President Peter Mutharika has dismissed General Ignacio Maulana as Malawi Defence Force Commander, Malawi24 can report.
According to Chief Secretary to government George Mkondiwa.Mutharika who is Commander In-Chief of Malawi Defence Force has since promoted Maulana’s deputy Lieutenant Supuni to the position of Army Commander General.
Former army spokesperson Clement Namangale will also take up a new post at the army as he has been appointed as deputy Army Commander.
Meanwhile General Maulana has been deployed to the National Food Reserve Agency ‘to manage food security’.
Mr president,you are commander in chief of Malawi defence force but yet you arent undergone military training.Mind you when intefering with these,next time…
Pitala mampazi ake ndithu
mr genel tiyeñi tilowe mtchile pabvuta apa nawoso atidziwe
Kkkkk kulakwa
Kenako achotsa nchito wamkulu waku G4SECURITY …..USELESS PRESIDENT mmalo molimbana ndi athu akumpa albinos bizzy kuchotsa athu nchito wofunikila …
Ife amphawi tizingokanda mpaka kalekale olo titasintha ma president, akupando akumwa tea wa nkaka ali mpheee
2019 is closer,paize peter..
Good news!!!
zinazi ndi mbuzi zaatolankhani samadzi kuwapatsa anthu nkhani zabwino zolongosoledwa bwino.
kaya
mway wake 2019 tizavotaso manyaka azipan zinaz atikwana
Good to our president
we dnt hv a presedent
Wachita bwino Peter apa mkuluyi wachotsa ntchito asilikari ambiri pazifukwa zaziii.
He wants more lomwe dominant In Government top positions
Boma la bambo Petulo nd ngoz mene akulira awa akuwauza kut fire si bho kma
Bwana President palibe chomwe mwalakwisa wel done gud job mwaaaa!!!!!!!!
I see no issue here, demotion happens anywhere. Let DPP run its gvt to its best,we don’t know de reason y then let his protect our food dere…. Let him show his abiity there
Akala a president magufuli wa ku Tanzania
#feesmustfall anyway..
Ndizinthu zomvetsa chisoni zedi kut tizilimbana nkhani imodzi modzi ndiye kwa inu odziwanu pitirizani ndikudziwako,koma chomwe mungadziwe ndichakut aliyense akudzionera yekha chabwino ndichoipa ngat m’malawi nthawi ndiyanu inu odziwanu,chidzadziwe mchipande powomora mumnthawi yokhazikikayo,
thyolo ilowe tsopano, popanda kuwona ma paper
Nothing much
ONSE akhale oipa nanga wabwino akhala ndani?
According to my own side, it can not happen like this without something Wrong, it might be something Wrong, that is why he is fired . Muthalika is a man who doesn’t want to see someone against him. I’m really Proud of Him. Congratulation Mr President.
Nanunso mumangosusa chilichonse chingapange Peter Mutharika muzakhala osusa mpaka kale.
Lupanga lophela nzako nawenso lizakulasa
Malume zavuta basi
Inu aChilima nchacha mukat malamuro amamulora ndiye azingochotsa anthu mwachisawawa,ingakhare ili mphamvu yake azitsata ndondomeko yabwino pochita zinthu,inuyo amwene musatenge amnzanu ngat osaganiza popereka maganizo awo pankhani iyi,mukati umbuli ndiye kut chiyani,palibe munthu odziwa zonse man,and no one iz above constitutional,
palibedi odziwa zonse nde oziwako pang’onofe tikukuuzani musapange makani. chabwino amaenera kusata ndondomeko yotani mmene mwalongosolera inuyomu.?
komaditu ameneyi wawonjeza moti adzipanga sama salarys awogwira ntchito m’boma azilandila munthawi yake choncho mpaka pa36
malawians complaining too much eishhh kutinso tifufuze enanu you know nothing management ya defense force your reporters they dont explain in details koma kungokubonisani nkhani, this man if you consult the soldiers they are clapping hands cause of corruption. Lets help in hand to develop our warm heart of africa aman himself will never satsfy all your needs. Stand your on ground Malawi
malawians complaining too much eishhh kutinso tifufuze enanu you know nothing management ya defense force your reporters they dont explain in details koma kungokubonisani nkhani, this man if you consult the soldiers they are clapping hands cause of corruption. Lets help in hand to develop our warm heart of africa aman himself will never satsfy all your needs. Stand your on ground Malawi
Pumbwa ameneyu sadztheka basi
thank u
Ndipo inu, just full of negativity…. They think munthu angangomuchotsa ntchito opanda chifukwa? Iiiooh k9na a malawi sitizatheka!
Hahaha kape uyu tionana 2019
Hahaha kape uyu tionana 2019
Malamulo amamulola kutelo. ngati zakuwawani tikakumane ku nkhothi osamangotokota za zii apa
Malamulo amamulola kutelo. ngati zakuwawani tikakumane ku nkhothi osamangotokota za zii apa
We still like him as army general munthalika know nothing about malawi army
We still like him as army general munthalika know nothing about malawi army
kwanu zimenezo kwathu kuno ayi
Chilima cadet iwe vaya uko.
Absolutely nothing…
remember the prsdnt is the chief commander. sukulu ya kwacha iyambilenso ndithu
Bring back our general useless man
Bring back our general useless man
Walakwa chani? Kodi munthu akangola kwisa pang’ono basi fire?
kkkkkk mukufunsa kenako mukudziyakhanso nokha kkkk
kkkkkk mukufunsa kenako mukudziyakhanso nokha kkkk
that is apolitical problem.ndale zakumalawi muzizidziwa
ndimaesa malamulo amamulola kutelotu. mbuli za anthunu
Ziululika mungofasa paja zikamapita kovuta zimayamba choncho
mukamba ziti kodi
boma lili mmanja mwa agalu ndikelo
Sizabho”
Komatu ndimakuwuzan, musavotele uyu’ ndi ntchona! Mumvekele ndi aprofesa) wa ma degre.
Cool Maulana, He Should Also Fire The 7 Cabinet Ministers Immediately, If Not ..Demos Basi.
Why?
Maybe he ploted a coup against corruption
Udindo uwu ngovuta chakachina 1997 wins anakhala miyezi 7,,basis kuchosedea
Udindo uwu ngovuta
Hehe! Nambo aweni, kunya nchipeta inu” Dzowona mkulu wa nkhondo, woziwa chibagela mkumuchosa?
ngati waona vuto mwa iwo, ali ndi mphamvu zomuchosa!!
zikomo. sukulu ikufunika kwa anthu awa abale
you nxt to be fired peter u must know that
Mmayankhula ngati mukunyera bwanji?MUSIYENI APM AWUSUMANE ANZANU NGAKHALE ZIKUVUTA KOMA SAKUNYOZA NGATI INU ACHEWANU . DR BANDA ANALAMULA MALAWI MWANKHANZA ANGAIWALE NDANI ANAPHA ANTHU AMBIRI ANGAIWALE NDANI KODI ZOTI ACHEWANU NDI ANKHANZA ASAKUZIWA NDINDANI MAKADI, KUTILANDA NKHUKU, MAZIRA ,MBUZI ,NGOMBE ANGAIWALE NDANI ?ACHINA GADAMA , MATENJE CHIWANGA WAIWALA NDANI KUMENYA MAFUMU KUCHOTSA MAFUMU MWANKHANZA ANGAIWALE NDI NDANI MUSOVA MULEKENI APM AYENDETSE BOMA MWAUFULU NDIPO MAULANA ANAMUPANGA APPOINT NDI APM YEMWEYO NDIYE CHOLEPHERA KUMUCHOTSA NDI CHIYANI
Kuganiza kwainuku ndiye ngati mukunyera, muzitiuzaza Kamuzu pano? Ife Kamuzu sitikumuziwa tikuziwa izi. Ndiye sabola wakale sawa. Ngati mulibe mfundo ingokhalani zakukanikani vomerezani. Maulana anakukanirani zautsiru zanuzo. He is a true professional Soldier very appolitical amakana nonsense. Ndinkona mwadana naye. Go on Maulana, Your Conscience is clear. No traces of filthy character. Anthu mumadana ndi chilungamo. Go to the forest, straight trees are cut down while the croocked ones are left to live. Dikiranimuone zinazi ngati asilikai simugwira ntchito ya a police kumazunza otsutsa boma. Mwayiwala Maulana ndiyemwe anamukanila Joyce Banda kukatseka Tally Centre ku Commessa in upholding the constitution kuti mulowe mmboma. Lero ndi oipa? Akanakhala enawa okonda ndalamawa akanakatsekatu. Dzimvere mumtolo. Long live Maulana.
Kuganiza kwainuku ndiye ngati mukunyera, muzitiuzaza Kamuzu pano? Ife Kamuzu sitikumuziwa tikuziwa izi. Ndiye sabola wakale sawa. Ngati mulibe mfundo ingokhalani zakukanikani vomerezani. Maulana anakukanirani zautsiru zanuzo. He is a true professional Soldier very appolitical amakana nonsense. Ndinkona mwadana naye. Go on Maulana, Your Conscience is clear. No traces of filthy character. Anthu mumadana ndi chilungamo. Go to the forest, straight trees are cut down while the croocked ones are left to live. Dikiranimuone zinazi ngati asilikai simugwira ntchito ya a police kumazunza otsutsa boma. Mwayiwala Maulana ndiyemwe anamukanila Joyce Banda kukatseka Tally Centre ku Commessa in upholding the constitution kuti mulowe mmboma. Lero ndi oipa? Akanakhala enawa okonda ndalamawa akanakatsekatu. Dzimvere mumtolo. Long live Maulana.
Eya mulongwanga auzeni osusawa akagwele uko.khaya afune khaya asafune BPP mpaka 2039 wooo! APM boma.losankhidwa osati akalinde. Akasowa chopanga auzeni abwele ku THEBA kuno ndizawalembe ntchito leave my president alone.Just wait 4 ur time iz coming in 2039.AKUZINAMIZA KUT TIONA 2019 KODI NGATI ALEPHELA KUPHA KALULU ADAKALI OYEMBEKEKEZELA AKASWA ANGAMUGWIRE?
Kkkkkkkkkkkk auze zoona APM NDI MOTO WAMDONDO SAKUCHEZA AYI MASO ALI CHISOGOLO .MUNGOTI SIZIKUYENDA MULI PHWIIIII MUFUNA AZIKUPASANI ZA ULERE GUYZ MWAUPONDA.NDIPO MUZAPHATIKIZANE TIZIPANI TANU TAMTHUMBATO AZAKUNYENYERENI LIMODZI PALIBE MPATA KUPEREKA KWA ACHEWA BOLA TIMPASE MTUMBUKA ALAWEKO NAYENSO KUTI AZAUFILI MU 2129
Sono apa ma comments ose zikuonesa athu pita simukufuna kkkkkkk Zilibwino kusonyeza mavoti zizavuta kubera ? Malawi mwamanga fundo imozi
amupatsa chibonga kuti adzikalondera ku food reseve
it seemz u dnt knw the differenc btwn firing n realocation.mwangoonetsa umbul wanu.shame on u un professional journalist
although am nt a dpp fan bt plz malaw 24 dnt mislead pipo here.he z nt fired.he haz been realocated to work at the derpartment of NFRA.Auzen truth an2.zofuna zanu mudzakwanitsa kman kumaona posocheletsela an2.nkhan ya medi bwanj cmunalankhule.mexa med nd wapolice by prof.kma al ku migration
manoma woyeeeeee
There’s nothing the man iz doing.
There’s nothing the man iz doing.
There’s nothing the man iz doing.
Amuchotseranj?
Amuchotseranj?
Ndiwausilu pitala….akufunika makofi ameneyo
walakwa chani munthuyi mtundu wa amalawi akufuna kudziwa chenicheni chomwe mkuluyu walakwa
Munchotsa bwanji yet Recruitment is just around the corner sizoti mutengeso manyaka anu DPP (cadets) paja akumalowera pawindow ena ndikumabwezedwa
..ine ndikuyembekeza the day he wll take a bold stance to fire those 7-f****ng corrupt ministers,implicated in the cashgate report.
Kukhala m’malawi ndikulimba mtima imagine mpakana,lero no birth certificate mayiko anzathu onse alinawo ,mmalo moti apange kaye izi akulimbana ndizochotsana pamaudindo hahaha ndakulilira Malawi dziko langa olo kumwalira lero mulungu sakadziwa kuti ndine mmalawi chifukwa chopanda,certificate kkkkkk work up muhlakho
Amwene inu sukulu mumakhalila ma zero nkhani sizikukhuzana apa
hahaha gyz
i knw peter mutharika hi knws to fired only but to do something that MALAWI to change never hi doknw kodi munasakhidwa kuti muzichosa anthu tchito kapena kuti musithe MALAWI kukhala wabwino??????? im not happy nd family for mutharika munangobadwa dzelu zanu ndizimozi eti mumangosokoneza malawi basi im not going to vote u again bava inu malawi anatha anali kale please change ur mind peter we want to see malawi to come like before mutharika u mus go
kumalemba chichewa chokhachokha baba chizungu mchovuta…..
za zi basi malamulo amamulola kutelo olo asanalakwe kapenanso atalakwa
Tsopano yemwe amukwezayo amulakwiranso? aMalawi tili ndi vuto lomangoona negative impact of the story yet the same President has appointed another person to that position but we don’t commend him . are we not just shooting ourselves on the foot? although he sound like not doing good, but he has promoted someone .a thing worthy mentioned
vivungu kkkkkk
thanx Mr Leyton phiri
he’s good at firing people wait tomorrow will fire him too.
Kkkkk he born talented in fir’ng pipo, we need to demonstrate his talent by fire him, after we demonstrate then pipo will say his talent spks for him
hahahahaha ?? Prince Kings Mvula
Kkkkkkk
Something is wrong somewhere.
Ndangati angafune tilande dziko la Malawi coz am ready to create group called #Boko_Malawi coz #Pitala akutizuza hvy than #Tembo plz youth of Malawi we must wake up coz land bill iyi sindikuimvetsa bwino momwe yalowela plz contact me but sindiku panga force mfuti xilipo mix otsutsa atithandiza zipangizo xina monga ma galimoto chidule ndikungopha bwampiniyu
Pure treason
mukamba nkhani iti mmukungobwebweta nchimbulimbuli
kkkkkkk akayamamba nkhani imeneyi siupezapo mmalawi angakhale mmodzi kamba ka mantha
kkkkkkkk A Malawi mantha dziko lili lanu asaaa
Akuchotsa maulana kusiya ma ministers 7 omwe ali mbamva zeni x2.kodi ma ministers akewo akuwasiyikanji?
kodi amuchotsa kamba ndi mbava?
Another nonsense!!!!
Muthalika is the one useless.
kaya. Amuchotsabe
This may breed civil wars
mulinso ndi maganizo opusa bwanji
He Has Done Well.Thats What Is Needed As In De Form Of Reformation
7 Cabinet thieves plz,bora msapange lomwe state nd.mafiring anuwo
comment reserved
Kkkkkkkkk koma Mr M kumchosa commander,,,, akuchosa phuno uwone, tisavetu kuti uku kuli sikando ndiye zikuvuta uwona
It is good dat he has given other post but what was exactly happen its what we have to know can somebody tell us plz
About turn!!!! Patsogolo,pambuyo tembenuka timatero tikamapanga parade kkkkkk dats hw lyf goes on rest in peace mr man
????
President Peter Mutharika has fired Commander of the Malawi Defence Force General Ignacio Maulana and replaced him with Lt Gen Sapuni. Secretary to the government George Mkondiwa confirmed to media the dismissal of Gen Maulana. Former MDF spokesman Clement Namangale been promoted to the position of Deputy Army commander. Gen Maulana has been deployed to the National Food Reserve Agency ‘to manage food security’, says Mkondiwa.More details to follow.
Nkhan muziika yonse ,osati kumatipatsaso ma direction enaso ngat simukufuna mungosiya
Mukuchotsa general commander bwanji m’malo mochotsa nduna zakuba zija,plz Mr President b careful ndimbari yachitetezo maka a MDF,sitkufuna kut timvere kut agalukira ena,mapeto ake bwana President inuso ndikuchotsedwa pampando mwachipongwe,
mungodikila mudzalowe u president inuyo bwana. ndimaesa malamulo amamulola kutelo
koma akuti amuchosela chan koma mulakho ai mavuto
I Lov Malawi
osachotsa nduna zakuba zija bwanji?
akuchotsa okuba kodi?
Maulana is a true and professional soldier, very appolitical and he does not tolerate nonsense. He might have refused stupid demands by politicians. Remember he Is the same one who refused Joyce Banda’s order to send soldiers to shut down Tally Centre at Comesa hall in upholding the constitution of Malawi for u to find ur asses in the Government. Now they are scaredof him why? What are they planning, wake u Malawians, Maulana is not a thief and his conscience is clear, they could not cox him into fraudulent acts. Take a look at the forest, all straight trees are cut first leaving the crooked ones to live. Politicians look for sotf people that they can manipulate. Wait soldiers will soon be used as police to harass opposition members. Something big is cooking up let’s wait and see. Dzimvere Mumtolo. Another Cashgate is building up in the MDF, mark my word. .. Poor Malawi
Eti eti aaaa vuto vuto aaaa
tieni tisamasokoneze nkhani. nkhani ili apa si ya nduna ayi.
Ndiye ofunika kuchokawo nanga inu mkuti bwanji?
That picture it shows USA flag not MW flag . Maybe he got fired becouse of that
Malo momalimbana ndi mavuto ali zikoli ,koma kumango chosa anthu tchito. chala changa ndinakulakwila
Impatiently waiting for the firing of the 7 ministers involved in the cashgate! That wil atleast convince donors!
to convince malawians baba osat ma donor….kod mudakalotabe kod kuteleku sumaziona mukuziiimila panokha?
Kkkkk Malawi is still a millenium away from being economically independent! We may just reduce ths dependence
These economic woes wil soon humble our president to act on issues blocking donor support. The worst is yet to come!
All are in the same category…
We Need The Reason Y??
to do what wt the reason
Udekhe2 Zakozo2!!
Koma gogo ameneyu ali ndi vuto ndialiyensetu….mawa achonsa inspector general wa police…..kkkkkkk
Kenako titangomva kuti ALL MALAWIAN CITIZENS ARE FIRED….WE’RE NO LONGER CITIZENS OF MALAWI….
kkkkkkkkk mwaganiza bwanji
Kkkkkkk anachosa kale amwene ngat akut anthu azilipila malo okhala awo si chimozimozi kukuthamangisani?
Kkkkkkk ngati unama Ezekiel Nyondo
ndizonadi man,koma osadanda tsiku lina imeneyi izakhala mbili mukudziwa kale komwe tikuchokela kudali ena oposa awa lero ndi history
Mawu
Hawu hii ayibo mukuruma kanjani amadoda kkkkkkk
kkkkkjk
shaaaaaa
God Should Do Something To Our Nation Koma Tisaope Amalawi.
ndimaesa ndi udindo wachetu kumangotsutsa za umbuli basi? mukuziwa chomwe amuchotsera kapena? lets b fair guys
KKKKKKKK ZOONA MAN
Kkkkkkkkkkkkkk iwee nde wanena zooona aise pitalayu sindikumuona bhoooooh kkkkk
@ chilima. Its quiet strange to us citizens to just hear sketch news. We have a right to know why? Why not reporting the reason? Are they planting the reason. Of course ndiudindo wake but u can’t just fire someone without reason. But on this i can smell a rat. Something fishy. No dispinary, no warning, no reason, no notice. What kind of adminstration is this? We are not fools. We voted him in to lead us with truth not secrets.
# Micheal Malamulo amati chani kodi pa nkhaniyi zikuonesa ngati titha kuchezerapo.? ngati mukuona kt palakwikwa bwanji apite ku nkhothi bwa
# Micheal Malamulo amati chani kodi pa nkhaniyi zikuonesa ngati titha kuchezerapo.? ngati mukuona kt palakwikwa bwanji apite ku nkhothi bwa
Kodi Pitalayutu adanena kale kuti iye alibe polobulemu, atha kupanga watever akufuna coz he’s already rich ndipo uplezdent uwu analowa ncholinga chopanga history ku family yauMntharika kuti alamulira Nyasaland ngati ufumu! kkkkkkk
Kodi Pitalayutu adanena kale kuti iye alibe polobulemu, atha kupanga watever akufuna coz he’s already rich ndipo uplezdent uwu analowa ncholinga chopanga history ku family yauMntharika kuti alamulira Nyasaland ngati ufumu! kkkkkkk
kkkkkkkkk nde mwati kenako tizamva kti all malawians Shani? kakakakaaaaaaaaa
kkkkkkkkk nde mwati kenako tizamva kti all malawians Shani? kakakakaaaaaaaaa
Grant whats ur main point. musokonezatu nkhani mukamba zosephana
Chilima kodi iwe ukmuikila kumbuyo?
Malamulo or pa company ukalakwa koyamba its first worning then second worning sopano uyu mukumuikira kumbuyoyu worning yake ilikuti? Adawa alibe pabwino awa sindimaziwaso kuti pali omukonda ngati inu adakuikani chibaz eti?
Eeeeh amwene muli kutali bwanji mutichedwetsapotu apa. mwati pa company eti ndiyakhe chonchi ndizosiyana company ndi dziko. poonjeza kuti mumve bwino company maudindo umachita kufunsila kuti ukhale pa possition inayache. pomwe udindo awachotsapo akuluwa amasakha ndi president munthu yemwe wamufuna iye ndikuona kwache ndipo ali ndi mpamvu yomuchotsanso pa mthawi ina iliyonse popanda kusokonezedwa ndi wina aliyense. zamveka kaya???
@chilima comon man we the pipo hv the right to information of everythn thats happening in our country….so we hv to kno wat happened kut the general shud b fired.
Kuthana kuthana ndale za pamalawi
Old people old ideas…
NKHANI ZA NATIONAL DEFENCE EN SECURITY ZIFUKWA ZIMENE MUNGAPATSIDWE RIGHT NW ZINGAKHALE ZABODZA JST WAIT MUMVA KMA PRESIDENT HAVE THE MANDATE TO DO THAT!
ARMY COMMANDER NDI UDINDO WA NDALE JST AS INSPECTOR GENERAL!
KU ARMY UKAFIKA UDINDO WA MAJOR GENERAL NDIYE KT WATHERA BASI JST AS COMMISSIONERS IN POLICE SERVICE
Kkkk Koma yah DENNIS NOMANDA ntchito ilipo nditthu tapezani buku la malamulo muwerengeko pangono abale. ndizoona uv got that rght. koma lamulo lagwilitsidwa ntchito ndi a prsdnt positha udindowo silikambapo kuti ayenela kukudziwitsani zifukwa zake ayi.
kkkkkk mpaka kuwerenga?? kma mkulu nde kukhala nazo serius2
Ndiye akachotsa amalawi onse adzamuvotera ndani kkkkk
That is the problem with u Malawian journalists. Give us story in detail. He was fire because………………………. of what? U have details of who wil replace and where he wil go. But the reason u dont tell us why.
evn if there is no reason man malamulo amamulola kutelo
evn if there is no reason man malamulo amamulola kutelo
What chapter. Its unconstitutional. A president have a right to apoint and fire pending outcome of displinary or inquary of the situation eg corruption charges, nepotism, civil and criminal charges or if the official under peform/not fit to hold the office and under qualify. But in this case none of any reason suit. He can just wake up and feel to fire a minister simply that he is a president. They are some procedure followed. Plz if u can verify the chapter which say that in our constitution.
then take him to court mr knws it all. sindikuonapo chamzeru mukukamba apa u hv jst prvn that u knw nthng about it
U have failed to point out the chapter to support yo point simple siumadziwa malamulo aMalawi. And its not yo fault. I did’nt say i knw everything like yo president. Talkn about the court, the justice in Malawi is biased like u. They are there to please their superiors. Of cause u can not get sense because simple dont know our constitution. Common sense” everything happen with a reason”. They are lot of pple arrested unlawful in Malawi simple political orcherstrated. They is no justice in Malawi. I want to tell u now that i have studied law. And i knw what i talkn about. Its not a sin for u to be blinded in judicial. We cant be all lawyers, engineer, pastors. If u were closed i would give u book lamalamulo aMalawi in chewa for free.
let me tell u.simunapite ku sukulu inu lets b honest.and how can i take sides for the stupid issue which doesnt concern my country? empty tins always make noise
If so suit yo self. I can refer u to pple whom u wil be suprise. I did my O level Cambrigde with 6 Bs and 2Cs 1 A in Zimbabwe and join Zimbabwe Police when i was 18 while i was doing my studies. I left police when i was 27yrs moving to Malawi with my family. I have worked with NG0s in Malawi. And right now i am doing other studies in RSA. I am Malawian by decendant. Siungandi namize malamulo aMalawi because they fall under British colony.
kkkk u see dont force the issue police and law do differ my bru elk nie nix van de Malawi costitution jou
O O!
Respect a fool to avoid noise.
aaah nanga police ya ku zimbabwe mukazitame kuti kusukulu munapitako zoona. mulibe manyazi eti
I think u need a doctor, something wrong in yo head. I am not a policeman anymore. I have work myself up. My secondary certficate was my way to univesity and achieved my degree in commercial law. My certificate qualify in any country even in Britian because its a Cambrigde certificate which was set by British exam board. Right now i am finishing my engineering degree in South Africa in a well known Univesity . I have been booked internership in New Zeland. Iwe busy kufutsa anthu zasukulu. What is MSCE to me. I am going places mjomba. I wil learn as much as i can. My limit is the sky. What are u gaining asking me? #Nothing. Trust me 1 day udzakumudwa with other pple’s succes. What do u have yourself nothing. Only FB account. I just feel for u. Kusadziwa ndikufa komwe. MSCE “D” is a pass in Malawi, what is that? Rubbish.
Now the truth is out. And u were arrongant saying he can fire anyone without a reason. The reason is out. Any word mr know everything. Kik common sense is not something u buy from Kandodo kikiki
Ndiye mwafasakotu
???
Shaaaaa pafuka nthuzi ndiyekuti palimoto
#BreakingNewz malawians fires the government of prof peter munthalika due to financial problems >>>> all the latest news on kelvin katsonga news 23
???
why?????
eshi