With a few minutes to go before the much touted naked protest over the killing of people with albinism, Malawi24 can confirm that contrary to what most Malawians expected, Bon Kalindo will not stage the protest naked.
The information that Malawi24 has, however, indicates that Winiko as he is fondly known will be in the nude as he marches to Parliament.
Winiko himself has confirmed that he is not going to protest naked citing that the laws of the land prohibit people from walking naked.
He has however said that he will just be in an underwear.
Malawi24 will give you a coverage of the protest.
Its not gud guys its very painful
its illegal to walk naked… Akanamalola mkulu uja akanayenda mblanda buy he respect the law
Ife owoona za m’dulidwe wa Bambo tinakonzeka kuti tigwira nthito pa Protest imeyi koma aii ndithu.
Atleast winiko has tried zaonjeza izi kwatsala enanu muchitapo chani za kuphedwa kwa ma albino?
Misala iyo
That one is there to blind us as you that ,that one is related with our p…..so they are all one.
Ukunama winiko amene ndimamudziwa ine ndi yameneyu winiko kufa,ms albino adzalila kooopsaaa
Thanks for his advisers,munthu suzuzula choipa popanga choipa,
Bola Boma lakumva chomwe ukufuna naked its nothng
People should not be interested in the nakedness,but the message Winiko is trying to communicate,ihate people who make folish comments on other peoples efforts this thing orignates from ones creativity sometimes its healthy to stay quite if you are ignorant than to expose your total folishness by making nonsense comments kkkkkk
Sopano azimayi inu mumafuna awonese machende? mmmm mwauponda
Always thinking drama
Kuyenda maliseche sikungapindule kathu ku mtumdu wathu a Malawi,vuto ndi loti anthuwo akapedzeka sakundira chilango chofanana ndi mtchimo la kulakwa kwao.Mwachidule anthuwa akapedzeka tiyeni tiapange zina ndi zina
I have his live pictures iwe admin ndiwe manyi Winiko is sending massage to those murderers sikuti winiko akufuna kuonetsa machende ache kwamako aja or kwa nkazi wako uja. Winiko is honourable in this country iyeyu kuvura ndikuvala zomwe wavalazo zikuonetsa uumuthu ndikukhuzidwa pankhani ya albino. Winiko has beautiful wife and kids, Winiko has expensive clothes and cars koma zotsezo sanalabadire patsiku lalero. Iwe admin ndiwe galu uumuthu ulibe,how old are you? Do you have kids, do you have penis? Are you qualified to be journalist or you got job from back door, Mbuzi
winiko mchitsilu kwambiri.walandira ndalama ku bpp.chimutu ngati tsanja winiko wava
Kuyenda maliseche sikungapindule kathu ku mtumdu wathu a Malawi,vuto ndi loti anthuwo akapedzeka sakundira chilango chofanana ndi mtchimo la kulakwa kwao.Mwachidule anthuwa akapedzeka tiyeni tiapange zina ndi zina
Winiko anapezerapo mpata ogulitsirapo dzina lake ku maiko akunja.
Winiko anapezerapo mpata ogulitsirapo dzina lake ku maiko akunja.
Koma yaaaa
nanga tavula kalefe mutithandza bwanj?bwamuswe wanga waonedwa kale ndye mukukaxithaxo maganizo kma che nyooo
Kkkkkk ache Nyoo!wa atagona usiku awona kuti mmmm ndikayenda maliseche siziphulabe kanthu.
So imagine the authorities refuses them permission to march, it would have been an issue,you see pple r responsible dont dictate to them
This is a true comedian he knows how to act kwazizila guys tiyeni tingomumvetsetsa kkkkkk
This man is mad
nkhawa zanga izi sindilora…
nkhawa zanga izi sindilora…
Basi ndanyanyala ndikuvala ndizipita
wina anakagula malumo kuchosera dreadlocks ati paoneke bhoooo koma yaaaaa ganda boys vs ganda girls united
asaaaa! sono enafe,anaconda adakali leeende! ndi mphepo nde tikavalenso?kkkk
Mumuuze avule zotiyesa ife Ayi timakana
Bodza ili ma demo ayambika anthu avala maboxer winiko mukumunenayo sadaveleso zimenezo wavala boxer nt pant
winiko omandiseweretsa
No Value,msiyeni Akuchoka Popangitsa Mdulidwe Wa Abambo
Kkkkkkkkkkkkkkkkk ur not a man of ur words aaaa ndipo u didn’t born a fighter makani onse aja mmmmmm mwina akudyetsani chibazi chachikulu kkkkkkkkkkkkkkkkk money ndioyopsa aaaa sugangositha maganizo tiuzeni zoona
kkkkk anthu amuiwala winiko kuti ndiwa commedy moti apapa zake zaenda hahahaha
bola pamenepo
abale chonde yovulayotu nde ikanabeba mmmm maso anal ready tu kufuna kuona znandzna
hahahaha pipo
kkkkkk whats wrong wth ppo…they promised us and they shud fulfil thre promise
This means he is not a man of his words!!!! He is like others. So how can we believe that you are really concern if you cant keep your words,hon winiko? kkkk
No matter he is not naked but he is the only person who is more concerned than u en me
making too much noice doesnt mean much concerned!
Don’t be stupid en pretend u dont knw the threats he has been recieving on matching naked. Follow wat happens en make contrasts before judging.
thats exactly what i have done, thank you
coz theres alot to be done on the ground than just running for a so called demo.
Inu kukhala buzy ndi uyu mesa iye amati ndi nyoo! Kapena kuti SSS
Kukanakhala kumeneko,akazi ndi amuna onse chibadwile ineso nkhanafika
ifetu ku Dedza border tavula kale, tikungodikira whistle ilile
Weather yachita dala kuti anthu aope mphepo
Ife nde sitiimva timatcha naked ma sim card athu odula pa ntunda!!! tilikale pa starting line, no boxer mphira mphira Hapana khwefu! death sentence to Albino killers period.
sure doc
Pangani zomwezo bigy kkkkkkkkkk mpaka mphira mphira kkkkkkkk yooooh
Kkkkkk,ndikatodziwatu Ine Kuti Zikanika,kwatodzidzira Udyo
mukukhala ngat andale simuwaziwa bwanji amalonjeza zomwe sangathe kupanga pofuna kukuonani kupusa
Politics plus drama=stupidity.
NDINACHALILA KUKAKUNYAMULILANI TANKATI TANUTU NDIYE MUKUTI CHANI? MWAONA MPHEPOYI EEETTII! MUSAZANDIUZENSO
Zokuti winiko ndi comedian anthu munaiwala…amalawi sachedwadi kuiwala eti!!! Ndani angayende chibadwile?
Ndye ine2 ndavula kale? Mot ndkavale? Asaaah kma winiko wangondiziziritsa? Kikikiki ok axe
winiko undisamale
tinadziwa ife
waopa kuthilidwa mambama ndi nkaz wake #winiko
So kwaife tavula kalefe he gonna pay the damages. Watiputsitsa!
Aaaaaaaaa ndiye utibwezere ndalama zathu zomwe tawononga pogula Pant wanyuwani komanso vest yanyuwani!!
avulidwe basi asaaaaaaa angatipusise ife?
ndetavulilatufe utiganizira buanj?
Do not forget winiko is dramatist what ever he do is about drama
mesa anthu alikomweko zikutheka?
nde fodyayo ife tavula kale ngakhale eee kukuzizira nde ukutiso chani mixx
Kkkkkkkkk kwazizira mukufuna aume ndi mphepo iya
KODI NAKED STRIKE &ALBINO KILLING ZIKUGWILIZANA BWANJI? ZA DRAMMER BASI!
Inunso a MW 24 mumazitengera serious zinthuzi???????? moti mpaka pano sinazindikirebe kuti WINIKO ndi munthu wochita zisudzo????? ine ndimadziwa kuti sangayende mbulanda ameneyo inali mbali imodzi yochita zisudzo zakezo,,,, ndiye inu kukangalika kulemba apa za ziiiiiiiiiii
AMalawi24 amangotengeka ndinkhan zilizonse, amadya nyaupe kapena?
kkkkkkkkkkkkkk mwina akufuna kutchuka ngati zodiak koma aaaaaaaaaaaaaaaaa alikutali,,,,,azichita kudziwa ndi agalu komanso nkhuku zomwe kuti che WINIKO ndiwanthabwala zoona koma mbuzi za ku MW 24 osadziwa??????
KKKK Koma winiko umayitha
aaaaaaa nde sizibebatu,,, ya naked yomweyo lol
Inenso ndakwiya heavy taganiza ndinavula kaletu ine nde wandipusitsa
kkkkkkkk wapusisa ambiri,,,,, basi ati yama boxer,,, nde mungochapiratu
kma mumu
mumu kkkkkk
zovuta,, but all n all its not abt naked bt killing ov albino pipo,,
Andilapa ndiyendabe chibadwire basi
kkkkkkkk winiko #clazy,
aganize bo ameneyo
hahahahahhahahaha zomwe ndimadziwa ine ndizimenezi not zanuzo zovulazo kkk
Ndan sadziwa kut andale akumalawi r full of lies? akuopa mphepo ameneyo
Guys winiko akufuna aztyesa et
Kwazizira guys
Am already naked here waiting for protest so akutinso chan?
kkkkkkk where r u?am also here waiting 4 kalindo.
Here in Zomba city,am just standing alongside the main road or should i start protesting?
kkkkkkkkkkk kma yeah
Sured Ndakonzeka heve am completely naked
bora ana asathawe
Athawa chifukwa ninji?
athawa akaona za over size kkkkk
Ndikut ndili completely naked nde za oversize zake chani?
kkkjkkkkkkkk koma abale
bwanji wavala kabudula?
Triza umafuna umuonere eti? Kkkkkkk
zuchitikadi kodi
kkkkkkkkkk eya kaya aaaaaaa ndakwiya kobasi
kkkkk
triza umafuna umuonele chain winiko? kkkkk
bwera uzaone zaine