The times are tough and the money is very little and therefore there will not be the usual pomp and glamour that 6 July comes with, for this year.
George Mkondiwa, Malawi Government’s Chief Secretary, has disclosed that there will be no Independence Celebrations this year as it is has been the normal case claiming the ailing economy as the reason.
He argued that the celebrations could cost government a lot of money-something he says does not go in line with the current economic stand of Malawi.
Instead there will just be national service of worship, a statement from Ministry of Information, Communication, Technology and Civic Education says.
However, In March this year, the International Monetary Fund (IMF) made revelations that the country’s economy will attain growth ranging from between 3-4 percent this year.
Similarly, the World Economic Outlook Global estimates Malawi’s economic growth to rise from 3.1 percent in 2015 to 3.4 percent in 2016 and 3.6 percent in 2017, stating that global economic growth will be gradual and that will have an effect on Malawi as a developing country.
Among other things, the IMF says Malawi’s inflation will keep going down and the GDP for last year got placed at just 3 percent.
IMF said the country’s inflation has seen a 2 percent decrease to 23.4 percent in February 2016 from 25 percent in December 2015.
This was after the IMF hailed the sustained stabilization of the Malawi kwacha is due to the absorption of excess liquidity from the banking system by the Reserve Bank of Malawi, and fiscal discipline by the Malawi government and to prospects of the tobacco season.
Malawi walero…..
Stupid! 6th July will always be there. Talk about republic celebrations and we’ll understand. This stupid journalism is just one aspect that is contributing to the deterioration of everything in Malawi.
Panyapako Pathumbopo Uganize Bwino Koma Kupeza Ndalama Zopangila Mulakho Walomwe
ok ndamvetsesa the days will be as follows this year 1 july, 2 July, 3 July, 4 July 5 July then 7 July and so on zasintha no 6 July
MUKUNAMATU NDIYE MUSAmatidule sokho zokumba basi ngakhale malemu kamuzu sizinachitike mutulusa zanthumba mwanu ,
6july wil cme wsh it or not…koma muzit no cerebration on 6july thus o
Can we find some agents to sell this country? Mayb one will make a good change as it will b private country.
I know because none of your gogo’s died on this day
CHANI? ????? izi nde zachamba enafe ngat pali tsiku lomwe timalidikilila kut tsangalala ndi 6july ndemukut Chan ndalama zonsez zikutulukazi mukuzgwilitsila tchito a boma inu pano mukatinyadisile ndalama zathu zomwezo pa independence day sheeee apa nde tinvana kuwawa pangani zanuzo tonesane
CHANI? ????? izi nde zachamba enafe ngat pali tsiku lomwe timalidikilila kut tsangalala ndi 6july ndemukut Chan ndalama zonsez zikutulukazi mukuzgwilitsila tchito a boma inu pano mukatinyadisile ndalama zathu zomwezo pa independence day sheeee apa nde tinvana kuwawa pangani zanuzo tonesane
6 July simalephera tiona chaka chino,do 4gt tht ths iz homehrt of africa.osamatpangisa manyazi,
Sound not good thats underating those who established the day as amemolable day to every Malawian. Even maiko amene mulinkhondo when their day come they celebrate so why Malawi, first time to here this the likes of Kamuzu, Bakili etc their government were still facing problems but they did not stop celebrating on historicle day.. Help us God…
Nyasa times is publishing to say Malawi wants to buy new convoy and yet you are saying no cerebration on 6 July due to inadequate money, so where will the money comes from for buying president convoy.
ndekt Asapumesotu. ichi nde Chambaaaaa cha Mzimbaa
No freedom day,chifukwa cha maluzi koma yaah!
kuzangokhala msokhano wachipani bas……..
OK?
AMALAWI CHONDE TADZUKA.TINAYAMBA KUGONA LIJA NDI KALE TIZADZINDIKILA LITI KODI?TITI TIZINGOYANG’ANA CHUMA CHANTHU CHIKUPITA BAC?LERO AKUKUNAMIZANI KUTI KULIBE CHISANGALARO PA 6 JULY,KOMA AKUTI KULI MAPEPHERO KU BICC.KODI KUMENEKO NDIYE SAKAONONGA NDALAMA?
Kodi iwowo adaliko nthawi imeneyo zakomela iwo osatikwa ife, tagani anzanga tsikulomwalirila mchimwenewake analipanga chikumbutso. makolo athu kutibweletsela ufulu inu mukuti ndalama kulibe ndalamanso zabedwa kumeneko.
Koma dziko lathu tinene kuti lizalemera? Zaka zikudusa, pomwe maiko ena akutukuka, ife timangot tilibe ndalama. Nanga chisangalaro cha 6 july chinayamba chalepherapo? Panopa ndipomwe tasauka kwambiri? Wake up Malawi ndinthawi yopita kusogolo osat kubwerera mbuyo, zomwez mpaka tifunirepo ma Donars.
No 6 july,no holiday this year.
No 6 july,no holiday this year.
First time in Malawian history kulepheletsa 6 july.but how come they are planning to buy new cars for mutharika’s convoy? Where are they gonna get the money?
This day must be there, dont remove, what leader are you, opposing this day, then it tells us that you are not good leader.
6 July will be there but the usual independence celebration will not take place that’s good timing Government according to how our economy is
Pls pls kumamvesesa akuti ndalama zomwe zilipo akukapangila nsonkhano wamulakho walomwe kwa chonde mmuboma lamulanje osat za 6 july ayi
Yeah spending fo nothng as if we have anythng to show sinc the day
Kikiki mwaifufuta pa calendar? yangoyamba 1 kudumpha 6 kufika 31 kikikiki kodi iwe mdala akukumba pati ?
This might. mean that we are still in colonial regime and taking Mallawians as fools!
matchona ndi choncho izi ndi ndale za ana poti siku limeneli likukhuza MCP .Kamuzu ngati mtsogoleli woyamba ,inu musafufute mbiri ya dziko siku limeneli ndirofunikira kwa mbiri kwa ife amalawi
big up to the Government for closing this gap for money looting!!!! use that money for our economy!
wow! Malawi24, you mean 6 July has moved from the calender
Eeeeee! Nkhope zake zimenezi, mpake 6 July celebration kuchepa Ndalama amwene.
Thus why i hate my country bcoz its always doing stupit things
zakhala bwino enafe tizakhala busy ku show ku sheffar ndibwino izakhale pa 7 july po. boma iloooooooo
Good Idea
Thumbs Up! Save those meagre resources. That’s a way to go!
Bodza iri 6July iripo chaka chno
Kod phndu yovota ikuoneka apa? Nthaw yomwe tnataya yopta kovota, bwez ena akadapanga nayo phindu.
so you mean after 5July it will be 7th???!!!!
kkkkkk ok???
Ilipo ya zitete ndi mbewa!!!!
Koma Malawi 24!!!!!! Couldn’t there be another way of expressing this heading?????
A good gesture but still the meagre budget should have been used either to furnish QECH, KCH or MCH (a selected hospital in Malawi )
Tikachoka pa 5 tifika pa 7 heti?
or ikhalepo or isakhalepo chidziko sichikusintha ichi
Shame my Malawi, where are u going kkkk
AMalawi mphavu zosangalalira azipeza kuti atangodya zitete ndi mbewa zokha basi kkkkkk
No,it will be there!kkkkkk
Poor reporting,6 July is ther and will be there,the only thing that will b absent this year z celebrations.Learn to be proffession
Yo!zodabwitsatu zimenezi no 6 july?first time kumvatu zimenezi,koma Mr Ibu mutiuza zambiri
Ambuyeeee!
Mmmmmmmmm no longer 2 call ds couty 2 b malawi nw ds s “Nyasa”
Rest in Heaven Cassius Clay aka Muhammad Ali, the world’s Greatest!
ngati ndi choncho uyoyo asakhale ali zungulizunguli kumapangitsa misonkhano kwa miyezi 5 auzidwe ndalama zingaonongeke
Ziliko eeee
Kuzangocha tili pa 7 ??????
Why celebrate with this sick economy? Mogufuli of TZ is a true African who knows African problems and he doest need celebrations. For what? Thumbs up for this wonderful gesture . When is the new Bingu National Stadium going to open? Rumoures were perabulating around that the stadium will be onpened on 6 July. May be on Mothers day .
Why celebrate with this sick economy? Mogufuli of TZ is a true African who knows African problems and he doest need celebrations. For what? Thumbs up for this wonderful gesture . When is the new Bingu National Stadium going to open? Rumoures were perabulating around that the stadium will be onpened on 6 July. May be on Mothers day .
Kkkkk koma ndaseka no 6 July this year nde omwe tinabadwa pa six ife mutitani?
Zimayamba chonchi, tsiku lina, sabata lina, mwezi wina ndi chaka china (2019) muzamva kuti sitikhala ndi GENERAI ELECTION malinga ndi mabvuto a zachuma mpaka mtsogolomu chuma chiyamba kuyenda bwino.
Inu mukudandaula convoy mtima mmalo ndikutumizirani yanu kuchokera ku EURO
Ndalama zopangira 6july palibe but zogulira galimoto za convoy 8 nde ziripo??? Kkkkkkk
#DAMN#
zachilendo,malawi ikusokonekelatu apa.
HAHAHAAA
Zotsazira sizabwino ndaoneratu kut watsazira #magufuli
Mubwere nonse kwathu patsikuli mukudandaulanu mwamva?
Kodi patsiku limeneli mukuti kumakhala chani?
U so silly admin…There’s 6July no matter what….jst say u will not watch free gule wankulu at Kamuzu Stadium. ..
Ikhalapo pa civo
Mugufuli wathu kkkk
Ikhalepo isakhalepo ine zanga pheeee
A Malawi 24, 6 july alipo chaka chino koma Chikondwelero kulibe.
Thieves hav stolen our 6 July together wth money 4building Phalombe Hospital…kkkk..6 July or no 6 July kwacha will neva defeat Dollar…
kkkkkk No 6 july nde chaninso nanu date pa calender panupo sikuoneka?
Point of collection 6 July ilipo koma pitala xakadya
Thats busheet
No sence
Aaaa Zopusa!
Ndikulira voti yanga. Bolani thawi yovota ndikanangopita Ku mowa
Ndichifukwa ndizafela konkuno boma la malawi lochitisa manyazi. Mp mukuwapasa ndalama zambiri! Osauka palibe chomwe mukuwachitila! Ndiye nkumati bwelanikoni kunjako zoona?
Ngati mukuti kulibe 6 july ndiye watenga 6 july ndani abweze. Malawi 6 july ikalabe koma zisangalalo kulibe. Or musiye/mupange what the difference?
Yeremiya Adaneana Kut Nkovuta Kut Munthu Wochokera Kufumbi Kuongolera Mapazi Ake Kutanthauza Kuti Tilibe Mphavu Yozilamulira Tokha Tikufunikila Ulamuliro Wa Yehova Ndi Mwana Wake Yesu Izi Tatopa Nazo
last days be happly thus how life goes
6 july iliko koma ma celebrations ndiwomwe kulibe. Point of correction kkkkk!
Yaaaaaah. if they say no 6 july then tikadzachoka pa 5 mawa lake lidzakhara 7 july
date lokha liripodi .
Every year 6 July its independent day to all Fall Malawian people y this year u say tht nonsense usandikwiyitse pls
Thts is big stupid to government n don’t b shy to say dat nosence ife tipanga ngati eni ake adziko idyani ndalamazo popanda ufulu umenewu ukadakhala president Iweyo 4ko4 udali pheee komwe udaliko pano Athu amene adatiphwanyila ufulu akhale zitsiru shit
Chaka chokololadi
6 July will b zea, talk about celebrations.
Night of prayer basi nanga nkumadzatani
Kodi malawi wanga akupita kuti? Ndalamozo boma likhala nazo liti?aaaa malawi walelo ndi ziphinjo zokha zokha,ndalama kumangowana anthu am’boma nokhanokha nde mukuti boma ndalamba lilibe? Izizi ndi zamalawi waulendo uno.
You are a liar admin, I have seen 6 July on the calendar, it is there, which calendar are you using?
Chibadwire ine koyamba aka kkkk
In other words, we will just count 123457…6 wll be missing this year if my calculation is correct.
no 6 july kkkk
6 July is there and will always be there as long as the calendar is there,only that the ‘celebrations’ won’t be there!
We want to buy ‘jalopies’ so why waste money on ‘celebrations?’
Everything is up side down.
KOMA ZOGULILA CONVOY YA PRESDENT NDIZIMENE ZILIPO
Voting 4 unusual leaders brings unusual leadership.
achita bwino, no gain at all
NO 6july mbuzi yolemba nkhani agalu nde Luna panda 6july tizadumpha kufikapa7?
So 4rom 5 we will go straight to 7 July kkk.Most ov ur headlines u guys leave alot 2 b desired
Koma Ku lomwe festival’s……zimapezeka ndalama??????
Mvuto lotenga mbuli nazooo ku nyumba yamalamulo.
U just agree with everything ……shame Malawi ..
Fucken president …….
…#mbuli.com
6 jully iliko koma zochitika za boma kulibe. sono mukamat 6jully kulibe tidzajampa kuchoka pa 5jully kufika pa 7jully??
Malawi wa lero hahahaha ma nyasa
agalu inu last year boma litapanga mwambo wachikondweleroçhi munanyodza boma kutukwa mtsogoleri wadziko lino mwati paĺibe çhifukwa chokondwerera chifukwa mavuto ndiambiri mdziko muno lero boma lomweĺo lalepheretsa chikondwerelochi kamba ķamavuto azaçhuma omwewo mukutinso ayi ndie mtsoģoleri mufuna atani?kungozolowera kutsutsa basi zikomo mķamwa mwànumo adźatulukamo liti asatàna inu?
Zoona man
Nde Amalawiwo Amenewo Alibe Pabwino
malawi sazatheka…chomwe amafuna samachidziwa
Kodi munthu wakumalawi ali ndipabwino,, chomwe wachinyoza lelo amazachiyamikila mawa
Umbuli komanso kusakonda dziko lawo ndikomwe kumaapangitsa
anthu alibe pabwino, apa ndavomelezana nawe mbale wanga.
Misonkhano akumapangayo ndalama zikuchokera kuti mesa mzaboma muti nyonyonyo ndalama palibe zazi
kape iwe misoñkhano unenayo amapanga 1 to 30 ali ku opposition uķuona ngati misomkhànoyo wayamba kupanga coz ali mboma iwedi nďi mbuzi bwanji
Mitu yano mwava, mukuona ngat panopa pomwe ziko lilibe ndalama? Kumeneko ndiye kukanika usogoleri. Kuzolowera kuba basi.
hhhhhh mmmm Sizibwino
koma mukuva kuti akugula galimoto zatsopano za convoy.Ena akuti basi stadium yatsopanoyi sakuifuna,
Sikuzabwelaso Boma lofuna kutukula malawi mpaka kale aliyese olowa ndale amapitilamo kuba.ndatukwana abale
MMMMMM YICHITIKE NDITHU CHIMOZI MOZI MUMENE MUKUMAPANGISILA MISONKHANO YANU ANDALE NDALAMA MUMAZITENGA KUTI? YIKHALEKO BASI
zanu izo.nd mlomwe wanuyo bola kumakhasambitsa mkhalamba ku UK kkkkk
Kugawana m’tundu komaso maboma ndiko kukuchitsa kt pasamakhale mwambo okumbukira anthu omwe adamenyera ufulu wadziko lino.TIDACHITA MWAMBO OKUMBUKIRA IFA YA BINGU. NDE BWANJI KAMUZU?.KUSANKHANA MITUNDU KUMENEKU.
Ndiye chamba chimenecho,zinayamba zachitika kwathu kuno zimenezi? Akuona ngati ndife ma foreigner amzake?
Nde zachamba2
zachilendo
Ife 6 July tilinayo kuno ku ziko laeni. kkkkkkkkkk usova Malawi.
Zachamba basi,ife tipanga
Ndalama zimenezo adazimwera kale 6 july asadafke. Dpp imamva zake mutuwa simudati!
Thats a strange development ife as malawians…we derseve to be happy on that day…..mwina poti enanu kunalibe sia malawi thats why lero mukuziona zopanda phindu….koma kwa amene anazuzika ndi azungu atauka mmanda lero angakuphulitseni makofi……shameless and greedy leaders for their own…..benefit!!
Kkkkk no1
6 July alipo koma zisangalaro ndi zomwe akuti kulibe chaka chino,inu naa ngati munatchoredwa mphuno ndi aZungu & mukufuna kusangalara pa tsikuri mwa inu nokha mukhonza kutero koma boma siripanga nawo zisangalaro chaka chino,kukhara ngati akutero kkkk!
Gud move,munthu sungapangtse sadaka ana ako akusowa chakudya mnyumba
Mwati No 6 July! Why? Has It Been Skipped On De Calendar?Kapena U Mean There Shall B No Independence Celebrations On 6 July Dis Yr
Hahahhahahha mwabela xa magufuuli akanganya inu eti
Ndye ndisamuonetu mwapwiya muluphaleyo akuchita chipumi biiiiii pa cerebration ya Alomwe ndkamugendera komweko
Mbuyo monsemu zimachitika mufuna mudye ndalama?
my malawi
my sorrow! chinanachilichonse chango sokonekela, anthufe tithawira kuti? akuti ndalama palibe koma ena ndipamene akusolola!! kaya ndendalama zake ndiziti? celebrations or no celebrations malawi will always be the same!
On my carender 6july is there,bt say No more activities as we were doin past years.
kukhala m’Malawi sikophweka!
As if u give a damn about starving Malawians!
koma nyau zokha tivalatu chaka chino? Timadyela khundabwi izi..
Sizitheka amalawi musailole akufuna akudyereni masuku pamutu ameneyi
koyamba kuva
Ku malaw kulibe dola no chrismas celebration hahahaha evrything is impossbo in Malaw.
Kkkkkk mbewa basi
kkkkkkkkk
Tinene kut ayamba kunva?????? Amatero akafuna kut adye papakulu!!! Apusitse ndan?? Aaa!!!
kkkk lembani bwino zinthuzi.date limalephereka kod?mot tkazachoka pa 5 tsku linalo date lizakhala pa 7?
Tikaphe mbewa tikagulitsa ndalamayo tipangire mwambo monga mwazaka zonse.
Akufuna ndlama za badgert iweneyo zilowe mthumba mwake ngati simukudziwa mudziwe lelo
Good job you are wise.
mmmm….ndalama ndidiwazi koma akupangira zinjoyi,…siakut afuna agule new convoy…
No july celebrations koma timva kuti president will hav a “development” rally somewhere. They hav even approved several billions to buy a new fleet of cars to replace his convoy. Koma akuti boma lilibe ndlama. Imeneyo ndiye dpp
Kuseva
boma labwino loganizila amalawi. sikut lilibe ndalama koma zigwire ntchito ina
Yogulira ma convoy ake?
Finally tipumeko zinazi
thats malawi of 2day
No 6 July celebrations.
kkkkk etieti ngat kut tzangochoka pa 5 kufika pa 7?
reporting akuti Kkkk
Koma dairy a Presdent akuyendatu
hahahaha!! boma ilo zinthu zavta!