Police in Blantyre city have arrested a woman for being found with 14 bags of Indian hemp locally known as “Chamba”.
The woman, Eliza Mitumbu aged 33, was keeping the bags of the hemp at a construction site situated at Chapima heights in Blantyre.
Confirming to Malawi24, Blantyre police deputy spokesperson Andrew Mayawo said well-wishers tipped the police about the illegal stuff that was kept in a building being constructed at Chapima heights in Chirimba Township.
“Actually we got a tip from people around Chapima that a woman was keeping bags of Chamba. We were told that they are 12 bags but when we went there we found two more,” said Mayawo.
The police have since sent the marijuana to Bvumbwe research station as part of the process of the trial.
Mitumbu hails from Kika village, Traditional Authority (TA) Mulumbe in Zomba city and she is yet to appear in court to answer the charge of illegally possessing illicit drugs.
Police are also ganja smockers wats the difference?
Musalimbane ndi mzimayi, ndi business imeneyo akufuna azithandize, very sad mumagwira munthu akatenga makala, ziboliboli mukuti ma document, pamene mukulephera kugwira aja anaba ndarama za Misonkho, mukulimbana ndi abale anu ovutikanso SHAME ON YOU , Paja ndinu osusuka eti? Ras dema anaimba kale apolisi ndinu afalisi nkhope ngati ndi afisi.Msiyeni mayiyo kamangeni omwe akusuta mkumasokoneza ntaunimu OTHERWISE ine ndie ndiku grader2 high grade ndikufuna kusuta CHAMBA , mtondo wa nkhotakota CHOGONERA ndi ubatchala wu ndiziBema night yonse, and Next week ndi ya Kumagulitdano GANJA, Nazi, CANNABIS, Nda 3litse mafana mu ghetto yathu
Paribee nkhani pamenepo
Caught with holy Weed! God will burn u Officer ok!
canabis akakuzunga eee! chakwanu leka
Is it not obvious thy burn one bag and eat the rest mxieee!akusowa ntchito yogwira mbava
Apolice chifukwat samalemela vimbuli
Check this out
Koma chonsecho kumat chamba ndi makobili
Mbuzi za apolisi
?
Malawian police are colified on arresting robers and chamba selers not albino killers thats why peter is serious on these who are following cuture practice instead of puting his serious on albino killers. BUD GOVERNMENT
Ndi Mkhalidwe wawo umenewo kgwira wachamba kuleka kugwira akuba ndi kulondera kunyumba kwanga masatifiketi osokeresokerawo mukufuna muzitiputa dala, kuyaluka kosakhulaniko lekani kugwira ogulisa ”chamba” bwanji si mukumumanga yemwe analenga chambacho……hahahahaaaaaaaaaa musiye ntchitoyo si kukukhalani mubwere kwathu ku @ kutoilete muzizandiiingisila ntchentche mwana wanag akamanyera bola musazangwirire coz ndisachosa nonse ntchito kukaponyani kumental mitu ziboliboli zoperewera nzeru yakasemedwe….skoll yake iti munapita inu YAKWACHA yomweyo hhaaaahahahaaaa ntchito yanu si mmaiziwa si mutukukabe olo muwagwireamphawi akapolo kuzolowera thangata system bwanji inu simukulima chanu mukumaphaso alumino ndinu meaonekera poyera kkkkkkkk…hohohohhohohohohoh
Zazii!! Malo molimbana ndikugwira okuba,mukulimbana ndimunthu opanga bussness yot apeze ndalama yothandizira banja lake,Kod mukufuna kut abee?
Zimenezo nde zachamba sono ife nde tizikapeza kuti ngini heyiii amasulidwe basi
kkkkkk police ya mw kukokomeza wachamba kukephera kugwira akuba zaugalu bas
Walking fee must fall
A Malawi stop being jelalasi chamba it’s not bad like drugs that women try her luck to herp his family koma inu thamangani ku police kuka munela. Why don’t you tell the police those people who killing a napwele? I wish I was in Malawi right now I should herp her money for lowyer and pay bail for her.
kkkkkk koma iweyo, iiii aa Malawi tatopa ndichilungamo awuze
sanalakwise ntchito zikusowa, apangabwanji munthu wa mai alindiana uyu amathandizika momwemo mmasuleni,mmuka mange okupha athu
Mutayeni mkazi ameneyo ma crooks a police inu… That’s Malawi’s gold.
Just legalise
Abuse to a woman
Bwanji
BOMA LA KU MALAWI NDI LOVETSA CHISON
AMASUTA AMENEYO.
AMASUTA AMEYO.
Kodi apolice akalanda amapitanacho kuti nawonso tiwasegulile mlandu
Kodi tiyamba liti kuchilima?
zinazitu mudzinena zona,mongadi matumba achambao akwana 15?
Nde chimene chitazatukule dzikoli ndi chan ganjayo alibe vuto amutaye mayiyo sanapheko munthu ndi business ya mtendere
Chonsecho ndalama amafuna kukagula chakudya ndi fees pompo koma wakatangale mkumusiya wopha ma ma albino ndi njauju mkuwasiya Mulungu akukuonani
amalawi stdzalemera!anthu asyen achte chomwe akfuna ngat nkupenga apenga okha, #ganja business yot tkhoza kutukukrapo
Ku Malawi umbuli zuzatha maka amithiko kumanjawa chifukwa chake mpaka pano akumangoyenda pansi kupita ku ntchito inu mukuganiza mayiko anzathu akutukuka chifukwa chan? Economy? Mayaz guyz ife kwathuko tilibeko migod ya gold, diamond copper even petroleum
Fuck U Police,,, Agalu Aboma Inu Kukhomerera 2much,,, Mpite Mzikasamala Banja Lake Inu,,, Indian H Iribe Chfkwa,,,
ngati mukufuna kuona maloza apolice mundipeze kuno ndiponso ndinalemba pa post kuti ndili nacho kuno ndinali ndi 13 bags wet 50kg koma pano ndasala ndi 6 bags mubwele kuno muzaone inu zisilu eti muzandipeze ine kuno muzaona mwina mungomva ndipo sindizasiya kulima mpka kale
Feesmustfall
kod chamba chimapha athu chifkwa chiyan mumatimanga mukatipeza ndi chamba chomwe ndi zomera mmesa mumati chuma ndi thaka mutiganizilepo.
Jealousy is on high demand in Malawi those police are the ones smoking chamba but if they find it with just a person they aredting pretending like they know their job, apolice oyenda ndi ndodo m’malo mwamfuti zaziiiiii
NDIYE FODYAYP AMENENE MUNAVIMOREZA KUTI AZILIMIDWA MESA NDI CHAMBA CHOMWECHO?
chamba ndi dilu hv kusiyana Ndi kumphar Alobin
Mzimayi walakwa chiyani? DPP Idaloleza kulima chamba osati kugulitsa ndi kusuta malamulo anu ndi otani ????
aaah apolice kma amakhala operewera nzeru buanj? mesa it was legalised? mwina chizungu cha legalised sakuchidziwa kapena?
true
Inenso Ndli Nacho Ma Bag Atatu Muwauze Apolicewo Awere azandmange.
vuto lakwathu kuno nkosauka koma atsogoleri simufuna kuvomeleza coz inuyo zanu zikuyenda,remember ukakhala pansana pa jobvu msamati kunja kulibe mame,mukufuna tidzitani ifeyo?tigulitse chamba mwatimanga,bushiri atipatse chimanga mwnamuletsa tipite ju jubek mwati agwileni azibwela kunu pamene job zikusowa,nde ndizimangilire mawandimangaso kkk
Tinapanga kale legalize, mwina amumangawo ndi ma trainee sakudziwa
mutayeni pali zazikulu zoti muchite
I fot it has been legalised kd. Mukukaniza bee
Mukuleka kumanga mbava zikuononga chuma chazikozo mukumanga mzimayi yemwe akupanga sogolo lake fuck police
Akufuna Basi Alwys Tizipempha Kwaiwo,ndalama Zimeneziiii
chifukwa chani mesa ndi chovomelezeka
Chifukwa chani?? mumafuna azipanga uhule?? mmayesa ku Malawi kwanu kuno ntchito zikutsowa.
Mmafuna Chambacho azitenga achina Morgan Heritage kapena a Bisy Signal??
Dziko lopondeleza ma citizen ache ngati ili sindinalionepo.
Kukhala nzika ya Malawi ndi mavuto,, tobacco ndi izo alimi akumangoziphazo coz of ma stress.Zolowetsa ku munda ndi zogulitsa otsagwilizana SHAME!!
Nde yake,mabebie mukumawakondela kwambiri iyaaa
The government agree… we can smoke in public why now.shit police
Nanga wa Albino bwanji ,zaugaru basi iye ndi bisness ntchito zikuvuta akanatani
Why netting her?I thought its open market nowadays?