The Ntchisi First Grade Magistrate’s Court has convicted and sentenced
a 40-year-old man to six years imprisonment with hard labour for house
breaking and theft.
The court heard that the convict Shandacha Ndalira on July 11 2016 at
Kapiri Village in the district broke and entered into the house of
Philemon Kampala and stole one blanket, 25 kilograms of maize and four
wrappers (zitenje).
The convict pleaded guilty to the charges of house breaking and theft.
Passing judgement, First Grade Magistrate Yohane Banda said the
offender deserve a custodial sentence to deter other would be
offenders.
Ndalira comes from Mbewa Village in the area of Traditional Authority
Chilooko in Ntchisi.
Really? Then cashgate thieves should be….
lkkkk ndiyokomera a cashgate dzikoli
I think ma Judge mudzilodzedwano komanso mudziyenda mosamala once we catch u watha! Wina waba ndarama zomwe amvutika ndi anthu ochuluka mukumuuza 2 yrs wina wabera munthu modzi u say 7 yrs manyazi mulibe?!
How can I explain this testimony to the public about a great man who help me out in serious illness I have HIV AID for good 3year and I was almost going to the end of my life due to the way my skin look like all I have in my mind is let me just give up because life is not interesting to me any longer but I just pray for God every day to accept my soul when ever I’m gone lucky to me my kids brother run to me that he found a doctor in the internet who can cure HIV online he help me out on everything, the doctor ask for my deities, so he can prepare the herbal medicine for me from his temple after all he ask is done one week later I started getting more stronger my blood start flow normally for 4 to 5 days I start getting Wight before a month my body start developing my skin start coming up after 2month I went for HIV test and I was tested negative I’m so happy that I can say I’m not a HIV patient if you have HIV/AID or any sickness he can still help you in getting your ex-back to you please contact him via whatsapp +2348162447651
Shaa! Koma ngati akufuna kutchuka ayi waonjeza kunena zoona chilango chakula ichi
That is ridiculous how can you give such a harsh sentence for for that crime when some other people are stealing billions and get laser charges
Now i see that this kind of judgements happen throughout Africa
Our criminal justice system is a joke. No consistency at all. It is steeped against poor people and in favor of rich people. Kuba Nkhuku, zitenje, njinga zosakwana ndi K1 million yomwe one is given 7 years jail term. Kuba K60 million in cashgate kupatsidwa 3 year jail term. What nonsense is this? Where is this country is going? To the dogs? Are these magistrates not ashamed? Do the magistrates and judges have bosses or supervisors? This is shameful. A failed state indeed!
INJUSTICE EVRY WEA IS A THREAT TO JUSTICE ANY WHEA………………….MARGISTRATES GROW UP PLIZ…………..
SEVEN YEARS …………………………………RILLY?
nde kumalawi kumeneko
Ndende za ku mw anamangila amphawi
Aziba za nzeru..7 zachepa..
Osamaba pang’ono etiiiiiii
Haha anthu akuba ma million yeyu kuba blanket…ndi kape et
7years olo 6years which is Truth
7 years for a blanket, 3 years for a Cash gate conviction.
Kkkkkkkkk ayayayah mpaka 7yrs…Wina kusololora Ti Ma million Kungokhala 2wks Mulandu atseka….Adzaweluza Yekha inu pheeee
Chigamulo chokondera a CASH GATE / UNIMA GATE etc.You are giving them soft punishment why this DZUKA MALAWI
Hihi M dubs nd deal
Pliz I don’t understand these magistrates anymore, how can this poor man be sentenced to 7 good yrs just because he stole simple things like these while ministers and MP’s are being charged months for stealing billions??? Chinapita kuti chilungamo my fellow Malawians? God pliz save my mother land
Nanga anaba 557 billionq
Kkkkkkk dziko ndi lokondera
Amene mukutsutsanu muzaziona
oba zazing’onowo azimangidwadi coz nde anthu oopsa poti amabela amphawi.
7 years???????? Aaaah learn to be serious sometimes please!!!
Kkkk kufanana ndi oba ma billion ya mitsonkho ya a Malawi.
kundende ndikwa amphawi basi
Zochitika padzikoli zikukomera achuma njiratu zawo mzotetezedwa palibe choti alabade olo ngakhale aphe munthu mawa mumva kuti atuluka olo ngakhale abe chuma mumva kuti zilibe umboni
Yet cashgate less
Chilungamo Palibe, bola Anakaweluzidwila Kwa A Mfumu
the judgment is fair, house breaking is a serious offense
Why mara these cashgate robers are given 3yrs with hard labour ?
Malawian magistrates alibe chisoni, they act like a robot wen carrying out their jobs, They give sentences as if we have a lot of prison space. Kodi tilibe ma community Service Sentences for this small irrelevant crimes.
Okuba ma millions akukhala 1 yr koma zilikoli kupanda ambuyake konseku eishii
Raping justice. ..
Which z which? 7 or 6 yrs
Ntchisi ayayaa
K k k kuba chipironi mix kuzzilaku? eeeeeee size yabho!!
it’s too much Mr judge, maybe becoz of this devaluation,ndiye Kasambala kukhala zingati?
7 Yrs coz of blanget flour and zitenje amphawife tili pa fireeeeee!!!
Zogwetsa mphwayi zomwe ma judge athuwa akupanga. Odula ziwalo miyezi iwiri koma okuba chinangwa maximum sentence.
Pamenepa akutiphunzitsa kuti tikafuna kuba tiziba ma mita not bulangete zitenje nkhuku mbuzi aaaaaa zipindula chani mapeto ake tizivutika ulere
zokhumbana basi Ena aja anaba ndlama ku Lcity osamanga kuwa tchaja zaka ngati zimenezo bwanji?
If ther z no employment wat du yu think pipo r they going to du apat frm stealing? mo ova the population z continuing 2 increase, All foreigners must go
DZiko m’lokondela iyi mmmm eish!.
Zopusa.
Dziko lapansi silizatheka
Kundende ndimalo aanthu osauka koma olemera oba ma billion aboma ali phee kunyumba,,,,,,,MALAWl
The magistrate must go back to school. His judgment is out of emotions and based on personal issues. In Malawi many are suffering in prison for nothing because they don’t have money to hire a good lawyer to rescue them from such unreasonable judgment. That’s why the State President uses his discretion to release such prisoners once a year.
Kusiya kulima kudimba kumakaba zooona.kuntchisi ndikuchimake kwamadimba
u can’t fight the system …just work hard, join the system and revenge lol
u can’t fight the system …just work hard, join the system and revenge lol
Mwina oweluzayo amafuna anene kuti 7 hours ndiye anangolakwitsa, that’s very unfair !!!!!
KOMA OPHA ALBINO MIYEZI AWIRI MMMMMM AI CHILUNGAMO CHAVUTA BAAS
mwayamba ndi 7years nkumaliza ndi six yearz,fotokozeran Bwino Pamenepa
Omwe anaba ma billions a DPP 7 minters kulephela kuwamanga koma oba blanket kumugwira cry my beloved country kusiya mbamva zenizeni kulimbana ndi munthu ovutika kuba blanket 6yrs oba ma billion 6month.
ndie kuti zitenje chilibe chizungu chake eti
koma amphawi ife ndie tivutika basi sure magistrate kumwamba sukalowa ai wamva udziganizilako anzako
Kkk
Opanda mainafe tili pa mavuto ndithu…adya misonkho yathu aja ndye miyezi awili basi….shame
Dziko…….mmmh!!!!!
….a magistrate mwawonjeza chigamulo chanu! Bwanji ena akuba ma billion mukuwapasa zilango zophweka, nde kuti mumakondera? Kapena lamulo limasitha munthu ukakhala olemera?
Ogwilila ndiye kumawapatsa zaka zitatu mxiewww
Zankutu! Mbava Zamabilion 4yrs.Oba Bulanget Chifukwa Cozizira 7yrs!
Dziko lapansi ndilokondera ili pamene awa anaba ma bollion akupatsidwa 2 years
kkkkk koma dziko lapansi abale.wina anaba millions pano akanayendera galimoto ,kukhala nyumba yaboma,wina six yrs kundende kamba ka chipiloni.
mmmmmmmmmmm