One of Malawi’s gospel musicians Thoko Katimba has spoken out onwide spread reports that he once impregnated Miracle Chinga, daughter to the late gospel songbird Grace.
Speaking on Sunday during a live show in front of thousands at Squirrels Park in Mzuzu, Katimba surprised people when he called his fiancée to the stage to deny the pregnancy accusations.
“I want to break all bad rumours that were surrounding you people that I impregnated Miracle,” said Katimba.
When his fiancée joined him on stage he said: “This is my fiancée and if all goes well we are going to wed next year, I was regarding Grace as my sister which means Miracle is my daughter too, how can I do such silly thing,” said Katimba while holding his fiancée.
In the past, there were spreading reports that Miracle was pregnant for Katimba.
The Anaphiri hit maker lost his wife Margaret Katimba in 2013.
Wagwira chikolopa
Wagwira chikolopa
Wangomgawira ka H paja thokotu…..
.
Iiii mwana uja anatenga basi
Oky
ngat sizoona kt thocco anapeleka mimba, Mulungu akhulukilr pakamwa ponse pamene pakamba nyansi komanso ena amene anapeza mwayi woonetsa nyansi za mkat mwawo pakupeleka ma comment opusa namazitenga ngat anzuru,,,,, mwalankhula dziko lakumvan ndipo takuziwan ngat mumafuna kuziwika ku mtundu wa a Malawi,,, ngat ili ngila yowanamizila anthu thocco pofuna kufufutitsa mbiri yako Ambiye akukhululukile coz this is not the best way of handling it, Mulungu sakhululukila munthu amene safuna kuvomeleza tchimo lake, it’s better anthu akunene koma Ambuye akulandile….. Miracle, rhe truth is on your heart of who did it, usatukwanitse maina ochuluka auze anthu choonadi ndikubwela pamaso pa Mulungu mogonja, He forgives so dont run from Him but rather run to Him.
Oyenda ndyesu amaenda nd m’didi
katimba anakwqta kwa miracle thru miracle sex
Tamva
Ishiii ndye akbiz wat ma plain 2 much a da ao
thoko katimba impregnated mirracle, pregnant’nt she??
Thoko ukufuna umuphenso mwanayo nanga wapha angati mbuyomu kkkkkk
Koma guys..kumudziko mwafasako…basi sindizabwerando
MIRACLE CHINGA MOFFAT WAS NEVER PREGNANT… THATS THE HIGHLIGHT… SHE WAS NOT AT ANY POINT OF HER LIFE, PREGNANT..GET A LIFE AND MOVE ON WITH POSITIVE THINKING.
miracle ndi hule
mukulakwitsa mukatero….. mul nd umbon kut miracle ali nd mwana? samalan nd pakamwa panu, ganizan mul inu wina akunamiziren, kapena munamugwra akupanga chigololo? mau a Mulungu amat usanenere umbon onama,,,,, dzko laipa ili, khoza moyo wako usayang’ane zatchmo lamzako, ngat akuchmwa apempherere osat kunyoza
Thocco ma plain too much
Mmm zoyamwila kwa mama kkk
ok?
Miracle anabereka mwana when she was in std 8….
Serious??
mwanayo alipo bwanj pamalilo sananene kt grace wasiya ana ndichizukulu
Nd zoona buanj sakutchula ine, umafuka pali moto
nyaninso uyu ndioimba?
kkkkkkkkkk
Secret is btwn thoko,miracle en god nobody els pls let god b god mzovutilako izi jst mind ur speech
I hate u,Thoko
Zisiru izi ukhritu wabodzao iyaaah mumatikwana ndikunyazisa dzina loyera la mulungu
ndinu mahure NONSE
Chisilamu chidalaka fisi …..!!!!!!!
Kusowa Mkhani
Kumalawi
Ndiyeno
Icnt trust u thoko
Athoko mwanyengaso mwana wamasiyeyu mpakana kumpasa mimbi?kumangochi kujaso ndimene muziwira zosokoneza banja lamai aja osangokwatira bwanji achimwene?uzimu wanu ukupita patsogolo kapena pambuyo?
Thoko katimbandi huleka
Amalawi kodi vuto lanu mchiyani!!kodi kutenga mimba anayamba ndi Miracle?ngati ndi choncho iwe Frank Banda unabadwa bwanji.kodi ndani sadziwa kuti amalawians24 ngamisala?walakwanji mwana?bala wako mwana udzimuloza chala numati mimba mimba osati miracle chonde STOP!!!
Una nchindadi asakudziwandani zaiwe ndi mwanayu kodi,kumangoti ndimapemphela ufiti nkumapangaso chokani shupitiiiiii
Man of god alibe ma desire kod mukamati man of god nde kuti xani nyere ilibe man of god
Eish koma aMalawi
What?
Limbikan ntchito osati kukamba zazanu
Amalawi mabodza ,kkkkkk, paja Satana anayenda ndi minyendo kumalawi nchifukwa chake uphawi sudzatha ,mabodza
Kkk Koma
Masiku ano bola kuziwa chimene uli pakati pathu ndi Mulungu basi.Anthu padziko pano akunamizira mdzina la Mulungu pamene akuchita zotsutsana ndi zimene mwini wake namalenga akufuna. Repent!!!!!!!!!
kod abusa samva ludzu musiyen thoko azimukambula miracie
Kaya ndi chi thoko chanucho
Oimba zauzimu mmalo moti adzionetsa khalidwe labwino.Iwo ndipomwe alikalikiri ndizopusa,kumakhala ndimbiri zoipa.anthu oipa!!!!!!!!!
God may forgive us
Komanso ngati Katimbayo ananena poyera kuti mimbayo ndiyake ndiye kuti alibe nzeru, chifukwa munthu wa nzelu zake sangaime pagulu nkumafuula kuti wakuti uja ndamupatsa mimba ndine, olo mkazi umukonde bwanji sungalengeze, angofuna kumuvula kenako amusiye
Zaboza thoko anamasura tundu Wa amalawi ku robbiz park kuti sanayambepo wapanga chibwezi ndi miracle ndipo sazapanga naye chibwezi coz miracle akamaona thoko Ali ngati Ancle ake not what u think amalawi munakhara bwanji tisaipise mbiri or dzina LA mwanayi musiyeni agwire tchito yofalisa uthenga Wa ambuye chomwe mungaziwe maitanidwe amakhara osiyana ndiye mimba ingakhare 2 yrs mmmmmmmm zisakuwaweni siyeni mwana afalise za ambuye uyu
This just a last kick of a dying horse . If you are a true Christian why should you sleep with someone outside marriage . He is not better than Miracle Chinga they both committed fornication so he must stop painting a bad image to the girl.
Leave the girl to alone
Pempho Lange ndiloti Miracle Chinga should come forward and tell us who was responsible for her pregnancy. …otherwise this doesn’t make sense…all in all aliyense amalakwisa….siwoyamba uyu
tawerenga nao
Anatoshowana kodi?? Anatomva kukoma eti!??
So is this true that miracle is pregnant and the one who pregnated is Man of god thoko katimba ?I thought Mr katimba is a married man why????
mukamava chibwana ndichimenechi mupangachi
Alaliki alero ndiomwewo,,,,, amasochelesa anthu bc
KODI MMESA ACHIMWENE CHE KATIMBAWO AMATI SAZAKWATILANSO AKHALA AKUKUMBUKILA IMFA YA AKADZI AWO AJA???NANGA ZASINTHANSO?
iyaaa
Only fools comment on what they don’t know and they don’t have evidence
Oyimbira bussiness awa osati kufalitsa uthenga wa mulungu ayi
KODI KUMALAWI ANTHU MUNAKHALA BWANJI KAYA AMAPANGA KAYA SAMAPANGA ZAKE ZIMENEZO ZONSE AKUDZIWA NDI MULUNGU MWAPINDULA CHANI A THOKO MWALAKWITSANSO POYANKHA AMALAWI KADUKA NDI NAMBALA ONE PRESIDENT MUNTHALIKA ANAKATI ADZIYANKHA CHILICHINSE ANTHU AKUMPANGA ACCUSE IIIIIIIIIIII PANA ASAKUYENDETSANSO BOMA AMALAWI KAWO NDI KADUKA KADUKA KADUKA KOMA AKUTI NDI ANTHU OPEMPHERA
naye kuyima pachulu, nde too late
is Miracle the first woman to be pregnant in Malawi?…how many mothers do we have in Malawi?…..i
Tiuzeni zoona.
Iwill not kip on smiling to false prophets +prophetnesses who r deceiving my pple thru God’s nem so take care!!!!
Just like her late mother Miracle amangochindidwa ndi aliyense, Thoko’s new fiancee shud be worried, this man married a former MBC lady whose husband died after a long illness for money, she died too lero angochinda anyhow, too bad! Mtengano uwooooooh!
Waiting waiting
Okay
Oyii meu boss
mwampekela kale miracle nkhani?hmmm nsambi mwana.
Ngakhale wakuba amapephelanso!
ZopandA vepi who gives a fuck?
To pregnant her or not, that wil never stop me going to toilet. Yo heart is the yo witness. So what do u want us to say.
Miracle sera que nao tinha nada de faser alem de namorar com um senhor dessa idade? Se essa historia é verdade no mundo não tem boa pessoa vces malawianos não pode aceitar que bestera aconteca no seu mundo na minha parte to muito triste. Com miracle e seu parceiro thoko isso é grande vergonha… malawi!!!!!
Isso é verdade. Miracle é muito criança para o senhor grande como esse. O mundo esta acabar mesmo.
Nao entendo falo ingles sou Malawians
wo findet man in der Hölle dieser Sprache?
Mwanyazits.a onse oyimba nyimbo za uzimu. Inde kuweruza kwake namalenga,komabe tisasanduke zikwangwani zongolozera ku moyo osatha koma ife osakafikako.tiyeni tilape ,tisinthe makhalidwe athu oipa.mulungu tikhulurukileni ife anthu adziko lapansi sitidziwa chomwe tikuchita tikupempha izi m’dzina la yesu khritu amen.
chenjelani nawo atumiki onyenga ngati awa akuimba zaufumu wakumwamba km mphamvu yake anaikana kd tingati wanyamula mbendela yanji amweneyo
Of Course Ndmakonda Kmvera Nyimbo Zake Kma Lero Ndasya Cfkwa Mwanayo Ngwachigololo Kwmbri.Zoona Ungmanene Zmenez Kuno K Mpoto?Ndkazamvanso Nymbo Zako Ndzaphwanya Wireless Imeneyo.Foolish!!!
NGATI AKUYERA MASO MULASENI BASI
Zausiru basi.
He is rud, dont play with God
En den watz new der,,itz she 1st lady 2b pregnated ?Lols
Ukakhala ufitiwo zichitani koma osanamizira kuti ndinu opemhera.
Ndiye aziulule lelo it was 2014 pa mene timava khani iyi,kulibe mimba ya zaka zi wili
Ndipo vuta kukhulu pilila pa khani iyi chifukwa ndi kale tinava kuti thoko katimba apeleka mimba kwa mwana wa grace
Its only God hu knows de truth.
Malawi24 Can we have serious news please! Why promoting immortality and really who cares if chinga daughter is pregnant and who is responsible for the pregnacy! Malawi has more pressing problems than to hear about who did who.
word sound power!
Osamapweketatsatu zaunsiru
Eish
katimba ndi hule yayimuna
KKKKKK
God help Malawi mmmh inu muziyamba kumvesera Kaye be4 saying anything mwina ndizaboza muzapusa nazotu …….
Shame
KUYENDA NDI YESU NKOKOMA ZEDI!!!!…
Koma Miracle yo ali ndi mwanadi kapena mimbayo??
Ilike this
Amene sanachimwepo awagende miyala awiliwa.
Angoni mwandigwila pamtima VCT first kkkkkkkkkkk zonsezi kumapeto kwa dziko just hv faith on Loard only!!!!
Nchani kodi amalawii….?
Kkkkkkkkkkkk nkhani zake uhule okhaokha basi panyasaland sipazathekaso
ndinakutuluka kale
Ndiye ife chikutikhuza ndini za mimba zanuzo usilu basi
Zausiru who knows alikuti mwanayo
Miracles know who impregnated her. Zibwezi zake amaziziwa yekha. Yemwe anamugwira ntchito yotamandikayo akumudziwa yekha. Bwanji osamufunsa kuti aulure yekha?
Chimidzi iwe, wasowa zolemba eti, uzafa imfa yowawa
anadya uyu asakane
Kenaka uli ndakukhululukirani ineee! Osamangobunyula bwa?
Nde ngati pali vuto..?ngati mkaz ndiokongola gwirani naye ntchito basi asaaaa
No wonder thats why he is called Anaphiri.
Vuto lokhalitsa ndi azimayi
arsenal the gunners 3, chelsea 0 zingayambe kuyiwalika.
If you make buziness with stupid people,bizness becomes stupid.
fuck malawi 24,,,,you are busy spreading lies,,,,,foools on facebook!!!,,,,,
Ndakhulupirira wa satanic uyu
So disgusting story
Zautsiru
am surplised these are Malawians I know if some 1 got talent they are fond of jealousy they do their best to accuse somo one falsely. I like you Thoko am waiting for your next album keep on
Mwana uja alindizimatako zabho big up Thoko ponyowesa maliseche amwanayo Umakwana but wapanga zopoila ukabashuta porno ukanagulisatu heve
Mmmmmm koma abale munali oyimba okhulupilikatu yooooooo.
Nde kupereka mimba in past ndikuonetsa chibwenxi chake zagwrixana pati? Katimba aazitolere
Koma Thoko Uhule Uzasiya Liti Koma Kamwana Iwe Ungosiyakuyimba Zauzimu Ndiwe Galu Mbuzi Nkhumba Ukufuna Uzingowa Matenda Kodi Nanga Ndichani Usawone Siketi Pa Chigwe Mpakana Udikilire Kuti Uwone Yemwe Avale Kkkk Koma Iwe
k
zomwe tikudziwa ndizoti akazi pano amangofuna ndalama uyu mukuti feeace kaya hule saga khumudwe oro thoko atapezeka pa sex.musamatinyozetsere GOD wathu ine ndinasiya kalekale kukhulupilila thoko.thawi zonse mbili zoipa sham on u T
zomwe tikudziwa ndizoti akazi pano amangofuna ndalama uyu mukuti feeace kaya hule saga khumudwe oro thoko atapezeka pa sex.musamatinyozetsere GOD wathu ine ndinasiya kalekale kukhulupilila thoko.thawi zonse mbili zoipa sham on u T
This Miracle must be very stupid,,,what a shame!!
mmm! Thoko #unadyaiwe! ngati ukukana nde anadyd ndani #zimenezizi?
Thoko mmmmmmmmmmm ?
amalawi 24 ndakukhululukiran ine ndakukhululukiran ine #thoko_katimba
20 minitues ago
AAA mesa miracleyo ankakana kut alibe mimba.nde APA bwanj? Koma guyz
ANAGWIRA CHIKOLOPA? Kodi!!
Kod pamenepa amabungwe muti chani?Loading…..
Kod pamenepa amabungwe muti chani?Loading…..
Kungomu onogera mwana wa malemuyo tsogolo bansi
Wakula apa ndi uhule,kweke ameneyo kunatha and chomwe angachite THOKO angoyamba kutolera ana omwe anafesa dzikoli,coz anawo akewo alipo ambiri.
Gospel anaphi wadya basi
Gospel anaphi wadya basi
Ummmmmh guys,,,tisamuipitsire mbili nzathu…
Kodi mwana wa grace sangachindidwe?mufuna munene chani iye pokozerapo sipamamuyabwa,aliyense amafuna kuchinda kapena kuchindidwa asiyeni athane basi
pakuti mulungu anakonda dziko lapansi kotero anapeleka mwana wake wokondedwa kuti yense wokhulupilira iye asatayike koma akhale nawo moyo wosatha….
Mmm wamufunsiratu panopa kma mwanayo siwake adzangolera.watsekereza ma hope onse pamenepo kkkkkk.
Z sh prgnant?
She was &she has a baby now.
Ndimene zimankhalila
Ndimene zimankhalila
http://www.zambiantunes.com/2016/08/download-mack-go-ft-dj-pasta-bantu-bachimwa/
Izi ndiye zopusa tsopano
Uhule basi.
Not long ago people were busy talking about Miracle money,today Miracle pregnancy and tomorrow…? Who knows mwina miracle president kkkkkkk
zovuta izi mmmmh naye Thoko osangokhala phee bwanji chilungamo ndimumtima mwake basi nkhani yakalekale kuikambaso pano mwina mwapeza kumene kapena katsunako aThoko kkkkkkk
Vct first
Yoneco
People why making afuss about Miracles preginancy? She is ahuman being not an angel. How many girlies are getting preginant out there ,every one is asinner thats why Jesus Christ came to redeem us.
NO SMOKE WITHOUT FIRE! WHY ONLY YOUR NAME WHY NOT OTHERS! YOU HYPOCRIT YOI MESSED THIS YOUNG CREATURE! YOI CAN DENY, BUY YOU CANT BEFORE OUR LORD.
Miracle pregnant
moti sunalawe
uchinda siwalesa bola machindidwe.kkkkk tokoma situkhala kutha nawonela ukala hahaha.ndipo mau amati pali pose pali m’ng’aru muthirepo madzi ndicholinga chakut maonekedwe achinthu awoneke mwachilengedwe kkkkkkkk pali m’ng’alu kkkkkkk kaphazi ka isa
KHOLINGO .nyama yapakhosi kkkkkkk
Kkkkkk.wamkachisi amadya mkachisi
Palibe Wolungama Pansi Pano Amene Achita Zabwino Osachimwa (Mlaliki 7:20).
Thoko Katimba sacrificed his wife for money. .. he wants to sacrifice that innocent lady again? ? what’s his problem. so Bushiri told him to do that. .. dude God knows
Kkkkkkkkkk koma kumalawiko!!!!!!
xake izo
Anthuwotu amayimba nyimbo zamulungu for money osati kuti iwo ndiwopembeza ayi making money mdzina la yesu mtima yawo nyansi zokhazokha
thoko katimba why u do fuckin shit
Ife sitikufuna kudziwa ataaaaa! munali awili,zitikhudza bwa?
My name is Kyzah Mulumba and this a testimony of how i became HIV NEGATIVE, i have been suffering from HIV for the past six years, i have spend a lot of money finding cure for HIV/AIDS until i found this true man who cured me completely with his powerful herbal medicine, i have tried different means to get this virus out of my body, all the possible ways i tried did not work out for me, i came across doctor olumo through some amazing testimonies concerning how Dr Olumo has cured different people from various kind of sickness like HERPES,HIV/AIDS, CANCER, with the help of his powerful Herbal Medicine, so i was encourage and i contacted Dr Olumo i told him about my Sickness, He told me not to worry that he was going to prepare some Herbal Medicine for me, after some time in communication with Dr Olumo he finally prepared for me the herbal medicine which he sent to me through courier service and he also gave me prescriptions on how to use it, after taking the Herbal medicine for some days, i went for test to confirm and the result was totally negative ,i went for test again in a different hospital still the same negative , Today i am fit and healthy to live life again, I am so happy for the good work of Dr Olumo in my life, if you are having a simillar problem kindly email HIM on { [email protected]} OR CONTACT HIM WITH HIS NUMBER OR CHAT WITH HIM ON (WHATSAPP) (+2348138956767) together we can live an HIV free life.
Katimbayo Sanalaule Anthu Amapeleka Mimba Kumene Ndipo Iyeyo Sanagwiririre Koma Anagwirizana
Even Mr Katimba refuse the resposible of this pregnant, but the trueth will forcing to comfirm 1 day.
Why are you so serious about the rumours.
Mutipangitsa kukudabwanitu.
Your headline should have revealed whether Thoko denies or accept the responsibility rather than beating about the bush.!That is what captures the readers attention!
Word
Zonse adziwa ndi ambuye ife tilibe chonena!
Bodza Thoko mukumunamizira mimba ya saulosi chilima iyi
Labour loading kkk
Thoko Katimba is gay he can’t do that!
Komanso chifukwa chani pamaliro a Grace mkulu uja polengeza amati Thoko Katimba wandiwuza kuti ndimunyengelera Miracle kuti nyimbo zamayi ake azitulunse?nkhani iyi ndiyowona forsake Thoko Katimba.
K.k.k.k ndzaulula @ its peak!!!!!!!
I fe Monga achipani cholsmula cha DPP tati tisuse zomwe Amalawi 24 zomwe alemba zoti Thocko katimba alakulapo zamimba ya mwana wa malemu grace chinga izi zikuchitika ndicholinga kususana ndi ulamuliro wabwino omwe uli mdziko muno wa Dr professor Peter muthalika zonsezi akoza ndi otsutsa boma #_Taba_23 minutes ago
Sizkukhdzana ndi ndale
ya different status
kkkkkkkkkkkkkkkk…..achipani cholamula mwalumpha malire
kkkkkkkkkkkkkkk khani zatopetsa
Kod mukudabwa chani?Tonse tudziwa kuti Thokozani yo ngwasataniki nde mumati angatchuke ndi mbiri zabwino?
Aliyese ali ndi chofowoka chake usaweluze mnzako pot kuweluza kul kwake kwa Mulungu…. Bolaso Thokoyu kma winawe unampasa mimba mwana wako tazivele kay chison iweyo usanayambe ku comment zako zonyozazo.
Thoko Katimba takes his loved one t the stage. One of Malawi’s gospel musicians Thoko Katimba has spoken out onwide spread reports that he once impregnated Miracle Chinga, daughter to the late gospel songbird Grace. Speaking on Sunday during a live show in front of thousands at Squirrels Park in Mzuzu, Katimba surprised people when he called his fiancée to the stage to deny the pregnancy accusations. “I want to break all bad rumours that were surrounding you people that I impregnated Miracle,” said Katimba. When his fiancée joined him on stage he said: “This is my fiancée and if all goes well we are going to wed next year, I was regarding Grace as my sister which means Miracle is my daughter too, how can I do such silly thing,” said Katimba while holding his fiancée. In the past, there were spreading reports that Miracle was pregnant for Katimba. The Anaphiri hit maker lost his wife Margaret Katimba in 2013.
Noughing can’t hide under the sky down,1 day the trueth wll upon to the earth its better to comfirm.
Iwe nde munthu iwe….
INE NINADYA CHISIMA CHOZIZIRA M’MAWA NDE M’MIMBA MUKUNDIWAWA ZEDI.KAYA NDITANI KT MULEKE?MPHEPO CHITULUTSILENI KOMA SIMUKUZIZILA
Kkkkkk umwe mkaka Wa amasi
Kkkkkkk koma #SnetaKwenda bankha wamunthu…
Tell me pipo is can u confirm whether the girl is pregnant?
Thank you for saving me a click
inu kod miracle yo ali ndimwana? kapena anataya
She z nt pregnant!!!I attended the show!!!
Miracle anabeleka mwana when she was in std 8
So whea z the baby #Lwitiko? nanexo namva iz
Zakuthupi izi dnt blame thoko….ndani sana chimwepo apa?
Kma zoona zmenez?
vuto la Malawi ndilimenelo… mumafuna zonse zabwino zikhale zanu… nzanu anadya mwabwino koma mumafuna inu mutadyapo basi
A_Malawi_Simuzatheka_Sithani Ma_Khalidwe…
Abale Tiyeni timuthandize thoko akufunikira derivarance please amene muli naye pafupi Organaise it please!
Ali ndi charger ya Nokia yamutu waukulu andibwelekeko
oyimba osalandila yesu thoko mkale anayamba kumveka mbiri zoipa si wa yesu asakane
Ena atawelenga yose nkhaniyi atha kubweraso nkudza deleta ma comment awo coz ali off code.
Ndizaulura
Kkkkkkk
mafco v noma
SEARCHING
Kumafalitsa mau amulungu ngat zenizen mxm Uhule thoo!chimdya makanda ngat iwe nkazi wako anafa ndi Eidz kalekale apa waphaso mwanayu,Naweso Milacle ndihuletu iwe mwanamwana ngati iwe kum’meza Thokko katimba?Umafela chani pamenepaja? Fotseki
koma ngati ndi zoona izi. THOKO KATIMBA ndiwe mfiti. wamuononga mwana wabwino bwino uja. kodi simmesa chinzimai anakwatira thoko chija chinamwalira ndi matenda aboma wa.ndiyetu waononga basi miracle zako zada.
So what
MMMMMMMMMMMMM AKUNAMA MULUNGU SI IYEU IM NGATI MLI NDI UPULUMS IFE TICHILISEN INU MKIMAITHA INE NILI KU CEP TWN KM AMAKUKINDAN MWTHOZA
Bullets panoma singadutse come pa 8 mapoints akupita ku lali lubani
Wow
mbulu 2 noma 1
Fusan Miracle yo ndie akuuzan zoona
Only your God knows the truth! Whether you successfully convince the public or not ! You shall face The Arm of justice !
ankadwelera ameneyu apa
You send your girlfriend a text; i love you, she replies love you too,you send i miss you, she replies love you more.But once you send her mk1000 she can’t send back anything……..girlfriends are always after monie.
Koma mwana iweeeeeee ? ? mmmmm silly u kkkkk
kkkkkk and when u fuck them they even kulilira ngati zenezeni angofuna to plse u to robe more
Ur saying true brother
kkkkkkk koma yah,,,,.
Koma Cisale eish
True And When U Say To Her You Are My Sweet Banana Amamva kukoma koma ukati Ndiwe Nthochi Yangayokoma Amakwiya
That’s true
Kkkkkkkkk
Nde muti Anaphi ogwira chikolopa anamuchta impregnate Miracle imene ili miracle pregnancy et??
tizingokhalira nkhan za ma mistake a anthu zomwezo? ineso mwana uja ndnagwamo bwanj simunandlembe?
Gwalad ndi deal reality talk amaitha otsabitsala ku Gospel mayaz
kod miracle ali ndimwana?
A Thocco thukuta kamukamu pamwanapo??ansaa
Always i dont trust Katimba bcoz he has bad record and he’s rude fucken pussy
He also wanted to take my Girl koma my girl told me namuuziratu man munthu uja ndi hule
mayi akakhala hule,, ana obwadwawo nawo amakhala mahule,,, iwe ukuchita kudabwaaaa
thoko katimba ana osewa ali nawowa, azikazi wasiya angati ndipo. ngati mukumbuka bwino pa nthawi ya maliro a grace chinga amalankhula ngati wakubanja zinatheka bwanji anthu akwa chinga kumulora kulankhula ngati wakubanja?, asakane lero mwanayo anamupasa mimba ali ndi zaka 16 ndipo silero dats y kwa chinga anamuvomela ngati mpongozi wawo. akatele ndekuti afuna apelekeso mimba ina. Nde tiuzetu kuti anampasa mimba miracle yo ndindani?
Nthawi katimba anamsankha alankhulira oimba gospel nt aku banja, akubanja amene amalankhulira anali uncle ake a Grace
Mukadxapexa ntsuko utamwanyika panseu dxiwani kt nkhatanso ili capomwepo!sizozembaxo apa!!
Izo izo
KKKKKKK kuthira mwayesu
zodiak batteries
Odi uko….
kkkkkkkk
Kkkkkkk mwina ndiya zimu woyela
mwinadi
Oimba za uzimu lero ndinjoka zoopsa
Mukakambirana mundilembere weekly report….xxxx
chikutikhuza ife ndichani? musazapositenso ngati izi, ndi mimba zomwe, nde umalawiwo umenewo
Fuck u Thocco a madala like u impregnate a little girl? Shame on u
interesting
iwe utan apa?
kkkk iwe wapezekapo bwa
ndimakusata iweyo
mmm ndakaika
kkkk criuse
Ndakukhulukirani ine anzanga……. By anaphi
KOD MA CONDOM KULIBE HAAA? NDKUFUNSA INU THOKO & MIRACLE. Nde Tiziti Zochitika Pansi Pa Dambo Zaululika Etii!
Ndiye muziti agaru oimba zauzimuwa ndi ma born again ??? Panyapanu
Kkkkkkkkkkkk
Mimba anampasa ndani
Munthu ku thupi
eeee ine pheee kuwelenga nawo ma comment
Kkkkkkkkkkk komano zawonjeza abale
Thocco anachita zofoira, nkhani zimenezo akanangokhala chete osayankhulapo kanthu. A Malawi amakomedwa ndi nkhani zamabodza. Mwina inangokhala njira yofuna kuwaonetsera anthu ka fiancee kakeko.
kod miracle ali ndimwana? nanga mesa nkhaniyi ndiyakale kale?
Alibe mwana
Mayi ake anamuchosetsa mimba
Apo ndiye ndamva
mh mimba yot inatchuka ndikumuchosesa? mh kma abale
Hahahahahahahahahah
Oyimba Akumalawi Mahule,kuli Ku South Africa Ban 3years Osapange Zoyimba
aThoko nanga mimbayi ndiya aGondwe? ndiye muyimbenso ina pamenepa nyimbo.kumasamara pakamwapanu pangadzauluke mbereswa tsikulina learn to “Walk the talk”
Zikhoza kutheka inu kuvela nyimbo zake nkusinthika nkuyamba kutumikila ambuye ndintima wanu onse, pamene oyimbayo wakumoto, mwaicho, sikwabwino kukhulupilila munthu, tiyeni tizingovela uthengawo basi, zakuchimwa kwaiye akukudziwa ndi chauta mwini zonse
Zinyengananani iyaaa
he was just regarding Grace as his sister according to this statement it means he can do everything towards miracle
Eish U Pple
watichiyani thokoyo?
Koma chifukwa chani suvala malaya a size yako malaya lende usovatu
Thoko katimba mkazi wake amene amamwalira ndi Aids oyimbayu waphulitsa Miracle shaaaaaah.Malawi waola
Sikwabwino kunena status ya munthu mwini wake asana telo nkulakwa komaso kuphwanya malamulo, kaya ali ndimatenda kaya alibe, musungileni ulemu wake, monga inuso mukusungila status yanu,,, palibe akudziwani kt mthupi mwanu muli motani,
Kwaiweyo sikwabwino what am sayn is true hate this or like this thoko katimba anatenga HIV kuchokera kwa amai anatisiya aja.
NANGA IWE UNATENGA UNATENGA KWA NDANI?????
Am nt involved in that situation and i will not unatenga matendawo ndiweyo ndichifukwa chake zakupweteka nanga simulupo ambiri amene mulinako kachirombo
Zoti iwe ndi hule ndinaziziwa osayambe kuyimba
Pitiliza uhule wakoyo uzaziona mapeto ake
GUYS ZINDIKILANI KUTI MUNTHU KUKHALA OYIMBA SIKUTI NDE KUTI ALIKUMWAMBA AYI, NAYE NDI MUNTHU NGATI IFE TOMWE ,, IFE TIZINGOTOLAPO UTHENGA WATUMIDWA NDI CHAUTAWO BASI, PLZ STOP JUDGE PEOPLE, ALIYESE ALINDIZOFOOKA ZAKE,
Pedophiles needs jail..Anakwatira Amayi aakulu pano akulimbana ndi ka mwana…mawu ngati nkazi…Guyz munthu osaphetira atibera,,
On top of that he z HIV posotive paja akazi awo anatisiya atapezeka ndikachirombo koyambitsa matenda a AIDS
ndikuuzani maso amanyenga nchere umaoneka ngati Sugar…lawani kaye musanathire mu kapu
koma yaah
Sies
Ndiye watiphera kamwana kaja? koma!
Kkkkkkkkl koma
anthu inu, kodi munthu akakhala ogawa mau amulungu sachinda, walakwisa pati poti ndimwana wa malemu grace chinga, alibe center thokoyo mvunguti alibe? zilekeni tirigu ndinansongole zikulire limodzi zizaoneka nthawi yokolola, akwatana kale mimba ndiyo mutani mufuna muweruze ndinu Mulungu? nanuso kapezeni kanu katsuna mukaonese mimvunguti mwangoiunjika mmapant yo, mzanu akadya walakwisa, Mmalawi sazathekaaa, mithulo, nsanje, kuba, matama mulekeni mzanu akwatire
Shaa! Koma achikulire inu. Ine mau kundisowatu baxi
Kkkkkkkkkkkkkkk
Kkkkk thumb up boss….you just nailed it.
Mn kumene ndikuyankhula?
nonsense
man #ken bwanji, madzi akataika saoleka, pochindanapo anthuwo zosatira amaziziwa, latalata chosatira ndimimba basi, ena akuti amangidwe wachinda kamwana chikondi chilibe size, nsapato yokha ndiyomwe ilindi size, kumunyoza munthu poti wapereka mimba nkulakwisa,
mr njiwa , opasidwa mimbayo atakhala mwana wanu kapena wachibale wanu mungatani, thokoyo wakwatamo kale mimba waipereka?
kkkkkkkkkkk
hahahahahahhahahah ine mmimba kundiwawa ndikuseka
nde atiuzetu kuti mimbayo anapeleka anali yani komaso kwa chinga anamulora bwanji kulankhula ngati wa chibale pa nthawi ya maliro a grace?, pano aziti anali nzake chabe chosecho anali mpongozi
mimbayo nja thoko katimba, amakwatananaye mwanayo, ngati mukufuna kuva zambiri tiyeni ku inbox ,
EEEEE koma kathoko kamakwata?
Kod thoko mesa ali ndi mkaz kod ndiye akhala amkazi awiri
Inu ndi amene mumadziwa kuyankhula bambo
Hahahahahahahah takunvan baba
hahahaaaaa !! koma #Alfred ndilibe nawe chilomwe ndithu kwandiuma mkumusiku kukanakhala kukamwa nkananyambitila ……kkkkkk
Kkkkki nde mwat mivi kapena mivungut
Kkkkki nde mwat mivi kapena mivungut
mvunguti.com
#mimvunguti ikulu ikulu yangounjikidwa mma pant izigwira ntchito yake, Thoko sanadeweze koma kutibula basi, kkkkk
6-5=? pasavute
Apa Nde uzingoyimba za kumowa timaziwa kale Mbili zako!sitizigulaso nyimbo zaka za chikunjazo. Ndiwulula uja Ndameneyu!Muyaluka ndizanuyo.
Kyungu paja wakwatiranso!
ÑÂJÆ0P ŰŇCĞŰŁÌ2WÅ
Kodi alipo yemwe sanachimwepo? Atole mwala amugende thoko?kkkkkkkkk ifenso tinanva ..
Kkkkkk pass me the weed
Tiziwona Mulungu mwa inu tikamaku onani.if you r realy born again chonde njira yanuyo tilondole reni.
Go For DNA Before u let us know ,ti commenta zaboza
Ndie vuto ndichani?ndioyamba kutenga mimba iyeo?kapena munamvapo kut anaphiwo ngokugwamo nde mukudabwa?
Man U Zampira Mlibile2 Guez Mkuwona Bwaa?
Ife tingokuyimbirani nyimbo ya thoko kuti ; undilonderanji Santana, anthuni bwanji kumayipisa mbiri ya anzanu.
Kkkkk adamu walakwanji?hahahaha
Thats Rediculous!!!!!!
Oh last days the bible say okhulupilila sakujejema
Arsenal 3-2 Chelsea,,,. zamimbazo zisandikhuze, nzofuna iziii
komarelo kwatentha heavy
ife nde zutikhuza bwa???
Kuulura zapansi pa thambo!
Mwangodzolowera kuipitsa mbiri za anzanu akamachita bwino.
….(singing)…anthuwa ndiafiti opemphera…
Ife bola timvako uthenga wabwino omwe umapezeka mnyimbo zako koma khalidwe lako azaliweluze ndimulungu
Perfect
MULUNGU adzakantha ntchimo ndi munthu amene walilandila ntchimolo
MULUNGU adzakantha ntchimo ndi munthu amene walilandila ntchimolo
Koma Arsenal ndadananayo mpaka kukuzura Chelsea 5~~~~0
wayitha
Ndakwiya nayo Arsenal man::::zikomo boss
it is not easy to have our names written in the book of liife…repent or die
ndinayamba kuzimva kalekale nde mukufuna tathauza mimbayo yatha zaka 2 osamapanga post zopusa
Page zambiri zimakhala zaboza mulembapo queen & kamuzu centre akuzigulitsa zinapita kt mukutanthauza kt ku ma show analiko amavina ali odwala ? Ziwani kuipitsira mbiri ndimulandu !!
nyasa bullets,,,
Never thought
What is ur buznes?
Mwakalipatu chemwa
Ndakwiya nanu kwambili
Hahahaha! mesa tapeza nkamwini wamawu anthetemyaa! koma fb ayiayiayi!
Watha basi mwana wopusa
lie!
lkkkkkkkkkkkkkkk
Ndewasekatu sasha
F
Ambuye wandilotesa iwe kut ukhale nkhiti yanga muzakayankha nokha
Wakayakhayekha kikk
Owooh
Mufuna mumuipitsire mbiri eti????
Kkkk
Hahahahaha kusekafye! kuseka bakamba.
Kuseka ichinechinefye.
Seaching….
Kodi Eti? Ok…Zikwangwani.
Hahahahaha kusekafye! kuseka bakamba.
Thoko i knw hm frm his grass root, ndizoonadi zimenezi, usatana sanauyambe lero
kkkkk mpaka panenepo Tonie?
Eeeh kunena tchutchutchu madala
Amwene ingokhalani phee kuti mwina anthu azingokaikira za Uchitsiru wanu…
Mhmm a Juwawo pa social ntwrk munayamba kukhalapo liti? This is about making fun, entertaining, educative nde inu mukudza ndiotani? Thokoyo mbale wanu bwanji? Ha ha ha ha ha ha
Kodi ukuyankhulabe axe??
Hahahahahaha
juwawo miracle ndi baby yako kodi?
May be, bt it showz kuti anamukana
Koma zikunena manwa! ndizowona usi sufuka popanda moto kuli oyimba ambiri a Gospel Azibambo, koma samvekamveka ndi mbiri zoipa ngati mkuluyi! chikayiko Enafe timakhala nacho! why always mr Katimba okhaokha!mmmmmm!!! Asithe Awonjeza!!.
Hahahahahahahahahahahah
Mwayambap Kma Page Iyi Ash
Thocco amene ndimamudziwa ine, sangapange zimenezo.
uzakhumudwa
Wa ambuye andilotesa umayenda m’mbari iwe
nawo oyimba ndi anthu ngati ifeso
nawo oyimba ndi anthu ngati ifeso
Koma nkhaniyi ndizoona
Hahahahaha! I dont care what people talk about Thocco, he will remain my favorite gospel artist.
Amene mukuti nkhaniyi ndiyoona, mulinawo umboni ????
iweyo ndie lawyer wa Thoko??
koma adha…..
????????
not true
Following
Kkkkkkkk koma Nyasaland!
mdzaulula part 2
Hahahaha kusaseka mkulimba mtima
tamva nawo
but why do this gosple singers look like they are saints
Kkkkk MDZAWULULA???????
comment loading. ………
kkkkkkk Malawi at its peak!!
Gospel pa malawi……kkkkkk