Musician and lawmaker Lucius Banda has released a song that is condemning abortion and same sex marriages in the country.
In the song, Banda faults Malawi government for attempting to adopt western culture that will likely devalue Malawian culture.
Banda in the song claims that if the country wants to adopt such immoral acts because of poverty then that is against God’s wishes since Malawi is a God fearing nation.
The Balaka Parliamentarian adds that God did not create James for Adam in Eden since God knew that Eve deserved him because they were of opposite sex.
On Tuesday, Malawians held demonstrations led by Episcopal Conference of Malawi and Evangelical Association of Malawi to show strong rejection of the proposed abortion bill and to oppose the legalisation homosexuality in the country.
The demonstrations brought together all Malawians disregarding their religious backgrounds.
Tiye nazo soldier
Always Lucius samawopa munthu or Boma enanu ndi a DPP mumadana Nate komachoti muziwe Lucius never discouraged with people or gvt of to day ndipo chomwe wafuna chimatheka enanu
mumalimbana ndi Lucius zake zimayenda ndipo mukhoza kukhala mmodzi wa antchito ake,wins aliyese anamunyozapo Lucius amachita retreat chofukwa at the end womunyozawo amazachita manyazi ndipo amazayamba kumusilira . Amalawi tiziyamika kukhala ndi anthu ngati Lucius…. Bigup !! Sir Banda ndimakunyadilani continue to teach Malawian . Ndizasuporter Lucius all the way!!!!!
People tend to forget that we live die once, then live (after which our own deeds now will determine the after fate)
My musician soja ulemu wanu
what i have seen here is 90% of people ur against Gods power by bringing the same sex marriage but one word for you the Lord is watching you one day u go cry for ur stupid
Go ahead soldier,we’re behind you
I like this guy amakamba zoona…… Mathanyula ochotsa mimba onse to hell
Maturity sir lucious …salute
Auze lucy
Me hate mathanyula……
Ndizoona enafe ndiwokuba, enafe timatamba, enafe ndiwokupha enafe timachita zinthu zambiri zomuchimwira Mulungu. Koma balibe gulu la mbava lomwe linabwera poyela mkunena kuti akufuna ufulu wawo woti akamaba asamathamangitsidwe. Inu tchimo lanuli lapambana chotani kuti mpaka pakhale lamulo? Osamangochita bwanj uchitsiru wanuwo?
Palibe chimene angaope chimene mungaziwe iye ndi soja was aphawi sangayakhule alive choyakhula OK
Muli bho abanda
True son of Malawi
M’Malawi muno tikanakhalamo anthu olimba mtima ngati lucious bwedzi Malawi wathu ali Wabwino
ZIMVELE NTOLOO KKKKKKK
Pa nzeru zake komaso pa maganizo ake waimbabe nyimbo basi! Enanu mmafuna apange ma demo inu osapanga bwanji? Demo amapanga munthu mmodzi? Akayambitsa inu mumuthawe atsale nazo yekha basi! Za ziii!
Kunkhani yoimba tizinena chilungamo lucius banad and sikeffa chimoto akuziwa kuimba
Let him sing and speak out about what he sees,,, no matter some of us we don’t like him. But in other areas this guy doesn’t fear anything and he has done a lot
Ali nyatwa
umakwana soja
Auze soldier!
This is sir which i knows
Muthu wina aliyese amene amadana nacho chilunqamo ali ndi tchinga,koma iye mwini samaona,pamene dziko likupita kumapeto satana watilanda nzelu za chibadwidwe,pitiliza kuwuza mtundu wa amalawi mwina anqadziwe choonadi.
Kodi inuuu zija za mtiiii zija sizimwnezi?
Dziko lathu ndilamanyi tiziti ose amene ali kunyumba yamalamulowo palibe amene anabadwila muchigololo
Well done Bambo mp
Am ANTI-abortion bill… why bring an innocent child into the world if u r too poor to take care of it or if u r nt gonna love it and take care or it?
Unless the government is gonna take/adopt the babies that were to be aborted and take care of them… but like we knw… the government can’t even feed/provide for the people right now…
and also, women should be given the right to choose what should be done on their bodies…
babies change everything…
if u knw u dnt wnt the baby, or cnt take care of it, abort it…. period…
Abort it? Really? If u knew that ur poor n u can’t manage to take care the child why can’t prevent kutenga mimba than killing
how about u tell the boy to keep his dick in his pants instead….
Jame Walero so u saying if u r poor u shouldn’t enjoy sex?
Then use protective measures to avoid it …isn’t simple?
U know those thongs aren’t 100% protective right? Also, it would be grt if access to such was easy… probably free and of good quality
I dnt see why people should be against same sex marriage… if someone is gay, how does that negatively affect ur life? Let them be. Let them love…. it’s really none of ur business if someone loves and sleeps with the same-sex like seriously… Malawians should stop wasting their time on useless issues… focus on combating poverty instead or something like that…
Remember Whatever happens around you brings either positive or negative effects.with your mind can u advise someone to do rightious things,bcoz in everythn happens u wil be sayin;non of ur bznes.ur there to guide and teach hahaha!
Do you think by allowing this malpractice poverty can be combated,,,,,,, no & not
Firstly, what makes u think it’s a malpractice? It is coz the society or religion says so? Secondly, either way, that’s; legalizing homosexual marriage or not will nt affect issues like poverty in anyway… so it’s kinda useless to focus our energy on such …
@reginald, not everyone is religious… we all don’t believe in God so the concept of righteousness does not apply to all. Seriously people If it doesn’t directly affect u either positively or negatively, u shouldn’t focus on it… that’s wat wrong with the Malawian society, we tend to magnify futile issues and ignore issues that matter the most… that’s y we r stagnant development-wise
Nazooo Banda
who am I to judge? let God be God.
Watayisapo angati iyiye????
Anatha uyu amayimba kale
He speaks without fear ask late bingu on section 65 bill antil they arrested him he compose songs as a memories so that people should not forget solider wa amphawi komaso amalankhula mu parliament ameneyo let us enjoy the composition
Tinvele zimenezi
Umandiimilila soldier
The law of God never changes homesexual is still a great offence before God no matter how good you make it look it still sin.
Stimulating!!! Keep Soldiering On Lucius!!!
Munthu akamapanga za homesexuality amakhala kut akumulakwila ndani?…kapena akuphwanya ufulu wa ndani…?lets not jst generalise thingz,akamati abortion sikuti anthu azingotaya mimba chisawawa zimayendela ndi ma conditions ake,abortion ikuchitika/imachitika,alipo yemwe saziwa kapena?dis is in ada wayz kuthandiza kut atsikana azi user njira za bwino zochosela mimba ena amafa,ena amakhala osabeleka.
Mmene mukuonekera ndi zimene mukuyankhula zasiyana,Akulakwila ndani? Is that aquestion from you Sir?
Mumatiyimilira wankulu
DZUKA MALAWI ANDALE AMAFUNA DOLA BAS TICHITEPOKATHU DZIKO NDILATHU
What about satanic ? Why did sing nxaaa
Everybody commented here is highly uneducated sorry but its true, i feel sorry for my country malawi, full of dumb and jealous people
Who is he to dictate how people live their lives! It is for the same conducts that God will punish us-#Say_no_to __ homophobia
r u gay???
funk you wa gwela bweno Imwe chisilu
Kingston Alpacino LK …thank you for your question.. I am not, but I don’t hate anyone either.hope that answers your question
As for you Ellard,I sorry I don’t have time for people like you who will go as far as hating and swearing at people you don’t even know
He has spoken his mind,is it an attack?
Inu amene muyakhula against LUCIUS muli ndi vuto ndinu bwanji mukututumuka bwinotu bwino kapena inunso mumathanyula
Tikumudziwa kut boma livomeleza zimenezi koma plz Pakhale chitetezo chokwanira kwa anthu amene azipanga zopusazi……… Chifuwa nde kukhala kuzipha zitsiru zimenezi ……… Tizipha ngat agalu achiwewe…..ife takhonzeka kugwira ntchito yotamandikayi. Tikungodikira kut ayambe utsiruwo chifukwa Mulungu siopusa polenga munthu wa mkazi ndi wamwamuna. Ngat mumaopa kuchimwa ……… Sodomu and Gomola chinachitika ndichani? And zinachitika chifukwa chiyani?? Welcome to death to those who prepare Homosexual
My friend siya phazi usasiye mulomo ukuxiwa chomwe ndikuthandauza
Ayi
Tayamba kale ku bena ikupezka ma cd ma guy
Its good keep it up, good night
Ufiti,nyanga,usatniki chuma chamangazi atnthuwa ndi ana asatana akumindima opha anthu usiku ndi usana.
Great nxt time condemn satanic
Ndizaukapedi good move
Nde soja i know
Wanthu wanthu LB.
Ummmmh nayenso ndi munthu,amazindikira komwe akuchokera komwe akupita,Amangwetu mufuna atsitsidweso bus ticket yoduladula theradi afika nawo 2019.God bless Malawi
Lucious Banda More Fire ! Me too detest homo sexuality
Mukangovomereza Maukwati amuna kapena akazi okhaokha muzafa infa yowawa.Komanso ndi chenjeze kuti simulowa 2017.
Kamlepo ndi machine omanga ndi chain
To #Mordicaih. We are not saying nzeru alibe. NO! What we are saying is he is a low maker. He can stand in parliament and say something that can change things. Not by composing a song out of parliament. Zinali zomveka kale lija asanalowe mu parliament tinkaona ngati ndiolimba mtima akhonzadi kusintha zinthu koma ai
You need to know that message in a song will last for a longtime than just a day deliberation and its good that this big man like Banda is open about his position on this Matter.
Nop! We don’t need to talk about this for a long time. Once speak, once change. That is parliament. Bwanji nkhani za ma salaries awo samadziimba. Amalawi nde amatcha kamodzi dzikoso lamva
I like u
Guys NDITHANDIZENI,ndiinagwetsa foniyi.Moti yaphwanyikiratu screen…sikuonekanso bho bho.Panopa ndi pa facebook or pa whatsapp.?
Uli pa Twiter
We are behind you man of God
Oooo
Banda his man of Malawi it will take time to 4 all of to understand that. Mudzayamika akafa.
Aaa wofoira uyu Lucius alibeso nthawi yopanga ndale za mu nyimbo pano. Ali Mu parliament wakanika kutsutsa pano adziimba nyimbo chifukwa anthu adziyankhulira okha popanga ma Demo. Why didn’t he sing a song before demo? zikakanika azizipopa kuti ndiiyeyo? shupit
Limenero ndie dziko komaso mukuyenera amalawi azanga kudziwa ndale, akuphimbani maso kuti muzikamba nkhani zimenezii ndicholinga choti musakambe mavuto aNjala omwe agwa dziko muno changamukani amalawiii jacapuu
KKKKKKKK! ULURA @ . NET.
Umakwana
Eeetu anthu andale ndiwochenjera amafuna kuphimba anthu masoo
Iwe news 24 bwanji sukulemba nkhani ya chigawenga ca ku DRC chomwe akuti achimanga show us the picture plz
tinan kt tipeze song?
Lucius Banda ndi munthu amene amawona mavuto omwe amalawi akukumana nawo. Sanayambe lero kapena dzuro kuyimba nyimbo zodzudzula boma mukati muwonetsetse nyimbo zake zakale monga muchimbale chake choyamba anamunapo Dr K Banda muzimbale zambiri wa khala kunena za mavuto omwe ali dziko lanthu lino ndiye mukati alibe nzeru kapena mfundo ndi bodza kungoti nyimbo zake simumvela..
Jailbird nu respect
Respect
Ok
Hot game man vs man anamwariwa tiwatani
Yebo soldier yose boh
Mburi
Amalume
come on Malawi, these things are bound to happen and there’s nothing we can do abt it
kkk nyimbo zako anthu adasiya kuzitengera serious coz ukapita ku parliament palibe chanzeru chomwe umakamba. FOTSEKI
Amatiimilira Soldier
Soldier ndi kape asamatinamize coz iyeyo ali Ku parliament konko akuyenera kumalakhula konko not through music
Music imafika paliponse than anakangoyankhula
Malawi wanga likupita kuti kapena ndimphamvu yadziwanda Malawi wanga watani Iwe.
kkkkkkkk koma!!!!! nthawi ya Bingu ija munalikuti wawa?
Nice 1
Mayi mayi mayi ndamva kurira kurira anan kurira ana kurira umuyo wa muthu umayambira pomwe mayi wayima ungatheso kuchura dzina lamwana amene atazabadwe moyo wa muthu urinapo pake poyambira ukampha poyambira osazinamize ndithu mwampha muthu osaganidza kuchosa pa thupi chonde Malawi takanisisa lamulo lolawula kodi mayi wanga akadachosa mimba ineyo!!!!! Kadakharapo nono nyimozi sikadayimba nyimboyi ndithokoze mayi wanga pondisunga ndi moyo, tisamayambe zithuzi lamulo loterori takana takana tosefe takana veser 2 galu wamphongo adakana kugwadira mphongo dzake mamama nanga bwanji muthu akupangiranji tilemekeze ukwati wamamuna ndi kazi tiyang’ane komwe tachoka adarenga Adam sadapase James mamanewo oooooo hhhhh kaya ndimakobiri maringa ndi umphawiwu kotonewo oomh oooooo tisamatengere zithuzi ndi kutari komwe tisamamuyambe mulungu ooo ndimitima yachikondi tigwirirane manja kukanisisa lamuro lowononga zikoli tosefe takana takana tititiiitititii titititi ndimitima yachikondi tigwirirane manja kukanisisi malamulo lowononga zikori tosef takana takana takana totsefe takana tataka tosefe takana takana
Lucius banda new song against orbotion
Amatha inuso man ulemu wanu
Nanenso Ndkudabwa Kut Akulimba Mtima Ndichiyan? Chzungu Mutu Mulibe Kapena Akungot Ndisazafe Ndsanacheze Ndi Mzungu Kkkkk!! Azingolima Mphanje Ngat Akusowa Chochta!
Soja Sikuti Akayakhula Kalikose iye Bola Wanenelatu Mwamuva!
analakhula chani ku parliament iyeyo?…..poti anali kumweko
Uyu ndiye Soldier ndimamudziwa uja viva Lucius
Zofunika sir banda but ndudabwa ena ali against you pa homosexuality my friend u’l meet the creator
GOD fearing country my foot, Anthu inu mumatamba usiku. Lesbians and Gays are human too. Just because you sin differently from others doesn’t make you saint. God is the one that is going to judge all of us.✌leave it all to him
If ur one of them sorry,not in Malawi,only time will tell tiyamba zokuphani mukapezeka
I’m no gay bro but it’s unfair to treat them like this. Who are we to judge? Dont you sin? Come on its 2016. Passing the bill won’t affect your lives. You will still live and do what you do.
Please respond to the argument he has made and not jumping into conclusions. Buy the way, inu simunachimwepo? Ngati mumakhulupiradi mulungu, I hope u understand that sin is sin and u r not holy. So if we had to kill omwe achimwa Bwezi inu muli ndi moyo?
Mbuzi ya munthu’ kuphelera satana zoona mmmm
Tamukayikirani akulu….munyamata wakutowa ngat iwe kubakira ivi…..
we r not judging but rather rebuking the sin i hope we as Christians we r bind doing so rebuking the sin so that the sinful pple should turn their ways n follow Jesus we not judging but condeming the sin
Chisiru iwe ngati umamenyesa yakumbuyo zako izo
people of Sodom and Gomorrah were sinning differently but God punished these cities because of this particular sin mwina ndiwe homo broz.
I’m no gay bro but if you really read the Bible, it says these things will happen and it’s a sign that the son of God is near. So if you are really holy, stop focusing on trying to stop the bill rather pray harder kuti mukalowe ufumu wakumwamba.
I think zikwanje zinja zigwireno ntchito
KKKKKK! ALIYENSE APA AKUONETSA CHIMENE ALI. TIYENI NAZONI.
Guyz be serious……… Mulungu siopusa polenga munthu wa mkazi ndi wamwamuna……… Eish ngat mumakhulupilira Mulungu and ngat mumaopa kuchimwa … Kod ku Sodom and Gomora zinachitika zotani? And zinachitika chifukwa chiyani??
WARNING boma likangolora zopusazi ziwani kuti tiziyenda utsiku mmanyumba mwa anthu amene azipanga zopusazi ndikumapha mmodzi mozi mwa iwo…
Hahaha kulakhula ngati wamxelu koma mmmmmh zamanyi zen xen,,,,,,,guy????????,,,,,,ndiye kut chan???????,,,,,,,,,,,,,xoputsa etii!??????,,,,,,,,,
#CHIMWEMWE,Palibe kusekerera,bible likuti nkwiyo umadza kwa ana osamvera.Werengani Aroma 1 v18~32 “KUIPITSITSA KWA ANTHU[especially v26] chifukwa cha ichi Mulungu anawapereka iwo ku zilakolako zamanyazi;Pakuti angakhale akazi ao anasandutsa machitidwe ao achibadwidwe akhale machitidwe osalingana ndi chibadwidwe[ LESBIAN] v27) Ndipo chimodzimodzinso amuna anasiya machitidwe achibadwidwe cha akazi,natenthetsana ndi cholakalaka chao wina ndi mnzache,amuna okha okha anachitirana chamanyazi[HOMOSEXULLY]ndipo analandira mwa iwo okha mphoto yakuyenera kulakwa kwao(v28] Ndipo monga iwo anakana kukhala naye Mulungu m’chidziwitso chao,anawapereka Mulungu kumtima wokanika,kukachita zinthu zosayenera;[v29]Anadzala ndi zosalungama zonse,kuipa,kusilira,dumbo,odzala ndi kaduka,mbanda,ndeu,chinyengo,udani[v30]Akazitape,osinjirira,akumuda Mulungu,achipongwe,odzitama,amatukutuku,oyamba zoipa,osamvera akulu awo,[v31]Opanda nzeru,osasunga mapangano,opanda chikondi cha chibadwidwe,opanda chifundo[v32]Amene ngakhale adziwa kuweruza kwache kwa Mulungu,kuti iwo amene achita zotere ayenera IMFA,azichita iwo okha ndiponso abvomerezana ndi iwo akuzichita## mau a Mulungu sadzanama,anthu anchitidweu akuyenera imfa period.
Tchimo mpaka kulipangira lamulo dala…. Koma tchimo ili mmmmmmmm
may b u dont have kids or sunakumaneko ndi ma gay zopusa amapanga zobhowa pofuna ukhale mwa modzi mwa iwo God hate sins
Fool
Yemwe akupanga lamuloli bwanji ali ndi mkazi ndi ana?
I like this big man
Good
Mp wathu uyu amatinenela zakukhosi kwathu mwana otumika kptup
Am for homosexuality bill and am anti abortion bill, see you can love one bill without loving the both.
Parliament ndi nyumba ya satana aliyense akalowa mmenemo ziwanda zimawagwilitsa ntchito moyenelera jst imagine the whole parliament MP yemwe akukambako zanzeru ndi mmodzi bax………KAMLEPO!!
we busy talkin’ about abortion n same sex marriages instead of developin the country .. wtf is abortion bill, how zt gonna change our lives for the betterment… we got lots of problems :electricity,water,hunger,roads, drugs in hospitals,.. why not these things
??✌
Ndizako zimenezo
Exactly my point… we like to focus on futile issues… being gay/lesbian doesn’t hurt anyone
Iweyo ulibe pakamwa sungayankhule wenkhe?
Zoti ndi soja wa amphawi amadziwa ndiiyeyo soja wanji wamantha oimba nonse mukalowa ku parliament ndi style yanu mumangoti ziiii siinu oyamba baba tilibenso ndalama yogulira nyimbo zanuzosimukutimvela cisoni anthu inu kodi
Osamati tilibe; mbuzi iwe eti
Gift mbuzi ndiwe mapwala opotokawo
Guyz sizotukwanizana izi ndlama siziyankhula phunzilani kukhala an2 ozichepasa ambuye azakukwezani?
Lusungu respect a fool to avoid noisy osalimbana naye coz we r not talking abt him
kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk
uyo ndu munthu wamkulu
Go on
MUNTHU WANKULU KWAMBIRIII…..NYANSI TIKUKANITSITSA, AID OR NO AID, ZOPUSA AYIIII
Musakhale ngati business simuidziwa guys.
Mfundo ayimba munyimbozo kuti akazinene ku parliament nyimbo yakeyo adzagulitsanso ngati ?
Palibe asafuna Ndalama.
A Jozy ndakumvani pamenepo zoona
All the best big man
Koma Amalawi Nkhani Iliyonse Mpakana Mtengepo Potsutsa. Walakwa Chan Waimba Mvani Kaye Uthenga Wake. Mmmm Timasiyana Ndi Mayiko Anzathu.
Gud nyimbo imenei yiwafikile ao ndikunena ao ali pa m’ pando wakutsongolowo! kuli chisalu chofilacho !
A’ve never seen Lucius not speaking in parliament he is quite …..I also see fear in him
Nice 1 souja
Tiyibena Pompano Yathu Ija Yomapezeka Ndi Nyimbo Isanatuluke
Kkkkkkkkkkkk mwatelo wakulu
Ndiwamantha Uyu! Moova Iweyo Ndi Amene Ukupanga Malamulo Panopa, Do Smthng Choletsa Mchitidwewu
Big up abambo ,how is balaka
Nice
Ku parliament amawopa he is quite and samalankhulapo kalikonse ,,even kupempha zitukuko sindinamumvepo basi ukukayimba nyimbo yomwenso iweyo ndi amene uyenela kutipatsa mayankho…..I see fear in u now
MMMMMMMMM
musiyanise uphungu ndi oyimba..Anasitha zithu soldier
nde luso limenelo.akuyitha,we speak in different ways bro,poyamba paja munamumanga coz ankatokota,nde musiyeni apange chomwe amatha.kukhala chete sikupusa koma kuganiza bho.
nde sudziwa munthu wa mantha.
Paja samakhalakotu ekha
kodi kuyankhula kupose apa? how many people listen to parliament delibarations and get views clearly in malawi and how many pple wil listen the song and get the information?tamaganizani chemwali kkkkk!!
Mkufuna kuti ayankhure..when it bites him you run away…
Apa wayankhula kokuti aliyense amve. Muzayamika liti??
He has been singing a lot of songs but nothing happened….the place where he can talk and change things is in Parliament or doing demons like what Winiko did….well said Sister…
mwana wa chidapamba Banda ndi MAN.cc manyaz akupeze
Lucius ndikape sizokambila kumbali
But at least patali patali akanamalankhulako kwangonti ziiiii
Zaugalu
Mmmmmm Phunzilani Kuyamikila Anzanu, Zomwezi Nsanje, Koma M’nyasaland Tsadzatheka Mpaka Yesu Adzabwela Ndithu,,,
Whom to give you the solution Mama?revisit your comment
L Banda,more fire Big,mwina akakanva akasintha,(Jeremiah 26)
Zoona tichepetse nsanje
Big up Sir
ma gay amatha kukhalaso anthu ngat omwewa
Simudalakwise aBanda koma zinaloseredwa kale m’mbuku HolyBible.TSOKA OKWANIRITSA MALEMBA
Amalawi tiyeni tipemphere kolimba, kuti Mulungu atimenyere nkhondoyi. Akuluakuluwa asagwiritse ntchito Umphawi wathu kuti atibweretsere mchitidwe oipawu. Amene akusangalasidwa ndi mchitidwewu, apite ku Western komko. Ife takana.
matanyula ku Malawi ayi…….