDF soldiers they fight in group, not by individual,after that drama, they will come in numbers to revenge. I hope that tym around they will loose again

  21. Whether you want or not;U are under (MDF)I am begging you to do like wat your friend did to them!!! And your will see guys, don’t talk shit out of the blue.

  22. Have u forgottern that everything these days is from China which means fake,yesterday i slapped one fake soldier on my way from Limbe do the same Zenco and see wat happens.

  23. Amakatani ku dziko la eni kungolowa dziko la alomwe apanda ma documents pakufunika ku malowa ndi pasport madera amenewo kupanda apo adzikuswani asilikali a mudzi

  24. Asilikali akusowa ntchito, angodikira pang’ono ngati angalimbe ndi Tanzania. Why killing a fellow Malawian? Chamba muzisuta pang’ono. Akanangomuphanso msilikaliyo bola. Auze a dotolo atsirize. That shows Mulanje is not in Malawi, WANDALE IS THE OWNER

  25. How can a Lhowe reader allow Lhomwes to be killed, He is The Chief Commander of this Nation akudziwa kuti asilikali ali ndi mphavu zambili, but he is misusing this sector. Mmalo momapanga improve ku Forest Security, kuumira ndiye ndi zimenezi “Lhomwe against Lhomwes.

    1. Nonsense that’s why dzina lako lili #Laudon. Ask everyone the meaning of your name i hope suzalembanso comment yoputsa ngati imeneyi

    2. Malamulo Alibe Kuti Uyu Ndi Mlomwe Kaya Ndi Ndani Ayi Ngati Mukupanga Zopusa Mwadala Popeza President Wa Dziko Lino Ndi Mlomwe Mzanu Chonde MDF Ikuthani.Funsani Azanu Aku Lilongwe “Dzalanyama” Adazisiya Kumeko!

  26. Kumeneko ndikumulanje musamale mutha nonse ndi nkhanza zanuzo kulibe anthu ogonatu kumeneko mumufunse George chaponda anathamanga asakufuna

  27. Nde zopusa ayambazi y shooting a fellow Malawian komaso un armed person what for “afuna mkhondo spite ku dafor ,have manners anakulowesa ndi achibale eti stupit akuchita bwino

  28. Kungoti amalawi ine sindimawavetsetsa zomwe amaganiza mmitu yawo chifukwa azathu achitezowa akakhwimitsa kwambiri mphamvu zawo nkuti alakwitsa akuchitira nkhaza anthu,akawalekeleraso palakwikaso nkuti achitetezo aku malawi ndi ofoila palibe chomwe akuchita amalawi sadzakozeka pakufunika mmalo otetezedwa asanyengelere munthu ndi izi tikuzionazi nkhalango kumatha munthu ootcha makala kupilikitsa munthu olondela nkhalango ndiye nkumati Boma likulekelera pano apeza njira yothetsera vutolo ndiye tisadandaule,ngati munthu akuchita makani pachinthu choletsedwa ndi boma khaulitsani kuti mchitidwe otelowo uchepe!!

    1. Ok nde mpaka kuomba mfuti ? Osangomugwila ndikumpasa hard punishment. Ndasusana ndizoomba mfutizo simkhondo iyi man

  29. Alomwe anzanga menyani ndipo iphani msikila aliyense amene azombera munthu…..Lamulo loombela alitenga kuti?bwanji osangogwila anthuwo kupita nawo ku police den ku court ……

    1. Nde Boma Luti Chiyani , Poti Anthu Wamba Akapha Munthu Woti Anapha Mzake Amati Amangidwe ,ndipo Nkhan Imakhala Pokopoko Pa Wailesi , Zidziwikila Pamenepa Ngati Malamulo Aku Malawi Ndiosakondela.

  30. Ukadzaona mwamuna omenya mkazi wake dziwa kuti ndichitsiru cha munthu amuna adzake sikuopa kwake ngati iwe gundwani okumwa mikodzo yako ngati ndiwe dolo kaishoshe ya nyanja akubandule ma Tanzania uwone kkkkkkk shame!

  31. Mukamabwela mubwele ndiya manja yokhayokha mukabwela ndiya mfuti ifenso mutitengele muzangozisisiya pa chitakale ntiphane basi

  32. Pliz asilikali athu osayereka kukabwezera anthu akumulanje ndi mfiti zoopsya ,this just asign to show there power that they are mfiti samaopa munthu kapena chinthu,,mukabwera ndi matata anuo kenaka iwowo azangotumiza njuchi so i warn not deliberately to go.

    1. Kkkkkk wakwiyadi ndimfiti di eti!! ,,,ngati mwakwiya man zikuwaweni zenizeni zaonesadi umbuli wanu ndikusazindikira kwanu muonjezele kumwa kachasu kapena mutafune alovera kut mumve kuwawa kwambiri,shame on you!!!

  33. Mmalawi muno anthu ammbili aphunzilira Sukulu ndalama za nkhuni ndi makala ndiye musamaiwale pamene mwayamba ganyu

    1. No need for fear, Mozambican soldiers will protect them since their leader has failed. Pamtundu m’kamayambana ena amalowerapo. Watch Out!

  34. Mmmmm china chilichose chalowa china,mbava zikukulu zikuvutisa mmalocation mu ndiomwewa asilikali athuwa apolice ndi ma prison warder oyang’anira akaidi.msilikali malamulo amfuti sakuwaziwa muziko lamtendere ngatili basi pot ndine msilikali iyenso anaishosha dala yekha he deserve to be beaten,masoldier akale analiaukali but ozindikira osatitamsiku ano tokwefura uniform osamanga zingwe za jombo,,

  35. as much as I recommend the good job our soldiers are doing by preserving our resources, their brutality on fellow country men who they are supposed to be protecting is unjust…. wish authorities had talked to them

    1. They shud kill them!Sometyms for sam1 who dint go 2 xul its had 4 him 2 understand samting,amangopanga makani opanda phindu.Komaso amaganiza kuti mfuti ija amangonyamulira manyado?mmmm ndiophera munthu osamva kaaaaaaa…

    2. He kill and he was just beatened with the whole village then who is strong? Kkkkk #patrick try to understand me this villagers they’re mad.. It means zoti nkhalango ikuyang’anilidwa ndi asilikali samadziwa??.. And am sure this villager mitengo imeneyi akanalowa nayo m’mudzi this same villagers bwenzi akut asilikaliwa ayamba katangale.

    3. mitengo yomweyo nkulu woombeledwayo akanakhala kut wapitanayo Mmudzi akananenaso kut asilikali akupanga chinyengo, nde muziganiza mbali zose guyz.,….. nsikali wachitabwino cz ena atengelapo phunzilo pamenepo and zaonesa kut nsilikaliyo ndiolimba mtima ndiomwe timafuna asilikali otelo

    4. How can a sordier shoot a man who was not evn carying a gun or a machete …???..its not fair evn sordiers has the rules to follow …they dont kill sivilians …their duty is to protect us ..

  36. Amadzimva sugar sugar ngati angamenye nkhondo Ku Afghanistan asilikali a Malawi
    akuzunza abale awo mu chikangawa popanda chifukwa iwo kumawona ngati madolo

  37. munyanya ma soja aku malawi mumakatani dziko la mulanje opanda chilolezo ndi dziko lililose malamulo ake amakhala choncho ka anthu adziko la mulanje ndi choncho koma ife ku malawi kuno nde ayitu dziko labwino ndendi Zambia tu basi maiko enawa aishiiiiii

  38. Mmmmm china chilichose chalowa china,mbava zikukulu zikuvutisa mmalocation mu ndiomwewa asilikali athuwa apolice ndi ma prison warder oyang’anira akaidi.msilikali malamulo amfuti sakuwaziwa muziko lamtendere ngatili basi pot ndine msilikali iyenso anaishosha dala yekha he deserve to be beaten,masoldier akale analiaukali but ozindikira osatitamsiku ano tokwefura uniform osamanga zingwe za jombo,,

  39. wamenywaa nsirikali kkkk. but what prompted the shooting coz idont think the cultivation of the restricted area itself caused the guy to release the triger. nde UTSAMUNDA sudzatha2 ku Malawi. there will b total chaos in that area if this will not be handled as soon as possible…. MDF soldiers pliz keep your ammunition n trigers for Tanzania kkkk osati abale anu ngati ife

  40. Guys mwaputa mavu pa chisa kuteloko. Mubvale zilimbe ndisawone olira, ndiseka makutu angawa ndi ma headset kumamvelera music basi

  41. mmanjamo kuti phwaaaphwaaa phwaa phwaaa anchita bwino akanangomupha.zimasamalika mbuli zimenezi. I will never ever stop hating soldiers for a reason I know. anandipanga nkhanza

  42. Alomwe mwaputayi ndiyachabe yawo tsimatherapo ndie mumenyedwa sidzinaoneke muwafunse anthu akwachikanda ku zomba zidawathera bwanji muchotsedwa mano sidzi naoneke.

  43. Kumalawi chilichonse chalowa pansi.Mpaka soldier kuthidzimulidwa?
    Komanso masoja penapake mumawonjeza.Zowona kumalimbana ndi anthu opanda futi?

    1. Nkhani ya nyanja its a political issue,ngati ma politicians akukambirana nkumamvana do u think mdf ingangonyamuka kukayamba kumenyana ndi tanzania,nkhondo imakhala ndi malanulo

  44. Uku Ndiye Kumputa Mu Soldier. Bwanji Osayipereka Nkhaniyo Mmanja Mwa Boma. A Mdf Ali Ndi Malamulo Okhwima And Atapezeka Olakwa Azathana Naye Waoyo.

  45. amatumbwa anthu amenewa makamaka kuno ku MJ.amangomenya ndi ana komanso nkhalamba zomwe.
    i think zinawakwana sopano.

Comments are closed.