By October 16, 2016
Patel Fakawo

Patel Fakawo has been arrested.

An 18 year-old man has been arrested for wearing a police uniform and impersonating a traffic officer in Mulanje, Malawi24 can report.

The man, Patel Fakawo from Mwineya village, Traditional Authority Nkalo in Chiradzulu was found stopping vehicles at Makande junction along the Mulanje-Midima Road while wearing a Khaki police uniform.

However, some passengers who were in a minibus he had stopped, got surprised to see him wearing red civilian shoes.

So they assisted one another and apprehended him before later handing him over to police officers at Nkando police unit.

Meanwhile, investigations are underway to establish where and how he got the uniform.
149 Comments

 1. musamange munthuyo kutheka ampepetula kwao nanga munthu albe nd JCE yomwe akaima panseu atavala unform ya aplc kmaso nsapato ya red ndkumaimitsa magalimoto anthu ckupanda nzeruko kumenekn

 2. Kkk mwana wanzeru ameneyu!!!!!!

 3. Yaa imeneyo ndi deal yabwino anaona Mbava za Police zimatakamukila mu Seumu ndenayeso amati ayese kklkkk.Naneso ndikufuna ya mirrigretion ndikatakamuke pa Dedza boda

 4. Mwasiya kukumba mbewa mwatulukira yaupolisi? Kkkkkk nde mukanabulira ka jombo, panja a Police athu kulezera mwina iweyo ukanakhalako wa sober

 5. sanalakwitse munthuyu a police nanuso ndinu mbava munampatsa ndinu nomwe munthuyu uniform yanu yolandirayo

 6. Where did u get the uniform

 7. adah awawawa amatha ndi nyatwaa bhahahahaha

 8. Akufuna ya police ameneyo angolembedwa ntchito bc ndie wamkulu wapolice ku mulanje tsopano

 9. Diction and verbatim pleeeaaaaaase!!!

 10. Akadya ku chipatala osadwala,?Atani munthu kuti akhoze zikusowera ntchito mu !Munthu achite Education asachite sizikusiyana.

 11. Kkkkkk ndani safuna atamayimitsa ma galimoto pa nsewu? Ukaipa dziwa nyimbo

 12. Eeee mufunseni anaipeza bwanji uniform kenaka muyambe kuwasaka awa ankanama kuti president wamwalirawa akalowe aleke chibwana ufulu kuwutengela pa mgong’o eti asakusiyeni mungazaphese anthu ochuluka ndi heart attack mbuli inu

 13. Wachepa koma ameeneyossso

 14. Ulibho ase apolic wo amajaila amawona zangati azivala woka koma zovalazo ndi zaboma kkkkkkkkkkkkkkkkkk

 15. Kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkooooooooooooooooooooooooookkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk

 16. Kodi ameneyu tinenekuti constable kapena sajent either lauftent general ndani kkkkkk

 17. Big u will repit ?????????)))((()())(((((((()))))))(((no

 18. mwina anapatsa ndi wachibale mufunse bwinobwino.Amakhumbila ntchito imeneyo boma lingomupititsa ku training basi.

 19. Vuto lake sizimavuta kupeza zovalazo

 20. Mesa ndmalaya palibe chfkwa chomumangira pamenepo

 21. KKKKKKK MALAWI MASUZGO NGANANDI CHOMENE.

 22. Kkkkk mpwanga ukafela kundende

 23. Arrest even those who are in police training schools, joined without interviews. Corruptive Nation ………

 24. Koma ndi mwana osati muikulise nkhani ponena kuti a 18 years old man ayi ameneyu ndi boy,akanakhala akufuna kuimila u president mungamulole? Nde mwana ndi mwana mungomuwuza kuti izi sizofunika

 25. Anawonjeza naye azakefe timangovala ma boxer okha zinazo ndikuwasiyira kkkkk.

 26. Fuxo nkumati. waitenga kt???

 27. Makolo ankakuuza kuti phunzira azakhale wapolisi iweyo unkaithawira xool taona panopa kkkk

 28. Nde malamulo akut chani ukapezeka utavara uniform ya police mmmmm palibe nkhani apa

 29. Wapatsa ndani uniform

 30. Agjo Chyx says:

  Nanga Anakakhala Kut Amaphuzitsa Ana Kuwenga Mukanamugwiranso?Musiyeni Palibe Section Chomwe Waphwanya.Ingomuthokozani.

 31. Ndiye vuto ndichan za bomazo.

 32. Maesa anatchena…

 33. Kkkkkkk evn malemu Ezeki adamufunsapo nzake Jacob kut chipewa cha police mudachipeza bwanji??? Zamanyazi izi munthu he is not a police man koma wapezeka ndi uniform ya police , adayitenga kuti tiunikepo apa?

 34. tangomulembani ntcito.swagga yamuima mfanayo

 35. Eeesh akanalemeratu uyu.

 36. PA MALAWI KIKIKIKIKIKIK INE NDIKUFUNI NIZABE MACHINI, Kasinja Kikikikikhki

 37. Kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk,,,koma analimba mtima2,alandile ulemu wake pokamponya KUCHICHIRI

 38. you are hero wayitha

 39. bwezi akupita nayo kumowa azikamwa wawulele

 40. athu akubainu komaiwende gwanyadi zitibelani muzakayakha sikulomwe litazakupezeni thaw lililose losayembeke zela athu mukwabelao simukudziwa kutizithuzo anazipeza munjila yanjikuti azipeze anachitakuzivutikila kutiazipeze zipangani ndi thaw yanu nafeso izakwana thaw yathu

 41. Kuonjezela chitetezo

 42. Sakuyenera kumagidwa chifukwa .mavuto pa malawi awonjeza

 43. Kkkkk koma…. musiyeni…samadziwa chomwe akuchita..nanga mpaka sapato ya red…police yake yakuti….kkkkkkkk

 44. Kkkkk! Ndizomwe Amathaminglapo Apolice Zopanda Mphavuzi ,koma Akava Kut Mbava Zafut Zikhuswa Benk[bank] Amazibikila M’timaoffice Tawo Fraid Ov Kutcholedwa Makongono Khakhakhakhakha, Ine Ndkubwela Nd Ya Arm Yonse Tizaone[ Tz].

 45. Kkkkk! Ndizomwe Athaminglapo Apolice Zopanda Mphavuzi ,koma Akava Kut Mbava Zafut Zikhuswa Benk[bank] Amazibikila M’timaoffice Tawo Fraid Ov Kutcholedwa Makongono Khakhakhakhakha, Ine Ndkubwela Nd Ya Arm Yonse Tizaone[ Tz].

 46. Leave him wangovala makaunjikawo .He is just following the 4corner stones of our country

 47. kkkkkkkkkkkkkkkk

 48. Alick Modi says:

  Timve ziti? Ena akusatsa za HIV pompa ena akutiuza za nkhani kuti wina wamangidwa atapezeka ndi jombojombo ya police eish!

 49. Hello friends, my name is Susan Mwanza this a testimony of how i got cure fully from HIV/AIDS, i was diagnose with HIV/AIDS FIVE year ago, i contacted a doctor who later gave me some treatment, but it was like the treatment he gave to me were not enough i was desperately in need of something that will get rid of the deadly virus from my body, my life was miserable i lost my job and few of my friends, not quit long a faithful friend of mine came to me one afternoon telling about what he saw on net a testimony of how DR Abumen cured people from various kind of virus including Herpes, i was like this is a scam, but he old me he believe in what he had read on line’ he told me he will contact DR Abumen on my behalf and he did so, after some days he receive a parcel containing DR Abumen herbal medication, he present it before me to use it, that when am cured i should pay back the money it cost her while negotiating for the medicine, after taking the medicine for some days according to DR Abumen instruction, then i decided to go for check up and i was happy to see that no sign of the virus was found in my body, i am very thankful to my friend, if you are having a similar problem or you need his help you can reach him on (doctorabumen@gmail.com) or you can call or chat with him on whattsapp through +2347085071418, please share to save life.

 50. chamba mudakali ana

 51. osaphwekesa ntchito yapolisi fisi iwe

 52. I hate cops they ar full of corruption they lyk money too much

 53. Zaziii, ngatisiwa police wanu infrom waitenga.sifukwa simunabwereke inuo ndemwwamanga koma anakakhara kuti munabwereka ndinu munaka mpata bello,kupusa

 54. Mmmmmmm ndiyake anampasa bambo aka asanamwalile bwanji kodi nkhazazi

 55. Mumaitha man, ndakunyadra kkkkkkk

 56. Frank Nice says:

  Kkkk..anauchekad ulutsi ndatha kuona ndye akaxebenza zaka zngat ku prison…?

 57. Incase u ddnt click on the board letter heading read >>>> AM JUST A VOLUNTEER BECAUSE POLICE IS FAILING-Suspect It is reported that an 18-yr-old has been arrested for wearing police uniform. His name is Patel Fakawo from Mwineya village, T/A Nkalo in Chiradzulu. This morning he was found stopping vehicles at Makande junction along the the Mulanje-Midima Road while wearing a Khaki police uniform. Some passengers in a minibus got surprised to see him wearing red civilian shoes. They managed to apprehended and hand him over to police officers at Nkando police unit. Preliminary Investigations show that hw got the umiform from Patricia KaliatCia and was one of the fake Police recruited who were booted out early this year at Police Training School

 58. Kkkkkkkk amisala ndi ambiri obwera poyera ndi ochepa

 59. Ali Uyuli says:

  he was just helping…police Dutties..leave him…amafuna achepetse Ngozi Nzapanseu chabe..kkkkkkkkkkk

 60. Alomwe sazathekadi kkkkkkkkkkkk….

 61. Vuto a Malawi 24 nkhani mukaiyamba simutha kuimaliza, uniform ya police imapezeka ndi a police ndiye iyeyo anaipeza kuti?

 62. koma ndiye anapeza dilu yabwino ameneyu , olu ineyo kuzipeza zovala zimenezo ndikhoza kusangalala poti ndizingopita nawo mmawamawa kukayoimisa galimoto zitatu basi ndalama yachakudya yapezeka kkkkkkkk.

 63. Kkkkk, Reform. Iwe chipewa cha polisi unachitenga kuti? …. directive …. kkkk….

 64. Thats what i call Self Employment..

 65. Tem Dizzo says:

  ULOVA ngati wanyanya kugulisa zinthu mukuwalanda so mukufuna anthu azitani

 66. Kkkkkkkkkkkkkkk yachita kumukhalatu

 67. Okay…………….. Ngati sizake zovalazo mwini wake alikuti???????

 68. Muciyeni m,nyamatatu ndiosalakwa,,,, Ndikati soooo! Anamupasa ndi a malume ake aja anali asajenti ujeni aja kkkkkkkk

 69. Inu Apolice Akumalawi, Why Mwamanga Wapolice Waku United States Of Mulanje And Thyolo? Apolice Aku Malawi Mukayankha Mlandu Pamaso Pa ICC Pomanga Wapolice Wadziko Lina….. By Vincent Wandale!

 70. point of correction!!!!!! man not arrested…. but police arrest their friend

 71. Where do these impersonators get these uniforms?

  • AM JUST A VOLUNTEER BECAUSE POLICE IS FAILING-Suspect It is reported that an 18-yr-old has been arrested for wearing police uniform. His name is Patel Fakawo from Mwineya village, T/A Nkalo in Chiradzulu. This morning he was found stopping vehicles at Makande junction along the the Mulanje-Midima Road while wearing a Khaki police uniform. Some passengers in a minibus got surprised to see him wearing red civilian shoes. They managed to apprehended and hand him over to police officers at Nkando police unit. Preliminary Investigations show that hw got the umiform from Patricia Kaliatia and was one of the fake Police recruited who were booted out early this year at Police Training School

 72. Ask him where he got the uniform then charge him

 73. That young man is very naught

 74. Aaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaa amazing’ono zimenezo komaso ndimwana ameneyo sanakhwime nzeru

 75. kulimban zozzra sopano kusiya khan yofunikir kwambir yakusow kwa presdent

 76. Nmasu leni ameneyo siwolakwa ali ku school amati aphuzitsi akamufusa kuti ukadza maliza school umafuna utadzakhala ndani amangoti wa police nde amadabwa kuti zinakanika nde amati akaona wa police wavala amangoti ntchito yanga iyooo ndengati yapezeka pena pake aku enela kuupha ulusiwo mumasuleni ngati mukuona kuluza ingo mulembani ntchito ya police zo mvala ali nazo kale

 77. SORRY SOKALIYENDA

 78. Mumufufuze bwino ndekuti pali apolisi ena amene amagwirizana nao Amamubwereka zovala kuti aziba

 79. Mumayambitsa Ndinu Nomwe A Police Kumabweleketsa Ma Uniform Ndi Mifuti Kwa Zigawenga Kuti Zizikabela, Mufufuzeni Bwino Bwino Ameneyo Atchula Amene Anamupatsa Uniform Imeneyo.

 80. Why arresting this innocent young man? The only thing the Government could do is to offer him a police job send him to police training school other than arresting him. This story is exactly like what happened to the composer of a song called Soka kuyenda in early 80s who ended being offered a job as a police man in appreciation for his song which tackled the ploblem faced by police officers when in duty

 81. Where did he get those uniforms

  • Answer>>AM JUST A VOLUNTEER BECAUSE POLICE IS FAILING-Suspect It is reported that an 18-yr-old has been arrested for wearing police uniform. His name is Patel Fakawo from Mwineya village, T/A Nkalo in Chiradzulu. This morning he was found stopping vehicles at Makande junction along the the Mulanje-Midima Road while wearing a Khaki police uniform. Some passengers in a minibus got surprised to see him wearing red civilian shoes. They managed to apprehended and hand him over to police officers at Nkando police unit. Preliminary Investigations show that hw got the umiform from Patricia Kaliatia and was one of the fake Police recruited who were booted out early this year at Police Training School

 82. Albert Idi says:

  kkkkkkkk muthuyu amasilila atakhala wapolice mulembeni tchito

 83. Ndiwosalakwa ameneyo ndikuti tchito ya police amaiduna hvy

 84. Mwina yinali njala, kufunafuna chakudya, nanga titana,

 85. Kma wa traffic chipewa chake chimakhala chonchi mmmmm

 86. aaaaa how come a polisi aku malawi kumanga wa polisi wa dziko lina? mtopola2 umeneu…..kkkkkk

 87. Kutheka Abale ake anamwalira so Asamagwidwe ai apolice ndiachinyengo

 88. kkkk komatu zikumukhala zovalazo ndy bwanji osngotsegula police unit mbali yakumeneko mwina kulibe tu unityo. ndy uyu akuwathandiza apolice osadziwa job akut wapalamulanso mlandu. itanani ama gagula aweluze ndi iwo. kkkkkkkkkkk

 89. Guys mwalakwitsa munthu ndiwa benitu uyu

 90. Amalakalaka kuti atakhala galu wosaka!!!!!!!!

 91. Asamagwidwe amasulidwe ameneyo nayeso ndiwa police woona za ufa muchitundu

 92. Chimz Bawa says:

  Anaipeza bwanji

 93. maybe he has got his relatives who working under malawi police service & he got from that pple

  • AM JUST A VOLUNTEER BECAUSE POLICE IS FAILING-Suspect It is reported that an 18-yr-old has been arrested for wearing police uniform. His name is Patel Fakawo from Mwineya village, T/A Nkalo in Chiradzulu. This morning he was found stopping vehicles at Makande junction along the the Mulanje-Midima Road while wearing a Khaki police uniform. Some passengers in a minibus got surprised to see him wearing red civilian shoes. They managed to apprehended and hand him over to police officers at Nkando police unit. Preliminary Investigations show that hw got the umiform from Patricia Kaliatia and was one of the fake Police recruited who were booted out early this year at Police Training School

  • he was illegaly recruited through p.kaliat

 94. Eish alibe mantha eti kkkkk

 95. Don’t arest him coz he was just practising to be a cop,remember,practice makes perfect.

 96. Kkkkkk ok koma Ku m’phanje kkkkkkkkk make me funny so

 97. Ine phee kumudikira Peter…. Paja mma 1 pm eti?

 98. Muyezen misala kaye mwanayo priz aboma ndapota nanu…………

 99. KKKKKKK OK ine ndiye ndavala m’phati yao kkkk sandimanga?

 100. vuto ndikuzima zima kwa magetsi

 101. vuto ndikuzima zima kwama getsi

 102. Mwasalanso nanu mumangidwa mesa mumanamiza anthu kut presdnt wamwalira inuyo manyazi bwanj matako anu agalu inu

 103. musiyeni mmene lavutila dzikoli mumati atani

 104. Mulemben ntchito kupolice ko

 105. kkkkk koma zinazi

 106. Kufuna kupanga mbiri nyamata wooo ayindithu Amwene zko lakuziwani

 107. Musiyeni nayo ndi police wa A WANDALE KKKKK

 108. When you have done something long and you have cuaght do’nt impersonate to be as a worker from somewhere, the best way its to say truth and In Malawi its prohited to do like that

 109. Zimangovuta izi… Amakhumbila atavalako basi kkkkkkkkk

 110. Ngwa police uyu sajent meja petel kkkkkk!!

 111. Chilungamo chiwoneke. kodi iyeyo anayipeza bwanji?

 112. Bwanji simmanga ovina Ben…naye akufuna kutchuka basi kkkkkkkkk

 113. eish verybad koma kodi chimakhala chilichani kodi ifeso tilindi age yomweyo sitimaganiza chomcho akufunika yesu ameneyo

 114. Where did he fa**kn get is that’s what u have to tell us

 115. Chilungamo chiwoneke. kodi iyeyo anayipeza bwanji?

 116. kkkkk….koma #malawi sadzatheka guyz!

 117. mumufufuze-zovarazi-wasitenga-kuti

  • AM JUST A VOLUNTEER BECAUSE POLICE IS FAILING-Suspect It is reported that an 18-yr-old has been arrested for wearing police uniform. His name is Patel Fakawo from Mwineya village, T/A Nkalo in Chiradzulu. This morning he was found stopping vehicles at Makande junction along the the Mulanje-Midima Road while wearing a Khaki police uniform. Some passengers in a minibus got surprised to see him wearing red civilian shoes. They managed to apprehended and hand him over to police officers at Nkando police unit. Preliminary Investigations show that hw got the umiform from Patricia Kaliatia and was one of the fake Police recruited who were booted out early this year at Police Training School

 118. kkkkk-G””’Chief-comander-of-malawi-police-