Thoko Katimba speaks out on Miracle Chinga’s ‘pregnancy’


Thoko Katimba
Thoko Katimba
Thoko Katimba takes his loved one t the stage.

One of Malawi’s gospel musicians Thoko Katimba has spoken out onwide spread reports  that he once impregnated Miracle Chinga, daughter to the late gospel songbird Grace.

Speaking on Sunday during a live show in front of thousands at Squirrels Park in Mzuzu, Katimba surprised people when he called his fiancée to the stage to deny the pregnancy accusations.

“I want to break all bad rumours that were surrounding you people that I impregnated Miracle,” said Katimba.

When his fiancée joined him on stage he said: “This is my fiancée and if all goes well we are going to wed next year, I was regarding Grace as my sister which means Miracle is my daughter too, how can I do such silly thing,” said Katimba while holding his fiancée.

In the past, there were spreading reports that Miracle was pregnant for Katimba.

The Anaphiri hit maker lost his wife Margaret Katimba in 2013.

402 thoughts on “Thoko Katimba speaks out on Miracle Chinga’s ‘pregnancy’

 1. ngat sizoona kt thocco anapeleka mimba, Mulungu akhulukilr pakamwa ponse pamene pakamba nyansi komanso ena amene anapeza mwayi woonetsa nyansi za mkat mwawo pakupeleka ma comment opusa namazitenga ngat anzuru,,,,, mwalankhula dziko lakumvan ndipo takuziwan ngat mumafuna kuziwika ku mtundu wa a Malawi,,, ngat ili ngila yowanamizila anthu thocco pofuna kufufutitsa mbiri yako Ambiye akukhululukile coz this is not the best way of handling it, Mulungu sakhululukila munthu amene safuna kuvomeleza tchimo lake, it’s better anthu akunene koma Ambuye akulandile….. Miracle, rhe truth is on your heart of who did it, usatukwanitse maina ochuluka auze anthu choonadi ndikubwela pamaso pa Mulungu mogonja, He forgives so dont run from Him but rather run to Him.

 2. MIRACLE CHINGA MOFFAT WAS NEVER PREGNANT… THATS THE HIGHLIGHT… SHE WAS NOT AT ANY POINT OF HER LIFE, PREGNANT..GET A LIFE AND MOVE ON WITH POSITIVE THINKING.

  1. mukulakwitsa mukatero….. mul nd umbon kut miracle ali nd mwana? samalan nd pakamwa panu, ganizan mul inu wina akunamiziren, kapena munamugwra akupanga chigololo? mau a Mulungu amat usanenere umbon onama,,,,, dzko laipa ili, khoza moyo wako usayang’ane zatchmo lamzako, ngat akuchmwa apempherere osat kunyoza

 3. Athoko mwanyengaso mwana wamasiyeyu mpakana kumpasa mimbi?kumangochi kujaso ndimene muziwira zosokoneza banja lamai aja osangokwatira bwanji achimwene?uzimu wanu ukupita patsogolo kapena pambuyo?

 4. Amalawi kodi vuto lanu mchiyani!!kodi kutenga mimba anayamba ndi Miracle?ngati ndi choncho iwe Frank Banda unabadwa bwanji.kodi ndani sadziwa kuti amalawians24 ngamisala?walakwanji mwana?bala wako mwana udzimuloza chala numati mimba mimba osati miracle chonde STOP!!!

 5. Una nchindadi asakudziwandani zaiwe ndi mwanayu kodi,kumangoti ndimapemphela ufiti nkumapangaso chokani shupitiiiiii

 6. Masiku ano bola kuziwa chimene uli pakati pathu ndi Mulungu basi.Anthu padziko pano akunamizira mdzina la Mulungu pamene akuchita zotsutsana ndi zimene mwini wake namalenga akufuna. Repent!!!!!!!!!

 7. Komanso ngati Katimbayo ananena poyera kuti mimbayo ndiyake ndiye kuti alibe nzeru, chifukwa munthu wa nzelu zake sangaime pagulu nkumafuula kuti wakuti uja ndamupatsa mimba ndine, olo mkazi umukonde bwanji sungalengeze, angofuna kumuvula kenako amusiye

 8. Zaboza thoko anamasura tundu Wa amalawi ku robbiz park kuti sanayambepo wapanga chibwezi ndi miracle ndipo sazapanga naye chibwezi coz miracle akamaona thoko Ali ngati Ancle ake not what u think amalawi munakhara bwanji tisaipise mbiri or dzina LA mwanayi musiyeni agwire tchito yofalisa uthenga Wa ambuye chomwe mungaziwe maitanidwe amakhara osiyana ndiye mimba ingakhare 2 yrs mmmmmmmm zisakuwaweni siyeni mwana afalise za ambuye uyu

 9. This just a last kick of a dying horse . If you are a true Christian why should you sleep with someone outside marriage . He is not better than Miracle Chinga they both committed fornication so he must stop painting a bad image to the girl.
  Leave the girl to alone

 10. Pempho Lange ndiloti Miracle Chinga should come forward and tell us who was responsible for her pregnancy. …otherwise this doesn’t make sense…all in all aliyense amalakwisa….siwoyamba uyu

 11. So is this true that miracle is pregnant and the one who pregnated is Man of god thoko katimba ?I thought Mr katimba is a married man why????

 12. KODI KUMALAWI ANTHU MUNAKHALA BWANJI KAYA AMAPANGA KAYA SAMAPANGA ZAKE ZIMENEZO ZONSE AKUDZIWA NDI MULUNGU MWAPINDULA CHANI A THOKO MWALAKWITSANSO POYANKHA AMALAWI KADUKA NDI NAMBALA ONE PRESIDENT MUNTHALIKA ANAKATI ADZIYANKHA CHILICHINSE ANTHU AKUMPANGA ACCUSE IIIIIIIIIIII PANA ASAKUYENDETSANSO BOMA AMALAWI KAWO NDI KADUKA KADUKA KADUKA KOMA AKUTI NDI ANTHU OPEMPHERA

 13. Iwill not kip on smiling to false prophets +prophetnesses who r deceiving my pple thru God’s nem so take care!!!!

 14. Just like her late mother Miracle amangochindidwa ndi aliyense, Thoko’s new fiancee shud be worried, this man married a former MBC lady whose husband died after a long illness for money, she died too lero angochinda anyhow, too bad! Mtengano uwooooooh!

 15. Miracle sera que nao tinha nada de faser alem de namorar com um senhor dessa idade? Se essa historia é verdade no mundo não tem boa pessoa vces malawianos não pode aceitar que bestera aconteca no seu mundo na minha parte to muito triste. Com miracle e seu parceiro thoko isso é grande vergonha… malawi!!!!!

 16. Mwanyazits.a onse oyimba nyimbo za uzimu. Inde kuweruza kwake namalenga,komabe tisasanduke zikwangwani zongolozera ku moyo osatha koma ife osakafikako.tiyeni tilape ,tisinthe makhalidwe athu oipa.mulungu tikhulurukileni ife anthu adziko lapansi sitidziwa chomwe tikuchita tikupempha izi m’dzina la yesu khritu amen.

 17. chenjelani nawo atumiki onyenga ngati awa akuimba zaufumu wakumwamba km mphamvu yake anaikana kd tingati wanyamula mbendela yanji amweneyo

 18. Of Course Ndmakonda Kmvera Nyimbo Zake Kma Lero Ndasya Cfkwa Mwanayo Ngwachigololo Kwmbri.Zoona Ungmanene Zmenez Kuno K Mpoto?Ndkazamvanso Nymbo Zako Ndzaphwanya Wireless Imeneyo.Foolish!!!

 19. Malawi24 Can we have serious news please! Why promoting immortality and really who cares if chinga daughter is pregnant and who is responsible for the pregnacy! Malawi has more pressing problems than to hear about who did who.

 20. Miracles know who impregnated her. Zibwezi zake amaziziwa yekha. Yemwe anamugwira ntchito yotamandikayo akumudziwa yekha. Bwanji osamufunsa kuti aulure yekha?

 21. arsenal the gunners 3, chelsea 0 zingayambe kuyiwalika.

 22. am surplised these are Malawians I know if some 1 got talent they are fond of jealousy they do their best to accuse somo one falsely. I like you Thoko am waiting for your next album keep on

 23. Mwana uja alindizimatako zabho big up Thoko ponyowesa maliseche amwanayo Umakwana but wapanga zopoila ukabashuta porno ukanagulisatu heve

 24. Koma Thoko Uhule Uzasiya Liti Koma Kamwana Iwe Ungosiyakuyimba Zauzimu Ndiwe Galu Mbuzi Nkhumba Ukufuna Uzingowa Matenda Kodi Nanga Ndichani Usawone Siketi Pa Chigwe Mpakana Udikilire Kuti Uwone Yemwe Avale Kkkk Koma Iwe

 25. zomwe tikudziwa ndizoti akazi pano amangofuna ndalama uyu mukuti feeace kaya hule saga khumudwe oro thoko atapezeka pa sex.musamatinyozetsere GOD wathu ine ndinasiya kalekale kukhulupilila thoko.thawi zonse mbili zoipa sham on u T

 26. zomwe tikudziwa ndizoti akazi pano amangofuna ndalama uyu mukuti feeace kaya hule saga khumudwe oro thoko atapezeka pa sex.musamatinyozetsere GOD wathu ine ndinasiya kalekale kukhulupilila thoko.thawi zonse mbili zoipa sham on u T

 27. Wakula apa ndi uhule,kweke ameneyo kunatha and chomwe angachite THOKO angoyamba kutolera ana omwe anafesa dzikoli,coz anawo akewo alipo ambiri.

 28. Kodi mwana wa grace sangachindidwe?mufuna munene chani iye pokozerapo sipamamuyabwa,aliyense amafuna kuchinda kapena kuchindidwa asiyeni athane basi

 29. zovuta izi mmmmh naye Thoko osangokhala phee bwanji chilungamo ndimumtima mwake basi nkhani yakalekale kuikambaso pano mwina mwapeza kumene kapena katsunako aThoko kkkkkkk

 30. People why making afuss about Miracles preginancy? She is ahuman being not an angel. How many girlies are getting preginant out there ,every one is asinner thats why Jesus Christ came to redeem us.

 31. NO SMOKE WITHOUT FIRE! WHY ONLY YOUR NAME WHY NOT OTHERS! YOU HYPOCRIT YOI MESSED THIS YOUNG CREATURE! YOI CAN DENY, BUY YOU CANT BEFORE OUR LORD.

 32. uchinda siwalesa bola machindidwe.kkkkk tokoma situkhala kutha nawonela ukala hahaha.ndipo mau amati pali pose pali m’ng’aru muthirepo madzi ndicholinga chakut maonekedwe achinthu awoneke mwachilengedwe kkkkkkkk pali m’ng’alu kkkkkkk kaphazi ka isa

 33. Thoko Katimba sacrificed his wife for money. .. he wants to sacrifice that innocent lady again? ? what’s his problem. so Bushiri told him to do that. .. dude God knows

 34. Anthuwotu amayimba nyimbo zamulungu for money osati kuti iwo ndiwopembeza ayi making money mdzina la yesu mtima yawo nyansi zokhazokha

 35. My name is Kyzah Mulumba and this a testimony of how i became HIV NEGATIVE, i have been suffering from HIV for the past six years, i have spend a lot of money finding cure for HIV/AIDS until i found this true man who cured me completely with his powerful herbal medicine, i have tried different means to get this virus out of my body, all the possible ways i tried did not work out for me, i came across doctor olumo through some amazing testimonies concerning how Dr Olumo has cured different people from various kind of sickness like HERPES,HIV/AIDS, CANCER, with the help of his powerful Herbal Medicine, so i was encourage and i contacted Dr Olumo i told him about my Sickness, He told me not to worry that he was going to prepare some Herbal Medicine for me, after some time in communication with Dr Olumo he finally prepared for me the herbal medicine which he sent to me through courier service and he also gave me prescriptions on how to use it, after taking the Herbal medicine for some days, i went for test to confirm and the result was totally negative ,i went for test again in a different hospital still the same negative , Today i am fit and healthy to live life again, I am so happy for the good work of Dr Olumo in my life, if you are having a simillar problem kindly email HIM on { [email protected]} OR CONTACT HIM WITH HIS NUMBER OR CHAT WITH HIM ON (WHATSAPP) (+2348138956767) together we can live an HIV free life.

 36. Why are you so serious about the rumours.
  Mutipangitsa kukudabwanitu.

 37. Your headline should have revealed whether Thoko denies or accept the responsibility rather than beating about the bush.!That is what captures the readers attention!

 38. Komanso chifukwa chani pamaliro a Grace mkulu uja polengeza amati Thoko Katimba wandiwuza kuti ndimunyengelera Miracle kuti nyimbo zamayi ake azitulunse?nkhani iyi ndiyowona forsake Thoko Katimba.

 39. I fe Monga achipani cholsmula cha DPP tati tisuse zomwe Amalawi 24 zomwe alemba zoti Thocko katimba alakulapo zamimba ya mwana wa malemu grace chinga izi zikuchitika ndicholinga kususana ndi ulamuliro wabwino omwe uli mdziko muno wa Dr professor Peter muthalika zonsezi akoza ndi otsutsa boma #_Taba_23 minutes ago

 40. Aliyese ali ndi chofowoka chake usaweluze mnzako pot kuweluza kul kwake kwa Mulungu…. Bolaso Thokoyu kma winawe unampasa mimba mwana wako tazivele kay chison iweyo usanayambe ku comment zako zonyozazo.

 41. Thoko Katimba takes his loved one t the stage. One of Malawi’s gospel musicians Thoko Katimba has spoken out onwide spread reports that he once impregnated Miracle Chinga, daughter to the late gospel songbird Grace. Speaking on Sunday during a live show in front of thousands at Squirrels Park in Mzuzu, Katimba surprised people when he called his fiancée to the stage to deny the pregnancy accusations. “I want to break all bad rumours that were surrounding you people that I impregnated Miracle,” said Katimba. When his fiancée joined him on stage he said: “This is my fiancée and if all goes well we are going to wed next year, I was regarding Grace as my sister which means Miracle is my daughter too, how can I do such silly thing,” said Katimba while holding his fiancée. In the past, there were spreading reports that Miracle was pregnant for Katimba. The Anaphiri hit maker lost his wife Margaret Katimba in 2013.

  1. INE NINADYA CHISIMA CHOZIZIRA M’MAWA NDE M’MIMBA MUKUNDIWAWA ZEDI.KAYA NDITANI KT MULEKE?MPHEPO CHITULUTSILENI KOMA SIMUKUZIZILA

 42. Kumafalitsa mau amulungu ngat zenizen mxm Uhule thoo!chimdya makanda ngat iwe nkazi wako anafa ndi Eidz kalekale apa waphaso mwanayu,Naweso Milacle ndihuletu iwe mwanamwana ngati iwe kum’meza Thokko katimba?Umafela chani pamenepaja? Fotseki

 43. koma ngati ndi zoona izi. THOKO KATIMBA ndiwe mfiti. wamuononga mwana wabwino bwino uja. kodi simmesa chinzimai anakwatira thoko chija chinamwalira ndi matenda aboma wa.ndiyetu waononga basi miracle zako zada.

 44. Only your God knows the truth! Whether you successfully convince the public or not ! You shall face The Arm of justice !

 45. You send your girlfriend a text; i love you, she replies love you too,you send i miss you, she replies love you more.But once you send her mk1000 she can’t send back anything……..girlfriends are always after monie.

  1. True And When U Say To Her You Are My Sweet Banana Amamva kukoma koma ukati Ndiwe Nthochi Yangayokoma Amakwiya

 46. thoko katimba ana osewa ali nawowa, azikazi wasiya angati ndipo. ngati mukumbuka bwino pa nthawi ya maliro a grace chinga amalankhula ngati wakubanja zinatheka bwanji anthu akwa chinga kumulora kulankhula ngati wakubanja?, asakane lero mwanayo anamupasa mimba ali ndi zaka 16 ndipo silero dats y kwa chinga anamuvomela ngati mpongozi wawo. akatele ndekuti afuna apelekeso mimba ina. Nde tiuzetu kuti anampasa mimba miracle yo ndindani?

 47. Thocco anachita zofoira, nkhani zimenezo akanangokhala chete osayankhulapo kanthu. A Malawi amakomedwa ndi nkhani zamabodza. Mwina inangokhala njira yofuna kuwaonetsera anthu ka fiancee kakeko.

 48. aThoko nanga mimbayi ndiya aGondwe? ndiye muyimbenso ina pamenepa nyimbo.kumasamara pakamwapanu pangadzauluke mbereswa tsikulina learn to “Walk the talk”

 49. Zikhoza kutheka inu kuvela nyimbo zake nkusinthika nkuyamba kutumikila ambuye ndintima wanu onse, pamene oyimbayo wakumoto, mwaicho, sikwabwino kukhulupilila munthu, tiyeni tizingovela uthengawo basi, zakuchimwa kwaiye akukudziwa ndi chauta mwini zonse

  1. Sikwabwino kunena status ya munthu mwini wake asana telo nkulakwa komaso kuphwanya malamulo, kaya ali ndimatenda kaya alibe, musungileni ulemu wake, monga inuso mukusungila status yanu,,, palibe akudziwani kt mthupi mwanu muli motani,

 50. GUYS ZINDIKILANI KUTI MUNTHU KUKHALA OYIMBA SIKUTI NDE KUTI ALIKUMWAMBA AYI, NAYE NDI MUNTHU NGATI IFE TOMWE ,, IFE TIZINGOTOLAPO UTHENGA WATUMIDWA NDI CHAUTAWO BASI, PLZ STOP JUDGE PEOPLE, ALIYESE ALINDIZOFOOKA ZAKE,

 51. Pedophiles needs jail..Anakwatira Amayi aakulu pano akulimbana ndi ka mwana…mawu ngati nkazi…Guyz munthu osaphetira atibera,,

 52. anthu inu, kodi munthu akakhala ogawa mau amulungu sachinda, walakwisa pati poti ndimwana wa malemu grace chinga, alibe center thokoyo mvunguti alibe? zilekeni tirigu ndinansongole zikulire limodzi zizaoneka nthawi yokolola, akwatana kale mimba ndiyo mutani mufuna muweruze ndinu Mulungu? nanuso kapezeni kanu katsuna mukaonese mimvunguti mwangoiunjika mmapant yo, mzanu akadya walakwisa, Mmalawi sazathekaaa, mithulo, nsanje, kuba, matama mulekeni mzanu akwatire

  1. man #ken bwanji, madzi akataika saoleka, pochindanapo anthuwo zosatira amaziziwa, latalata chosatira ndimimba basi, ena akuti amangidwe wachinda kamwana chikondi chilibe size, nsapato yokha ndiyomwe ilindi size, kumunyoza munthu poti wapereka mimba nkulakwisa,

  2. nde atiuzetu kuti mimbayo anapeleka anali yani komaso kwa chinga anamulora bwanji kulankhula ngati wa chibale pa nthawi ya maliro a grace?, pano aziti anali nzake chabe chosecho anali mpongozi

 53. Ife tingokuyimbirani nyimbo ya thoko kuti ; undilonderanji Santana, anthuni bwanji kumayipisa mbiri ya anzanu.

 54. Page zambiri zimakhala zaboza mulembapo queen & kamuzu centre akuzigulitsa zinapita kt mukutanthauza kt ku ma show analiko amavina ali odwala ? Ziwani kuipitsira mbiri ndimulandu !!

  1. Mhmm a Juwawo pa social ntwrk munayamba kukhalapo liti? This is about making fun, entertaining, educative nde inu mukudza ndiotani? Thokoyo mbale wanu bwanji? Ha ha ha ha ha ha

  2. Koma zikunena manwa! ndizowona usi sufuka popanda moto kuli oyimba ambiri a Gospel Azibambo, koma samvekamveka ndi mbiri zoipa ngati mkuluyi! chikayiko Enafe timakhala nacho! why always mr Katimba okhaokha!mmmmmm!!! Asithe Awonjeza!!.

Comments are closed.