Mutharika fires Maulana: appoints new Army commander


President Peter Mutharika has dismissed General Ignacio Maulana as Malawi Defence Force Commander, Malawi24 can report.

Ignacio-Maulana
Maulana: fired from the army

According to Chief Secretary to government George Mkondiwa.Mutharika who is Commander In-Chief of Malawi Defence Force has since promoted Maulana’s deputy Lieutenant Supuni to the position of Army Commander General.

Former army spokesperson Clement Namangale will also take up a new post at the army as he has been appointed as deputy Army Commander.

Meanwhile General Maulana has been deployed to the National Food Reserve Agency ‘to manage food security’.

193 thoughts on “Mutharika fires Maulana: appoints new Army commander

 1. Mr president,you are commander in chief of Malawi defence force but yet you arent undergone military training.Mind you when intefering with these,next time…

 2. Kenako achotsa nchito wamkulu waku G4SECURITY …..USELESS PRESIDENT mmalo molimbana ndi athu akumpa albinos bizzy kuchotsa athu nchito wofunikila …

 3. Ife amphawi tizingokanda mpaka kalekale olo titasintha ma president, akupando akumwa tea wa nkaka ali mpheee

 4. I see no issue here, demotion happens anywhere. Let DPP run its gvt to its best,we don’t know de reason y then let his protect our food dere…. Let him show his abiity there

 5. Ndizinthu zomvetsa chisoni zedi kut tizilimbana nkhani imodzi modzi ndiye kwa inu odziwanu pitirizani ndikudziwako,koma chomwe mungadziwe ndichakut aliyense akudzionera yekha chabwino ndichoipa ngat m’malawi nthawi ndiyanu inu odziwanu,chidzadziwe mchipande powomora mumnthawi yokhazikikayo,

 6. According to my own side, it can not happen like this without something Wrong, it might be something Wrong, that is why he is fired . Muthalika is a man who doesn’t want to see someone against him. I’m really Proud of Him. Congratulation Mr President.

 7. Inu aChilima nchacha mukat malamuro amamulora ndiye azingochotsa anthu mwachisawawa,ingakhare ili mphamvu yake azitsata ndondomeko yabwino pochita zinthu,inuyo amwene musatenge amnzanu ngat osaganiza popereka maganizo awo pankhani iyi,mukati umbuli ndiye kut chiyani,palibe munthu odziwa zonse man,and no one iz above constitutional,

  1. palibedi odziwa zonse nde oziwako pang’onofe tikukuuzani musapange makani. chabwino amaenera kusata ndondomeko yotani mmene mwalongosolera inuyomu.?

 8. komaditu ameneyi wawonjeza moti adzipanga sama salarys awogwira ntchito m’boma azilandila munthawi yake choncho mpaka pa36

 9. malawians complaining too much eishhh kutinso tifufuze enanu you know nothing management ya defense force your reporters they dont explain in details koma kungokubonisani nkhani, this man if you consult the soldiers they are clapping hands cause of corruption. Lets help in hand to develop our warm heart of africa aman himself will never satsfy all your needs. Stand your on ground Malawi

 10. malawians complaining too much eishhh kutinso tifufuze enanu you know nothing management ya defense force your reporters they dont explain in details koma kungokubonisani nkhani, this man if you consult the soldiers they are clapping hands cause of corruption. Lets help in hand to develop our warm heart of africa aman himself will never satsfy all your needs. Stand your on ground Malawi

 11. Mmayankhula ngati mukunyera bwanji?MUSIYENI APM AWUSUMANE ANZANU NGAKHALE ZIKUVUTA KOMA SAKUNYOZA NGATI INU ACHEWANU . DR BANDA ANALAMULA MALAWI MWANKHANZA ANGAIWALE NDANI ANAPHA ANTHU AMBIRI ANGAIWALE NDANI KODI ZOTI ACHEWANU NDI ANKHANZA ASAKUZIWA NDINDANI MAKADI, KUTILANDA NKHUKU, MAZIRA ,MBUZI ,NGOMBE ANGAIWALE NDANI ?ACHINA GADAMA , MATENJE CHIWANGA WAIWALA NDANI KUMENYA MAFUMU KUCHOTSA MAFUMU MWANKHANZA ANGAIWALE NDI NDANI MUSOVA MULEKENI APM AYENDETSE BOMA MWAUFULU NDIPO MAULANA ANAMUPANGA APPOINT NDI APM YEMWEYO NDIYE CHOLEPHERA KUMUCHOTSA NDI CHIYANI

  1. Kuganiza kwainuku ndiye ngati mukunyera, muzitiuzaza Kamuzu pano? Ife Kamuzu sitikumuziwa tikuziwa izi. Ndiye sabola wakale sawa. Ngati mulibe mfundo ingokhalani zakukanikani vomerezani. Maulana anakukanirani zautsiru zanuzo. He is a true professional Soldier very appolitical amakana nonsense. Ndinkona mwadana naye. Go on Maulana, Your Conscience is clear. No traces of filthy character. Anthu mumadana ndi chilungamo. Go to the forest, straight trees are cut down while the croocked ones are left to live. Dikiranimuone zinazi ngati asilikai simugwira ntchito ya a police kumazunza otsutsa boma. Mwayiwala Maulana ndiyemwe anamukanila Joyce Banda kukatseka Tally Centre ku Commessa in upholding the constitution kuti mulowe mmboma. Lero ndi oipa? Akanakhala enawa okonda ndalamawa akanakatsekatu. Dzimvere mumtolo. Long live Maulana.

  2. Kuganiza kwainuku ndiye ngati mukunyera, muzitiuzaza Kamuzu pano? Ife Kamuzu sitikumuziwa tikuziwa izi. Ndiye sabola wakale sawa. Ngati mulibe mfundo ingokhalani zakukanikani vomerezani. Maulana anakukanirani zautsiru zanuzo. He is a true professional Soldier very appolitical amakana nonsense. Ndinkona mwadana naye. Go on Maulana, Your Conscience is clear. No traces of filthy character. Anthu mumadana ndi chilungamo. Go to the forest, straight trees are cut down while the croocked ones are left to live. Dikiranimuone zinazi ngati asilikai simugwira ntchito ya a police kumazunza otsutsa boma. Mwayiwala Maulana ndiyemwe anamukanila Joyce Banda kukatseka Tally Centre ku Commessa in upholding the constitution kuti mulowe mmboma. Lero ndi oipa? Akanakhala enawa okonda ndalamawa akanakatsekatu. Dzimvere mumtolo. Long live Maulana.

  3. Eya mulongwanga auzeni osusawa akagwele uko.khaya afune khaya asafune BPP mpaka 2039 wooo! APM boma.losankhidwa osati akalinde. Akasowa chopanga auzeni abwele ku THEBA kuno ndizawalembe ntchito leave my president alone.Just wait 4 ur time iz coming in 2039.AKUZINAMIZA KUT TIONA 2019 KODI NGATI ALEPHELA KUPHA KALULU ADAKALI OYEMBEKEKEZELA AKASWA ANGAMUGWIRE?

  4. Kkkkkkkkkkkk auze zoona APM NDI MOTO WAMDONDO SAKUCHEZA AYI MASO ALI CHISOGOLO .MUNGOTI SIZIKUYENDA MULI PHWIIIII MUFUNA AZIKUPASANI ZA ULERE GUYZ MWAUPONDA.NDIPO MUZAPHATIKIZANE TIZIPANI TANU TAMTHUMBATO AZAKUNYENYERENI LIMODZI PALIBE MPATA KUPEREKA KWA ACHEWA BOLA TIMPASE MTUMBUKA ALAWEKO NAYENSO KUTI AZAUFILI MU 2129

 12. Sono apa ma comments ose zikuonesa athu pita simukufuna kkkkkkk Zilibwino kusonyeza mavoti zizavuta kubera ? Malawi mwamanga fundo imozi

 13. amupatsa chibonga kuti adzikalondera ku food reseve

 14. it seemz u dnt knw the differenc btwn firing n realocation.mwangoonetsa umbul wanu.shame on u un professional journalist

 15. although am nt a dpp fan bt plz malaw 24 dnt mislead pipo here.he z nt fired.he haz been realocated to work at the derpartment of NFRA.Auzen truth an2.zofuna zanu mudzakwanitsa kman kumaona posocheletsela an2.nkhan ya medi bwanj cmunalankhule.mexa med nd wapolice by prof.kma al ku migration

 16. walakwa chani munthuyi mtundu wa amalawi akufuna kudziwa chenicheni chomwe mkuluyu walakwa

 17. Munchotsa bwanji yet Recruitment is just around the corner sizoti mutengeso manyaka anu DPP (cadets) paja akumalowera pawindow ena ndikumabwezedwa

 18. Kukhala m’malawi ndikulimba mtima imagine mpakana,lero no birth certificate mayiko anzathu onse alinawo ,mmalo moti apange kaye izi akulimbana ndizochotsana pamaudindo hahaha ndakulilira Malawi dziko langa olo kumwalira lero mulungu sakadziwa kuti ndine mmalawi chifukwa chopanda,certificate kkkkkk work up muhlakho

 19. i knw peter mutharika hi knws to fired only but to do something that MALAWI to change never hi doknw kodi munasakhidwa kuti muzichosa anthu tchito kapena kuti musithe MALAWI kukhala wabwino??????? im not happy nd family for mutharika munangobadwa dzelu zanu ndizimozi eti mumangosokoneza malawi basi im not going to vote u again bava inu malawi anatha anali kale please change ur mind peter we want to see malawi to come like before mutharika u mus go

  1. Tsopano yemwe amukwezayo amulakwiranso? aMalawi tili ndi vuto lomangoona negative impact of the story yet the same President has appointed another person to that position but we don’t commend him . are we not just shooting ourselves on the foot? although he sound like not doing good, but he has promoted someone .a thing worthy mentioned

  1. Kkkkk he born talented in fir’ng pipo, we need to demonstrate his talent by fire him, after we demonstrate then pipo will say his talent spks for him

 20. Ndangati angafune tilande dziko la Malawi coz am ready to create group called #Boko_Malawi coz #Pitala akutizuza hvy than #Tembo plz youth of Malawi we must wake up coz land bill iyi sindikuimvetsa bwino momwe yalowela plz contact me but sindiku panga force mfuti xilipo mix otsutsa atithandiza zipangizo xina monga ma galimoto chidule ndikungopha bwampiniyu

 21. President Peter Mutharika has fired Commander of the Malawi Defence Force General Ignacio Maulana and replaced him with Lt Gen Sapuni. Secretary to the government George Mkondiwa confirmed to media the dismissal of Gen Maulana. Former MDF spokesman Clement Namangale been promoted to the position of Deputy Army commander. Gen Maulana has been deployed to the National Food Reserve Agency ‘to manage food security’, says Mkondiwa.More details to follow.

 22. Mukuchotsa general commander bwanji m’malo mochotsa nduna zakuba zija,plz Mr President b careful ndimbari yachitetezo maka a MDF,sitkufuna kut timvere kut agalukira ena,mapeto ake bwana President inuso ndikuchotsedwa pampando mwachipongwe,

   1. Maulana is a true and professional soldier, very appolitical and he does not tolerate nonsense. He might have refused stupid demands by politicians. Remember he Is the same one who refused Joyce Banda’s order to send soldiers to shut down Tally Centre at Comesa hall in upholding the constitution of Malawi for u to find ur asses in the Government. Now they are scaredof him why? What are they planning, wake u Malawians, Maulana is not a thief and his conscience is clear, they could not cox him into fraudulent acts. Take a look at the forest, all straight trees are cut first leaving the crooked ones to live. Politicians look for sotf people that they can manipulate. Wait soldiers will soon be used as police to harass opposition members. Something big is cooking up let’s wait and see. Dzimvere Mumtolo. Another Cashgate is building up in the MDF, mark my word. .. Poor Malawi

 23. Koma gogo ameneyu ali ndi vuto ndialiyensetu….mawa achonsa inspector general wa police…..kkkkkkk
  Kenako titangomva kuti ALL MALAWIAN CITIZENS ARE FIRED….WE’RE NO LONGER CITIZENS OF MALAWI….

  1. ndizonadi man,koma osadanda tsiku lina imeneyi izakhala mbili mukudziwa kale komwe tikuchokela kudali ena oposa awa lero ndi history

  2. @ chilima. Its quiet strange to us citizens to just hear sketch news. We have a right to know why? Why not reporting the reason? Are they planting the reason. Of course ndiudindo wake but u can’t just fire someone without reason. But on this i can smell a rat. Something fishy. No dispinary, no warning, no reason, no notice. What kind of adminstration is this? We are not fools. We voted him in to lead us with truth not secrets.

  3. # Micheal Malamulo amati chani kodi pa nkhaniyi zikuonesa ngati titha kuchezerapo.? ngati mukuona kt palakwikwa bwanji apite ku nkhothi bwa

  4. # Micheal Malamulo amati chani kodi pa nkhaniyi zikuonesa ngati titha kuchezerapo.? ngati mukuona kt palakwikwa bwanji apite ku nkhothi bwa

  5. Kodi Pitalayutu adanena kale kuti iye alibe polobulemu, atha kupanga watever akufuna coz he’s already rich ndipo uplezdent uwu analowa ncholinga chopanga history ku family yauMntharika kuti alamulira Nyasaland ngati ufumu! kkkkkkk

  6. Kodi Pitalayutu adanena kale kuti iye alibe polobulemu, atha kupanga watever akufuna coz he’s already rich ndipo uplezdent uwu analowa ncholinga chopanga history ku family yauMntharika kuti alamulira Nyasaland ngati ufumu! kkkkkkk

  7. Chilima kodi iwe ukmuikila kumbuyo?
   Malamulo or pa company ukalakwa koyamba its first worning then second worning sopano uyu mukumuikira kumbuyoyu worning yake ilikuti? Adawa alibe pabwino awa sindimaziwaso kuti pali omukonda ngati inu adakuikani chibaz eti?

  8. Eeeeh amwene muli kutali bwanji mutichedwetsapotu apa. mwati pa company eti ndiyakhe chonchi ndizosiyana company ndi dziko. poonjeza kuti mumve bwino company maudindo umachita kufunsila kuti ukhale pa possition inayache. pomwe udindo awachotsapo akuluwa amasakha ndi president munthu yemwe wamufuna iye ndikuona kwache ndipo ali ndi mpamvu yomuchotsanso pa mthawi ina iliyonse popanda kusokonezedwa ndi wina aliyense. zamveka kaya???

  9. @chilima comon man we the pipo hv the right to information of everythn thats happening in our country….so we hv to kno wat happened kut the general shud b fired.

  10. NKHANI ZA NATIONAL DEFENCE EN SECURITY ZIFUKWA ZIMENE MUNGAPATSIDWE RIGHT NW ZINGAKHALE ZABODZA JST WAIT MUMVA KMA PRESIDENT HAVE THE MANDATE TO DO THAT!
   ARMY COMMANDER NDI UDINDO WA NDALE JST AS INSPECTOR GENERAL!
   KU ARMY UKAFIKA UDINDO WA MAJOR GENERAL NDIYE KT WATHERA BASI JST AS COMMISSIONERS IN POLICE SERVICE

  11. Kkkk Koma yah DENNIS NOMANDA ntchito ilipo nditthu tapezani buku la malamulo muwerengeko pangono abale. ndizoona uv got that rght. koma lamulo lagwilitsidwa ntchito ndi a prsdnt positha udindowo silikambapo kuti ayenela kukudziwitsani zifukwa zake ayi.

 24. That is the problem with u Malawian journalists. Give us story in detail. He was fire because………………………. of what? U have details of who wil replace and where he wil go. But the reason u dont tell us why.

  1. What chapter. Its unconstitutional. A president have a right to apoint and fire pending outcome of displinary or inquary of the situation eg corruption charges, nepotism, civil and criminal charges or if the official under peform/not fit to hold the office and under qualify. But in this case none of any reason suit. He can just wake up and feel to fire a minister simply that he is a president. They are some procedure followed. Plz if u can verify the chapter which say that in our constitution.

  2. U have failed to point out the chapter to support yo point simple siumadziwa malamulo aMalawi. And its not yo fault. I did’nt say i knw everything like yo president. Talkn about the court, the justice in Malawi is biased like u. They are there to please their superiors. Of cause u can not get sense because simple dont know our constitution. Common sense” everything happen with a reason”. They are lot of pple arrested unlawful in Malawi simple political orcherstrated. They is no justice in Malawi. I want to tell u now that i have studied law. And i knw what i talkn about. Its not a sin for u to be blinded in judicial. We cant be all lawyers, engineer, pastors. If u were closed i would give u book lamalamulo aMalawi in chewa for free.

  3. let me tell u.simunapite ku sukulu inu lets b honest.and how can i take sides for the stupid issue which doesnt concern my country? empty tins always make noise

  4. If so suit yo self. I can refer u to pple whom u wil be suprise. I did my O level Cambrigde with 6 Bs and 2Cs 1 A in Zimbabwe and join Zimbabwe Police when i was 18 while i was doing my studies. I left police when i was 27yrs moving to Malawi with my family. I have worked with NG0s in Malawi. And right now i am doing other studies in RSA. I am Malawian by decendant. Siungandi namize malamulo aMalawi because they fall under British colony.

  5. I think u need a doctor, something wrong in yo head. I am not a policeman anymore. I have work myself up. My secondary certficate was my way to univesity and achieved my degree in commercial law. My certificate qualify in any country even in Britian because its a Cambrigde certificate which was set by British exam board. Right now i am finishing my engineering degree in South Africa in a well known Univesity . I have been booked internership in New Zeland. Iwe busy kufutsa anthu zasukulu. What is MSCE to me. I am going places mjomba. I wil learn as much as i can. My limit is the sky. What are u gaining asking me? #Nothing. Trust me 1 day udzakumudwa with other pple’s succes. What do u have yourself nothing. Only FB account. I just feel for u. Kusadziwa ndikufa komwe. MSCE “D” is a pass in Malawi, what is that? Rubbish.

  6. Now the truth is out. And u were arrongant saying he can fire anyone without a reason. The reason is out. Any word mr know everything. Kik common sense is not something u buy from Kandodo kikiki

 25. #BreakingNewz malawians fires the government of prof peter munthalika due to financial problems >>>> all the latest news on kelvin katsonga news 23

Comments are closed.