Rashid Gaffar blasts Nomads executive for hiring ‘Bullets’ die hards as coaches

Rashid Gaffar

Be Forward Trustee Chairman Rashid Gaffar has blasted the main executive committee for hiring Big Bullets die hards Eddington Ng’onamo and Eliya Kananji as coaches for the club.

Rashid Gaffar
Rashid Gaffar : Has made the claim.

He was speaking during an indaba with Wanderers supporters at the’ club house on Tuesday afternoon where the supporters committee was summoned by the trustees and the George Chamangwana led executive committee.

The said coaches were fired a fortnight ago following a derby defeat to rivals Bullets in the Super League at Kamuzu Stadium.

However, Gaffar believes that the executive committee made a huge mistake in hiring the two coaches who were once Bullets coaches some time back.

mike-butao
This executive has been slammed for making ‘haste’ decisions.

Loudly, he blamed the main executive committee for bringing on board Ng’onamo and Kananji, who, according to him, are Bullets supporters.

“We are not currently doing well in the super League because our executive committee brought on board coaches who are Big Bullets die hards no wonder we are struggling in the top flight. Had it been that the two coaches were Nomads die hards, we should have been somewhere in the standings,” he said.

He also lambasted Yamikani Kaliyapa’ supporters led committee for the ongoing wrangle within the club saying ever since coming on board, they have done nothing apart from pocketing millions of kwachas from the team.

According to information at hand, trustees and main executive committee are planning to remove the entire Kaliyapa committee before the weekend.

The Nomads are on position six with 35 points from 23 games and it will be a miracle if they win this year’s championship.

Advertisement

104 Comments

 1. Kkkkkk! shame on u admn, this is football anything can happen. Imagin what happen today between Bullets and Silver? avoid combination of things, football and spiritual matters.

 2. Unless we c the game of football from entertainment point of view we will remain ignorants of what sports are all about. Shame on us!

 3. Basi or mukambe zambiri zolira lira mauleeee azakhabe mauleeee mpaka kale kale the peples woyeeeeeeeee mukhalilatu kulira kwanuko ife zathu zikuyenda Ama NBB …

 4. MUSADE MA COACH VUTO NDI AKULU AKULU NOMWENU CHIFUKWA MUMAFUNA KUMALOWELERA NTCHITO ZAMA COACH KUMAUZA CHOCHITA KOMANSO MAPLAYER SIMMALIPIRA MUNTHAWI YAKE. MUKAPANDA KUKONZA ZIMENEZI MUSINTHA MACOACH MPAKA 1OOOOOO NKUMALUZABE.BB MORE FIRE!

 5. Ndaona macomment onsewa koma wina aliyense akukamba zokomera team yake zimene zisali zoona tiye team ngati ili ndi vuto posatengera team yomwe timasapota tili ndi kuthekera koti ndikhoza kupereka maganizo athu pokonza zolakwa zomwe timaziona kumateam ena we r 1 national taonani maref akungoimbira zokondera potengera team yomwe imasapota ma executtive ena amagulitsa magame zomwe zili zoononga mpira kwathu kuno chitsanzo china coach wa #Sayama zulo anasintha goalkeeper yemwe amagwira moti #Dwangwa imazunzika nkutheka analandira ndalama zotsatila zake zigoli zikangogola ndipo komwe wapitako mwinanso tsoka ntchito nkukathera or kumenyedwa komwe chonchi zipolowe mumpira sizingathe ayi kuonjezera apo maplayer akumalawi amamenya koma moyo wawo amakonda ndalama osati kulimbikila payekha ngati amachitira anzathuwa m’maiko awo ndi chifukwa pokutha pa chaka amakhala player watha kuno kwathu wina aliyense akanati azimenya mpira ngati Fischer ndikhulupiliranso kuti national team yathu ili nd maplayer abwino pomaliza #Man U yatenga coach wa #Chelsea morinho taona zigoli mpaka 4 zomwe zisalinso zoona potengera team ngati Man U nkatimu mutafufuza pali kanthu koma zimazaziwika ntchito itatha kodi maCoach mtima umenewu akamakuchotsani ntchito chifukwa chakatangale muzilowera kuti poti nazonso ntchito zikusowa?????? Am #Winner’s fan.

 6. Where were you when Wanderers were crowned as the beer champs? Why didn’t you say that in the first place?

 7. kodi KB itakung’ambani coach analinso Edie and Kananji.mesa nawonso anachita kuchotsedwa ku bullets pamene simachita bwino? vuto lanu ndi kusupuka,amzanu anawachotsa inu mukukatola,musaiwale chimene bullets chataya wina sangachitole nkumupindulira,koma chomwe enanu mwataya chimakhala chaphindu ku bullets

 8. Gaffar is right something fishy is happening at Wanderers. Ndiponso Madeira ndi Butao si Manoma. Anabwera bwanji ku Manoma afufuzeni. Kaliyapa akuwononga mbili ya team amatenga 12% ya ndalama zapa gate chifukwa chiani? Mr Gaffar mwachita bwino kulakhulapo kuti tikonze team. General secretary ndi Team Manager akhale anthu akuti anamenyako Noma, enawa ndikuwona ngati amagulitsa ma game. Coach Kananji akapanga line up ma officials amasitha line up. Amagulitsa game.

  1. Kkkkkkkkkkkkk team singayendetsedwe ndiokhaokha adatsewelapo kapena oyikonda okhaokha sono kuti muyambe kutengela zimenezi musalako ndi ma Nigeria ndi Japanese ajatu coz mMalawi aliyense ndiwa BULLETS kkkkkkkkkkkkkk uko amangofunako nchere.

  2. Alick Kazembe ndi Magie Sundu mpira wa Bullets ndi Silver wantha bwanji pa Kamuzu stadium? Fisd Cup. Chonde ndiwuzeni ndinatalikira.

 9. Bambo ife safuna ameneo onyozana uja eti?.Ngati inu khuta Chapati wabinobino uja khala Sabola Kambuzi uja.ife safuna.pitani khalani pasi Wanu binotu.Inu banji inu khala vuta wonse uja?pabuyo wake azanena kampani wanu wama Truck uja BigBullets ameneuja athetsanso.Inu safuna khala Malawi wathu uno pitani kanu uja IRAQ mezani uja Sucide basi.ife pambuyo tizaimbira inu nyimbo uja wathutu Saziwa eti?

 10. kkkkkk…….koma guyz kunoma kuri amisara ambiri et………ndiekut zaka Ten zonsezi zomwe Noma yakanika kutenga TNM ndie kut maCoach anari a NBB?

 11. Kodi akamapanga hire ma coach ma trustee samaikapo maganizo awo, a Gaffar wa mesa anali atauzidwa zoti ma coach apangidwa hire ndi awiriwa? Tsono akubwaza mwano oterewu lero chifukwa chani anga sanadziwe panthawiyo? Kukula mphuno sikudziwa kumina, chimodzi modzinso kukhala ndi ndalama sikudziwa za mpira asiireni omwe amadziwa za mpirawo azikamba inu zikayendetsani ma business anu

 12. Dont say like this Mr Gaffar.Talk as if u are a responsible person.Did you not knew that Kananji was a Bullets fan.If yes as u r talking,why did u hire him to take charge of ur so called good for nothing squard?As a patron u would have known this before.More over Kananji have done his good job for by bringing a bit of a smile on ur miserable supporters all over.Learn to appreciate where it is necessary.Solve ur squables in ur house amicably before thing go from better to worse ok.

 13. Zankutu mayesa inali ntchito, zamafano basi musawaphere mtsika matimu ena akuwafuna, mbola ndi ma player anu, mwina muyese inu ndi Yasin ngati ma coachplayer muziwina dala.

 14. Tell R Gafar to stop dreaming during the day. He knws nothing about football. Iye koma kuvundukula ma skirt a mahule basi.

 15. Akakamba zamasapota a BULLETS ndiye alikoditu moti pama player 11 aliwonse a Noma 9.5 ndi ma die hard a BULLETS kkkkkkkkkkkkkk ndipo ngati mukakamila kulemba ma player a Noma ntchito ya u coach za league iwalani.

 16. I support the motion executive iyi ndyosaganiza that’s why Franco Ndawa naye zinamuvuta ku Bullets zimafuna munthu amene amaitsata team yo amamva kuwawa mmene amamvera masapota team ikamaluza nanga munthu ndisapota wa Bullets mukuganiza angamalowetse team yolimba akamamenya ndi team yomwe amaisapota?

 17. A Gaffar, mwasowa fundotu yapa akanakhala kuti ndi ma diehard a bullets akanakuthandizani kutenga chikho cha mowa chija? Osangonena kuti ku wanderers kuli vuto bwanji?

 18. Vuto la Wanderers executive too much promises eeee tikupatsa galimoto,iyayi tikumsngila nyumba,iwe tizikupatsa ndalama kuposa aliyense whats player join your club mwathana naye you dont even remember those promises.Izi ma player zimawayenda mmitu mwawo.Pomwe BULLETS ikamagula player sichitanso kunyengelela imangopita ndimawu awiri;achimwene takupezani kuti mukatumikile team ya wanthu,agree or disagree??? basi kkkkkkkkkkkkk so easy.

 19. Osangoyamika kuti kananji watengetsa Carsbelg cup kawili bwanji ameneyu ndiwopusa akanakhala ndi trst wa Bullets akanapatsidwa mamba

 20. ndizoonadi bwana gaffar siampira, palibe chimene mwakambapo2 apa sir, osamangopanga zandale zomwezo bwanji sir

 21. Umbuli upose apaaaa???? kkkkkkkkkkkkk kenako ikhala misala ndithu.Coaching ndi ntchito chabe sizitengelanso kuti adamenya team yakuti yakuti okanika ndima player-wo and mutsikimiza ma game atsalawa kuti Wanderers sizampira.Chamangwananso ndi die hard wa BULLETS????,Nanga Franco?,Gerald Phiri??,mwakhala mukuchosa ma coach mazanamazana plus omwe mwawaitanawa adachotsedwaponso.Vuto lagona pama player komanso executive.

  1. Kkkkkkkk NBB inalakwisa kwambili kugonjesa manoma ambili tsopano kumanoma akuoneka kuti mitu yawo sikuganizanso bwino chiwinileni nbb muja zikundinvesa chisoni kwambili mmmmm

  2. Kuteleku a BULLETS akamaimba kuti Noma mitu sikugwira amanena zoona eti ndimkaona ngati ndi nyimbo chabe koma lelo ndasikimiza siiziiiiii kkkkkkkkkkkk

  3. Anyani sasekana zikundu ndithu tinaonela inu mitu kusagwira karonga itathana nanu mitu simagwira mpaka anthu angapo anachosedwa mukuwaziwa nokha lero thawi yathu yochosa yafika inu phee

  4. #Enerst i think waiwala iwe Karonga itadyamo palibe emwe adachotsedwa mpaka chitimu chidatenga Presidential ndipamene national team idatenga ma player 6 pobwelela nawo team inabalalika idayamba ma draw okha okha.Nkhani itafufuzidwa zidapezeka kuti ndalama za sign on fee plus salary sadapatsidwe ndipomwe anthu adayamba kuthotholedwa.Then apasidwa team was still struggling then zidanziwika kuti coach akuchepela achoke komanso TD akuononga chuma adachotsedwa.BULLETS idachosa anthuwa pazifukwa zokhunza BULLETS osati chifukwa choti yamenyedwa njeeeeeeeee.

 22. Koma uyu ndiye ndi mbuzi ya munthu,zaka zonse yakhala kapado fc yosatenga league amaphunzitsa ndi Kananji ndi Ng’onamo? Teamyo ndiyo yokanika

  1. Cornelius, koma waganiza bwa??? Wandifunsira funso labwino kwabasi, winaudi ndi umbuli kapena akungofuna aoneke ngati akugwira ntchito chi Gafachi, chikho cha mowa chija mesa ma coach ake anali omwe mwawachotsawa? kikikiki ha ha ha ha ha!

 23. And 4 Ur Own Information Who Coaching Last Year Wen U Gat Thae Carsberg Even This Year Is It Not The Same Kananji U R Fooling 2 Day?

 24. Timeout no point Mr Gaffar if Wanderers has got a cup it is the carlsbeg which you grabbed after beating Bullets in Lilongwe with the same Bullets diehards coaching.

 25. Mvula ikagwa kuchuluka zolila lila,iye Gaffar wadziwa liti zimenezi?Kodi mmene amkatengedwa Kananji ndi Ng’onamo bwana Gaffar anali kuti?Izi ndiye mbwelela zenizeni komabe musova.

 26. Kkkkkkkkk! Abwana palibe zimene mwakambatu apa coz pa nthawi imene executive yanu lmatsankha macoach awiriwa inuyo munali muli kuti fundoless zimenezo abwana mwaganiza mochedwa sure komanso mwaonetsa kuti mpira simuudzuwa sure

 27. Zkamavuta nd chonxo machulutsa ma becoz munkaleka ku munena Elia kananj muja adakutengetsani chkho cha carsburg last year mpaka chaka chino zaziiiii

  1. Wanama iwe kumalawi mpila ukamakhala masewela chabe bwezi kulibe zowawa maka bullets zamasewela sakhala nazo koma nkhondo kuposa ndale ukunenazo

  1. Inu simumatha mpira full stop!!!.Last yr mudaikwapula BULLETS mu Carlsberg final under those coaches and this yr mwaikwapula Silver kawiri konse kodi aipa lelo?.Kusachita bwino mu league ndimmene mudabadwila imakuvutani basi.
   Akukupusisani kwambiri.

Comments are closed.