A gang of irate people in Dedza district has burnt to death an 18 year-old man for stealing beans and clothes.
Police spokesperson in the district constable Cassin Manda confirmed the incident and identified the deceased as Petrol Jalani of Kalinde village Traditional Authority Kachere in Dedza.
He said Jalani broke into the house of Mrs Enelesi Binali and stole two bags of beans and clothes before walking away.
But on his way to his destination he saw people who were hunting the mice and he started running away.
The group noticed that he was a thief and they ran after him. When they apprehended him, they set him ablaze using tyres and he died on the spot.
The police later visited the scene of the incident and took the corpse to mortuary where a post-mortem will be conducted.
Meanwhile Manda has condemned the killing saying such acts are against the constitution of Malawi.
He said: “Malawi police believe in fair trial whereby a person has a chance to defend himself in the court of law.”
AMalawi muli ankhanza kwabasi. Anthu onsewo osaoneka wachifundo kumuteteza.
Ghosh!
Ochewa oku Dedza omenewo
kkkkkkkk
Akatopanawe M’mudzi Chilango Chake Size Ndiimeneyo
Ivi vichitika kulongora boma nkhongono zakutondera wakuba lilije lekani wanthu pakuteteza katundu wawo wakontcha uyo wakola nganikale pala paulamuloro wa bakili
kumuotcha munthu chifukwa chakuba Nyemba coz ndi mphawi.. munalekelanji kumuotcha kasambala bwanji?????
zoonah !!!!
Osangosiya kubako bwanji kuti asamaotchedwe simple
Nanga osangosiya kubako bwanji kuti asamaotchedwe
This is satanic and heartless.
Guys Munthu Wakhala Akuvutitsa Uyu Atamugwira Analonjeka Kuti Amusiye Awapatsa MK2,000,000 Ine Ndimakhala Chakomweko kupitanaye ku police mawa amakatuluka
That’s only one way to end thiefty and milder in Malawi
Koma mukulakwa mawa ndinu or abale anu,nyemba zovala basi
RIP
Very bad
Shaaaaa a thief deserve to dieeeeeee dzanthu zopanda chitukuko
zooona mbwanda ndi tizovala mpaka kumupha munthu? allah akibaru
If he had not stolen, he wouldn’t have been killed. Refrain from stealing to avoid mob justice.
I respect your comment Mr Muyawa…..?
Ndichani a Malawi Nyemba basi, Zomvesa chisoni Mulungu alowelerepo.
Koma zomaphanazi no no no, enough is enough, kuba nkhuku kupha munthu I really dnt understand, what is the government doing about this.
kulakwa
Zili bwino zedi mwina wina watengelapo phinzilo
wakolora ameneyo
Very sad when people take law in their own hands..just for some food he was killed..shame!!
Imvani anthu amene muķuchita izi you are beyond sharia laws, Chitani izi kwa munthu opha nzake koma not oba nthochi, beans or chani?
wapita mkuba kwake ameneyo
Man musanene kuti anthu atayilira akuchita zomwe akufuna chifukwa, cha ulamuliro wapresident ai. Bodza limenelo kodi dziko muno makhothi ntchito yake ndichiyani, ndimayetsa boma linamnga makhothi ndi cholinga choti tikakakwirana tizikadandaula kumeneko azitithandiza? Ndiye inu ulamuliro wake mukunenawo ndiuwuti, popeza apolisi aliponso momuno oti inuyo athakukuthandizani ngati wina wakulakwirani. Muganize bwino, chifukwa anthu amene achita zimenezi, ena pomwepo ndi anthu opemphera akhristu. Koma chifukwa, cha satana m’dyelekezi ndi amene anakula mumtima mwawo ndipamene achita zinthu ngati zimenezi.
kodi ukuti chani iwe axe??
Zomwe wanvazo adawa akunena zoona
Komatu kudedzaku,,,,, chachikulu chitika…
Wosapha nduna zaboma zanaba ndalama zakhanikhani mukulimbana ndiwanyemba
Wonderful
Kuntha mantha a Malawi masiku ano akungopanga zinthu zoipa momwe angafunile, chifukwa a kudziwilatu kuti palibe chilango chomwe angalandile under Peter’s government. Mchifukwa chake a Malawi atayilira…
Nayenso, amaleka kungolima nyemba zake,amuchita bwino
Osapha Team ya Cashgate Ija bwanji?
all those who took part in burning the deceased must be arrested and brought to justice..
nyemba basi anthu otembeledwa
Koma opha albino palibe ndi mmodzi yemwe anatenthedwa.Koma nkhani yanyemba anthu?aaaa anthu oipa akang’wi ng’wi inu.
Biblically, sin its sin but we are the judges but God himself.
that z nt true
iiiiiiiiiiiiiii malawi uja lero heeeeeeee kudeza kokha abale mmmmm kaya!!
There is no security in Malawi the government is very weak that’s why
Why should you give thieves a chance to defend themselves No wonder the Malawi Police Service is busy protecting the worst thieves of all Time “APM and Team DPP ” an am sure they will be given a 100% chance to defend themselves against 577 Billion cashgate Foolish MPS
No men
Really beans and clothes that can exchange with someone’s life
R u serious?
Kom guyz nyemba zovala?kumupha zanu?
Zimayamba pang’ono pang’ono. Zulo nyemba, lelo nyemba ndi zovala, nanga mawa? Kenako mumva naye wayamba kudula anthu ziwalo, ndiye muzizatino chani? Mphoto ya ntchimo ndi imfa basi, palibenso kuchitila mwina
Why this My fellow Malawians? Judging ur friend yet Him above z there & has placed His crue 4 such cases, that z the police. May his soul rest in peace, sorry.
Bg up guys anthu amenewa amasowetsa mtendere
what is weeding.amene ayankhe bho alandila airtym.anthu alindizibwana poyankhula.zintchito zabambowa asagananazo pamodzi
man olo chimanga chogwidwa ndi mbozi timazula, tonse tili ndi machimo athu ngati pafunika weeding tonse tikuyenela kufa. monga inu muli pure?
100%
zovesa chisoni ndi mwana wang’ono munangangomulanga than killling anakakhala ndi phunzilo
Dz will never change
My homeland
Aaaaa mpaka chifukwa cha mbwanda kumuotcha nzanu
Pena pake anthu akudedza ndi osowa umunthu
Good development,,you have done nice job people their in Dedza,,,salute!
Nyemba zenizeni kumuwotcha mnzanu zoona? lyf is too sour in Malawi now anyway may his soul rest in peace
nde yake
Why didn’t report him to authorities than killing him,malawi is now becoming hell in Africa,killing albinos ,that this,i just don’t understand where this nation heading to.