Mnyamata wa ku Chanco akomoka pa chisembwele
Kunali chipwilikiti ku sukulu ya ukachenjede ya Chancellor ku Zomba zitamveka kuti ophunzila wina wapasukuluyo anakomoka ali mkati mochita za chisembwele ndi msungwana wina. Malingana ndi ma lipoti amene talandila, ati mnyamatayu anapita mu chipinda… ...