Malawi Police net Woman for chamba possession

Arrested

Police in Blantyre city have arrested a woman for being found with 14 bags of Indian hemp locally known as “Chamba”.

The woman, Eliza Mitumbu aged 33, was keeping the bags of the hemp at a construction site situated at Chapima heights in Blantyre.

ArrestedConfirming to Malawi24, Blantyre police deputy spokesperson Andrew Mayawo said well-wishers tipped the police about the illegal stuff that was kept in a building being constructed at Chapima heights in Chirimba Township.

“Actually we got a tip from people around Chapima that a woman was keeping bags of Chamba. We were told that they are 12 bags but when we went there we found two more,” said Mayawo.

The police have since sent the marijuana to Bvumbwe research station as part of the process of the trial.

Mitumbu hails from Kika village, Traditional Authority (TA) Mulumbe in Zomba city and she is yet to appear in court to answer the charge of illegally possessing illicit drugs.

Advertisement

57 Comments

 1. Musalimbane ndi mzimayi, ndi business imeneyo akufuna azithandize, very sad mumagwira munthu akatenga makala, ziboliboli mukuti ma document, pamene mukulephera kugwira aja anaba ndarama za Misonkho, mukulimbana ndi abale anu ovutikanso SHAME ON YOU , Paja ndinu osusuka eti? Ras dema anaimba kale apolisi ndinu afalisi nkhope ngati ndi afisi.Msiyeni mayiyo kamangeni omwe akusuta mkumasokoneza ntaunimu OTHERWISE ine ndie ndiku grader2 high grade ndikufuna kusuta CHAMBA , mtondo wa nkhotakota CHOGONERA ndi ubatchala wu ndiziBema night yonse, and Next week ndi ya Kumagulitdano GANJA, Nazi, CANNABIS, Nda 3litse mafana mu ghetto yathu

 2. Malawian police are colified on arresting robers and chamba selers not albino killers thats why peter is serious on these who are following cuture practice instead of puting his serious on albino killers. BUD GOVERNMENT

 3. Ndi Mkhalidwe wawo umenewo kgwira wachamba kuleka kugwira akuba ndi kulondera kunyumba kwanga masatifiketi osokeresokerawo mukufuna muzitiputa dala, kuyaluka kosakhulaniko lekani kugwira ogulisa ”chamba” bwanji si mukumumanga yemwe analenga chambacho……hahahahaaaaaaaaaa musiye ntchitoyo si kukukhalani mubwere kwathu ku @ kutoilete muzizandiiingisila ntchentche mwana wanag akamanyera bola musazangwirire coz ndisachosa nonse ntchito kukaponyani kumental mitu ziboliboli zoperewera nzeru yakasemedwe….skoll yake iti munapita inu YAKWACHA yomweyo hhaaaahahahaaaa ntchito yanu si mmaiziwa si mutukukabe olo muwagwireamphawi akapolo kuzolowera thangata system bwanji inu simukulima chanu mukumaphaso alumino ndinu meaonekera poyera kkkkkkkk…hohohohhohohohohoh

 4. Zazii!! Malo molimbana ndikugwira okuba,mukulimbana ndimunthu opanga bussness yot apeze ndalama yothandizira banja lake,Kod mukufuna kut abee?

 5. A Malawi stop being jelalasi chamba it’s not bad like drugs that women try her luck to herp his family koma inu thamangani ku police kuka munela. Why don’t you tell the police those people who killing a napwele? I wish I was in Malawi right now I should herp her money for lowyer and pay bail for her.

 6. sanalakwise ntchito zikusowa, apangabwanji munthu wa mai alindiana uyu amathandizika momwemo mmasuleni,mmuka mange okupha athu

 7. Chonsecho ndalama amafuna kukagula chakudya ndi fees pompo koma wakatangale mkumusiya wopha ma ma albino ndi njauju mkuwasiya Mulungu akukuonani

 8. Ku Malawi umbuli zuzatha maka amithiko kumanjawa chifukwa chake mpaka pano akumangoyenda pansi kupita ku ntchito inu mukuganiza mayiko anzathu akutukuka chifukwa chan? Economy? Mayaz guyz ife kwathuko tilibeko migod ya gold, diamond copper even petroleum

 9. ngati mukufuna kuona maloza apolice mundipeze kuno ndiponso ndinalemba pa post kuti ndili nacho kuno ndinali ndi 13 bags wet 50kg koma pano ndasala ndi 6 bags mubwele kuno muzaone inu zisilu eti muzandipeze ine kuno muzaona mwina mungomva ndipo sindizasiya kulima mpka kale

 10. kod chamba chimapha athu chifkwa chiyan mumatimanga mukatipeza ndi chamba chomwe ndi zomera mmesa mumati chuma ndi thaka mutiganizilepo.

 11. Jealousy is on high demand in Malawi those police are the ones smoking chamba but if they find it with just a person they aredting pretending like they know their job, apolice oyenda ndi ndodo m’malo mwamfuti zaziiiiii

 12. aaah apolice kma amakhala operewera nzeru buanj? mesa it was legalised? mwina chizungu cha legalised sakuchidziwa kapena?

 13. vuto lakwathu kuno nkosauka koma atsogoleri simufuna kuvomeleza coz inuyo zanu zikuyenda,remember ukakhala pansana pa jobvu msamati kunja kulibe mame,mukufuna tidzitani ifeyo?tigulitse chamba mwatimanga,bushiri atipatse chimanga mwnamuletsa tipite ju jubek mwati agwileni azibwela kunu pamene job zikusowa,nde ndizimangilire mawandimangaso kkk

 14. Chifukwa chani?? mumafuna azipanga uhule?? mmayesa ku Malawi kwanu kuno ntchito zikutsowa.
  Mmafuna Chambacho azitenga achina Morgan Heritage kapena a Bisy Signal??
  Dziko lopondeleza ma citizen ache ngati ili sindinalionepo.
  Kukhala nzika ya Malawi ndi mavuto,, tobacco ndi izo alimi akumangoziphazo coz of ma stress.Zolowetsa ku munda ndi zogulitsa otsagwilizana SHAME!!

Comments are closed.