Mnyamata wa ku Chanco akomoka pa chisembwele

Advertisement
Sex

Kunali chipwilikiti ku sukulu ya ukachenjede ya Chancellor ku Zomba zitamveka kuti ophunzila wina wapasukuluyo anakomoka ali mkati mochita za chisembwele ndi msungwana wina.

SexMalingana ndi ma lipoti amene talandila, ati mnyamatayu anapita mu chipinda cha mtsikanayu kuti akachite ntchito za kwaipa. Koma ali mkati mochita ntchito za kwaipa kapena kuti kuionetsa monga akunenela anyamata amakono, iye anakomoka.

Apa akuti zinamuopsa msungwanayu ndipo iye anayamba kukuwa kuyesa kuti mnayamatayo wafa.

Anthu atakhamukila kumaloko kuti akaone chimene chinali kuchitika, anapeza mnyamatayo ali kwala pa kama wa msungwanayo, ali chibadwile. Ena ati anali atavala ka chishango kozitetezela.

Atamuunika anapeza kuti iye sanasiye kupuma iyayi koma anali chabe okomoka.

Advertisement

552 Comments

  1. Zofuna Zmenezo, Kodi Chigololo Ikhale Disease Yot Mpak Kufenta Nay, Anakumana Nayo Mens Ameney , Amangova Kt Imapha, Bola Waxankh Moyo Coz He Was In Between L & D

  2. Delta Hotels Toronto,is Currently recruiting able bodied workers from all over the world to fill in the following vacant positions such as:Room Services, Hotel Receptionists, Kitchen References,Hotel drivers, Pool Management, Gardeners, Security Services etc….Application lasts from now till 30th November 2016….for Applicants in America/Europe/ Asia kindly whatsapp miss Lisa on +16474920576 and for our African applicants whatsapp mr Josh on +221708781126 for guidance. …Wish you all the best of luck and will be delighted to meet you all here soon….Thanks….

  3. Mkaz Ameneyo Ndkumane Naye Axat Ipisele Cv Ma Boy Ife, Ndpo Nd Dyela MiCc Ya Sabola Yambili Kt Naye Azakomoke Ka Tatu, Achisilu Amenewooooooo!!!

  4. Zozi ona utakula kalezi sizabwino anyamata amazitama ndi nkhani yowa gona atsikana uyu nde waziwona wagönedwa ameneyo uswazi siwa bwino npaka kwala kufuna kufela pamwamba kkkkkk za chisoni atsikana aletsedwe nde apresdent ati bwanji nkhani imeneyi ndibwezi akunamizila #FROZY akanakhala alipo kuti ndamene akupangitsa ndi coca cola zosesi kuti anthu adzikomoka

  5. It seemz dis guy z a new comer n dis delicias game, but i hop somethn went wrong during de activity just do it again as w learn thro mistake dis tym u ‘ll not fant try 2 find anoda x and beta place. Rememba guleyu amadana nd phuma take care kuesera zida ndikoopsa ukagwidwa chonchi. Wory not peopl r duin koma kwakula mkusagwidwa Nde anthu asakuchulukire mzeru ngat sachita.

  6. vuto lake mukumamwa mankhwala, achina #washa_washa_in_bed #delay_spray_tablets #more_rounds_in_bed_pills mukafuna kapanga sex… lelo ndiizo2 mwakomoka nazo kkkkkkkkkkkk.

  7. Collings Kaunda, Fanikiso Ngwira, Kamsoso Ofana Ofewa Mtonga, Samuelmcadam Mfune, Flexter Mesinai Nkhoma, James Bk Madede Nyirenda, Mavuto Zachariah Belege Nyilenda, Isaac Goma, Gabriel Mvula

  8. True sex before marriage sin but some people is difficuit to doing this .some people sald God! Why god you creat a girls so the look diseas will come.is dangarous diseas. May be you creat animal only or you creat weman only.bcom if the weman only may be no virus found bcos some people we for get for this parasite.he say asweet is in to our paper are not delicious.

  9. Zats sweetest things when you eat too mutch you get heart attack kenaka umakomokadi ineso zinandichitikila ku IQ academy kkkkkkkkkkkk mafuno a bwino mzanga

  10. vuto la ana okonda za dama ndilimenero. …gongon ameneyu ndiochititsa manyazi/komaso ndi munthu omvetsa chisoni chifukwa kukomoka ndi pakati pa moyo ndi ifa. …asamale kwambiri anapita ameneyo nkutheka mwinaso wavulalira mkati ngati unakomoka nde nkatimo muli bwanji. …ana tisamangotengela anzathu timavutitsa nazo makolo. …kwa ine zah chisembwere zakozo pita nazo ku gehena. …komaso akadamupondako mutu galu ameneyo kuyipitsa mbiri zah ziii zinthu zoti zimapangidwa malo obisa kumachita kuululitsa chonchi. ….mbuzzzziiii yen yen! !!!!!!!!!

  11. Shame, Mulungu Akutiona. Mmalo Moptra Maphunzro. Ambuye Tipulumusen Ku M’bado Uno Wokhotakhota.

  12. Nthawi zina akaziwa amaonjeza manyekulilidwe akazakupotolera uku kuzakutayira uku wekha kuyamba kulankhula zinenelo zosadziwa kuli kumva kutsekemela

  13. LET HIM COME BACK AND EVEN SAY SORRY TO YOU.

    HERE IS HERBALIST AND TRADITIONAL HEALER TO HELP YOU..+27725564721

    Are you depressed ,feeling disappointed by your lover that he is changed you nolonger understand him any more then here is Herbalist Healer Shamim to help you flash away all those that are after him…

    Do you have any one prisoned but you want him be bailed out then come be helped,Are your kids not listening at you make them listen and understand you or be at good terms with them
    Am good in

    Bringing back lost lovers

    Stop Cheating and Breakups

    Flash away all those after your lover

    Students Pass Exams

    Bringing Back lost or stolen goods

    Iskhafulo or sea water

    Stop divorce

    Come for my manyonix Man power for your man hood

    Is any one hating you at work stop that

    Make your boss like you

    Get promotion at work

    protection spells to protect your properties

    Lock heart of your lover not to love any one else

    Ubheka mina ngedwa

    Remove or put iscitho

    Stop family misunderstandings and fights

    Come i cleanse your home

    Are you having Bad dreams come be helped

    Make your lover marry you and do as he promised you

    Are you having haunting spirits in your home i remove it away

    Make your lover feel you and get satisfied of you in bed

    Lock heart and his man hood be yours only.

    I have a cream which can make your penis big and strong permanent.

    CALL or Whats app +27725564721

  14. ndiwe mbuzi ya munthu anthu ambiri kunyenga kukuwasowa ndiye iwe mwayi onyengawo waupeza nkumakomoka nsana wako vuto ra zinthu za china ndirimenero ndikanakhara nkaziyo ndikanakunyengabe urichikomokere mpaka utafa kape iwe,

  15. Ayeneradi kukomoka coz zinthu zija ndizokoma kwambiri maka ukafika pajapo poiwalisa mavuto paja.zoti magetsi ndi madzi akuvuta.

  16. Mkazi ameneyo ndi mufuna(ndi Kusowa anthu ngati amenewo kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk)kukomoka kkkkkkkkkkkkkkk (asakhale mkaziyo ali kujako komwe amadwala kuja kkkkkkkkk

  17. Kkkkk kukomoka atamvalanso chishango ndiye akadzapanga plane adzafelatu ameneyu angozisiya kuti akhale Moyo wautali sizinamuyanje ayi

  18. Mukakumbukila bwino anthunu winanso anazabibidwa kupolly ndipo fans imati its a new style called BIBIDWILISM NDE nayo chanco posagonja yangoyambisa KOMOKALISM or KOMOKAOLOGY we don’t know iyi ndinkhani ya okhawo ammacollege, tigwiliseni totiyo mani!auzeni ma hende abwele uwili!

  19. Ana akumpanda ameneo, Osaziwa CHIBISALIRANO. Okawona Chancol adakawona Zose, amamuyamwa MAGAZI iyeyo namva Nyu! nyu! nyu! satanic imeneyo, waziona.

  20. Kkkkkkkkkk
    Tendrix Sizwe Bauleni Augustine Kalizga Gondwe WasFrèñçhíé ItzFrëñçhìé WillFréñçhíê Ace-wayne Shagazza Salifye-sukhe Sukali U’åv Found Ōzh

  21. Nkhani iyi yandikumbutsa za banja lina mwamuna anadwala kwambiri ndiye atapita kuchipatala adotolo atamuyesa mwamuna uja anapeza kuti ndi sugar ndiye a dotolo anamuwuza mkazi wa abambo aja kuti amuna anu tawapeza ndi sugar amayi amvekele asaah ndimadabwa kuti galu ameneyu kukoma kumeneku bwanji ali ndi suga eti

  22. Iiiiiiiii zandinvesa cisoni mpakana kukomoka y???? Guys pamene wakomokera munthu eeee sizocheza iiiiiiiii zinalipotu pamenepo mpaka munthu ziiiii

  23. Mnyamatayi adali ndi phuma, kumafunika pang,onopang,ono, kuyamba wagwira kae maka kamsonga kabere lakumanzere, ukatero uzayang,anisese Donas uzaona pakutuluka timazi toyera mbee.
    .. Nde ukagwirapo uzamva kupuma kuti tuku-tuku-tuku eya nde uzaisisite yakoyo ndikuyamba kulowesa mwapang,ono pang,ono, kenako mkazi uja amazaziongola ndithu kusonyeza kut wamufika, nde umayamba up down up down, koyambiliraku imapululura kenako imaxagwira mseu pamafika pena pojejema mukatero lekani kae up n down uja kuti muthire bwino cremola yo eeetu osangot Chanco iyai bwelanisoni kuthezo kuno

  24. Mwangosowa zolemba,mot inu tizit simuchinda akazi? Choikira nkhan yopusa ngat imenei pa air ndichan? Musiyeni okaona nyanja anakaona nd #mv uwu zomwe

  25. Mwangosowa zolemba,mot inu tizit simuchinda akazi? Choikira nkhan yopusa ngat imenei pa air ndichan? Musiyeni okaona nyanja anakaona nd #mv uwu zomwe

  26. WOYI WACHITA OVER MMM MWINA UKOTOMBA KATHITHI UZAZI WA BUT WACHILAMO FIRST UKO UKOPUKUSA WAA AZANGA” I,M SORRY”

  27. Akhululukilidwe Kanali Koyamba Kuchta Chigololo. Amamva Kukoma Ndiye Samadziwa Kut Timabwenza Magiya Ikamakomesetsa. Ndiye Mskana Amakoma Zedi Mpaka Mtima Imalumpha. Zmachtika Mwna Anali Wa Mikanda Mskanayo

  28. Shaaa mpakana kukomoka ndikudikura? Pamene amzakefe timangokuwa ngati chinyau kuti hihihihi..!!!! Koma osakomoka.lol

  29. Kkkkkkkkkkk… why I like Malawi 24 is their expert reporting of punani issues. Keep it up guys. We learn from you. These are everyday lessons in life. Real life in our society!

  30. Mlhako umenewo mtsikanayo anagula tseketseke kwa CHONDE Ku Mlhako.

  31. Anyamatwa enanu ndinu oyaluka hvy zinthuzi mwina mukuzionela kuukulu mutakula kale nde mukapeza chance mumakhala nazo phuma kuti mudye mudye basi poti zapezeka ,lero nde ndiizo wakomoka nazotu kkkkkkkkkkjk shaaaaaaaah kuyaluka mopusa

  32. Kukhalitsaku. Kodi ngati atchulapo zoti ndi atumbuka omwe achita zimenezi ngati? Ndiye ndikudabwa kuti wina akutchula mtundu wa anthu. Kumaganiza mukamayankhula zinthu.

  33. Basino geli ndi geli kuvayila zimenezozo? Koma yah ndi style yanji yomwe maniwo anakomoka nayo? Kkkkkkkkkkkkkkk koma zinazi inu

  34. This is normal in sexual health. Fainting, got stuck (vaginalis captivus), hallucinations, mamuring, etc due to different interpretation of your orgasm, a mysterious feeling ever. A human is only animal that enjoys coitus to make humans love it. This is because of a promise of God to fill up the earth

    1. Am not saying reason for sex but how pleasurable sex is. For example lions (and other cats in a felidae family) have a very painful sexual intercourse (males have spiked penises). Why? The lion’s population must be lowest to avoid destruction of lower trophic level in an ecosystem (I mean lions will destroy more animal if they are more). As a result a female lion feels very painful and doesn’t like the male to mate her (the lioness) hence there is a natural contraception (hurting sex). While in humans sex is very sweet for both male and female hence each needing each other to increase fecundity or fertility rate. I didn’t mean why people have sex. Yes there several trends of sex for pleasure in Kingdom animalia for non human species like in primates (apes and monkeys), macaques and bonobos

    2. Clifton, Simasiku otsiliza ndizotheka. Simalodzaso ayi anthu amatha kufa kumene or kukanililana chifukwa chokoma kwa kugonana. Ena mpaka kubwebweta, kutukwana, kubibidwa kumene etc.

    3. Gregory, when people get stuck during sex is normal. it is called penis captivus. it is caused when a woman is over excited during orgasm. The cervical muscles relax and open up, then the head of penis (glans) engages or enters the uterus and got ‘arrested’ by cervix sphincter which rings around the penis head and you get stuck. This occurs when a woman took long time without sex. But we cannot rule out juju.

  35. This is what will be happening to all who like sexuality as part of playing! This is so, due to what GOD said that “sex before marriage is sin, and the award of sin is death…!” So this will be happening for is angry with these behavior……!

    1. 1 Akor. 7: 8 Tsopano ndikunena kwa osakwatira ndi kwa akazi amasiye kuti, ndi bwino akhalebe mmene ineyo ndililimu. 9 Koma ngati sangathe kudziletsa, akwatire, pakuti ndi bwino kukwatira kusiyana ndi kuvutika ndi chilakolako

  36. My name is Mwafrica Kimani I Never believed i was ever going to be HIV Negative again,Dr Abumen has given me reasons to be happy, i was HIV positive for 6years and all the means i tried for treatment was not helpful to me, but when i came on the Internet i saw great testimony about Dr Abumen on how he was able to cure someone from HIV, this person said great things about this man, and advice we contact him for any Disease problem that Dr Abumen can be of help, well i decided to give him a try, he requested for my information which i sent to him, and he told me he is going to prepare herbal medicine, for me which i we take for some days and after i should go back to the hospital for check up, well after taking all the treatment sent to me by Dr Abumen i went back to the Hospital for check up, and now i have been confirmed HIV Negative, friends you can reach Dr Abumen on any treatment for any Disease he is the one only i can show you all up to, reach him on DR ABUMEN on his [email protected] call or whatsapp him +2347085071418.

  37. vuto lomadzisunga udyo umazagwa nazo mavuto tsiku loti uyesele kuti zimakhala bwanji mapeto ake amakhala amenewo chifukwa cha phuma ndazipeza ndazipeza mpaka thukuta kamukamu waziona ameneyo…1

    1. hahahaha nanga anthu enawa man amachita kubowa,,ka kumapezeka munthu za 18 koma mkazi osamuziwa mapeto ake amakhala amenewa,,,,

  38. Kumbali ya ine zizachilendo ndinavaposo za mkazi winawake adali pabanja lake labwino bwino.koma kamba kosakhutusidwa anapeza chibwezi kenako mpaka mkuthawitsana kumusiya mamuna wake.koma kuchokera pompa amati akamagonana ndi mamuna anathawitsana nayeyo mkazi amakomoka

  39. That’s just one of the things when you don’t know what you are entrusted to do. Makolo kumalimba mtima mwana ali ku sukulu not knowing akusambira muzigololo. Chonde siyani mudzipita kukaphunzira osakhala zimenezo.

    1. I am also at college but that doesn’t mean we have to loosen our morals. Or you are telling me that thats a good place for good moral degradation. Think of how much you are investing in ur education. That is for undetermined people. Suppose he died there what would u be sayin here

Comments are closed.